Mutharika condoles Muluzi over daughter’s death

Advertisement
Peter Mutharika

President Peter Mutharika has sent condolences to former President Bakili Muluzi over the death of his daughter Esmie Muluzi Malisita who was struck by lightning in Blantyre.

Malisita was struck by lightning together with her friend Hazel Busile at the former’s farm in Mpemba.

Writing on his official Facebook page, Mutharika described late Malisita as a humble and considerate woman.

Peter Mutharika
Peter Mutharika condoles Bakili Muluzi.

“Those of us who interacted with the deceased will remember her as a polite and well-mannered religious woman who treated everyone with love and consideration.

“Our condolences to the deceased’s father former President Dr Bakili Muluzi, Honorable Atupele Muluzi and the entire family; the Malisitas and friends for the shocking loss”

“Reports say Mrs Malisita was in the company of her friend Hazel Busile who has also died in the same accident. So to the Busile family and friends, we also offer our condolences,” Mutharika wrote.

Meanwhile the body of late Malisita will be laid to rest on Friday.

According to reports, the Muluzi family is waiting for Malisita’s mother Annie Muluzi who is in the United States to come so that she should attend the burial.

Advertisement

193 Comments

 1. Pepani banja lofedwa makamaka ili losaukali Mulungu oziwa kutothoza akutothozeni ifa simathelo amoyo koma ndi chiyambi chamoyo wina wasopano ombuye wanga akhululukileni machimo awo omwe anachimwa pano paziko ali moyo kaloweseni kumtendele amen

 2. Moto umapita kwasala tchire, tiyeni tizimva chiso azathu zikawagwela. palibe wambeu aliyense ndi go komweko. ine ndili ndi chisoni chifukwa cha ngozizi.

 3. Tikuvutika chifukwa cha anthu awirinu…Zija mukudziwana zija zikutiyikitsa mavuto.Kazipepesanani odala azathu oyenderana muzovuta pamene ku mariro a Wame ndi Chikwamba phazi simudapondeko.

 4. Zachisoni…..komanso thawi zina amakhala chauta kubwezela…..ukamabela ina zima koma koma iweyo ukabeledwa zimawawa…iye wapha watha ana…..ayeni like matafale always RIP. kalonga stambuli kumangochi, lero zagwela kwaiyeyo….zikuwawa how much more kwamunthu ophedwa ndi munthu oti ukumudziwa….nanga ndatukwana?

 5. President of Republic of Malawi, kumusokhano wachipani kuvala suit yakuda kupita kumaliro kuvala Grey ndiye tiziti ma advisor anu amaitha tchithu? Bwana or America yanu uuuuuuuuuu yapa yapara

  1. Bakili ndi msilamu ndipo kuchisilamu chisoni chimakhala mu mtima osati pa chovara,pepani ngati ndalakwitsa kuyankhako

 6. Pepani Achair, Umenewo Timati Umunthu Kuziwa Zovuta Ndare Pa Mbuyo Mutharika Ndiwanzelu.Chakwera Akutanganidwa Ndizongokangana Ndi Mutharika Osaziwa Zamariro Kkkkkk.Mizimu Ya Anthu Omwarirawa Ikautse Ndi Ntendere.

 7. Very much disappointed. Very shocked.We’ve lost a very dedicated Mother in our Chonde VG.May Her Soul Rest in Peace.

 8. Anthu angopepetsa mbali ya a Muluzi basi why??? Ine ndikukupepesanso ku banja la a Bussily potaya mwana wawo Hezel pangoziyi ndikuti pepani anamalira nonse

 9. kod chipepesochi chikukomera 1 side y mesa winayoso ndimunthuso just bcoz fukwa choti enawa ngotchuka kapena ine ndingoti mulungu mwini zose alanfile mizimu yawo anthu amenewa ndipo iwutse muntendele

 10. Pakumvesedwa kwanga ndimaona ngati gozi ya chiphaliwali pachizungu lightening kuti yapha anthu awiri.koma chiyambireni ndikungokumva nkhani ya omwalira modzi yekha.kapena umbuliwu chizungu sindimamva bwino bwino eti? Ndi umbulili wangawu ngatidi ndi zowona kuti amwalirawo ndi anthu awiri akubanja losachukalo landirani kupepesa kwanga. musadandaule limenero ndiye dziko lapansi lomakondera koma Olemera

