The South African Government has released from Lindela Camp Malawians who were arrested for staying in the country illegally and had stayed at the camp for at least five months.
Malawi24 understands that all Malawians who were arrested before July have been released and allowed to go back to the communities.
One of the released Malawians told Malawi24 that even though the number of Malawians freed from Lindela is high, there are also many Malawians left there.
“I can say like half of the number of Malawians have been released today, but there are still many Malawians left there,” said a Malawian who has joined the community in Honeydew from Lindela.
He was arrested together with his friend in June this year by Muldersdrift police officers on his way home from work alongside.
The Home Affairs department in South Africa has since given the released Malawians 90 days to find money for transport and go back to Malawi.
South African government stopped deporting illegal Malawian immigrants staying in the country due to financial problems. It is said deporting one person costs the South African government about R4000 (K200000).
The Malawian government also recently told Malawi24 that it does not have money to deport the imprisoned Malawians.
Before the release it was reported that there were over 1000 Malawians at Lindela camp.
Chipululu simofela timangodusa zana amuna izi
olo mutanena chani_chani sikuti chani kapena chani……..sikuti tinva ai ife tinazolowera
Auze maze, enawa ndi nsanje
aaah man mamuna umamanga mudzi pomwe wafika basi olo chokolo timalowa
Zoona kumene, ameneyo nde mwamuna,
kkkkkkkkkkkkk
Nkulunkulu anibusise iziningi Africa,kuyafiwa ngalena kodwa sinalo ithemba lokuthi kuzulunga se siyagoduka
Thats why Malawi umphawi udakapitilirabe patsogolo we r here in mzansi chifukwa chofuna kupeza bwino taganizani pano mukuti 2000 notes hahahaaa kuli bwino ndifere konkuno offcoss akakugwira kulindera amakusunga koma umadya bho n’ umakhala mwaufulu mpaka 3 month umayambaso ntchito ukatuluka so dont comment usless zifani ndinjala ife tikudya ndikumaona patsogolo
Mafumu yankhulani mwanzelu ngati munabadwa ndi umun2 kupezeka ku SA,then kugwidwa kupta ku Lindera sikufuna kmno munthu amati mwina asintheko umoyo wake,tangoganizilani dera lanulo an2 omwe anapita ku johns apanga chitukuko chotani,ku RSA kugwira ganyu ya r200 zinthu zomwe ungagule kapena kutumiza ku Malawiko ndi pafupifupi mk9000 mukuona ngati pafika malawi pano simuli ku ndende yakunja,dairy tikumaona muma social network mukutukana kmnso kunyoza atsogoleri andale kt sakukuthandizani sichina km umphawi ndi womwe mukupangira zimenezo
My fellow makawian it’s part of life now ur time to be free
That’s what we call PART OF LIFE nobody knows tomorrow……chomwe chikufunika nďiķuSaGiver basi Lindela añajuďuĺila fanz ngati ifeyo nde ndichisomo chamwiñiwakeyo kusabathidwa…..nde enanu muthoķa mbwerera kuti paNYASApo pali bho,. pamene zopinģa zili kuuuu
The dots think that Malawi is ahell but they dont think about their own stupidity.I am here in SA but SA is not a better place to be if you have ever held that satan moves with his legs its here in SA Malawi is achristian country the only thing its a poor country so let us just keep on with our prayers and God the Almighty will bless it but if you keep on with that offensive laungauge then you are bringing yourself and your country a bad luck because God is not happy with your perverse toung
ndikunva chifundo kuwna amalawi akunyoza dziko
Shame
We’re creating job opportunity to all 3 countries civil servants are robbing us at border posts to pay themselves.
Home affairs shud also grant working permit for that duration of 90 days so that they find money for transport
Thank u south Africa we all Africans
Our government must talk to South Africa government so that we can be free without that yoooo sizoboshwa njalo
Never come back home akatigwira tizibwereranso kokuno
Kkkkkk
CHAKULA MDI NSANJE BASI CHIFUKWA ALIYENSE AMAKHALA MALO OMWE ZINTHU ZIKUMUYENDERA NANKHA OMWE ALI MAIKO ENAWA BWANJI SIMUKUWAITANIRA MAMGO ANUWO HAHAAA!!!!!!!
