Vote Now: 2019 Malawi Election Opinion Poll

Advertisement
Malawi elections MEC

[poll id=”2″]

You can alternatively vote on our Facebook Page:

or Twitter

Thank you for your participation.

Advertisement

931 Comments

 1. This is an excellent move to asses the political atmosphere in the country. I will not be surprised to see the same outcome in 2019.

 2. This is an excellent move to asses the political atmosphere in the country. I will not be surprised to see the same outcome in 2019

 3. Kamuzu amkafuna Chakuamba kuti azalamulile after him ndipo ndiyekhayo ndikana mvotela ine.nde pakuti anavaya sindizavotanso moyo wanga onseeee.

 4. APM. Palibe anga make…chakwera is an empty tin ..olo mutamufusa kuti lodi inuyo mutatenga boma lero blackout zimenezi mungathese bwanji…He will say we will put some measures….bolaso JZU

 5. Amene azakavote ndichitsilu kwambili cz ma vote anthu amagwila ntchito kukuikani pa mipando yonona simuyamika olo kukozetsa niseu kumee mumangokamba mwati muzakozetsa mpaka term yanu kutha popanda mwachita . Koma jukachitika Malilo nde kalikiliki kukagula chibokosi chodula munthu wakufao mmenemo amachita kusowa K50 yoti akagule fisesi wamalambe kapena kafroze kuti akhale ndi moyo.once wangomwalila inu liwilo ndi chibokosi pekapeka kodi malilowo mumanya kapena?????? Ndantchula dzina ngati??? Hayiiiiii,;;, kkkkkkkkkkkkkk ndakusokosela mkulinga utava

 6. He has good vision to unite Malawians and he is principled

 7. It’s obvious I and majority of malawians would vote for Lazarous Chakwera as he is the only hope for us who want our country to transform in all spheres of life not these thieves

 8. Mungotaya nthawi ndima voti anuwo whatever you can like someone still he will walk on your head, and getting a rich over and over again, be awake guys and do your things, ngati mukuti just use dollar panels

 9. as of now malawi we r no longer to b independent oir leader’s r ful of greedy wat d hell is 50+1 playing with malawin citizens eti maybe Is tym to co back zamunda to run d country our leader’s hv failed us cashgate anaba ndalama za dev. pano akupanga form 50+1 kutipanga play ife esh akazawina azyambeso kuukirana leading to worse poverty and downfl of malawi

 10. Munthu wozindikira sanganene kuti sangavote, umunewo ndi umbuli, nanga bwanji mumadandaula zinthu zikakhala kuti sizikuyenda bwino mdziko monga ndi mmene akuzimiramu magetsi, be wise enough people this is our country

 11. sindiri pa fesibukhu kuti ndikavote. pepanii post yanui mwaika pa page yolakwika yoti enafe za ndale ndi apongoxi athu. mokupephani chotsani mukutichititsa manyazi.

 12. sindiri pa fesibukhu kuti ndikavote. pepanii post yanui mwaika pa page yolakwika yoti enafe za ndale ndi apongoxi athu. mokupephani chotsani mukutichititsa manyazi.

 13. Lachulukila ndi dyera ku Malawi kuno, kwa achinyama ife tingolimbikila kuti Malawi wathawi yathu asazafane nduyu tikhale olimbikila ndi kuzidalila kmanso mulungu pasogolo

 14. Mukafunse Julius Malema..adawina by election pamudzi peni peni pa Zuma,..Zuma adapeza mipando 4, opposition idapeza mipando 21, kubwera general election,Zuma reigned supreme..beating the opposition knees down…do not be over excited by the results of a by election..it represents a miniature fraction of the national vote..

 15. Guys ndayenda mulimbe _ mu,ndilande ddp 51%,mcp 49%.muchikwawa ddp 50% mcp50%.ndiye kubwera mulilongwe area 23 ddp 10% mcp 90% area25 ddp 5% mcp 95% ndiye muwona nokha amene adzawine ndani

 16. pipo are looking 4wards not bacwards ndipo palibe chipani chomwe chili chotsusa chomwe chingamake boma paka kuwina tsogoleli alindimoyo ndakayika unless atamwalilatu ndiye ndizotheka koma za zongwe wakudayi mungochedwa ndikumunganizila sangawine ngati mumazisata ndale muyambe kuyang’ana muluzi matengedwe ake awudindo kuzabwelaso Bingu muwone kuzabwelaso joe banda kt utsogoleli amawupeza motani muwona ndimopadukila boma kumalawi munthu yemwe amawina ndiyemwe waba chipani kuchokela kuchipani chizake belv me teloku mugotaya nthawi ndikugani zakuti sizingakuthandizeni

 17. The way in Malawi we vote, we don’t vote for better change or vote for what contestants have offered us but we vote for home boys that’s all.

