MCP brings on board another Pastor: Livingstonia’s Munthali joins politics

Advertisement
Chakwera

After attracting current party president Lazarus Chakwera from the pulpit of Assemblies of God, they have now roped in another minister of the word.

The main opposition Malawi Congress Party (MCP) cannot just stop bringing in big names as this time it has roped in Synod of Livingstonia’s Reverend Maurice Munthali.

Munthali(Left): Has joined MCP.

Munthali who will retire as a reverend on December 31 was presented as a new member of Malawi Congress Party by party president Lazarus Chakwera at a rally held on Friday at Phwezi School Ground.

The preacher served as General Secretary of the Livingstonia Synod between 2004 and 2012 and has been a huge critic of the Democratic Progressive Party government for years.

MCP Second Deputy Secretary General Eisenhower Mkaka hailed the coming of Munthali saying it is a good way to end 2017 as the party continues to grow in all directions.

Before the rally, Chakwera visited families that were affected by floods at Phwezi in Rumphi recently.

The MCP president donated K1 million to the flood victims.

Recently, Tarcizio Yetala who served as deputy minister under United Democratic Front (UDF) government also joined MCP.

A political analyst told Malawi24 this week that 2017 has been a great year for the main opposition party.

Advertisement

178 Comments

 1. Asanabwere Khristu, adzaoneka wokana Khristu. 2 Atesalonika 2:7 Pakuti chinsinsi chakusaweruzika chayambadi kuchita; chokhachi pali womuletsa tsopano, kufikira akamchotsa pakati. Yaaaa tidziwapempherela azibusa athu CHITAYIKO CHAFIKADI. WOTAYA AKUTAYA. WOTOLA AKUTOLA. 2 ATESALONIKA2:1-9 WERENGANI MOFATSA. ALI NDIKHUTU AMVE CHIMENE MZIMU AKUNENA MASIKU ANO.

 2. PAC is full ndi brainless pastors omwe akufuna kusocheresa nkhosa za chauta shame on you so called pastors while ur being used by opposition a magazi mmanjawa.

 3. I’d rather see pastors ruling this country not these educated thieves we have in government .. Anthu oti amakutukwanani ndikukubelani dzuwa lili pantunda

 4. Nice decision Rev Muthali,tikufuna athu abwno ngat inu,kale dziko amatsogolela nd athu a Mulungu ngat omwewa osat mbala nd mahule zomwe zikusakhidwazi zaka zino,kod tifunilanj mtendele pomwe timasakha athu opanda mzimu oyela

 5. Pastors who join politics,we expect them to practise clean politics.Where there is truth let them accept,in case of disastors positive and tangible suggestions,solutiond and respected criticism should avail.

 6. Ichi ndi chitsimikizo choti dziko lapansi lakwanira ndi ufumu wa satana.
  Yesu adakana ufumu wa satana mdziko lapansi lino kufuna kufuna u Mulungu wake omwe anabwelera pa dziloli.
  Choncho onse odziwika mu ntchito za u Mulungu sayenera kugwa mu chuma.
  KUMBUKIRANI NKHANI YA LAZARUS

 7. Inu ndinu mchere wadziko lonse lapansi inu ndinu nyali yadziko lonse la pansi abusa a kulowa mu M C P chifukwa 2019 a kulowa m’boma ndiye akufuna kudzakometsa dziko la Malawi ndikuwalitsa dziko la Malawi. Amen

 8. Pastors now turned into abuse words instead of saying glory to b God. Turned Into Liars Group. Turned To B Used Pple under poor destination

 9. This party is full ov evil pipo kkk they failed to steal in the church and now they think kuzaba misonkho yawovutika mmm mulungu muwalange a galuwa

 10. Ticking bomb about to explode wise men are running where its safe to hide.come on in you that are forsaken by this family inherited chieftaincy