nosense,why cant u write about hunger where by government iz giving malawians sogham instead of giving them maize?dont u know that people r leaving malawi for southafrica due to lucky employment?nevermind people who were detained in lindela r out now n still here in r.s.a.they r moving on there lives than staying in such troublesome government of malawi
Atapasidwa matenda plus a john ndi mix
Malawi z lyk hell in earth,no wonder pple r livn to another country once thre get thre instead of changing their life their r now facing so many challenges lyk this,God bless Malawi
How Can God Bless Malawi Yet Those Who Are Inpower Are Much In Sin Activating.Kuphangilabasi. God B4 U Bless Malawi Punish Thoes hu Eat And Enjoy On There Own Then U Bless. Amen
Kkkkkk i know ur angry my friend, even mi am also,bt lets ask God to change their life
We are not selling Ganja or any illigal drugs in RSA we working and what am getting payed here in RSA some of u in Malawi u can’t get although am staying illigaly stop criticising other people.I always advise people to mind their own business take it or leave it we are not shaken but I can’t stay in Malawi.Malawi is the place to visit not to stay.Zilimbanani ndi ndale komanso ma land bills anuwo ife tilipano as long as sitikuba koma kugwira ntchito nkumathandidza azibale athu.Ndibwino kumangidwa modikira kutumidzidwa kwathu than kumangidwa kuti ndaba mbuzi kapena thumba lachimanga chifukwa cha njala
Kkkk Ine Phwete
Ku Malawi mkokhala munthu wamkazi osati mamuna ndevu pepeya ati amagwira job salary kuiona ngat ina wag
Indeed we de malawianz we have to work hard
Passport is somehow very expessive despite financial problems which most malawians are facing, it is a big challenge to a poor malawian. This problem has forced most poor malawians to go in R.S.A without a passport!
Derset z not place to die we jst pass to kenan
True,bro.Hope Mw sees a brighter day some day.Coz the humiliation z becoming unbearable.JAH KNOWS !!!!
Where are they?
Mukuti bwelani kunonu mulibe mzelu mwina mwakhalira cashgate.. Can u emagen if u r doing bzness ad u got 2 kids in secondary do u manage pay feez ad good leaving for them.? Stop talking nonses ad think deep. At the end play hard so that Malawi must change otherwise our children wil end up Mozambic if RSA close their border.
usalimbana ndi fanzi ya ku mzimba they are tracing their routes back to their original home hauhauhau hamba phambeli kkkkkkkkkk
Wow out of all other nations there in Lindela,they only release Malawians? I wonder
azanutu atuluka amene muli kundende yosatha ndinu muli kwapeter akutulutsilani thosauzande muyisova ife tikuwelenga rand kkkkkkkkkkk kukoma pajoni
Lindela simathelo amoyo ayi ndichiyambi chodziwika ndi boma la south africa ife sitibwela tazingodyani mbewazo ife koma nkhuku
What a Shem brother sister sleeping together. How can a loving husband force his wife to sleep with a snake this world of ours
Vuto azawagwiranso and akawamanga kawiri kulinderako, mpumulo paziko amalawi sitizaupezanso
Aaaaa!! Pano pajoni ndipokoma kwabasi, Taona anthu ambirimbiri akutukuka akumanga manyumba ngati ndiya minister waboma lamalawi, kugula magalimoto, abwino kusegulanso mabizinezi akuluakulu cifukwa cobwera kuno Ku Joni, ndiye amene mumanyoza anthu obwera Ku Joni kuno mukungotaya nthawi yanu pacabe, Anyamata akutukuka cifukwa ca Jobeki. Sintawi zonse kugwidwayi.