  1. He is not the right person ,do you know who chakwera is ? Let me abit tell you ,go to CCAP nkhoma theological school and possibly to CCAP Reveland you will find a big Bible may be you ever seen written by chakwera ,as of now people are abusa after reading bible written or translated by chakwera ,this man has grace that can read people to salvation ,osati zadziko matemu awiri basi koma APA tikuyang,ana zakumwamba, so I can not vote for him akuchita za yona amezedwatu ndi msomba mumuwuziretu chakwera wanuyo

  2. Yesu anauza afarisi akumufusa za msonkho kuti iye akuketsa kukhona , iye adati palikhope yandani ? Uyu chakwera maso ake wayika pazadziko ,zakutha ,why why why awarekere akubawa koz mbava sizitha or atawina and iye adzatengeka ndipo adzachita za mfumu saulo

 18. Ku Malawi amwene, as if we are all walking chickens with heads cut off. Sometimes you wonder kuti, koma enafedi ndi anthu kapena agwape? Ndi Inayake koma. I was here to read comments though, waiting for 24hrs of blackout ikwane just to have 8hrs on.

 19. Michael nkandawire mwayamba bodza tsono,,,iwe udakali ndizthu zakale ngat zja? MCP???? Bambo that party has been abolished n dt expect to come into the power again,,,pali mau amati ushud nt gv up preaching words of God,,,nde ao mukut a chakwerawo anatani kumangopanga dzampingo wao??aaaa idt lyk that man n he has done very stupid idea himself,,,,kufuna kulemera bas kma wauponda ndthu,,,,F that party get into the power uzaona they will be bzy to established the area’s along the district’s coz Athu sakuchizwa chipani chopusa chmenechja nde bola atupele bt nt ao ofuna kuyakhula ngat azunguwo pomwe ndwakwamponda mwali uko nanyoni weniweni olima tonoliya kkkkkkkk kkkkkkkk,,,,we r under American leadership nde ena osapta kuxul ndi ao akublema pita KT sakutha kutha kwake mukufuna muone chani Athu inu??? Vuto mukungoona magets akuzima dt uknow that its just a propaganda????that shud stop,,,,mundlakwsa Athu inu,,,2019 DPP again in power whether uwant or nt,,

 20. We have done alot of mistakes in the past,and those mistakes have costed us alot this time around no more regrets,4 is the answer for all malawians.

  1. I know there is so many problems but it did not start with him,he find the country in a mess,the kwacha was devalued, cash gate scandal, the disaster just mention a few,

  2. What stabilization are u talking about, u mean corrupt leaders , lies , jokes? My dear please dont use this word “stabilise” coz Malawi is not in that state, a lot of things aren’t going well , kwacha depletion, electricity being order of the day ( frequent blackouts), many leaders who are custodians of our country’s legacy are the ones being implicated in syphoning state resources . There is political instability in malawi that puts at risk the lives of us the innocent citizens, economic instability that has seen many of brothers n cctas going outside the country seeking a better life

  3. That’s kind of thinking that unless we change, malawi will never develop. What you’re saying is like this; someone fails JCE exams but they say, I’ll go to form 3 and while there I’ll re-right JCE exams. in short, APM has failed.

  4. If u know Malawi very well u understand where our problems come from,with devaluation of kwacha,it was madam joice banda who did it ,and APM,just inherit it, when u talk about electricity problems it is because luck of planning for the past leader’s, because Malawi only uses hydro power plants, and it was a prevelage in the past to have a house with electrity than today so our electrity was only for few people,

  5. /John Michembo,i can’t denied that there challenges in our country, but don’t be fooled that even if we put chakwera our problems will end the problem is bigger than that

 21. don’t even try to ask us to vote because nobody is thinkin of it,by the way lets put it in this way this comin year it’ll be the year of “revolution” tihink about it………

 22. Nobody Is qualifying to be President here. Each and everybody here has got his or her own weakness and this doesn’t need a proof. It’s obvious.

