BREAKING NEWS: Malawi Cashgate convict Treza Senzani dead!

Advertisement
Treza Namathanga Senzani
Treza Namathanga Senzani
Treza Namathanga Senzani has died.

Former Principal Secretary in the Ministry of Tourism, Treza Namathanga Senzani has died, Malawi24 has learnt.

She died today at Mwaiwathu Hospital in Lilongwe, according to reports.

Family members are yet to make a statement on this issue.

She was jailed in 2014 sentenced to three years and nine months imprisonment on offences of money laundering and theft respectively.

She was however let out of prison in October this year having portrayed  a ‘good character’ when she was behind the bars. Her jail term was slated to end October 6, 2017.

She had  pleaded guilty to stealing around $150,000 (63 million kwacha) from state coffers, part of a broader swindle worth at least $30 million and was convicted on her own guilty plea.

She became the first convict sentenced out of the more than 50 people arrested in connection with the fracas.

The scandal saw donors withdrawing their support to Malawi amid similar revelations – this time led by civil servants where billions of kwachas went uncounted for in a scandal better known as Cashgate.

Senzani was apprehended in 2013 having issued two Cheques to her own company, which according to police never had the provision of goods or services to the government.

MORE TO COME!

Advertisement

358 Comments

 1. We left everything we are fighting for here on earth wen we are dead, indeed mlaliki is right zonse nzachabe chabe.let’s not be greedy muzazisiyabe. Koma poti mwapita monga aja akhala akumwalira chifukwa chosowa mankhala nzipatala komanso zina zofunikira pa moyo wa munthu kamba koti ena anazikundikira okha. …. RIP

 2. Maliro osavuta kulira….i hope achibale anabisako dollazo…za cashgate ziyendetse mwambo…….Mix Bakili Muluzi….eeeh!!! Mwambo osavuta ngati umenewu…..sindinawuoneko

 3. Mphotho ya uchimo ndi imfa basi, anthu ena anamwalira chifukwa chosowa mankhwala kuchipatala iye akumanga mansion yake using ndalama za Boma? she deserved that!!

 4. Its only God the Almighty who can judge. Remember death is a part of journey every heart will go through. Its rather better to remain quiet if we hv no fact than to talk shit on public spaces. Shame!

 5. Malawi nation is facing numerous challenges bcz of the late triza namathanga & her friends lyk lutepo,anyway may her soul rest in peace

 6. Let her go. Mulungu akuchotsa wezi wezi anthu omwe anaba misonkho ya anthu osauka. Achainake akumachita kusowa mankhwala zipatalamu. Mbendera, kudontoni, lero ndiiyu. Wages of sin

 7. I’m very happy for the money you stole killed a lot of people in the country medical supply shortages go to hell

 8. Imfa ndichinthu chimene aliyense amaenela kumva chisoni zinachitika pakati pathu, tale ndipezelepo Mwai kuti A Malawi anzanga tatiyeni tiziitenga imfa ngati choopsa ikachitika pakati pa Abale anthu komanso ngakhale amene asali abale anthu sibwino kupezelapo Mwai kumanyoza munthu coz wafa & mukumudziwa kuti ntchito zake zinali zoipa Oweluza olungama ndi MULUNGU Yekha, aliyense akaweluzidwa ndi ntchito zomwe wachoka nazo pano pansi tisachiyense choseweletsa imfa ikachitika

 9. …most of us here are taking the position of God by playing judge over her. Read the scriptures and let them guide u. Amen.

 10. @mwajah,ku bona koti unaba umayenera kubwenza zomwe unabazo.maiwa nanga adabweza chuma chadziko la malawi?ada bonera pakamwa osati mumtima.ku bona ndi chithu chamtengo wapatali.

 11. iiiiii zirichonchonso? Tsono muja amati ulemelero ulikumwamba nde zikakhala bwanji poti munalemereratu pansi pano ndi misonkho ya ma lebala?