 11. Zaka 40 ndakwanitsa mwezi wathawu ndpo ndakhala nawo mmisonkhano yandale yosiyanasiyana koma zomwe zimatuluka mkamwa mwaanthu andale zimaonetselatu kuti alipatali ndichauta. 1. kutukwana anzawo wopikisanananawo 2. kugemula amzawo ngat enawo analengedwa ndisatana 3. kunama kwambiri bcoz zomwe amalonjeza samakwanilitsa. 4. amathawa komwe anasankhidwira kupita kutali ndianthuake ngat anthuwo ndimachewuchewu moti angamuchotse akatumba….ndie tiziti andale akapulumuka?? komanso amakonza ziwembu kwaanzawo kuti adutse moyela. ngati angapulumuke andale ndie kuti anthu ambiri tikapulumuka. MAULOSI AKUKWANILITSIDWA NDITHU.

 12. Palibe cholakwika ngakhale anali Davite anali mtsogoleri wa dziko analinso munthu wa Mulungu akunjawa atizuza mokwanira

 13. 2 Samuel 12 – Nathan Rebukes David – The LORD sent

  Nathan Rebukes David – The LORD sent Nathan to David. When he came to him, he said, “There were two men in a certain town, one rich and……..

  Nathan was a man of God where as David was a politician God used Nathan
  ………………………………………..
  1 Samuel 15 – The LORD Rejects Saul as King –
  The LORD Rejects Saul as King – Samuel said to Saul, “I am the one the LORD sent to anoint you king over his people Israel; so listen now to the……………

  Here Samuel was a man of God Saul was a politician. God used His Samuel.

  ………………………………………….
  Mark 6:14-29 – John the Baptist Beheaded

  John the Baptist Beheaded – King Herod heard about this, for Jesus’ name had become well known. Some were saying, “John the Baptist has …

  John the Baptist was a man of God, Herod the politician hated the messenger of God.
  …………………………………………..
  1 Kings 19 ESV – Elijah Flees Jezebel – Ahab told – Jezebel

  Elijah Flees Jezebel – Ahab told Jezebel all that Elijah had done, and how he had killed all the prophets with the sword. Then Jezebel sent a…………

  Elijah was a man of God Ahab was a politician. Ahab allied with Jezebel to hurt the man of God.

  Conclusion is for us!

 14. I get to wonder when u say politics need anthu osapemphera. Yet povota u need anthu opemphera omwewo to vote. If it’s none religious issue about politics then azipanga okhawo osapempherawo. We all belong to this country MALAWI. Malawi is one. Tiyeni nonse akufuna kwabwino tikonze dzikoli, we r all God’s Children.

  1. Ngati uli umfumu Wa satana, tinenekuti azibusa omwe amasankhidwa kuti ndi azilangizi a president si a zitumiki a Mulungunsotu. Tizisiye zikulire limodzi zidzaoneka pokolola bwa!

  2. Tisathawe ulangizi nkuyamba dyera,tsono tonse tikalowa active politics who is to teach the other poti iwonso ayamba kunama?

 15. Anthu oopa Mulungu ndiamene ali oyenela kuyendetsa dziko chifukwa azipanga zinthu mokomela mtundu onse wa dziko lomwe aziliramulira looo…

 16. It’s Time 4 God 2 Take In Charge Time 4 Devil Is Over, No Wonder Comets Can Tell That Light Has Come & Devil Is Afraid But Mind U That This World / Mw God Is The Incharge, Not Devil, Devil Wazuza Anthu Thawi Yayitali, Eni Ake Abwera Iwe Ukaloweso Mukhumba. Rev. Munthali Good Luck!

 17. Kkk mwawaona Azibusawa tikamakuuzanu kuti PAC ndi gulu la zikutumbwe zomwe zikugwirrsidwa ntchito ndi osusa lero ndi izi…. Munthali. Wakhala akudzudzula boma mudzina loyimirira. Livingstonia synod… this dynod is group of fake, crooks, selfish pastors.. they tried to ban Quota, They tried Federalism, they tried 50+1.to. no avail kkkkkk

  God loves ud mm

  1. Hahahaha.u r happy ndi quota system kutenga mbuli for univesirty,ma cashgate mukudya nowowo mungawone vuto ngati kkkkkkkk koma malawi.mukhala choncho ligwetseni kwambiri zikoli.

