Wanderers rain goals on Moyale

Advertisement
Be Forward Wanderers vs Silver Strikers

Be Forward Wanderers put five goals past Moyale Barracks to leapfrog Silver Strikers into the top spot of the Super League.

The Nomads beat the soldiers 5-1 in a game that was played on Wednesday afternoon at Balaka Stadium.

Moyale Barracks
Be Forward Wanderers put six goals past Moyale Barracks. (Library image)

So dominant were the Lali Lubani Boys that they scored five goals in the last 45 minutes of the game.

Isaac Kaliati, Jafali Chande, Joseph Kamwendo and Peter Wadabwa (2) were on target to punish the Kaning’ina Soldiers while Khuda Myaba replied with a goal for the away side.

The win means Wanderers are leading the league with 31 points from 13 games, two points over second placed Silver

The result is also a warning to Moyale as the two teams will meet again in 10 days in the Carlsberg Cup semifinals.

In another Super League match on Wednesday, Nelson Kangunje’s lone goal gave Nyasa Big Bullets three points as they struggled to beat Zomba based soldiers Red Lions.

Bullets now have 24 points from 13 games and are remaining with two games to wind up the first round.

Bullets and Red Lions will meet again next week at Bingu National Stadium in the semifinals of the Carlsberg cup semi-finals.

 

 

 

 

 

Advertisement

78 Comments

 1. Vuto la iwe neba ndilimenelo kulalata usaiwale kuti carsbeg ukubwera pa mzuzu stadium Charlse Kamanga Ndidolo Analowesera Dara Team Yosalongosoka Kuti iwe neba uziti umaitha koma iwe phee uzakumana nazo kuno

 2. ife tawina kaya ndi 5 kaya 6 tawinabe, Neba kaya suvomera kaya Madrid yachita chani kaya chani koma Noma yapha Moyale. Neba team iji ikukupweteka? Please Continue good work ma boys mpaka Satan amve kuwawa…. Noma inu Aaaa yafika pa utsiru ndi mpira.

 3. Bedroom journalism, the reporter has finally fixed his errors after posting fake news.malawi24 grow up

 4. Ine ndimanena kuti Noma/B4ward akakupatsani kumazika zala pansi ask neba timatulutsa kanfuno ife kupumila nkwapa asitikali mipala ngweee!!! koma 4-0.

 5. Koma chimakhala chili chiyani chithunzi mumayika cha game ina yosiyana ndi yomwe mukukamba… Tinene kuti mumangopatsidwa zotsatirazoo kapena mulibe ma camera kkkkkkk

 6. Malawi24 the whole news is rubbish…vuto lolembera news m’nyumba m’malo mopita Ku field.Game sinali Ku Mzuzu kma Ku Balaka,Zigoli zinali 5osati 6, Isaac kaliati,jaffalie chande,Josephy kamwendo and Peter Wadabwa 2 goals.China Noma sinapange leapfrog Silver but rather Noma returned to the top.It was silver strikers that leapfrogged wanderers eeeee …journalism!!

  1. Ngati smuzitsata ndibwino kungokhala chete osacommenta wamva madalitso…ine ndikunenane ndine sapota wa wanderers ndie iwe za 6 wazitenga kuti..ukunama ndie aise,Chester sanachinye chigoli vuto lake inu mumamvera pa radio kma ine i have official info from wanderers facebook page, website kmanso ma watssap page anoma ambirimbiri aise.Chimene ndingakukuuze upange verify wamva aise udziwe chilungamo.

 7. Madrid 5-1 Barcelona a wanderers nonse munziwe kuti ma team akulu akulunso amachinyana zigoli zambiri oyamba siinu padziko pano

  1. Inu mukuzitenga ngati oyamba inuyo Kodi? Kkkkkk Super sport untd idamenya Orlando pirates 6-1 doesn’t mean SSU ndiyaikulu kuposa pirates njeeeee

  2. Samazitsata awa akamvera mpira ndi wa pa Malawi basi that’s why amaona ngati wanderers ndi team yolongosoka chonsecho ili ndi 5 league titles since 1962 ????

  3. Komanso Alick Kazembe mutu wake sukugwila zoona ukafananize game ya barcelona ndi ya noma.. Game ya barcelona ndi madrid ndi magame tu awiri amenewo pomwe noma yachinya zigoli zonsezo mu game imodzi…. Kisokoneza zinthu neba.. Kkkk

  4. Mwaona zachilendo kutibulako team ngati Moyale zigoli zambiri ndiye mukudzitama kuti ndi team yayikulu. Kodi Blantyre United muja idachinyanya inu Anoma 6-2 tinene kuti Blantyre United is bigger than Noma or else Mzuni is bigger than Noma poti idakuumbudzani 4-2?

  5. Ngati pali big achievement ya Wanderers mumbiri yawo nde ndikugonjesa BULLETS ndi MOYALE basi pomwe anzawo a BULLETS amawelengela zikho ???

  6. Kani zamudinya kwambiri nebayu eti? Ndimaona ngati musangalala kuti takuphelani chirombo chomwe chinakumezani first game ku mzuzu? Koma chimpinimomwe fc sazathekadi akuluakulu. Noma pa 1 basi, 2 kupindika hahahaha!

  7. Inno Moyale ikuchita kubweza takhala tikuimbuza since 2009 mma cup komanso mu league.BULLETS imagwira ntchito yokha pa easy Neba wangosunga bag siyako imeneyo

  1. 11 years without being a champion is what you mean that Noma is big club? Beating Moyale cannot change the subject that Noma is still a pikinin team chifukwa team yaikulu ili ndi league titles ambiri. Inu ukulu wanu ndi WOKODZA OMWEWU BASI. MOTI MUKAYEREKEZA UPITA KU MOZAMBIQU MUKABWERA EA UYO UYO UYO NGATI KHALIDWE LOKODZERI MOKAONETSE KWA ENIKO.

 8. Damn you moyale, i had hope in you. Anyway big up my boys Big Bullets, whether you struggled to beat Red lions or not but at the end of the day, you brought home most needed points, 3 points that is. push forward guys, my christmass gift depends on you.

Comments are closed.