Chidziko chokanika chamalawi chingofanana ndilindelayo
Malawi is place to visit not to stay,,,,that’s why akatimanga timadzabwelaso,,,,
Malawi govt. Does not provide duty to it’s pple.to the other hand most malawians are thinkless and lazy
Dziko lamalawi kuvutika hvy
Evryone hv aright kukhala kuno ku south Africa sikuti ndicholinga chathu ayi koma mavuto amene tikukhara tikukumana nawo m’malawi wathu zoona fertiliser 20000 above thumba la chimanga 12,500 mkuganiza kuti tingagwire ganyu wanji kuti tikagure bag la fertiliser or chimanga sopano tikukhara kuno movutika sicholinga chathu ena mli busy kunyoza amene ali joni chifukwa mwina muli pa ntchito munapanga mwayi anakusankhaniko kuzera mwa abale anu chifukwa chake mkuona ngati aliyese ali joni is very stupid siose amene a kukhara kuno sanaphunzire tilikuso ambiri amene tiliophunzira kamba kosowa ntchito kwathu ku malawi chifukwa chake tili kuno msanyoze ntchito yimatha mzabwera mlungu simunthu woseweresa
Eeeeee basi ntendele kulibe guys ng’ona zinenepa
Mmmm koma bola akutulusani mukazatoler muzabweleranso!mchipululu simofera
Azititulusa koma mpanje ayi kumalawi kotan
Jons sinama tivota konkuno Rand is Rand
Enanu muli ndi mwayi munabadwa condom kulibeko ikanakhalako makolo anu akanagwilitsa ntchito kuti musabadwe nkaona ma commet anuwo eya its their choice to be in RSA and inu vuto lanu lilipati?
Abweraso amenewo chaka chamawach>>>amalaw stiphwekesa
Shame
Yemwe ali ready to work withing jhb just page me on 0739727252 ntchito ilipo, musiyeni bright ndi modzi mwa anthu omwe amaganiza kuti chigololo ndi destination
Ndipo bola zizichitika chitika
Mulungu simunthu kumangopepha kuti asekule makomo mugwire ntchito osavera zonena anthu
True
Iiiiii ndi ku malo kwabwino bwanji!!
KKKK bola kukhala kulindela 6months than kukhala ku malawi zaka zambiri.zikusiyana pati lindela ndi malawi(pa mpanje)?
Hahaha zakumva zipwetekesa mutu,zinayamba kale inu mwadziwa lero?
That’s November time, aliyense atuluke
We don’t go to RSA to steal or sell chamba.Its not easy to get work permit or ID there.We must just live as one bcoz we are all africans.If our country was economically stable we would not be here or else we would come to visit and go back home after a few days
Yet the DPP cronies won’t see these issues past their big noses.
Yu know what iknow bro
Well spoken
Zugwirizana bwanji ndi chipani izi?kuna anayamba ndi makolo athu tisanabadwe ai,lamulo la dziko basi
Thats True Brother Even Though Am At Malawi But I’ve To Coment On Dat
Welcome to Malawi land of black out and scorpions
Bweranikoni basi, kuno tili kumidima.
Come come guys muzafune maganyu tisamale anthu kumudzi chifukwa ku malawi kuli chi 2000kwachatu kkkk
Welcome back gys tidye volosi plus tiukupe bawa December yi
Zusiyana pati kundende ndi kunja kuno,its better kukhala Ku ndende than ndi Malawi walero,we’r here
Life goes on
malawi goverment the worse on planet earth
Mwamuna ndikabula amathera moyenda. Mbewa yamantha/yamanyazi inafera kuuna. Cowards will die seeking proper documents while real men are taking risks. Oh my fellow Malawians, learn to be courageous, see things beyond your nose and grab opportunities where someone sees nothing
Cant the Malawi govt negotiate with RSA govt to give Malawians already in RSA temporary residence permit
Komatu olo akumatitulutsa akatigwira they’re still gwira gwira
Amene mukunyozanu Ku Jonnes simunafikeko, Munthu amene ali ku Lindela sangafane ndi iwe amene uli ku Malawi ko , Munthu wa Lindera amagona malo abwino, magetsi ndi wayawaya, phwanyanso ya bho, ngati umakonda ku teya mpila uthanso kutelo apo ayi uzionera TV.Umakhalanso ndi mwayi o buka ndege ngati ukufuna kuchokako, Sungafane ndi mdyera ku nthiko iwe ukati wamwa tea nde wakukuta mango launch unena mango ophika ukhalira yomweyo yomangonyozayo anzako akudya Rand, Pano awatulutsa nde uwone ma njoyedweyo sanayambe ntchito ķoma adya phaks ya bho kufunanso machic nde ndi osayamba Life ya bho ija ase umaziwa pa modzimodzi panavundisa zungu ada zikhala choncho ndi Peter wakoyo fuky you .