 12. Ndikuuzani kuti izi ndizimene malemba akuchitila uboni .pakuti yesu chrisitu ananena izi pamene analinanu panja kuti usaphe , usachite chigololo , usabe , usachitile umboni onama .Taonani mai uyu anazindikila kuti analakwisa anaonakuti ndikwabwino kulapa kuti yesu chrisitu amuchitile chifundo ndikuuzani kuti lelo lino ndikhala ndilinaye ali odala amene andikumbukila muthawi zose Amen.

 13. Malawians HV unsolved real issues that needs their contributions ,amasiya zimenezo ndi kumacomenta za ziiiii zosagwilizana

 14. wow , the bitch betrayed joyce banda just like that mbendela but after that the only thing they achieve is to die early… You can’t support gay president over your fellow woman…Selling malawi at cheap price like that

 15. Thats God’s best way to eliminate the oppresors and i hope the rest will follow suit #u re nxt u can escape our judicial system bt u wont be able to deceive the almighty the creator of the universe anyway rest in Hell.

 16. Malawi politics is very dirty y an saying this it’s bcoz the way we allow corruption to happen & try to deal with it when some 1 is out of office eg now pple r talking about 7 ministers kut they stole lots of our momey but no seems to care ,what will happen when peter lose power in 2019 ? These ministers will be arrested & we as Malawians must wake up & elect leaders who r willing to take our poor nation forward not these self saving politicians like this man msonda

 17. Amene angadandaule ndi anthu akwawo basi bcz zimawasangalasa lero asalile ayi wokuba ameneyo ndipo a prison pomutulusa anamulanga kale amadziwa kuti atuluke sakakhalisa .

 18. Anthu oipa amenewa afe basi palibe chonenela RIP ayi iye wapha anthu angati amene amwalira ndi njala or muzipatala kusowa mankhwala chifukwa cha anthu oipa ngati amenewa

 19. Malemba akuti usakondwele ndi ifa ya nzako komabe inu okuba ndalama za cashgate inu tikawonana kwa mlengi komweko zitsogolani coz amphawi ngati ife tikungosaukilabe inu kumangolemelerabe

  1. Aliyense amathoka ndimomwe waonela so ngati ali achibale anu sorry kwambiri and R.I.P koma iwowa anaba ndalama so zilibe kanthu poti analapa okuba ndi okuba basi

 20. Other sports activities are there for seduces especially the women

 21. RIP NO MATTER U WAS A THIEF GOD WILL DEAL WITH U COZ WE ARE FACING UNCOUNTABLE CHALLENGES BECAUSE OF SUCH KIND OF PEOPLE RIP

 22. Aaaaaaa owonetsa khalidwe labwino kuposa aliyense uja, shaaaa koma imfa iwe bwanji osaonetsanso khalidwe labwino kwa iye, bola nayenso akaonetsenso khalidwe labwino komwe akupitako

 23. Tipepese anamfedwa pepani kwambiri koma ngati pahalf imene waseva ku ndende ngati ndati ngatitu amadya chakudya chaku Ndendeko eiiiiiiiiish pepani.Nkuzamutulusa kuti anali amaonesa khalidwe labwino ndiye kumutulusa pamenepa paliboza.Osawerengera zandalama anabazo ayi koma ndikhulupirira kwa inu achibale ana ake anayesako kuwafotokozera chilungamo.Mai Treza Mzimu wanu ukawuse mumtendere

 24. Mungot anaba, anaba ndalama za kwanu??? Kuba kumalawi kunayambika kale kale nde si nkhan yoloza chala munthu,mulibe mphamvu zoweruzira munthu, mwina anabona, ingomuziwani yesu, za cashgate mukambazo ndizosala# may her Soul RIP#

 25. I Smell Something Fishy,,in This Era Of Reigm Oppenents And People With Conklit Evidence Are Being Taminated,,,complite Ninjitsu Technics

 26. When you said she behaved well she should get out of prison, mudali mutamudyetsa kale cement? RIP we will find you there soon or later.

