The People’s Party (PP) continues to lose its members and the latest to leave is the party’s national organising secretary Salim Bagus.
Bagus has joined the ruling Democratic Progressive Party (DPP).
Making the announcement at a DPP rally, the politician said he want to work with the ruling DPP in addressing the challenges that have rocked the country.
“In Malawi, we have a problem that the opposition always points fingers at government without offering solutions, some of the challenges we are going through have been brought in by Professor Peter Mutharika, I will now work with government,” said Bagus.
DPP’s regional governor for the south, Charles Mchacha, said the move is a testimony of the productive work the party has achieved in the two years that it has been in power.
Since PP president Joyce Banda left the country after the May 2014 polls, the party has witnessed a massive exodus and internal squabbles over the choice of Uladi Mussa as interim leader.
Angofuna kudya nawo dollar kkkkkkkk go to hero
Akafike kape ameneyo
Is the choice of the salim Bagus ndiye ndalezo bwanji Atupele muludzi ali nduna Ku DPP koma anali Presidential candidate wa UDF anthu kumati ung’ono ung’ono ukiti ukiti akusiyani kale kale atupele .ndiye mukanene za salim Bagus kuchoka Ku PP apanga bwino Ku choka aliyetse Ali ndi choice !!!!

Dyela
Nandakhuta kwa agogo aka kachisilu kamunthu angakadandaule ndani? kachisiluka kakagwele ukooo, mukaona nokha ndikotopesa kandakhuta kwa agogoka,,,,,,
Rollingstone……
A Bagus zikuwavuta ndiye sindikudabwa.Anali ku UDF,napita ku PP,lero ati ndi DPD kkkkkk kaya amati PPD ena ndikumva ati DPP.Awa ndi ma nomads ongokhalira kuyenda osapuma koma chopeza palibe.
Recycle politicians khikkk
Dyera uyuuu
ZACHABECABE ZIKUCEDWESAN MUYANG’ANE KWA MULUNGU BASI SAMAKHUMUDWISA
Anakwawo Mbayende Abwerera Kwawo Mbuyangayi Mwatani Kani Inembo Ndili Nduli Mwakemo Kkkkkkkkk2019 Zilko Ku Chikwawa Central
Tired of these Recycled politicians eish!
Mukamapanga comment mudziona kae b4 commenting,enanu mukumapanga comment zinthu zopusa kut anthu akuziwen km becareful coz titha kukufufuzan mpaka kukupezani using ua fb information dnt think potu apa ndipa fb ndet sitingakupezeni,enanu tayamba kale ntchito yokufufuzan posachedwapa anyamata anthu akupezan muona mbonaona ndithu
Ngati ndani iweyo. Machende ako
Tsopano tiope zimenezo.
Ben n thossia ua on the list soon tikupezan muzanene bwino im not kidding,im working with the social network secret intelligence(sonsi) so just wait ena atengerepo phunziro pa inu
kikikiki
Tikufufuzani” who are u.ungachite chani kapolo iwe.uli biii.mano ulibe.what do u know .undipeze ine pamozi ndi agogo ako ndikuononge.fodya etiiii.
Wasala chakweta
Kkkkk mutha nonse kkkk
I know very well about that man he is after money not development
nothing disgusting like malawian politics its jst selfishness nothing else ,here today zea tomrow lke siku tansport .
Ma hule a ndale awa, ndi adyera, asakupusitseni amapita kumene kuli ndalama. 2019 Mcp ikadzalowa m boma adzatuluka Dpp nkulowa ku Mcp, anthu ngati awa ndi omwe akulowetsa pansi chitukuko cha dziko akakhala mmaudindo.
Chakwela naye walowa Dpp
Akafike munthu wopanda phindu #salimu.Ashawoooooooo wa zipani.
UDF was formed by BINGU&MULUZI DPP by BINGU PP by JB and BINGU plus JB come from UDF and PP from DPP they are the same FAMILY AWA kkkkk
Sindinamve bwino bwino Bingu kuyambitsa nawo UDF mwati?
ok at Ibrahima chisuse the FOUNDER was BINGU and B MULUZI that’s why anapasa uprezindent ngati CHINDA THANK U Go to GOOGLE the founder of UDF ok
Bagus UDF,DPP,UDF,PP,then Back to DPP.Opotunist Polititian
He will never go back to Parliament again ! He just liability and voters know that
Gift mandowa you r rt
AKADAKHALA MUNTHU NKADANJENJEMERA NAYE. KOMA BAGUS kaya nkachani
ife sitikugwedezeka naye apite ameneyo
Bwelan,bwelan,dpp 2019 boma iyooo!
Bwelani malo alipo ofunanu sitikuletsa DPP woyeeeeeeee!!