Umakhalaso ndi fon ku lindera
Awatulutsa kuwabweletsa ku malawi kuno maybe awasiyanso konko. My friend brother wake anamugwira nawo he was at lindela.
akumawasiya kuti azipita komwe amakhala konkuno ku r s a
Hmmmm kwa anzathu okhala kunja popanda mapepala okuvomerezani ganizani kawiri chifukwa boma lathu likulimbana ndi njala kusowa kwa madzi komanso magetsi ndikovuta kuti boma liyanganeso inu.Malawi ndalama zilimo chabe zimafuna kuchita kusaka ngati mbewa koma umakhala mwaufulu,remember kwanunkwanu.komabe poti RNA mawa inu kunva munasiya kalekale mmakutu munamatamo chungamu ndiye musovenge but if l were you even just after xenophobia l would be home by now chifukwa moyo nkamodzi siubadwaso kachiwiri olo mutachita kupita Ku America
Ngati anthu ndiochepa kumalawi akulephera kudya ndiye akabwelera enawo njalazo zizakhala bwanji?
Ngati anthu ndiochepa kumalawi akulephera kudya ndiye akabwelera enawo njalazo zizakhala bwanji?
Zopanda mutu kunonso tikusaka chimodzi modzi kumalawiko so stay out of this man en mind ur own business
the way other people they think about this issue is totaly wrong how can you compare life of people at and Lindela you been at Lindela before,its hard there bra 5months inside is it easy ,ofcourse many people they are suffering but when they wake up they can do something to earn a living
Kungwidwatu mkupita kulidera ! Imakhala nthawi kuti yakwana: koma kugwidwa kokukumbutsa kuti kuno si kwanu; ndiye ndi tsiku ndi tsiku , koma Sitimakhumba zonzampha ziwalazo! Chifukwa uta wa chitete tinaiwala kukunga kwake
iZO NDI NKHANI ZA ANTHU AMENE ALI KUNO KU SA. MUKALEMBA KU MALAWI24 IT DOES MOT MAKE SENSE COZ PALIBE CHIMENE MUNACHITA OLO MUNGACHITE MUNTHU AKATENGEDWA KUPITA KU LINDELA. NGAKHALE BOMA LANU, ACHAMANU OLO ACHA AMBWIYANU. ALWAYS PUT NEWS THAT WILL BENEFIT MALAWI CITIZENS AS U ARE A MALAWI NEWSPAPER.
And I quote “he Malawian government also recently told Malawi24 that it does not have money to deport the imprisoned Malawians.” End of quote. Does Malawi government also want to deport its own citizen?
Malawi24 ya bodza palibenso.
Never give up brothers,mphvumvu ngati zilipo bweraninso mpaka mutakwanilitsa zokhumba zanu Ku RSA.
Thanx 4 the Govenment 4 releasing them, but they should also give them #temporary permit 2 stay walk free at last.
Is not the pip they dont want to hve the permitts which allowed them to stay free,but the problem is south african government stops to give them the permitts thats why things is going to be bad more and more.
kazinkhalani kumalawiko lol
Thanx
munthuwamanja lendekudziko ladziteteko sangaganane ndiwakulindelatu kulinyama posiyanitsa ndidzombe kulitea posiyanitsa ndithobwakoma atayikidwa mubotolo lakoko eeeeeee bansindingapalamule sindimachedwayine
amene salimbika kuno or atapita jon amangotayako nthawi sangalemere amangobwerako ndi tv homefiet ndi matama basi
Kutheba nde kumeneko
Umphawi Sumapha Bwerera Kunyumba, Thomas Chibade
Tizadyanji kumenekooo?ziteteee?
kutulusidwako ndiye ulemelelo umenewo bro ndi Nthawi yosaka ndalama sopano
We are fine here,we dont need to buy your mangoes at k2000 each.
Koma akamabwera abwera ndi kanthu poti momwe amagwidwa ali ndi hule pokalowa ali khwakhwakhwa kuyamba kumuvutisanso ROBERT NG’AMBIE ngati iyenso anachoka chithawa kuno.Bweranikoni makolo anakulerani aja akuzunzika ndi khasu kuno amkati muzawasamala osaziwa kuti azizakoka mahule.Kwa omwe muli safe mupitirize ntchito za bwino awa agwidwawa mkusamva kwao
Good news ndionana ndizanga tionana naye pakathawi
Mungozitayisa nthawi mkumalimbana ndi a johnz kujon kulibe mavuto tikusangalala kuno ngat zakuvutani mupeze plan kut muzithandize
nkhani yabWino. koma amalo okoma kwabasiawa mmmmm ndi malo
Thanks south Africa
mwati mango ophika ife kkkkkkkkkkk asamalimbana ndi anyamata onjoya apa theba
Kkkkkk kunjoya ku Linderako kkkkkk my dear friend what a joke??