 27. her involvement in the saga, then the confession and returning some of the cash, the conviction and sentence, and then the release after serving almost half of it, now her death, leaves us with more questions un answered,RIP madam

 28. Rest in peace. taludza miyoyo ya anthu ambiri chifukwa cha anthu ozikonda ngati awa. pitani mukazale chinangwa Joyce banda akupedzani azapale makaka

  1. Popano tipanga party tikudikira kaye Makolo akonso nawo amwalire kti tizapangile limodzi party & soon ma parents akoso amwalira…i mean it..

 29. Three moments
  1. Treza is convicted and arrested ( cashgate issues)
  2. Treza is released from Maula for her best behavior whilst serving her term.
  3. Treza is dead………..RIP…….

  1. @Manzy amai akonso nawo amwalira popano tione ngati suzalira & ndinamvanso kti ndi a Hule..Galu mwana wa hule iwe ndima comment ako akutumbowo..stupit

 30. Anaoneka ngat akukondani anzanu kukutulusani kundende in a such questionable way, not knowing akukupelekezani ku manda.. Mwina chikhala ku ndende ximukanafa inu.. Anwae RIEP.. see u thr.

 31. chomwe ndimaziwa ine ifa ndiyowawa koma ngati uli moyo ukuzuza amphawi,kulila kwawu kuzaveka.pepani ofeledwa poti zowawa koma ndalama asakaza malemuwa ndizowawa kuposa ife yamunthu mumodzi poti miyoyo ya anthu ikuzuzika,kusowa mankhwala muzipatala,anthu kumwalila kamba ka anthu ngati amenewa.

  1. kkkkk inu khalani anthu akulu.ndipo zolemba zanga zakwana pamenepo.mukamazuza anthu wamba mukuona ngati zikuyendelani bwino.mwagwa nayo.kufuula kwaeni ndalama kukumveka patali.ndipo munya nonse mukuba misonkhoyo.ndizomwezo muxipeza,one by one ndisanafe ine komaso awo mukuwadyela ndalama.tiyeni nazoni mwina mukadyela kumanda koko.

  2. palibeso chisoni apa.anthu angati akufa pangozi zagalimoto kamba kosakoza misewu ndalama zilipo koma agalu amenewo kumadya kunyumba kwawo,angati afa mzipatala,angati akuzuzika ndinjala poti mu Admarc mulibe chimanga.palibe zochuluka nzeru apa poti wafa.galu ameneyo asogole ndithu nane langa lizakwana.

  3. Inu ndiye oyera? Moto umapita komwe kwatsala ntchire muzichedwa ndikuweruka pamene mathero ake simukuwadziwa inalapa mbala last minute pa mtanda kwake kwatha mawa ndiwe

  4. Abale ndi malilo olo muwanyomze sakumvani abale chonde zinazi mungochimwa nazo koposa kusiyila ambuye akamuweluze yekha

  5. iwe Gwaza,ndisanafe ine,onse oba ndalama zamphawi akamafa chocho,palibe chisoni.musaonese kuti nfinu anzeru kuzisilu zaanthu ngati zimenezi.inu simuziwa kiuti bola kufa munthu mumodzi kusiyana ndawiri?amenewo aphesa anthu ambiri ndipo asogoledi.

  6. ndipo ndikudabwa kuti bwanji iwo nzeru zawo osazigwilisa tchito pa comment yawo?komaso ngati alindichisoni bwanji osangolembadi yawo yachisoniyo.enafe palibe chisoni poti wafa.ndalama zamisonkho yathu asakaza amenewo,amanenepa,kuyendela magalimoto odula,zipatala za pvt zabho,eniake andalama kumafa.mufuwu uja ukumveka patali waanthu ovutika.