Bola Udakapita Ku Zipani Zina Kwa Mr Ibu Kokhaku Waotcha Iwe Ukuona Mbola Zili Kumeneku Nkumat Ndapita Ku DPP Ndiwe Mmodz Mwa Anthu Osalifunila Zabwino Dziko Kafike Nawenso Ukasolole
Bola Udakapita Ku Zipani Zina Kwa Mr Ibu Kokhaku Waotcha Iwe Ukuona Mbola Zili Kumeneku Nkumat Ndapita Ku DPP Ndiwe Mmodz Mwa Anthu Osalifunila Zabwino Dziko Kafike Nawenso Ukasolole
Lakula ndi dyera si kutumikira wanthu .Ife akuwona kuti dziko lonse lakwiya ndi utsogoleli wa abakha a DPP kumunka konko.
Lakula ndi dyera si kutumikira wanthu .Ife akuwona kuti dziko lonse lakwiya ndi utsogoleli wa abakha a DPP kumunka konko.
salimu bagus munthuyu asatipusise ayi ndimuthu opanda chitukuko akalunza amakalanda katundu ndi kungumula zomwe amayamba mukampeni ndi anthu opanda tchito dziko
salimu bagus munthuyu asatipusise ayi ndimuthu opanda chitukuko akalunza amakalanda katundu ndi kungumula zomwe amayamba mukampeni ndi anthu opanda tchito dziko
Chipani chosiidwa icho azikakamilayo ndindani mwini wake anachitha kalekale
Chipani chosiidwa icho azikakamilayo ndindani mwini wake anachitha kalekale
KUBWERERA mwana PA KUKU bere LAKE
KUBWERERA mwana PA KUKU bere LAKE
Welcome place njambili DPP woeeeeeee
Welcome place njambili DPP woeeeeeee
After kuba ndipamene akuthawa kt asaonekere ndi anthu okuba
After kuba ndipamene akuthawa kt asaonekere ndi anthu okuba
Kuiwopela patali asala a mcp kumapeto kwa chaka ayambapo
Kuiwopela patali asala a mcp kumapeto kwa chaka ayambapo
Its not 2late to come together as 1,zabwino saitanira.
Its not 2late to come together as 1,zabwino saitanira.
Muzisiye choncho
Sopano mbenjeleyo akutani pamenepo kkkkkk
Sopano mbenjeleyo akutani pamenepo kkkkkk
Theirs no readership in pp
Theirs no readership in pp
Ufuna ndalama zochuluka wayitha
Ufuna ndalama zochuluka wayitha
dpp 2019 bomaaa!
dpp 2019 bomaaa!
Expired politicians. Akafike alibe ntchito. Ankangolowesanso ziwanda nchipani ameneyu. Akagwele
Expired politicians. Akafike alibe ntchito. Ankangolowesanso ziwanda nchipani ameneyu. Akagwele
PP is finished and we only have Dpp and M.C.P parties in Malawi
PP is finished and we only have Dpp and M.C.P parties in Malawi
Zauchisilu basi
Zauchisilu basi
Salimu Bagus,mmm is he a politician,? I dont take that !How many political parties has he changed.Bagus and other Recycled politicians are the type of people who have made malawians poorer.Bagus wants political weight to fulfill his personal gains and not to develop malawi. In 2019 we dont need Recycled politicians .Watch out Dpp,mudzalandira mutu wa fiti kuyesa mpira.

akuteteza shop yake kuti angazamutsekere uyu. sadaiwonere patali maso achita khungu uyu.
akuteteza shop yake kuti angazamutsekere uyu. sadaiwonere patali maso achita khungu uyu.
he is idiot and crook need money from diphiphi
PP is dead never talk abt it anymore
Ndiye ndale zapa Malawi zimenezo.
kkkkk ķambalame kolawilira mmawa ati kudzangoiwonera patali kkkkk dpp 2019 bomaaaaaaa!
Kip on dreaming
Inu dziko ndi la chipani chimodzi asamatinamize anthu ake ndi omwewa amati chipani ichi chikawina ali komweko tiyeni kungokhala one party mwina mavuto angachepe
We dont want such politics. Zadyela basi
Welcome to dpp the clever is choice
Bogus akuti kuopa kuyanga ndere, kkkkkk
Kkkkkk anthu odziwa kuiwerenga game emeneo osakakamira ntunda opandamadzi DPP boma ilooooo!
Kkkkk. First look at the calibre and political history of mobile politiciansand the you may make sure observations. DPP was started by betrayers of UDF the rest is history.
Welcome all Pp
pp!! yatchona!! pp!! yatchona!! odi ukoo!! apa nde ofunika amakeniko odziwa ntchito azakoze galimoto ija.driver wakenso anathawa anamusiilayo sakutha kuyendesa..ayigwesela ku mphompho..
Salim Bagas Ndiwadyera Watuluka Ndikulowa Zipani Zingati Kuchoka Pomwe Adayamba Ndale?Amatelo Ataonakuti Zinthu Zayamba Kumuvuta.
Kutha mapulan.
Ayende bwino bola asadzabweleleso ai
…..ngati makatani
PP likely to follow Maravi’s footsteps.
Wachitabwino Kuchoka Mp Wathu, Wathu Amenewo
Fortune seekers