
Police in Dedza have arrested a 32-year-old Mozambican man for attempting to register as a Malawian in the ongoing national identity registration exercise.
Dowa police spokesperson sub inspector Edward Kabango has identified the man as
Patrick Machaka.
According to Kabango, the police got a tip that the suspect is not a Malawian although he managed to produce two Malawi Electoral Commission (MEC) identity cards for 2008 and 2013.
“Machaka went to Umbwi registration centre and lied that he comes from Kapalamula village in the area of Traditional Authority Kachere in the district,” Kabango said.
He has since been charged with furnishing false information for the purpose of obtaining registration which is contrary to section 43 of the National Registration Bureau Act and attracts a maximum sentence of 10 years.
Meanwhile, the police are advising chiefs to refrain from registering foreigners because it is an offence.
Malawi is conducting mass registration exercise for citizens to have an identity cards. The exercise is currently taking place in the central region of the country.
According to NRB, over a million people have been registered since the exercise began.
Umenewo Ndiye Umbuli Wa Amalawi Mmalo Mongomuuza Kuti Suyenera Id Bas Kumanga Ifenso Ndi Amalawi Koma Kuno Ku Mocambique Tikukhalanso Mwa Ufulu Koma Inu Mulimbana Munthu Osalakwa Pamene Zigawenga Zikukalamba Koko Zikuba Osazimanga Mbuzi Za Anthu Anthuwo Aumphawi Adaliraso Ku Mocambique Koko Maganyu
MALUME EVEN KUNO AMAKUMANGA
Amalume Ineyo Nditapita Kukalembesa Masedura Aunzika Anapeza Kuti Sindine Wakuno Anandifusa Zaka Zomwe Ndakhala Kuno Ku Mocambique Anapeza Sizikwana Kukhala Nzika Ndipo Ndinabwelera Panopa Ndikukhala Ngati Mulendo Nziko Koma Zaka Zikakwana Ndizabwelerakonso Anandimanga? Amalawi Amakaka Pa Zinthu Zochepa Okupha Arubin Ali Koko Okuba Ndalama Za Boma Ali Koko Asatanic Akuchitisa Ngozi Anthu Kumafa Mpaka Ena Kumaulura Osawamanga Amanga Pa Nkhani Za Zii! Okuba Akumwera Limozi koma Akuziwa Zachamba Bas
Mbava imeneyo ifinyeni.
Kumeneko ndiye kupusa munthu wa dziko lina apeze ID ya dziko lanthu? Kusayenda eti? Pitani ku mozambique komweko mukapangitse ID yakumeneko muone ngati sakakuphani. Mumaliphweketseranji dziko lanthu la Malawi kumangosutsa ndi zabwino zomwe!!!!!!? Pitani ku S A mukaone mmene ID imamusowera munthu wa dziko lina. Amangidwe basi walakwitsa. Iye alibe dziko lake?
Mbava ett!
ID gate
kkkkk.typical African behaviour!!!ID for what in a foreign land?cage him PLIZ
Kkkkk kufuna kukhala mmalawi
KOma ndithu iyeyo amasilira kuti akhale mmalawi kkkkk so foolish
They need to b much careful on the boarder sides especially in Dedza n Ntcheu…. Mulemba ambiri xoz ndi school n hospitals plus kudzaba kuno….
too late many foreigners including Burundians have already registered
Wangochitika tsoka ameneyo. Amnzake ambiri zidatheka
Well done Dedza Police, musamusiye choncho azolowera…
well done Malawi Police service, Yambaninso kuika ma Roadblock monga momwe amachitira Ku Joweni. mukatelo mugwira Ambiri. alimo ndithu M’Malawi muno angokhala ngati kwawo.
Blessed country Mozambique with resources. I proud of that even if can insult me, Eu sou Moçambicana
Tawamangeni y having a Malawian ID while he belongs 2 Mozambique? Think about ur country (;(a Malawi) u come 2 Zambia at ndikufuna nditengenawo NRC the law will visit u!!
Anthu ena opanda nzeru akudzuzula koma chonsecho akudziwa kuti munthuyu si nzika ya dziko lamalawi mumati amupatse ID anthu ena inu ndi mbuzi ndithu mene amapangila nkhanza tikamadutsa nziko mwao anthu amenewa mukana dziwa simukana nena kungoti iwe ukudzudzula iwe unangobadwa sunayendepo
Dzowonadi! m’bale zimene ziku bakira Anthu oyipawa ndi mbuzi zongobadwira kumudzi ndikumakulira komweko moti sizinayendepo zikati zayenda, ndiye kuti zapita ku ma dambo awo! ko tipula kuti adzaleko mbeu.