  1. Manifestos are always lies, how do u believe someone telling you he’s gona do this or that yet he doesn’t even know where the money will come from for such developments. Ndizomwe zikuwaonekera a peter pano zimenezo.

 23. Aaaaa enawo angamake kwa munthu wamulungu? Chakwela akuwina basi kaya wina afune asafune tambala wakuda atidzutsenso basi cz tinakomedwa ndi mbavazi

 24. Leaders are choosen by God on two things 1To give alesson to the people if samethings wrong is done or to save the people if they are om God side. Lemekezani alipowo kaye zinazo ziwoneka zokha 2019.

 25. Aaaa chakwela he is a vision leader and god must bles him each &every time he says &tels true things to malawian .

 26. Nkhani yovuta iyi, ngakhale kuti tizavotere anthu amene ali osutsa panopawo. Nawonso akazayamba kutilamulira azatsinthanso nawo, kubanso sikuzakhala nkhani kwaiwo chifukwa nawonso azakhala akuganizira za umphawiwawo umene alinawo kumabanja kwawo. Apa tinagulitsa dzikoli ku ufulu wazipani zambiri, ndikuona kuti ndibwinonso mwina ngati masiku a Kamuzu pamene anthu amangokhala osadziwa kanthu. Omwe ameyerekezanso, kuyetsa kusutsa mfundo zake amaona zosaona nthawi yomweyo.

 27. Iwe walemba izi sungaganize wekha ndukuina mmene anthu akuvutikiramu piano anthu akusamba opanda soap zokolora zikisowa msika, ndie anga voters mutharika wakoyo ndi ndani?

 28. Kod amalawi tizit kut simunadzukebe ndiliti lomwe tinavotelapo munthu amene tikumufuna ndikukwanilitsa zokhumba zathu? kod mavuto akuzipatala anayambapo atha nanga kuzimazima kwa magetsi kunayambapo kwathapo even for 24hrs, Amalawi tidzuke ndithu inu mwayiwala kut mu 2014 amene anavote ndi makina aja otchedwa computer ndiye muzivutisilaji kukayima paline ndikumapsya ndi dzuwa amene akufuna u president akazivotere yekha chifukwa amat aliyese azadya thukuta lake

  1. Inu mukayika…ma card ku hosp..ayufi..anandiponda dzala dza mwendo pa independence akuti ndadutsa mnzere..anandikwapula mpama cos ndatsokomola..youth week..kuima mokakamizidwa kuyambira mmawa akuti kufuna kudutsa a president..etc..ofcourse pali zina zoti zikonzedwe ngati magetsi kuti anthu apange ma business ..ena misonkho a MRA..chinyengo..tsankho..etc..

  2. Iwe ukuona bwanji…mabvuto ali ndi Mw afunikira ma medium and long term solutions for sustainability..i have observed one thing in Mw..timanyoza kwambiri mtsogoleri wathu mopanda ulemu..mmalo moti timupange support tikuganiza kuti zithu zingasithe ndi ciani..komanso tingatukuke ndi ciani a malawi..mulibe chotibweretsera ndalama..zotsatira zake dziko likuyendetsedwa ndi misonkho..ndinkadabwa kuti kodi mchifukwa ciani mu national athem anapepherera nsanje..a malawi nsanje..amayamika munthu akapita..let’s build malawi together…

  3. I hate unfair sharing distribution of resources kumangotinamuza ndi timusewu basi koma kutikawa 2mch.
   Imagine v who 64 mita just to re– ofc ya C/sec , inst vis anvr Cash gate ?
   Kkkkkkkk hommy I rspkt u vwz bro

 29. No man can end our problems, for Malawi now has become popular with scandals, fraud, stealing public confers and why voting. And I will no longer waist my time who ever the malawians shall vote for tidzavomelezana nazo.

 30. No one would like to still stay or live in darkness. So it’s obvious APM can’t pass 2019 the best way for him is to retire or resign

 31. Tinatopa kuika anthuwa pabwino ,akakhalaso pabwinopo kuba kwambiri,kumabelaso ndiovutika omwe,aaah alibe pabwino bola tizilimbana nzathuzi tizipeza chakudya cha lero,ine palibepo apo