  7. Wasala Joice Banda Amandinyasa heavy cz ngati kuli mavuto Azawoneni ku malawi ndi chifukwa cha mfiti yayikazi ngati imeneyi!!. izi zili chomwechi chifukwa Akuyendesa Boma lerowa nawoso alindi zofowoka zawo koma Amapezerapo mpata ponamizila mfiti imeneyi kuti ndiyomwe ikupangisa mavuto osewa chifukwa Anaba ndalama zonse za boma. padakapanda iye kupanga zimenezi Awa Abomawa! tikanawakhamisa mate kuti Anene chowona chake chomwe chikupangisa Mavuto onsewa.

  8. Onse a cashgate afe ndithu olo atamwalira sindingadandaule ndipo mu bible ananenatu usabe onse mumwalire ndithu mphotho ya uchimo ndiimfa zikumuwawa anadya nawo mufera limodzi

  9. May GOD FORGIVE MY SINS…. photo ya uchimo ndiimfa atero maremba oyera, komaso kutuluka kwake mndende is questionable.

  10. akuona ngati ndife okondwa ife,mene akutengela ndalama zathu kukundika mumatumba awo?mikwiyo ndikudandaula kwathu sikuzatha paka atasintha kupanga zoti ndalama zathu zipite kuzitukuko zosamalila eniakefe.

  11. Ndipo simukunama zithu zikuvuta kobasi maka zipatalamu 4 exple mlamu wanga alimchipatala kuvutika ndi ululu,kwabwela docter akuti odwala wanu akufunika mankhwala koma mupeleke k18 pin kuti tikagule kumachita chipatalacho n cha boma,kenako kudzabwela docter wachizungu kungoona file wathamanga kukatenga mankhwala aja thawi yosakhalitsa wafika noa pomwe ena akuti tigule,iz it fair? Allah adzamulanga munthu opondeleza anzake dollar anabazo akatsirizira pa grave po,nasefo tilimbuyomo poti dziko lavuta iri.komaso kwamene mukupitiriza kutipondereza God z watchig u il dilu wth u!

  12. kulibe kumvela chisoni anthu opondeleza,ngakhale Mulungu samakondwela nazo zimenezi.anthu kuvutika kamba ka anthu ochepa,omwe akuba ndalama zathu zamisonkho?sindizadandaulapo ine anthu amenewa akamapezana ndimavuto.ndipo nafe timwaliladi koma asogole kaye.

  1. Oops! I do think after typing. How much time lost thinking thinking & thinking later on tying. Hahahah! Tying goes together with thinking, better

  1. Zowona .wankulu munthu woti chibadwirweni sanapiteko kukapita wankulu kale nkukhalanso zimai bola akanakhala mamuna amalimba .Inenso maganizo anga ndikuganizanso choncho

 32. She might have had a hand in cashgate but her personal dignity is unquestionably intact. we all have our own flaws and are not perfect. May her soul rest in eternal peace.

  1. dignity: a quality or state worth of respect and esteem. This is to communicate my opinion that despite treza passing away while having involved herself in cash gate, there is something that shudnt be overlooked and thats the fact that she still deserves our respect as a human being.

  2. Imfa imaphweka ikagwa khomo lina koma ikagogoda pakwanu ndiamene umadziwa kuti ndichithu chopweteka kuluza munthu.. kaya ndiwakuba kaya ali ndimbiri zoipa bwanji kuweruza ndikwake namalenga..

  3. Her reputation was dented due to her involvement in cashgate. how do you say she deserves our respect? respect for what? respect for stealing tax payers money? respect for stealing millions of kwachas? be serious James.

  4. u reap what u sow,tiyeni nazoni,chisoni chifukwa wamwalila zachambaa.azuza ndikuba misonkho yathu ndemuzioneka anzeru pamalilo.mukamaba muziwe kuti kothela kwake ndikumeneko asaa.

  5. @ Ibrahim. sindikuweluza koma choti uziwe ndi choti amayi aja anavomela okha ndi pakamwa pawo kuti ndalama adabadi ndipo ananena kuti zina abweza. ndi momwe iwo analiuzila khoti. you better understand what we’re talking about here and we’re not saying kufa ndikwabwino. dealth is painful at all levels.

