17 August 2016 Last updated at: 6:42 AM

Kamlepo, Mutharika keep fighting: ‘Let APM kill me’

The country’s vice chairperson of Parliamentary Public Accounts Committee Kamlepo Kalua says he is ready to die for forcing the state president to fire cabinet ministers implicated in the K577 bilion cashgate scandal.

The development follows Mutharika’s speech at the official opening of the Sugar factory in Salima on Monday, August 15. Mutharika said Kalua should submit the names of cabinet ministers who are said to have stolen money from the public purse within 24 hours.

Kamlepo Kalua, Peter Mutharika

Kamlepo Kalua and Peter Mutharika in verbal war.

The president further cautioned Kalua to “shut up” his mouth if he knows he has no evidence about ministers whom he claimed stole money from public pocket. However, this did not go well with Kalua who demanded Mutharika to name the ministers and fire them if he is really the state president.

“I am also giving him 24 hours that if he is really the state president of the country, he has to disclose the names because he has the mandate to do so than giving me that position which belongs to him. If he is to use my blood, then am really ready to be sacrificed as I did for multiparty,” said Kalua.

The legislator also wondered why the president is telling him to go to Kamuzu palace with the names of cabinet ministers implicated yet the president himself has the names.

Kamlepo said: “He is shielding the implicated ministers but he has to know that these are Malawians’ money.”205 Comments On "Kamlepo, Mutharika keep fighting: ‘Let APM kill me’"

 • Henzman kalilombe junior says:

  Kkkkkkkkkk ndale za kumalawi wins akangodzudzula boma basi wanyula,zotsatira zake kuopsezana ndi imfa shame !!!!!!!

 • Wamisala uyu inu asatitayitse nthawi,aakuleka kumuyitanitsa Ntila Banda bwanji?

 • Eeeeeee koma nde zafikapotu mpaka pamenepo kumalawiko. eeeeeee.. ayi bansi ingopangani zoti muthese nyala basi zinazo ziyiwaleni muzangophana za ziiii

 • Mukagawana mitereshedi yanuyo nkumabwera ndi ma jox ngat awa si bho zimenyanana pot mukupanga mkhola mwanu mukamaliza nkhonya zanuzo mutiuzanso

 • That’s kamulepo the true fighter

 • Onse apita ndi ntengano poika malawi padzuwa ,mbendera wapita !!!!! Wasala ndani?!!!!!!!!!!! Kaya odiokooooooo

 • Guys za ndale tiziona nthawi tapangani zowathandiza anthu amene akuvutika ndinjala basi

 • olo nsabwe itaduka president wa ku malawi ndi His Excellency professor Peter Wamuthalika mufune musafune mukafuna kumchotsa mudikile 2019 muzagwenso agalu inu ….nawenso Kamlepo kalua ngati mpweya wako watha tsogola tizakupeza usapake machimo akowo anzako … DPP 2019Bomaaaaa!!!

 • olo nsabwe itaduka president wa ku malawi ndi His Excellency professor Peter Wamuthalika mufune musafune mukafuna kumchotsa mudikile 2019 muzagwenso agalu inu ….nawenso Kamlepo kalua ngati mpweya wako watha tsogola tizakupeza usapake machimo akowo anzako … DPP 2019Bomaaaaa!!!

 • kamulepo himself said that he was ordered by the court not to reveal the names to avoid destroying the evidence, then how come the same person was bzy saying muthalika is hiding names. akanena muthalikayo nde umboni susokonekera?