 32. KKK ZOSE NDI NKHUMBA , WHY AM SYN DIS ? ONE PETER HAS GOT DIRTY GENES IF U REMEMBER WHEN HE WAS MINISTER HE USED PLANE 2 OFFICIATE ROBOTS IN MZUZU SO HE IS A NON PERFMER , 2 JOICE BANDA WHEN SHE WAS IN POWER SHE USED OUR CASH 2 BUY COWS , & SOLD OUR JET , 3 ATUPELE HE IS UN OPPORTUNIST HE CANT BE A LEADER & 4 MR CHAKWERA THE MAN WHO LEFT GODS WAY & FOLLOW POLITICS COZ OF CASH MMM BEWARE 4 DIS MAN PIPO IS DE SAME AS JESUS IF HE CAN THE PHAREESES & DINE WITH DEM GIVE A HIGH SEAT 4 D SINNER CAN U BELIEVE HIM ? SO LET A NEW BLOOD STAND B4 DIS VIMPIRES .

  1. OK BOLA MUZA VOTE BWINO COZ IFE TINATHAWAKO KALE KU MALAWI AM BASED IN ZAMBIA 4 CLOSE TO 15 YRS COZ OF DE SAME READERS WHO PUT THEIR INTEREST FIRST SO IF U BELIEVE IN HIM KEEP YO FAITH MWINA ANA ANGA OBADWIRA KUNO KU ZAMBIA ANGAZABWEREKO KU MUDZI .

 33. Mukamavota kumakumbikira kuti DPP inawina 2014 ili ku opposition komaso italuza popularity chifukwa cha kusowa kwa fuel ndi forex. Zingayambe kuyiwalika.

 34. Mukuika 4 bwanji? Poti 1,2,3, akhala pa mgwirizano. Peter anawafunsira mbeta onsewo. Ikanipo Peter and Lazarus tisankhe. Mpamene azadziwe mwambi oti chulikechuluke ngwazipani uma………..

 35. As me i never vot 2 anyone coz wina aliese akakhara kt sali boma mfundo zake zioneka zothandza kma akasakhidwa amangoona zaku toilet kwake kuiwara ovotera

  1. Zoona braz, coz I remember nthawi ya Joyce Banda, bwana Peter Muthalika amati akamadzudzula ndikupela mzeru zawo aliyense amkawayamikira. Komano taonani lero lino ndi ali pa nambala 1 nkhaza kuposa atsogoleri onse omwe apita kumbuyoku.

 36. Breaking…..

  According to the votes counted by Mr Michael Mkandawire we hereby announce that with effect from today the 4th December 2017 until Jesus comes our admn is is is is………… Dr Lazarus Chakweraaaaaaaaa

 37. A good citizen can’t say that he will never vote.to be honestly the winner of erection of our beloved country can’t rule. The results of forcing their selves into the chair of ruling are what we are experiencing nowadays.we may let the winner ruling our country not a stealer like Peter.I wonder why some of the poking centres increases the number of people that cast the vote than those registered? Any way chakwera wooooye!!!!

  1. kkkkkk let see 2019 mwati chakwela eti kkkkk ndimene ndimaliziwila boma lathu lamalawi palibe chipani chosusa chimamaka boma paka kuwina tsongoleli alimoyo kkkkkk ndikukayikka ndipo ndikukayikaso kt zongwe wakuda angazabweleleso blv me

 38. even u urself need to have a strong mind, before posted this, cause it is not the president himself to change the way this country is, but our thinking CAPABILITIES, if not so expect nothing good but worse

 39. Akusowa zochita MWAWAFUSA AGOGO anu Kumudzi kuti io azavotela ndani chifukwa inu muli ngati ndinu anzelu pa Facebook page sinonse muza vote mungotayathawi yanu nokhaso owina mukumudziwa

 40. ndi m’mene zinthu zili kuno ku malawi palibe chifukwa choti kufusa wima kuti zithu zilipati, koma ine vote yanga ndiya chakwela 2019 basi !!!!!

 41. If u allow Bushiri to be a reader of this country problems like :blackouts,shortage of foreign currency, shortage of water,lack of employment, poor infrastructure, low wages n more things will be a history.

  1. Shaa! Koma ndiye kungakome, chilichonse ndi ma miracles basi ie miracle money, miracle miracle electricity, miracle cabinet kungoyamba ndale basi kuwinilatu

  2. Malawi does not need Major 1. But it needs people or the President who can work with Major 1. And the politicians should stop cheap politics in malawi and start sorting things and developing malawi. Secondly they must allow people to have duel citizenship and all people in USA,Europe , RSA and everywhere should come back to malawi. Its pity Malawi has been ruled by most educated presidents but they all failed. Please put a Form 4 president.