kkkkkkkkkkkk muzitipasa ulemu ndife omwetikutukula Malawi hahahahah
Keep it up Mr, si zimene zilikuno ku tz mbuli zenzen
Malawi paja nsanje nde kudya kwako,ofcoz they spend five months in lindela but they can manage to do lot of things after three months mosovenge
Kkk home is best guys
All the best guys kutchukumaso chimozmoz
A Ryan Disi, Bright Kamotoyo wanena basi, kaya mwanva kaya simunanve, bweranikoni mbwiyake, kikkkkkk
Malawi is not better place for human beings,to be in lindela z not the end of the journey rather is one of challenges that a lifeperson has to meet,Malawi government is the main source of the problems
ABSOLUTELY
Nkhani yabwino iyi Mulungu Alemekezeke
Mukuziwakale mulungu akanafu yesu sakanafa ndi mulungu yemweyo amene wawuza apolice kuti atiseye pamene wina amatitikhawula ngayezi mulungu simuthu
hahahaha kalinde paja ukudziwako eti
Hule ndi hule oro inu uli kumalawi konkuno akazi anuwo atha kuchita uhule kutheka ali nacho kumene chibwenzi,koma inu osadziwa kumangolera ana aweni inu nkumati onsewo ndi ana anu, osati tikhalire kwanyoza anzathu amene ali kumaiko akunja. kumakhala kusakasaka mwai muumoyo wamunthu
Auze moyo siophweka bro
Well spoken
?Mau
inu abright kamoto mukuyakhula ngati Mwapana pad bwanji kumatak
Free at last, Lets learn now to have proper documentations when we visit or stay in other countries, never the less we are just one people, black life matters, one people on Africa..thanks South Africa..
If either you got documents please don’t think IS that earlier to have good luck for you then if you got
You don’t know what you are talking about bro,,,,its not as easy as you may think
Amalawi pena mumandimvetsa chisonidi, kukutulutsa ku Ndende after 5 Months imeneyi nkukhala Gud News?? wat is gud about it?? Anzanu amatuluka after 3 weeks, bola kanganyanse…! kkk
I yoh kulibwino aka chinde mofatsa sopano
So where r they after being released? wishing them well,they r pipo from our land,al being africans but being discriminating each other,God is watching.
Ndibwino kutengedwa kukakhala ku lindela than kumakhala kumalawi
Kkkkkkkk mwatero malume?
Big up
Kkkkkk wina alila
How wil these people manage 2 get transport within 3 months? Has the South African Government given them a work permit? If they meet the Police in the next 2 weeks, won’t they arrest them again?
Welcome guys tithamangethamange mu BREE street
Ndiwe opusa brighton .
Hey u guys be quite
May only Jahova bless them.
Thanks south africa
Athunu musakambe zambili ingotini zikomo powatulutsa amalawiwo chifukwa nafeso kukhala kwathuko timafuna koma chifukwa cha….
I’m really confused who are in lindela pakat paife tili kumalawi kuno ndianzathu omwe atulusidwa ku SA .
Chief, nanga azitinamiza Joni yake iti? Ulesi basi kuthawa kulima, kuthawa udindo oyang’anira anao ndi udindo wa nyumba kwa akazi awo, kikkkkkkk, hahahahaha.
ganyu ku SA ndi R150 almist 7000kwacha patsiku pamene malawi ndi 500 kwacha .nde ungoosova wekha
Man try sometimes to mind your own business muzimvere chisoni nokha osati wina watch your tongue baba en speak like a man
Mr Thomson yankhulani ngati mun2 wamwamuna.
Kunena zowona mzimayi wamasiku ano ndiovuta, amazigwilako pang’ono ngati mamuna ulipompo koma ukacoka Aaaaai, gemu yatha amalowamo aliyense angafune, ndiocepa cabe amene amayesesa kukhulupilika iweyo mamunake utacoka. Koma timalolera, yndinkazi kakaka kuopa angandinyengere ndikacoka, ndiye muzafa ndiumpawitu??? Bola kucoka basi a!!