 • If happened kuti waphedwa I will continue from there

 • Team Kamleopo basi, I know this guy very well, what he is talking wheither u will like it or not but its true, ndichifukwa chake lero umphawi wathu wafika pamenepa. Now the the guy “Mbendera” who choose this regime is gone, so what can u say? Mulungu si James, just wait & see

 • KAMULEPO is a coward person why u are saying that LET APM KILL ME

 • If he is tired of his life; he can afford to kill himself

 • Maxwell mbendera

 • Maxwell mbendera

 • kodi Kaluwa ngati ali ndi umboni nanga bwanji osapitisa mayinawo ku bwalo la milandu kuti anzengedwe milandu anthuwo. Zoti akakhuta kumamuchosera ulemu mtsogoleri asiyiletu izi sizipasa ulemu udindowo. Kuli bwino angotchula mayinawo osati kumatitengera pa mgong’o kuti tizibva za mayina omwe iye mwini akulephera kuwatchula. Chabwino angowathula mwa un official

 • TIME FOR DELIBERATE AUTHORITY PROVOCATION TO ATTRACT BLIND IGNORANCE SUPPORT AMONG THE POST ELECTION LOSSERS. WHICH KAMLEPO ARE YOU TALKING OF?…IF IT IS THE LUNATIC DRAMATIC IN PARLIAMENT,THEN I FEEL SORRY FOR THOSE CLAPPING HANDS FOR ONE OF HIS ACTS. YOU NEED A BED AT ANY OF OUR SCHEZO CENTERS.

 • enanu ngat mwatopa jst ruddie urself. prz hw many president arested b4 hz period. so DPP iznt 2reast mudala bt malamulo, no1and isaid no who iz abv de law,mudala ngt zavuta u”ll solve nxt time.

 • junior zomwe ukuyowoya nd zo onad suzgo boma nd nkhungu mbamva zokha2 sizinga gwirane pafunika mapemphero aku ndata ikudikira akapanga za mbwerera

 • junior zomwe ukuyowoya nd zo onad suzgo boma nd nkhungu mbamva zokha2 sizinga gwirane pafunika mapemphero aku ndata ikudikira akapanga za mbwerera

 • Uad Masi says:

  Kamulepo akanena zimakhala zowona inu olo mufuse Atcheya.

 • lazy African ntchito imene mukuyiziwa ndiyongobelekani ngati makoswe kaziķo kangonpngono koma population yokhayo kuposa maiko akulu akulu nde kukumanaso ndi asogoleli a selfish hmmm nditi chani kweni kweni,,ndine waku mpoto,chimene ndikufuna kuku a Malawi anzanga ndichoti chachikulu chofunika ndikupewa njala osati zomalozana kuti uyu ndi waku mwela uyo ku mpoto palibe chitakuthandizeni,nanuso asogoleli tayesani kuteteza zikolathulo lokongolalo poonesa ndikuwakumanisa kuwawonesa aMlw kuti ndi amozi,a Kamlepo…tadikilani kaye nanuso zofuna kufela chilungamo plz plzz yesani kugwilizana ndi Peter nzelu zimozi ngati zimene akupanga a DA,EFF nd UDM ku RSA Bingu anasokoneza za chuma Joyce nayeso anadusa ndi zake pano mukulimbana zaka K577 billion cashgate,, eeeeish,muchikhala kuti mumati muli ready to die for fight hunger atlist I cud andestand that cause the main issue in Malawi is hunger nd poor of economy ndi misewu yathu ingono ingonoyo yoti bus ndi track sizitha kupatukana at a 1nce oyenela kuti yina iyime kukatchile 4rm Dwangwa 2 Salima apa Nkhata-Bay 2 Mzuzu nde wina akufuna kuyesesa kufuna kupanga kachitukuko ngati kameneko nde nkumakhala bzy nokha kumafuna kudulana manja chili chani kwenikweni abale anzanga thandizanani chitukuko ndikuthesa njala that’s t.