Agule awa,zinyawu
Just leave him, we all Africans,even some Malawians try harder to get other peoples national ID
where did see that people geting id in that way ? they must be reason for you to get id for another country not by lying that you are a malawian then gorvernent can give ID
wangokulila mu malawi momwemo sunayendepo iwe. uzaziona
I hv been all Africa it happens baba, even now a lot ppl will get those ID’s some will just pay money, so you don’t knw this MW
kalanditseni nyanja zatsogolo.Police yosowa zochita.Osamanga acashgate za ziii….
aphedwe ameneyo kapena akakhale kundende moyo wake onse coz mulandu umenewo ndiwaukulu
Kwawo ndiwovuta,akakhala,ndi I D ndiye kuti mwamupas,mwawi amakana,kutipasa magezi,ife!!!! Amanganiso,athu amene,akukhuzidwa kwa kumwalila kwa athu ambili,zulo
y arest him while cashgate convicts r stil wondaring up & down,hau much iz ID & hau much iz cashgate compare ur self , za ziii bas apolice osowa zochita koma akat tear gas
Ndinu aku mocambique
Kkkkkkkk,akudabwisaditu mkulu amenei.
u thnk id is a small thng?
Kkkkkkkk koma inunso muli ndizifukwa zonamatu
inuso ndiachitsilu aku Mozambique kod???
Do you think to its a small case? In mocambique kumakhala kovuta kuti munthu wakumalawi angodutsa chabe ndye i
Stupid man so u want him to be a Malawian
But Don’t Let This Distract You From The Fact That You Are Waist Of Sperm
Sanayendepo mkomwe,komaso sadziwa kutathauza kwa id a gibo,kkkkk
Pompa pa Zobue kkkkk Mozambique ndilibe nalo mau
kkkkkkkk Koma ngati mwathawira nkhondo kwanthu kuno! ndiye mumafuna mupeze nawo chitupa cha Udzikachi, ndiyetu pepani yakulakwani! back to maputo ife takukanani kkkkkkk.
Yayambikakonso nkhondo tu paja ndiye azikafuna kobisala. Anthu achipongwe, zimandiwawatu m’mene mumatizunzira munsewu tikamadusa
Mtchanganitu uyu
amangidwe kumene iwe ukukamba za cash gate umenewo ndiwo uchitsilu
cash gate ndi ma id zikugwilizana mwana wa mbuzi
IIIII awaso
umbuli ndi matenda sure,,,zugwirizana?
Akufuna kuti akamakapha anthu adazi azikati ndi amalawi omwe akupanga ziwembu
u should av gone 2 zambia its easy 2 get NRC here
thats good development.. these people are depleting our resources.. in tcheu hospitals are filled with Mozambicans .don’t forget we have free hospitals n other services meant for poor Malawians.
Malawi akuwonelera bwanji
MABLUNDI ALIMBWEE KUNOWA
Yah good work police
Kunoti Mun2yo Amali3ra Dziko La2li
moti mumange chaponda mukulimbana ndi zazi ngat iziiiiiiii kunodi ku malawi eti chili chonse amachitenga ngat mulandu
Iwenso uzipita kwanu ku mozambique kwa anthu ankhondo ndi osaphunzira kuja.
Mhu tiyeni naye nanga kwao kwatani? Its an offence.
why malawi is like this taking small cases seriously,you take ID case this serious untie Tio and his so so so u know the story,yet cash gate convicts are wandering the streets.ddnt the government have enough proof to nail them down and if so how many years on remand did you give them while you were waiting to gather the proof?
you just dont know what u talking. … have u ever travelled passing Mozambique? u really dont know how these people treat people just passing there country. or maybe u really dont know the meaning of id? U piece of #kak
Why mozambique always bringingproblems to Malawi?
Kodi mukuti tiziyenda ndi ma ID et? Zinayambika liti zimenezi
Kodi mukuti tiziyenda ndi ma ID et? Zinayambika liti zimenezi
Hahaha!!zochepa izi zomwezi mpaka 10 years,nanga aja oba ma billion. a cashgate aka muwatani poti azunza mitundu ya Malawi
Aaaah ntayeni ndiye kuti amalikonda dziko lamalawi
May be he is returning to his origin.
Ife kwathu zama ID kulibe izizi zayambaso liti
Waona kut kwao sikuli bwino
Analibe dola nde fact yake..
Kunena zoona amafunadi dola kaya ndiwe wakumalawi kaya ndiwe wakunja dola basi pa border
Even ulibe passport ngati uli ndi dola zose ziyenda bwino
Zomwezi paka zingwe kkkkk ndiye ma #Burundi fe atimangaso Malawi tamukonda basi tisiyeni
Is it in Dowa or Dedza?