  6. respect for her being human… I don’t feel it is a right thing to condemn her because she was involved in cashgate and that in itself is not a reason to rejoice at her passing away. I am not in any way supporting cashgate or any other plot that enriches few people at the expense of the majority. But I am at the same time willing to acknowledge that we all make decisions we come to regret later( mistakes). imagine Dan if she was your sister? Would you condemn your sister to death because she was an accomplice to public looting while there are those who were masterminds behind the whole scheme? Imagine she had been your daughter, would you disown her simply because some elite politicians made her a party to siphoning of hard earned tax payers money from gvt coffers? theft is wrong and retrogressive but it is far less enough to descend a person to the level of a mere beast… If she were my sister i would still offer an eulogy full of all her good deeds and her unique personal merits. (you made me write such a long piece but i dont mind as long as it sends my point home. )

  7. Hy @Daniel..wanena kut anavomera okha ndipakamwa pawo ndipo analonjeza kut ndalama abweza so why u speak as if mayiwa sanalandireko chilango ? now she’s dead u stll angry wth her ? kapena ukufuna kut anakabweza kaye ndalamazo thn amwalire bwino..ngat wina akuti tikuyenerabe kupereka ulemu kuti mzimu wawo ukautse iwe ukuti ayiso ulemu wachani so zikuthandiza chani zimenezo ??

  8. Nemar, that is undoubtedly true to some extent. But there is a saying that goes and i quote ” two wrongs cannot make a right ” cashgate interrupted a lot of service provisions in the country and she happened to be among those perpetrators who were brought to books and i hear she confessed and handed back some of the stolen money, now thats reaping what she sowed. I am not advocating that people who breach the provisions of the constitution should not be brought under the luminous shade of justice, on the contrary, the system has in place a way to ensure everyone who breaks the law faces prescribed consequences and that in itself is essential for an absolutely functioning society. At this rate, I wish to make it clear that i believe the people who are in our prisons for various reasons including cashgate deserve our respect because they are human too even though they are not perfect which is intrinsically what makes us human (imperfections)..

  9. Men She Accepted her Involvement In The Cashgate Atamupana Without That Sakanabweza Dollar Yo.Moreover Do U Think She Surrendered All The Money? .

  10. at herbalist, she probably was afraid of the law. everyone else who breaks the law holds the same fears. do you realize the ‘founders’ of cashgate, if you may allow me to borrow that expression, are walking around freely? Who should rot in jail between a chief in theft and an accomplice in theft?

  11. ngati anavomeleza dols snatengazo,anapeleka zonse?komaso anthu omwe muzipatala kamba kakosowa mankhwala pomwe ndalama anaba iwowo,kodi anawazusa?nanga omwe anafa pangozi coz misewu sinakozedwe koma ndalama anaba iwowo,anabwezelesa miyoyo yawi?nanga kusowa kwachimanga muma admarc anthu kufa ndinjala anawazusa?anaphesa anthu ambiri pandalama zawo,kudyelela,kunenepa,school zabwino,ana awo kutumbwa coz ndalama za anthu osauka.ndisanafe ine iwowo asogole,mbudzi za anthu.chisoni chifukwa choti wafa?zulo ndinasala pang,ono kuphedwa koma ndibapulumuka,lelo paka ndaonako post yambavazi.

  12. iye wangomwalira yekha basi, koma ndalama zomwe anaba zikanatha kugula mankhwala ambiri mu zipatala kotero kuti anthu 100 aja omwe anafa akanakhalapo ndi moyo lero