 • kkkkkkkkkkkk akamlepo kkkkkkkkkkk very funny , killing you for what kkkkkkkkkkkk news maker

 • Kamlepo ndikhalidwe lake amagwa khunyu ndiye akazuka amafuna makobili nthawi yabakili amavuta pano wayambilanso

 • I walani zonse za kale “Tiyeni tione zomwe za tigwera lero

 • This is unfair for the president to work with those who were involved in Looting public funds.This is not just rumours ur is real and every Malawian is waiting for a president to take an action not only Kaluwa. My Fellow Malawians do not Support leaders just because you are sharing blood yet your children can’t go to school due to poverty and you,same people defending thieves who stole your Money!! I just don’t understand this kind of world I’m leaving in.

 • It is unfair defending thieves yet they are ministers who are there to deliver good for their people.This is not just rumours it is real.And every Malawian is waiting for The president to take responsibility….

 • Fighting with air

 • kgaaaa!!kaziko ka Malawi kunvesa chisoni kukhalila kukangana chiphokoso chosatha,m’malo moti mu fokase za njala kuti mungaithese bwanji muli bzy kulimbana opanda ziii chimene mupindule ndichani mukakhalila kumalozana zala, mwe vivumbwa mulivi nazo zelu ndali zini ko Ku Malawi y don’t u try fight hunger nd poor in our beutful land ggsus… damn….sh**t fucktup lleaders in Malawi jst being selfish in the poor country MLW I wish I wasn’t born in Malawi pussy

 • Keep it up Kamlepo no one is above the law, this government is full of thieves. Arrest them all and let them lot in jail.

 • If Kamlepo is to die we will know for sure that he is dying for the truth and I personally in his side because always boma limakhala la makani,,,,,anthu awa sanzamva ndithu,Kamlepo will die for the truth in Malawi,and Malawi is undemocratic country.

 • Aaaaaaa who can kill KAMULEPO? Impossible.plz tiyankhuliren bwana anthuwa akubisana coz amadya pamodzi.

 • Akamlepo ofaifa kale ngati inu

 • Keep it up man.we’re behind you

 • APM seems to be panic with the isue of firing his cabet for the investigation to take place, he know that some of his ministerz who are also royal to the DPP were also involved in that cash gate scandal, even he him self, but because he is now above the law so things seems to be clean on his side, I doubt if Peter will allowe that to happen unless mmodzi wama minister ake atatuluka DPP ndikuyambana ndi Peter. But big up to Kamlepo for fighting the justice, we should not only put the name of Manondo, Kasambala and Joyce on this cash gate case, try to go through with the investigations, some DPP members and ministers were also involved with ths!

 • Musamuopseze Kamlepo Kaluwa,let the truth be known,thats why no wonder olemera angolemelabe,osauka kumanhosaukabe because of such irresponsible and selfish leaders in our country,amanhowona za kachipan komwe iwo akutumikirako osati za anthu onse ayi,look at the president now is failing kutchula kagulu ka anthu ochepa komwe kanaba ndalama zothandizila anthu osauka kusiya kusamala za chikugila chawanthu ochuluka amene ali nziko muno,shame on you and God will punish you all,

 • Kamlepo he is strong man like julius malema keep it up

 • DPP and APM until 2024 amene zikumunyasa athawemo mmalawi muno

 • Thas whare .achewa ndinu ztsilu. Mumakakhala kwa mkaz chifkwa chopanda nzeluko. Kwamuko think about the future of ur chadren and the life what we live, kamlepo faiting 4 malawian we are on behand him. Agaluwa amaba amenewo amabisala pachipande msana amaone. Kamlepoyo ali lead kuwolula kapas pa nthambo. So don’t foce

 • Di Coral Spriano Zeputala

 • Kamlepo akufuna kutchuka komatu ng’oma yolira kwambiri siichedwa kung’ambika.

