Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati akubanja komanso abale a wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima apempha kuti pa mwambo wa maliro pasakhale ndale zilizonse potengera kuti eni akenso sakanakondwa kuti… ...
Articles By Martha Chikoti
Thupi la yemwe adakhalapo mkazi wa pulezidenti wakale a Bakili Muluzi, mayi Patricia Shanil Dzimbiri, tsopano lanyamuka kupita kwawo ku mudzi kwawo ku Balaka komwe likaikidwe m'manda lachisanu. A Dzimbiri, komanso wachiwiri wakale wa mtsogoleri… ...
A phungu komanso makhansala ochokera ku chipani cha United Transformation Movement (UTM) ati nduna ya chitetezo a Harry Mkandawire komanso a Ken Zikhale Ng'oma asakhale nawo otsogolera mwambo wa maliro a wachiwiri wa mtsogoleri wa… ...
Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima akaika ku mudzi kwawo ku Nsipe m'boma la Ntcheu Lolemba sabata ya mawa. Poyankhura pa msonkhano wa… ...
Thupi la wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima kuphatikiza matupi ena a anthu asanu ndi anayi omwe amwalira pa ngozi ya ndege yomwe yachitika Lolemba mu nkhalango ya Chikangawa m'boma la Mzimba… ...
Professor Chiwoza Bandawe yemwe ndi psychologist wapempha a Malawi kuti alemekeze imfa yomwe yagwera dziko lonse ya wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima komanso anthu ena asanu ndi anayi omwe amwalira pa… ...
Former Malawi's President, Peter Mutharika, has asked God to intervene on the missing flight which was carrying Vice President Saulos Chilima and nine others. Writing on his official Facebook page, Mutharika says his family is… ...