 18. Be like King Josiah – put all homosexuals and abortionists to death. Then watch God bless Malawi. Malawi has hope, unlike the West and South Africa which have rejected God and are extremely evil.

  Youtube – khulupirira

 19. Even Charles Weya a footballer like Peter Mponda can join politics and win wake up in deep slumber politics is for every human being!In Venezuela the president Hugo Chavez was once a bus driver everything is possible if you work hard

 20. Solders;Police Officer;Teachers and all cival servants to me are proper to join politics.pastor Bishops ;Prophets:To listen to God and tell the piliticians what God is saying and obey.We can not compromise the calling of God to serve Him in church with politics ;All is Gods work but in differrent direction.The vehicle that changes direction because of its desires hits back.

 21. Many People Do Comment On Issues They Don’t Know, Umbuli Basi, Ine Ndine Wa Livingstonia Synod, Munthali Yemwe Mkunenayo Ndiopuma, Anachita Retire, Ndiye Mkuti Chani? Mziyamba Mwafufuza Msanalembe Ma Dpp Cadet Inu, AMOURICE MNTHALI NDIOPUMA (RETIRED) KWAO NDI KU MWAZISI RUMPHI. Msiyeni Azipanga Zomwe Akufuna sanje Zili Thoo! Mmitu Yanuyo.

 22. Inu amene mukuzuzula a Munthali inu ndi amene Mulungu anakupasani udindo oweluza anzanu? ngati Munthali wathawa nkhosa inu bwanji osayamba ubusa ndikukasamala nkhosa zomwe a Munthali azithawazo? Tisaiwale kuti bible limanena kuti “TONSE” ndiochimwa ndiye inu mukuzimva kulungama kumaloza zala anzanu.Mmene Munthali amayamba ubusa sanabwere mmakomo mwanu kudzakuwuzani kuti akukayamba ubusa apa wasiyanso kufuna kwake tamvapo azibusa ambiri akumakhala alangizi a president bwanji simuzuzula? Za Mulungu zimadana ndi matama ngati anuwo musiyeni mwiniwake azaweluze yekha.

 23. Tiyeni tonse tilowe ndale mwina zinthu ndikusitha anyamata okakha chikopa ma player ampira tiyeni,mwaona nzanu George watengatu mpando onona uja, kaya ndinu Abusa, mashehe,oyimba you’re welcome.masiku ano president akufunika nyamata 51year below.

  1. That is debate. No one is attacking anyone. Malawi we are still backwards. Musicians, soccer players etc are joining politics. Why being selective like pastors are not human being.

  2. Aaaaaaa koma ndipo inu wat is it that munthu opemphera akapanga join politics u tok too much? Sindikuonapo vuto mu mpingoso ndi momwe muli nyasi mmmm pali ma hule ena zachisoni amachita kutchula azikulu ampingo kuti mnzibwenzi zao shame n kodi anati akalowa ndale asiya kupemphera mm ayi dont judge si bwino chomcho

  1. Koma Mnthali Akumnena Apau Mkumziwa? Uyu Ndimubusa Opuma Pantchito, Osati Kuti Akadali M busa Ayi, Amalawi Bwanji Mmakonda Kujijilika Kumayankhula Zinthu Zosaziziwa?

  2. Check in the Bible mupeza many who led the Nation of Israel were men of God. Vuto la Ku Malawi nthawi zambiri timakonda kugwiritsa kwambiri maganizo athu osati mawu a Mulungu. God is the best jugde..