 • Kamlepo Ndiye ndanixo ?,kod mayesa akupasa 24 hrs kut utchule anthuwo Ndiye ukayakhulaxo za manyi ambuz zo bwanji kufuna kumuyesa president eti? Stupid

 • Anthu ena ngosekesa zedi abale. Eti kumnyoza Kamlepo ati kwawo nkuthengo chonsecho sadziwa pa khomo pa Kamlepo and kuona ku mudzi kwa yemwe akuteroyo kwawo nkomvesa chisoni zedi koma poti eti ndi wa ku mwera basi atumbwe. Kumaganiza ponyoza abale zinazi. Mpa gulu apa onani mmakomo mwanu mukuchokelamo abale. Tisamanyozane pepani

 • Akungosowa Olimba Mtima Ngati Chirembwe Oti Athane Ndi Azungu Achikudawa

 • Kkkkkkk koma kamlepo wayambatu kugenda kupolisitu apa kakakaka lyf is swt eeeh wina kumafuna dala kufa eish

 • Ndikudabwa kuti zikuchedwa pati?mesa nkhuku ikaswa imatulutsa ana kunjaaa?

 • Akumpoto achan apa kape iwe et mbuz yakutchile galu opanda mchila iwe

 • GR A NT says:

  Kaya zanuizo bola ine ndikuphwanya mavolosi patheba pano!..mkagwirana muzalembenso kuti ndidzapitilize kuseka!kakakakaka!

 • Kamlepo, stop fooling malawians! for how long will you keep on bullshiting?you first go and dry up the lake later on you clean up the government! we know you are the same due to being in opposition you seem to be good you hypocrites!

  • Munadyako ka cashgate ndichifukwa ukuyakhula choncho, sukuganizira nzika zina zikunzunzika kamba kusowa makhwala muzipatala, sxul akukweza coz ndalama palibe anaba.

 • Mmmmmmm awa atopa kale tawasiyeni

 • Kodi kamlepo Freddo akumakusutitsa chamba eti?

 • kamlepo tcha!!!!!!!!!!

 • go ahead abwana kalua tatopa ndi ma cashgate

 • No one is above the law Mr Kamlepo, we saw it in RSA with Nzuma.

 • am not a politician but idont like what Kamlepo’s saying,

 • Nkhani siyotu bwana Kamulepo muzinamizira zoti wina akuphani ayi, u are completely outside the subject. No one will kill just submit the names to the president. The president did not say that he gonna kill u, we heard when he was saying. If u want people to take ur utterances seriously bring forward the names, in so doing people will treat u as a an honest person who normally says the truth not za ganja. As concerned citizens we want u to shame the president if he is siding with his compatriots.

 • Kamulepo fuck off!!!

 • Sanabe nawo thas y akutokota ikumpweteka

 • akuphe iwe uli ndi chani galu . panya pako kamulepo ukungofuna kubwertsa nkhondo. chitsiru munthu

 • Mutengeleni ku mental ka mlepo yu,,,,,,

 • ndiwamisala kamulepo mutayeni apatsa anthu tchito

 • AAaaaaa wazeru sakudziwika

 • kkkkkkkkkkk eeeeeh two elephants are fighting udzufe mmmmmmm kulira kwa mmalawi wosauka

 • James Mkoko says:

  Iwe Kamulepo anthu (ABWENUUU) anakudziwa kale kuti ukasuta chamba cha KK Maliwa mutu wako sugwila, mmalo moti kachipani kakoko ka pp kkkkkkkk mulimbikile kuti mupambane nthawi yatha kale ndipamene mukulimbikitsa anzanu.
  Mwayiwala kuti unali paukaidi wakuja kwadziko lathu for 20years koma palibe chomwe chinakupindulila,. Inetu ndakhala kuno 3years zokha basi komatu Ngalimoto yemwe ndimayendela ine sitingafanane ayi olo pang’ono bolanso ija anakupatsa Dr Bakili Buluzi kkkkkkkkkkkkk
  Choncho usamale ukundidziwa inenso ndikukudziwa 100%*NDIKUULULA*

 • Munavotera nokha sanalowere kuseli

 • Regionalism at its best.

 • Ndinkaona ngati a Kaluwa misala ija inathatu!!!