 42. Maybe mlomwe mzangau but until know am still craying ! How can i forget Dada James mnyondo ” NASAF President ” Why God always you take most Important pple? You left this Idiots mmmmm Dada mnyondo ………!

  1. But you can’t compare to that man . That one my Brother aaaaaa how can i explain to u my dear ?in short He was really interigent and lnnocent Man for this country not this scopions

 43. Let dem politicians amass to themselves as much wealth as they can whilst 90% of Malawians r living below poverty line so they can really feel themselves gods here on earth

  1. Estar usiye kunchula mulungu pa zoputsadzo muope ndi kumupatsa ulemu . iweyo sumamuziwa chakwera ineyo ndinali asstant wake munthu uyu mudzamuona

  1. They have asked of which one would you vote for brother Ackson Kalaile Banda ,you can’t vote for three,politically that would be a spoiled vote, I feel sorry for the pp.by your choice, but for me,it’s none of the above, because they are all crooks

  2. Amos Chisisi they have numbered the candidates from 1 to 4, so my favorite is on number 3,before you comment boss please understand the dynamics. I have chosen number 3 not all the three but still if you can check properly there are more than 3 candidates so can you justify your argument?

 44. I stopped long go participating in elections because incomplete anticipation. So unless you education me the need why I should cast a vote again in the tripartite elections come 2019. Look how politicians have plundered this country socially and economically. The socioeconomic institutions of Malawi right now promotes unruly practices, constitutional bias, and socioeconomic exclusion of other social groups in society through corrupt leadership that is not accountable to its people and traparent in its dealings.

  1. Chris Mhone that belief is a lie. How sure are you that their votes would have put the right candidate in power? Even if we all voted still we will have different choices.

  2. #Matewere do we have to insult those who hold different views to ours ? Not at all, because everyone has a right to hold an opinion and freedom to express it. In addition to that, issues of grammar and politics, I agree with you that I need a lot of education, precisely, civic education, because learning is an everyday process until you die. So learn to be humble because I might be far better than you thinks I am. The problem with my post however is not real grammar but typing aid prompting words in and left unchecked. So no worry, you got my point if you were able to comment with an insult.

  3. I’m supporting ur point Mr Steve Mark, even me I don’t see the reason for squandering my time go for voting. When we vote we expect to see the change. So I dont see a better person among those candidates.

  4. its not an insult anyway some of us try to make a point in an aggressive way and the fact that you refrain from voting maybe you add up to a lot people that deny us the change we might as well be lacking the votes to have the change thru unparticipation of more people like you,always vote despite all that some of those things aint forever and how is God going to grant us a true leader when we dnt even vote coz tge only way to end that corruption is only when God intervenes trust me boycotts only makes us weaker and the corrupt powerful

  5. #Matewere, do not forget the fact that the constitution of the land grants freedom of expression and freedom of association to every citizen of Malawi. Therefore it is your choice in that freedom of association to participate or not. The law does not penalise anybody if you do not participate. Again, you can put your aggressive behaviour aside, in debate we need factual arguments not aggression. So if you have a point to make against someone just state your facts not portraying your dull mind through aggression. It simply shows that your intelligence quotient is very low.

 45. aaaa my foot palibe uyo ndikamuvotere apa..,muyikepo bushiri bola,koma zose izi ndinkhumba zachabe chabe,,kaya azawina ndichakwerayo sazasithabe zinthu bliv me,kaya ndi pitalayo palibe zot znthu zngadzasithe mmalawi muno.mavuto ose awa alipowa ndiagonagona samasinthika ndipo sazasinthikaso,anthuwa bola mwawayika pampando bas koma zot znthu zngadzasithe i dout,,pitala,chakwera ndi azakowo kagwelen uko.mukandilemba ntchito chaka chamawa ndiye kt ndizakuvotera iwe pitala koma ngat sundilemba ku educationiko vote yanga suzayiona.

  1. Mukunena Zoona Zokhazokha Mungoganiza Milandu Ya Cashgate Mpaka Pano Siziwika Momwe Idathera Moti Atabwera Chakwera Zonse Zikhala Momwemo Komanso Ife Amalawi Tikuyenera Kudziwa Kuti Ndale Ndi Bodza Basi Zonse Zomwe Amalonjeza Pa Campaign Amangofuna Zofuna Zawo Zitheke Basi

 46. No need to vote. we have never had fair results in Malawi. pple force themself into office. it was only in 1994 wn we hd true reflection of the pples wish.