  3. Sydney kutsonyeza kuti sanali mbusa oitanidwa ndi Mulungu koma inali ntchito chabe eti hehe,chomwe ndiziwa ine munthu wa Mulungu sapuma ntchito yake kkk

 24. kkkkk Otsogolera dziko ndi Akhristu komaso Mukhristu amalarikaso mawu .There is nothing wrong ambiri azatembenuka mtima panthawi ya campaghn .keep it up Rev Chakwera n Rev Munthali .kkkkk

 25. Azionele limodzi.Palibe kukhulupilira anthu amenewa,nanga angakhale bwanji atsogoleri abwino ngati akusiya kutumikira Chauta,nanga Chautayo awalora bwanji kukhala atsogoleri aziko poti mphamvu yake aikana?.AZIONA.

 26. Until when Malawi should we know that pastors,soldiers, policeman, president are all human being like you and me. I don’t see any wrong doing someone joining politics

 27. Kma mzimu wa kamuzu uliko ukungodaula kt zoona chipani chake chatengedwa Ndi anthu osayenera kulamulira.but all I wish mzimu wa kamuzu ukukathe iwe chakwera bcz I dnt see any sense kuchoka Ku za mulungu en join politics mmmmmmh…

  1. That’s the problem with faith fools!! You allow the Clergy to steal your money in the name of paper Sundays with a grantee of you kukalowa Ku mwamba whilst him akupanga politics.Shame on you!!

 28. Ubusa udali kale pano nkhani ndi ndalama mind u ubusa amachita kulembera ngati afunsira ya uphunzitsi zamaitanidwe zinatha,no wonder azibusa nkhoma/livingstonia synod kulimbilana malile shame Hell ikudikirani

  1. Mwina enanu simudziwa chipani chilichonse chotchuka ku malawi kuno m’busa alipo,funso nkumati akutsatanji ku ndale ndalama.masiku otsiliza anthu adzakhala okonda ndalama ndi izi tuziwonazi

  2. Mwina enanu simudziwa chipani chilichonse chotchuka ku malawi kuno m’busa alipo,funso nkumati akutsatanji ku ndale ndalama.masiku otsiliza anthu adzakhala okonda ndalama ndi izi tuziwonazi

  3. Munthu wina aliyense ali ndi ufulu otsutsa/kuyamikira pa za ndale osati kusiya nkhosa nkulowa mchipani.nkumawauza apemphere pansonkhano a governor/secretary general nkuyamba kutukwana.chauta akuwona

  4. Abale Mu Mu Livingstonia Synod Azibusa Amapuma Pantchito, Uyu Mnthali Ndiopuma Funsani Ife Eniake Ku Rumphi Kuno, Kuola Mkamwa Basi!

  5. Chifukwa chiani mphunzitsi akapuma amatha kutsegula schol yake olo kupita ku pvt? Zinazi zikuonekeratu kuti ndinankafumbwe basi. No mata anapuma iye ali ndi ukadaulo wa mau a Mulungu basi.

  6. Kkkk mmmm guys remember that tikati mau a Mulungu sikulowa kwambiri mu church ayi koma kuchita the will of God and kulowa ndale sikuti sungakalowe mu ufumu wa Mulungu, do the Will of the Living God, look around, Cristiano Ronaldo anathandiza osowa ngat iweyo through playing football, kupulumutsa anthu sikualalikila kokha but kuwalanditsa kuchilombocho , koma kwathu kuno when you talk of politics basi ndiosapemphera aaaaaa agalu Inu wake up do the Will Of God amenewo alandiridwa khomo ndilotsegula …. Thanks

  7. Allan Ngumuya kusiya gospel kulowa dpp, mbusa mzomera ngwira kusiya ubusa kulowa dpp, abusa a malison ndau anali ku dpp

  8. Zimadana ndi umbuli izi@ Mr Edson Ngwenya kufufuza kaye Munthali anapuma ,,mumafuna alowe DPP ?mwauponda
   Dzanja la Yahwe likaloza basitu MCP for real viva,,God Bless Malawi
   “Nothing for us without us”