 • sidzopatulana apa what is wrong with northern region?tiyeni tingoona zankhaniyi sindikunena izi kuti ndine wakumpoto koma pakati ndendimadana ndizomasankhana yesani kumvetsera nyimbo ya malamu Lucky Dube together as one ndiponso nyerere dzimatha kunyamula chithu chachkulu koma zina dzi?apezekanso kuti zili pamwamba pa chinthucho.

 • Kumpoto kwatani ngani yiliyapa ndiya ndalama k,amlepo more fi re my president

 • I’m in support of u KAMLEPO none will kill u the last man to be killed by these Dpp thugs is ISSA NJAUNJU becoz he was very quite . A president a Malawi ndi a chitsiru amati lero kunena zina mawa kunena zina. Atiuze 24 hrs zatha kuli ziii presidentiyu nchitsiru anthuni. Satithandiza uyu. KAMLEPO ulula chobisikacho kuti MALAWI adziwe choonadi ngakhale mbuzi zina za dpp zikudzidzimuka ndizochitikazo ambiri ali mtulo tofanato. CHANCO = 0 koma analamula kuti itsekulidwe kuli zii. KAMLEPO= 0 apereke maina a mbava 24 hrs isanathe kuli zii.

 • anthu odwaladwala amakonda kupanga phokoso akafa aziti achita kuphedwa

 • You are very right Kamlepo keep it up.

 • mcfield chewe says:

  Let the truth be known

 • Mwakhuta uko mwayamba kunena zogawanikana, ineyo si wakumpototo koma chilungamo chioneke ngat anaba anthuwo adziwidwe ndipo lamulo ligwire ntchito bt the truth z, Kamlepo is not leading ACB and Court, there the ACB and Court have mandet to put the thieves’ names on the ground to face the music. President shouldnt acuse or criticise Kamulemo. This doesnt matter race, ethenic group, regions of the country or wat ever you full pple talk.

  • Sindiwe wakumpoto koma wa PP chifukwa chake sudziwa kuti andale onse ndimbava including your president joyce banda.

  • Nde ngat ndimbava andalewo, nanga mbava yaikulu iwuziranji yaying’ono kupereka mayina ambava zinzake poti iyeyo akuzidziwa? Nkhani ndiyoti, chipani si dziko kapena amalawi, nde chulungamo chikufunika osati kuchokera kwa Kamlepo, y nt ACB and other stakeholders. I voted 4 dpp and i wl again in 2019 if possible. Thank you

  • Nde ngat ndimbava andalewo, nanga mbava yaikulu iwuziranji yaying’ono kupereka mayina ambava zinzake poti iyeyo akuzidziwa? Nkhani ndiyoti, chipani si dziko kapena amalawi, nde chulungamo chikufunika osati kuchokera kwa Kamlepo, y nt ACB and other stakeholders. I voted 4 dpp and i wl again in 2019 if possible. Thank you

 • Aona ngati angamuophyese APM omweo amaaophyesa aja kuti alowa ntchire anakwana

 • Who can kill you? Senseless man!!

 • Wachamba, mbuzi, mbutuma ndiweyo, muli ndi chani kwanuko, mbamva inu!.. mwatibela chuma chakukayekela, kaziwiziwi ndi migodi ina, tipatseni nyika yathu tiyambe kuwenga mafuta ,uwauze ambuyako North is rich wth blessed Jews.

 • Nkhotakota weed ikupweteka kamlepotu

 • wakhala pamkhate khoswe.

 • verbal war wil never take us any where

 • kamulepo mutu sugwila

 • verbal war wil never take us any where

 • Believe it to despise a leader or president is misfortune
  Read 1petro 1 if not 2 vs 15 and 17 respect your leaders as Nd talk Amicable

 • keep on Kamlepo many people are free becoz their truth makes them free. Those who are castigating or insulting you are the beneficiaries of cashgate scandal we are watching out

 • Kodi alipo president osaba.mwina achite kubwera yesu kuti azatilamulire

 • Phanani basi, Ife palibe kuluza ngakhale kupindula. Ife ndichimodzimodzi basi.