  13. bwana Nemar nkhani siyowachitila chisoni koma kuwalemekeza monga anthu. ndine osangalala kumva maganizo anu pa nkhani imeneyi kuti mukuona kuti nkosayenera kulemekeza imfa ya malemuwa kaamba kokuti akukhudzidwa ndi cashgate. ndikuvomeleza kuti ndalama zomwe zinabedwa zikanatha kugwiritsidwa ntchito muzipatala ndikupulumutsa miyoyo. koma maganizo anga ndiwokuti moyo wamunthu ukuyenera kulemekezedwa ngakhale atachita zolakwika chifukwa ambilife timalakwitsa ndipo sikoyenera kuweluza anzathu nafe tili ndimofooka mwathu. anaba inde nchifukwa chake anamangidwa koma tiine tilemekeze ndikupeleka ulemu kwa munthuyu. By the way I am in no way speaking from a view point bent towards a certain demographic for any reasons and I may strongly assert that I dont have any relations or indeed anyone I know who benefitted from cashgate. My moral campus directs me to follow a path that allows to some degree, to overlook the wrongs of others and see the dignity that God bestowed upon them. in a democratic society it is pleasing to have dissenting opinions and embracing differences is what moves us forward as a nation made up of different people.

  14. Mulungu mukufuna lelo pofuna kulemekeza chimtembo choti chinaphesa anthu pandalama zobeledwazo?mukanaziwa mene anthu amenewa akuonongesela miyoyo yaanthu osalakwa sibwezi mukuti apasidwe ulemu.mumaona ngati Mulungu amakondwela nawo.mitembo yaanthu ngati awa bwezi ikungotayidwa.ndilidi ndizofooka zambiri koma sindimaphesa anthu kapena kuwabela.ndimakhalila kudusa mumipeni kamba kambudzi zimenezo,kuba ndalama dziko kuliyika paumphawi paka kumakhala anthu onyozeka kudziko laeni kuno.kumapangidwa zipongwe pomwe agalu amenewo akudyelela misonkho yathu.bwanji osangowombela manja kuti ena atengelepo phunziro?

  15. Sikuti ndikumufuna mulungu ndiineyo iyayi, nkhani ndiya anthu okhudzidwa ndi cash gate. let me ask you, what do you consider the most atrocious crime that a person can commit in this life? And to qoute your saying “bwanji osangowombera mmanja kuti wna atengelepo phunziro?” this is surely a rhetorical question no doubt, but at the back of my mind i am establishing the fact that you think those people who die are sinners and very bad people than the living. You are absolutely wrong on that one. I have seen and heard of ‘good’ people dying prematurely and the seemingly bad people living years on end till old age. I base my argument on the fickleness of human thinking which is responsible for the decisions that people make in their day to day lives.. Mind you before cashgate drugs were running out in hospitals, roads were potholed, admarc had at times no sufficient supply of maize, schools had no necessary learning materials, etc.. Cashgate didnt bring these problems up from nowhere but it simply opened our eyes and pointed at a hole where our public funds were being drained.. Coming back to the issue in question, I now repeat my question; what do you consider to be the most atrocious crime that one can commit in this country or world at large.

  16. ok basi ndakumvesani kuti inuso ndinu imodzi mwa iwowo,mesa mwati cashgate sinabwelese mavuto,chifukwa chake mukupitiliza kubako,koma ifa ikafika mwayamba kuoneka ngati abwino?cash gate inabisidwa koma pano mwaziwika ndekuti zitukuko kuchoka kumbuyo koseko zimalephela nkupezeka ndimavuto mwatchulawo coz mumaba koma eniakefe osaziwa.ndeapa nditym yoti eniake tiyankhuleso amene mukutibela ndikutiphesa kuti ifayo sinatikhuze poti mwaphesa anthu ambiri ndipo sitizakhalaso nanu ndi chisoni enafe paka ifayoso next itatipeza.mwayamba kubisala mzina la Mulungu pano?tiyeni nazoni

  17. haha my good friend you really involve emotions in your arguing. Its impossible to be emotional and think logically at the same time. I have no hard feelings for you for holding an opinion different from mine. You dont at all get my point. I condemn cashgate but i dont agree in people speaking ill of the woman who has just died because her dignity is to be reserved at all costs. For your own information, I come from a humble home and its sheer inconsideration to put me in the same league with cashgaters. But if doing that makes you feel better then I guess it shud pass as a therapy for you. And hey, last time i checked, almost all prominent religions in the world advocated for forgiveness. I wonder which God you serve who instructs you to harden your heart and not forgive people when they wrong you. Lastly, it may interest you to know that I am a struggling Polytechnic student who was never born with a silver spoon on my mouth. Perhaps that may convince you that i have no affliations with the cashgaters but at the core of my heart i know they are just human too. “hate cannot remove hate, only love can do that. darkness cannot remove darkness, only light can do that.”-Martin Luther King..