Koma zili kumalawi k2000 yogwilana sugar k1500 olo atigwile sitisiyabe bola madzi momuno
how can people stay in another country illegally ts only here we tolarate that,please we have to do something though the economy iz not stable and ayao end atumbuka mukuwonjez zahona
Mapwala ako!
Stupid ndimayi wako amawonjeza
mukuta mwayend ku jon kapen ku tanzania chamb
Stupid, ku R.S.A kuli mitundu ya a malawi ambiri why kutchula a yao ndi atumbuka?…..kunganiza mopusa!
Zaziii Zankutu Moyo Onyasawo Osafunila Ena Zabwino iiiii Hmm
stupid idiot, son of bitch!!!
chikala chowe
kukhula Mchewa sikuti wapambana onse kuli a chewa anzako anzeru omwe timawapatsa ulemu osati iwe kape iwe, kugawanitsa mitundu basi munazolowera umbombo
am not a chewe
Hie
woza nawe sister
Pepani andituma kuti ndikuyankhen mahule ndimagamba
Mukalira yomweyo ndibwampiniyo panyopanu mmmxxxxmmmm
But how many of them….?
where in malawi? do we have our own lindela? ifenso timawagwira ambiri akunja but end results amatherakuti?.bola amalawi omwe azazana ku ndende za ku tanzania aone kuwala.
Iweyo nde mphaka wenwen
Siyathenga contam yako ‘kkkkk Amapula Egg yako kkk Zilili ku Meneko Achina BB. Oya dyomba Vp Mwanangu kkkk
kkkkkkiiii. Bola pamenepo.
Kukhala mundende five moths mkumat gud news, zachamba!!! Akhakhakha amenewa akakutulutsa amakupatsa 15 days ukuenda mwaufulu akangotha masikuwo akhoza kukugwilanso ndie mkumati gud news malo opanda ukhondo ngat amene aja kukhalamo mpaka miyez 5 eeeeh zovuta.
Shaaaa man ine ndiye ndikupita kumene bcoz Malawi wavuta uyu or akandimange no problem
Pa ntumbo pa kodi iwo akamatigwila zoti PASPRT yathu ili ndi VISSA samaziwa akunama zimene akumatigwila 6moth tikugwila jery so what?????
released them for a reason….. and the reason is for them to get their own way/money to buy tickets
Boma la South Africa lidaganiza zongomanga any illegal immigrant if he doesn’t have proper papers for at least 6 months, kenako atuluke ulele, koma ndima corruption asopanowa, ma officers Ena amafuna kena koponya m’matumba ao basi. Cifukwa pakalipano ayimisa Kaye kutumidza ma foreign nationals pandege kamba koti zimalowetsa pansi kwambiri chuma chadziko lino.
RSA govt stop sending illegal imigrant home since 2014 akuti boma la south africa limaononga ndlama zambiri potumiza anthu mmaiko awo panopa akakugwira umangoziwiratu kuti ndiwakulindera 5month then amakutulutsa
Ife tikudya mango mwa ntendere, osati mwa cheu-cheu, kikkkkk, azikupsyotani choncho.
Man tingapange manyi ake amenewo ayi kunotu kulibwino kwambiri.Matupi amasintha ndizakuduya zakuno man tamanga manyumba ana athu tikutha kulipira Xool fee sizamasewera.Kuno game iribwino
Chanzeru ndichan kukhuta mango osadya nsima, kugona osafunda blangeteso.
A man born on earth to suffer for his children and his family.
Mango kunoso alipo boss
Ife tikudya thukuta lathu osati mango.
ndiinali konko kungoti sindifuna zoyalutsa wanthu.
Enanu Mumaonjeza Two Dayz Mwayambakusasamalonda Ndiye Mabigilinso Aaaaa Zaziiii
thank u southafricans may Allah reward u more abundantly.
Osamangobwerako bwanji, kuti tizizadyera limodzi mango ophika kumudzi kuno.
Zidyani man mangowo thx
Nde bola kumangdwa kuno iya.
sitifuna
Kikkkkkk! Chief zikhalani ndi khalidwe
Mwangosowa transport yopitila ku jon ko
Kkkkkkk.
Mango ake a season waaa???
Ooh Paja akatha tilowa mu Maungu ndi Nkhaka
Zakhala bwino.