  1. This is why 50+1 is causing headaches and running tummies. The system offers very little chances to force oneself into office. It also eliminates nepotism and tribalism to a certain extent.

  1. Timaganizo takotu timeneti osati maganizo ya aMalawi tonse ayi, pita ku salima udzikakamba za peter muthalika ukaone ngati sadzakukwapulako makofi kumeneko

  1. Iweyotu ukuti kumangochi koma kuno ku nsanje bwela ndiye udzikakamba za Udf kapena Dpp uwone ngati sakuthethetsa makofi

 47. NOTICE: short comments plz.
  From Chairman of reading comments:
  From the board of reading comments we would like to emphasis that only short comments will be considered as comments. According to counting of every hour.
  Chakwera: 65%
  Muthalika :30%
  Others sharing: 5%.
  We will keep you update.
  Regards:
  Chairman

  1. zopusa basi chakwera sangawine wamva mbuzi iwe …..boma limalamula kawiri basi nde zakozo usiye wamva ungozitayisa nthawi

 48. one ngati mfumu ndamema anthu anga onse ndipo onse awonetsa chidwi chhozavotera wathuwathu CCCHHHAAKKWWEERRAA osati avumbwe enawa chifukwa atilanga ndipo takhawulatu
  .

 49. Palibe Ali ndi maganizo otukura Malawi apa.onsewa olo atati atenge boma, afuna kaye kuzilemelesa.Bola monarchy system of Government

  1. Nanenso Ndikugwirizana Nazo Mungoganiza Kuno Ku Lilongwe City Centre Mutha Kudabwa Mutawona Kuti Kodi Kuli Mp Chifukwa Ife Kuno Misewu Yathu Ndi Yokumbika Kumbika Zafikapa Bola Osavota. Capital City Kumaoneka Ngati Bwinja Komanso Mutapita Town Ya Lilongwe Kumavutika Mayendedwe Timatenga Maola Kuti Tikafike Misewu Ndi Yomwe Ija. Mavuto Alipobe Kumalawi. Palibe Mtsogoleri Othetsa Mavuto.

  2. Iweyo ukukamba zimenezi chifukwa chakuti amene umamuyembekezela kuti angasinthe zinthu ndi uyu wakanikayu koma dziwa kuti maso mphenya ya anthu amakhala osiyana siyana Zimbabwe adangolowa Mnangagwa pa mpando wa utsogoleri kwa masiku ochepa chabe zinthu zasinthilatu ku zimbabwe panopa zayamba kuyenda bwino tsopano ndiye iweyo ukanena kuti palibe angasinthe zinthu ndiye kuti azungu amati fabricating your self

 50. amalawi sazathekaso and ndinu anthu osayamika 1.peter sagwila ntchito ku escom and nthawi ya dpp ino muyende muone kuti wapanga zinthu zingati nde wina nkumati chakwera I can’t even bother voting mcp yankhaza

  1. Iweyo ndiwe kape of the year kodi galimoto amayendetsa anthu angati? Nanga dziko? Ndiye mdziko zinthu ngatizasokonekela monga momwe zililimu mesa vuto amakhala mtsogoleri? Iweyo sudave ku zimbabwe kuti nugabe adaononga chuma chadzikolo?

  1. Amwene Kuba Sikudzatha. Nsomba Ndi Nsomba Itakhala Pamadzi Angakhale Kuipititsa Pamtunda Singasinthe Chimene Ndi Kutanthauza Kuti Anthufe Tili Mmavuto Aakulu Angakhale Azungu Amangoseka Chiyambireni Multiparty 1964/2017 palibe chomwe chikusintha kunena pano zinthu zakwera kwambiri ndiye ndichimodzimodzi aakulu angakhale atabwera chakwera zinthu sizingasinthe,amangotimata phula m’maso anthu aja amadziwana kaya mutapita ku ndende ambiri ndi osauka simukapeza wa suit bola kungokhala osavota basi.

