President wa dziko lino Peter Mutharika wauza mtundu wa aMalawi kuti matenda a Covid-19 omwe akumayamba chifukwa cha Coronavirus apezeka mwa anthu atatu Ku Lilongwe. Izi zadziwika pamene anthuwo anaonesa zizindikiro zina zamatendawa ndipo atayedzedwa… ...
A woman has stolen a newborn baby in Chiradzulu after lying to the child’s mother that she is a sister to the baby’s father. The baby was stolen on Sunday at Mitawa Village, Traditional Authority… ...
Armyworms
Unduna wa ulimi, ulimi wa nthirira ndi chitukuko chamadzi wati ntchembere zandonda zikuonononga mbewu zosiyanasiya m’madera ambiri m’dziko muno. Mbozizi zagwa chifukwa chakusintha Kwa nyengo m’madea ambiri mdziko muno. Izi zili chomwechi potsatira mvula yankutho… ...