Kkkkkk mwatero
Kwambili kwake ada azigwira ntchito nanga ana ku mbanje adya chani amwene
Zoonadi chemwali
Eytu
Sure
Kodi nonsenu munali konko
Thats good thanks alot RSA
Ths is nt the first time for SA gvt to do ths
Good news.
Insha Allah
Agalu enanu simumatifunira zabwino anthu apatheba.munya manyi tikadapanga chitukuko
Better
So south Africans are good pipo and not the way we thot of them. RSA we salute you.
RSA you are different from taifa police.
Kkkkkkk eishi awagwiranso, the problem is , they take us to lindela and held us for 4-5 months then release us. While we already brock our plan.
thats grt news to hear tat
Good news.
Thanks South Africa God bless you guys not easy
aaaaaa bless them for what ngati akutuluka ulele simmesa akumalipira ma R1000 kuti atuluke
Kkkkk kod siulele?
its for free… after serving 5 months.. enanso ali nkati momwemo oti 5 months siinakwane.
Nkhani yabho anthu ena akudalira iwo kumudzi
Thank you RSA, Malawi has turned to like Zimbabwe, no food,no job,etc…you are the only hope for us….we salute you RSA!!!
Pepani konzani kwanuko
Nthawi zonse makamba zoipitsa dziko lanu kuwatama awa mukuona ngati akupatsani makobidi?tazinyadilani dziko lanu
zaziiiii anthu oipa ngati awa tingokhalira chisomo cha mulungu kuno and anthuwo kuti atuluke akumalipira ma R1000 .taganiza anthuwo asungidwa for 5 month’s mundende.nzabwino zimezo.hope hope ndiye kuti chani?.
Iwe Ndichtsiru Zoona!!U Need To Be Patriotic!
Ngati muli ndi patriotism bwanji mukusiya dziko lanu kumapita komwe mukunyozako? Malawi is dead n buried these days…nothing good…
Boza amwene samalipira olo cent musanamidze anthu
mmmh,searchng 4 grinr pasture
Abwana mulipo?
Where are they now?
Gd News!
Kulindera kumatikomera
But those people pay to get released.my cousin wer one of them and he paid R1,000.
and if u dnt pay you are released after 3-5 months
Where are they now?
My cousin is at his now.he get released yesterday.
So they have been allowed to stay in SA after the payment ?
It’s just corruption, anthuwo amatulusidwa mahala, ndithu,
after they are released basi they are free koma ukamayenda mopusa maso mwa mwa mwa amatha kukugwilanso umakalowanso. I know of a guy who got re-arrested just 2 hours into his freedom.
Komabe pali bwino kusiyana ndi depot 1000 is nothing ayipezaso akayamba ma ganyu
magobo
Kkkkkk
Adziasiya konko mpaka zaka 15 mwina azipanga ziganizo za bho!
sianthu onse ali ku RSA amagwira magobo
Nobody pays to get released
#Mathews you’re talking nonsense and you better shut up because because its not funny to pay hard earning money like R1000 for nothing..I once get arrested in 2012 and i paid R1600 to get released.Ngati simunagwilidwepo mpaka kulindera basi yamikani mulungu chifukwa enafe takumanazo nazo ku joweni kuno..You trying to be clever but wait your time will come,if not police then thieves tsosi will teach u a reason why you should always shut your big mouth and get to know life.
Ndiye
Not home affairz my be he pay to #Bosasa. Home affairz amakana ndalama bru amakuuza kut ngt uli ndi ndalama ugule tiketi ya ndege uzipita kwanu
u are talking nonsense here,u are trying to feed people lies shut up mafanas i came here 15 years back before you were born who told u that people to be released in Lindela needs money?
I agree with you @kachipande u can make plan while u are still in police station not in Lindela
Where do u kept if police catch you? is not police station? if you pay the police to Release you is not PAY?, If you have never paid police your hard earning cash then you’re lucky.some of us paid it way back..Mxim its you who is feeding lies ,if you came here 15 years does that mean you know everything you phopho?.I paid R1600 in 2012 and get release at Lindela.maybe you dont even know wer Lindela is..The same container that carry people direct to Lindela is the same container that carry me all the way from Lindela and drop me off wher i was staying.
uyabheda mafanas u don’t know anything about SA
Mxim
Anyway that’s great news if pple are getting lealised .