  18. nkhani siyofufuza zipembezo kapena kufuna kuti mukhale abwino pamavuto olo tinene kukonda Mulungu pamavuto ayi.nkhani ndiyophesa anthu kamba ka cashgate komaso ifa yamunthu ophesa mizinda yaanthu.kaya muli ku maphunziro aukachenjede koma muziwe kuti fuwuu waosauka uzamveka patali.mukondeni Mulungu lelo mawa mukalowa muma office kabeleni osauka ngati simuzakumana nazo.enafe nde ifa imatiphonya daily tikuziwa kuti tsoka likazakula zabayidwa ndipeni koma chosangalasa ndilibe mlandu ndimunthu,sindibela anthu.

  19. I am following and i feel very concerned and sad indeed, let God Be The Judge But Man Also Shall Be Partaker of their own deeds. one mans sin can kill so many people and can also stir up anger, strife and resentment. i have a feeling of both anger, resentment and sadnes after following your coversation because of the beastly acts of selfish cashgaters who unknowingly caused untold misery in many souls. i will not be hypocritical to pay any sympathy to please the multitude elites but side with many innocent souls who suffered and are still going through dangerous aftermath of cashgate. it will be more sinful for me to side with evil against which God calls evil, evil is evil no matter who performs it whether dead or alive, i dont know whether to say rest in what or whereever but all i know is you are destined somewhere for sure and let the lessons be taken by the living who are also dead.

  20. Well, Mr Nemar am not trying to sound religious here. Neither am I trying to show off as a good person. No, I wouldnt offer a review of myself as someone who is good and beyond reproach. I am however, expressing my opinion based on my personal beliefs and values, that brings into the picture the beauty of democracy which allows all of us to exercise independent thinking and hold whichever views we might desire provided they dont infringe upon the rights of others. you think these people deserve death and perhaps hell as well, while I think they shud be given a second chance and an opportunity for “salvation”. I totally respect your opinion and it is my earnest wish that you will respect mine.. Learn to argue without involving emotions so as to be as objective as possible and it is the only way you can be open to accept opposing ideas where they are proved to be credible. #Mapemphero_Suwande, i get you my good sire.. I remember the story about the adulterous woman who was brought to Jesus Christ by the Pharisees to be stoned to death. Jesus Christ said to those who assembled that those who had never sinned should be the first to cast stones, well we know how that story ended and no one lifted a finger to cast the first stone. According to God sin is sin. if you keep nine commandments and then break one the bible say you are guilty of them all. Imagine if you try and avoid killing, stealing, covetousness, etc but you disrespect your parents then you are guilty of murder, theft idoltry and all other sins thats according to the bible (James 2:10)…. I repeat, am not and i have never endorsed cashgate or any other such plot meant to enrich the elite while masses are suffering but i can never speak ill of Treaser’s death cuz there is a judgement day specifically meant for that..

  21. komatu mukumveka bho mr.uthengawo mutati mwauzako omwe akuphesa eni amisonkho bwezi tikuti dziko liyenda.koma vuto anthu anzeru mumangoziwa kukhala ndimapepala amukalasi ndikulankhula koma chisoni mulibe koma mukafa aaa tipasen second chance.shaaa ine ndikuona bola mukanapeleka kaye second chance kwaeni ndalamazo osati kwa okuba ayi.criminalz belongs to jail basi.

