Mtengo wa shuga wapitilira K3500
Pomwe kusowa kwa shuga kwafika pa mwana wakana phala m’dziko muno. Ogulitsa malonda omwe akumapezeka ndi katunduyu sakutchaja mosekelera ndipo m’madera ena shugayu watsala pang’ono kufika pa mtengo wa K4000 pa paketi imodzi. Lachinayi pa… ...