  1. munakankhala kuti munapanga course ya Journalism bwenzi mukumvetsa.ineyi ndi Newsworthy yomwe timaitcha prominence.EXAMPLE;tiyese kt president peter wachita ngozi and munthuwinanso wachitangozi tsikulimodzi,nkhani yomwe ma media houses akhalenayo interested ndxya presidentyo kusiyana ndx munthu wamba…Ndiye pazamwana wa muluziyo palibe zokondela.mwamva guys?

 11. Hahahaha. … am just happy that something like this has happened… had it been that it’s a poor man’s daughter nothing like this would have happened. pipo die. what’s new here? mwinanso she wqs sacrificing human blood… she has never brought anything. a daughter of a thief. .. someone is feeling sorry for him. he used our money to educate her useless daughter who has been opening legs to different men to nackanise her… she is dead…. she controbuted nothing to the development of this country. …. am done ……… but ndikutha kuona some pipo pretending to be holy on my comment .. if u try to something then u r just showing the world how stupid u r

  1. Which of your money he used to educate esmie,by the way it seems you are ignorant n you dnt even know of who esmie was,infact esme completed her education even before muluzi became apresident,it seems again n again that,you got aproblem on your own… l guese you are just another useles man…

  2. mulungu akukhululukile satana ndamene akukupangisa kulankhula mau apanda pake malemu amene ukuwanenawo anabadwa 1969 ndie zaskool zimene ukunenazo zikusephana kwambili

  3. man musamayese pa,,,,,,,,,iwe…..ufiti wa bambwako uti nyasenawo za shamba eti? zoona iweyo basi kufasa kumakamba manyi ngat amenewa bwanj iweyo zapa chi phwisi ayi ngat mwasowa zokamba kwanukonko muzikambilana manyi anuwo ,kwanu sikunafepo munthu? iwe fosha eti?® namachende.galuiwe

 12. Big man showing as gd example to condo frnd during in troubles like this while Chakwela are busy to insult big man on ZBS shame!.

  1. zoonadi malo mokhudzidwa ndi imfa yamwana wa former president ali busy kutukwana apm,mcp sikhudzidwa ndi imfa adazolowera kupha anthu.

  2. Out of topic .olo ndi half sizikugwilizana.kodi imfa ya mwana wamuluzi ndi tsiku lomwe chakwera ankayankhula ndi limodzi??

  3. Kuchuluka mbuli ndi tsoka la aMalawi.
   achavututsitsa ndi umbuli wosadzindikira thandauzo lake la ndale kuti nchiani?
   Awa ndi maliro, osati UDF, DPP, PP ndi MCP ayi
   Zagwirana pati ndi ndale?
   Mayi omwalirawa analinso andale ngati Bambo wao?
   Siyirani eni ache ndale zandale, president akusonyeza utsogokeri was anthu onse kuti ndi Tate wao, osati wa akumwera oka apakati okha ndi kumpoto okha ndi mysogoleri was a Malawi.
   Opusa ndi amene amayambitsa mkangano, mwaonekera zitsiru zachabechabe inu.

  4. Ziko la Malawi siripita pa sogolo mwachuluka mbuli. Tere pali nkhani yoti nkuyamikira ena ndi ku nyoza ena apa. Mukanakhala oganiza mwa umunthu bwezi mukutumiza mauthenga achipepeso kwa Muluzi.

  5. Wayamba liti kupita ku maliro psuta uyu?_Chakwera ndi manyaka mukuwayamikirawa ndi ndani amapita ku maliro? Kwa Gwanda analipo? kwa chair wa MEC analipo? Apa sipoonetsera umbuli wanu. Clueless people.

  6. Akachoka uyu olowa ndi atupele muluzi munya muona MCP Bangalore ndani kuti ibwerere mboma ikamange ma dam ang’ona ndi ndende za uzudzu kawiri MAPWALA ANU

 13. I also send my condolence to Mr chair Dr bakili mulusi for his daughters sudden death may her soul rest in peace

Comments are closed.