  22. yes Nemar. every sort of criminal must go to jail be it a sex offender, a thief, a murder etc… But these people though they are branded as evil, they must still be respected thats why punishing criminals by hanging them on gallows was abolished and death penalty is becoming obsolete and a thing of the past in most parts of the world. Even here in Malawi death penalty was abolished in the late 90s. by giving them a second chance i dont mean they shouldn’t be jailed and be left scot free, no i want them to get just prison sentences in proportion to their crimes cuz jail is for reformation of behavior so that the people can come back into society later on with changed behavior and mindset.

  23. NTCHITO ZA MUNTHU ADZANKA NAZO NDIKUKUMBUKA PAMBUYO APO MAI GWAZANTINI ATAMUWOTCHA MWANA WANKAZI NDI MADZI OTENTHA NDIMAMUKUMBUKA MPAKA LERO DZINA LAKE TCHAYI JACKSON KUNALI PUBLIC OUTCRY MPAKA ANAMANGIDWA NKUPONYEDWA NDENDE TSIKU LOMWE ANAMWALIRA INE NDINALI TOWN NKHANI ITAVEKA KUTI MAI GWAZANTINI AMWALIRA TOWN ANTHU AMAGALIMOTO ANALIZA MA HORN KUSANGALALA NDIKUFUNSA KUTI NDI CHANI AKUTI ANTHU AKUSANGALALA MAI ANAOTCHA MWANA WANTCHITO NDI MADZI AMWALIRA NDILI YA MIZIMU IKAKUMANA KOMWEKO KAYA KUKAKHALA ZOTANI NDE MADANDAULO A ANTHU SIABWINO TONANI LERO ZONSE ZINACHITIDWA ZATHA BASI KUKHALA OSAUKA KOMA KUKHALA NDI MTENDERE NDI CHINTHU CHABWINO TINGOTI RIP NANGA TITI CHANI

  24. They say Malawi is a God fearing nation yet the people cant forgive the transgressions of others when the bible says in (Isaiah 1:18) that though your sins be red as scarlet, they shall be white as snow and though they be red as crimson, they shall be as wool. There is no sin so great that God cant forgive then why shud we take it upon ourselves to send people to hell? Thats why most Christians are branded as hypocrites, preaching love in words yet in deeds doing the direct opposite. The woman in question went to jail and faced the consequences of theft. Now that she has died can’t we at once forget her grave mischief and treat her to a peaceful farewell? What ethical standards do you use to uphold such views as regarding offenders? an eye for an eye? Our religion is simply used to keep up with appearances when in fact we denied the power of God intentionally. Forgiveness is not easy. you have read the story of a man who after being forgiven a considerable amount of debt by his master, grabbed his fellow by the neck demanding what the friend owed him. The master then was extremely angered that he took him to gnash teeth in prison until he pays back in full what he owed him (Matthew 18:23-35). I can go on and on but I have no power whatsoever to influence your mind on issues such as the one we are tabling here. But i would like to make it clear that forgiveness is not letting the offenders free but treating them with respect even if they are in jail. I rest my case.

 33. boma likudziwapo kanthu pomupanga release nkumanama kt she is doing good behaviour mmmm kalipo kalipo apa….chilungamo chidziwike basi

  1. pomupanga release munthu uja nkuti anali atathana naye………don’t pretend kt amaoonetsa khalidwe la boh mayazi

  2. zaziiii chilungamo mukufunacho ndiye chiti muwelenge malamulo adziko lamalawi kwa oyimbidwa ndiosungidwa mundende mupedza answer. she is gone let her Saul rest in peace

  3. Maganizo ndi amene amupha ngati pa miyezi amakhalayo ngati amadya chakudya chaku prison zikhoza kutheka anamuyikila poison.Pajatu ku Prison amatha kukonzatu mogwirizana ndi Boma

  1. aliye amadziwa kuti one day he or she wanna die ndeno josh josh akunena zichani za chambazo. she must face de judgement coz ov wat she did to the poor souls by stealing misonkho yathu.

Comments are closed.