  9. Mukamati nzumera,allan analowa ndale mukufuna kutanthauza kut enawa monga achakwera akutsanzira iwowo? Tchimo sachimwirana.Anthuwa akapsa moto posatengera chipani

  10. Don’t Judge Others, Iwe Ukunena Mnthali Ubale Wako Ulibwanji Ndimlungu Wako? Chimtundu Chaanthu Alikumalawi Munthu Utha Kuchoka Ndikukakhala Kunja Makamaka Ndale Zachipani Cha Dpp Zongolimbana Ndianzawo Ine Zimandibowa

  11. Nonse amene mutukwana mulungu akuyendereni mwapadera-dera za mulungu sumapuma ukhoza kumutumikira mnjira zosiyana siyana ndukhulupilira ndale alowazo amtumikira mlungu.for your own information sindili mchipani chilichonse en sindidzajoyina forever ndi ufulu wanga kutero.kuyankhulapo pomwe zapindika kapena zaongoka ndili ololedwanso mopanda mantha

  12. Tili mnyengo zowawitsa chipani chilichonse chikamalamulira ena amanjoya ena ayi.olo panopa mcp,udf,pp,mafunde,Dpp atamalamulira winabe adandaula wina anjoya.tiyeni tidalire mulungu nkulimbikira zomwe timapanga bussness job etc

 29. Munthali nayenso kuthawa nkhosa za mulungu kukayamba kutukwana, koma pa Malawi pano kodi ndichiyani chikufuna kuchitika? Inu musayipitse mbiri yanu ayi, anthu wolemekezeka pamaso pa mulungu inu ndichiyani? ku mukweza satana m’mwamba kutsitsa dzina la chauta pansi, ngakhale mutawina kuyamba kulamulira basitu chikristu chitha nanga mungapitenso kukapemphera? Opusa uyo asangalatsidwa ndizimenezi, tsegulani maso anu penyani muntambo muwone mwana wamunthu alikubwera.

 30. y MALAW???Ena akusiya mpira kulowa ndale ena akusiya kuimba kulowa ndale uyuxo wathawa ntchito ya mulungu kkkkkkkkk yonah kkkk nzakoyo idamumeza nsomba 2014 atathawa zamulungu yasala ikakutayen kunja 2019

  1. Ndinene kuti busa amene akupanga ndale ndi CHAKWERA yekhe ma mmalawi muno lweyo ukunyoza popeza akulowa chipani chimene choti sichako ieeyo ndiwe wa DPP usaname kumenekoso aliko abusa kuli mzumara Ndiye mukamonyoza mukuwonetsa uchitsilu wonse

  2. Mr Phiri nkhan ili apa siya DPP koma kuthawa ntchito ya mulungu kolowa ndale nkumatukwana dats my point pls musakhuzitse DPP inu nd aja ot mvula ikawononga nyumba mumat DPP esh simuzatheka

  3. pls leave DPP out of this,zamasiku otsiliza anthu azakhala okonda ndalama ndizimene zikuchitika masiku ano kuthawa ntchito ya mulungu kulowa ndale kutopa ndikuba zopeleka zakuchurch kkkkkkkkk jesus is coming

  4. Unama Iweyo athu amenewa ndiwoyamba kusiya ubusa ndikuyamba ndale mngakhale history imatuwuza chulembwe kutu anali mbusa wosewa amenewa ukuwanenawa adakalowa DPP zonse ukulembazi sudakalemba

  5. HISTORY!!!!! akulu adasiya zamulungu????palibe chomwe ukuziwa about chilembwe,chilembwe adapanga chipani????man u can convice to join old party MCP may b achewa+nyau

  6. Choti udziwe mchewa ndi mchewa ndipovuta kusitha kukhala trible ina athu amenewa atopa ndichinkhalamba chakocho afuna kuwona zina

Comments are closed.