 51. akuluakulu apapa musamatiyese nzelu nazo izi 2019 its not far, koma DPP kukhuti basi~~~~~~~~~~~∆∆∆∆∆∆∆∆∆

  1. Aaah ife mtima wa Idi Amin tilibe akulu atipanga chipongwe asilikali aku Malawi monga president wakwatu sanayembekeze kuti asilikali ake amupanga chipongwe kkkkk

  2. kkkkk!ndiye anamuyenda ya panxi dear’amvekele;tikufuna kulimbana ndi akambembele akubela boma osadziwa kt mpeni waloza iye 🙂

  1. Benja u have not heard about this young lady who has the ambition to take you and me to new political heights a journalist by profession based in South Africa was interviewed here on our local TVs once or twice

 52. 1. I alrways a supporter of DPP.zinthu kumalawi kuno tikuziononga tokha eni ake.ndiomwewa utsutsawa omwe amapangisa kuti chipani chomwe chikulamula chisaonekele ntchito zawo.amalawi tiyeni tiseguke maso nkupeza njira zothanirana ndi mavutowa tisamangokangana nkumaloza zofooka za presdent.

  1. Monga kulephera kufufuza za ndalama zokwana K577billion akulepheretsa ndiotsutsa eti
   Kutenga ndalama mmakhonsolo mnjira ya blue night kukagwiritsa ntchito za chipani cha dpp chonsecho anthu tikusowa zinthu zambiri mmidzimu, ndiye anapanitsa ndi otsutsa, eti
   Mavuto amagetsi ayenera kupanga bill yowonjeza mphamvu zs magetsi akanapanga zimenezi mwachangu ndi otsutsa, eti

  1. Mukuchedwa ndinu man mu2 otembeleledwa chakwera once he z de president of dis countly am out of dis countly mukhale ndi dyabulosi wanuyo muone ngat zthu zizasithe it will b wesy dan now beliv me u

  2. No let the current president contineu things will change coz si chakwera joice banda kapena atupele koma if we give a big support to peter beliv me zithu zizakhala beta stop figure pointn lets work together as 1 nation bax sizikufunikaxo bambo anga alowe pa mpando mayaz bro… imva loud n clear

 53. Ndisanalembe yemwe ndikhoza kumuvotela,ndinayenda munsika Wa sungwi Ku 25.kuwafunsa maganizo….aliyense akungoti CHAKWELA!!!!!!!!! Mwana ,wankulu. …tikuti aliyense

 54. Ine number 4, mkazi wangaso akuti number 4, agogo nawoso akuti number 4, cousin wanga number 4. Mwana wanga woyamba number 4. Girlfriend wake akutiso number 4 dpp izipsa mtima

 55. Ine Szavota Ndato Agaluwa Ayambla Kutpusisa Lija Ndikale Munawona Chimdan Chochtka Mukapen Mokha Ikangotha Kapen Aytanzane Azibela Limozi Ine Vot Yanga Simuywona Mwava?

  1. mwaimva molakwika postiyi.opinion poll kwa anthu amene amatsatira tsambali sikuti ndi zenizeni.ngati simukufuna kuvota patsambali kungokhala

  2. Kufatsa apapa kumanamizana? Nanga popeza ineyo apapa ndavotela chakwela 2019 so ndichimodzimodzi palibeso kusintha ayi black out salibwino dziko litukuka bwanji? Kuba ndalama zaboma dziko lipita chitsogolo motani? Mcp 2019 boma basi

  3. We Have Been Hearing Of Afrobarometer Researches,thougha Av Never Voted Or Participated In An Anyway,i Prove Them Right.Theory Of An “Ice Burge”

  4. Zimandidabwitsa kwambili anthu akamati pali zinthu zosatheka.anthu amene amati palibe munthu amene angathetse mabvuto ena ake akulu ,iwowo amadzatinga opanda nzeru?munthu anabadwa kuti aziyimira pa yekha ,ndichilichonse chosatheka achipange kuti chitheke.see Zimbabwe now.

  1. Mavuto Sazatha Amwene Angakhale Atabwera Chakwera Bola Kungokhala Basi,chifukwa Chakwera Adachoka Kwa Mulungu Kukonda Za Mdziko.Komanso Ngati Wasiya Kolona Kukonda Za Mdziko Mulungu Samakhalapo. Chachikulu Kumangopemphera Basi Osalimbana Ndi Za Mdziko Nzopweteketsa Mutu,, Atsogoleri Amakhumudwitsa Amwene

  1. zaziii ngati atsogoleli anthu are like that’s palibe phindu munati bingu wamwalila talemela coz Joyce watenga boma izoo kulila chimodzimodzi palibe phindu mungolimbana zazii .chakwela wamanga nyumba ya 650million ndalama wazitenga kuti anthu akuba awa ine kuvota njeee zilibe phindu

Comments are closed.