 • Kamlepo upange zithu mwa kufuna kwanu osati kukukakamiza wina zimenezo ayi.

 • Atumbuka oyamba iweyo kamulepu kodi munakakhala achitukuko nde bwezi.kwanu.kuli kuthengo iwe akakukhiya muthalikayo nde muziti.walakwa chomwe sukutchulila okubawo nchani

  • Kamlepo sakulakwitsa kali konse. Sizoona kuti peter muthalika abe mpaka k240 billion plus nyumba ku malawi housing, ndiye kwa munthu wanzelu sangasekelere zimenezi.

  • Nde chomwe akuopa kamulepo nchani awulule onsewo boma.lili ndi malamulo ake sikuti pitalayo.achite usilu lamulo ligwile tchito basi

 • Kodi a kamlepo kulimbikila zoti akupheni bwanji? mwatopa ndi moyo? kupusa basi, give some facts not ur stupit death wishes.

 • bushiri inu mazoba eti..mukungonyoza prezident mesa anatipatsa ndi mulungu,and inuyo moyo muli nawowo anakupatsani ndani…?think b4 u speak..nkhañi yaikulu ndi njala basi not zokuba ndalamazo olo agwidwe sangabwezebe,koma iweyo ukabe nkhuku lero ukalowa muchitokosi palibeso zoti mlandu tauyimitsa kaye palibe zimenezo.guyz tiyeni za m’mbuyo tiziyiwale ife maso athu akhale patsogolo basi..ndikukhulupilira kuti mulungu adzamva madandaulo athu..thankx

  • Tikudziwa kuti sanga bweze koma ena amatengelapo phuziro, ukudziwa kuti peter muthalika adaba k240 billion plus nyumba ku malawi housing?

  • yes u r talking de truth koma zomangotukwana president sitingapindepo kanthu..

  • Ukanyambitsidwatu ka ndalama mayakhulidwe ake amakhala choncho , ukufuna kunena kuti ose amene aziba tiziwasiya ndikuyang’ana kutsogolo?

  • Mutharika was given to Malawi as a head of state by god, not God!
   And if you’re down with him, go to hell just as his elder brother Bingu

  • are u a Malawian or a foreighner? Do u want to say u dont know the problems that are in the country right now? Think before u speak coz u r speaking to the public, be careful with every word from your mouth…..

 • Akanakha wakumba nkhuku ndi okhala fitsi kapena andale ena mkanamva ajatidwa koma awa mu mwana mbu make mbu tikuona timva siku lina umphawi uzkusdani

 • It is very hard for APM to reveal those wanted ministers coz DPP gained power through corruption and their aim was to protect those cashgaters and to close this chapter thus why they took a thrown in such way so it is very very difficult for him to give names and he can’t fire them coz once hav been fired, they r the one going to say more about his late brother and APM himself

 • kodi adziko lakumpoto mukulowerela zakumalawi kuno bwa?suja mumati inu muzipanga zanu sinumso malawi?lero taziwa kuti chamba chimakupwetekani,kkkkkkkk kamulepo chamba kwambiri,sizikuthandiza.

 • Omega Bema says:

  Muli bwanji anzanga a kaliyati , Henry mussa,,George chaponda ,,bright msaka,,,Joseph mwanamveka ndi a Goodall gondwe ndimakunyadilani moni moni

 • Tisaye says:

  I know Malawians are CRAZZZY, but don’t worry it will stop very shortly. We will teach them lessons these thugs and we will rise to glory again. Believe me. Then the CRAZE will have gone.

 • Good direction kamlpo!we want truth to see the light out of darkness.Bring them to justice.Anankafumbwe a malawi

 • Keep fire burning Kamlepo pitala is also behind of the stolen money musatipusise apa

 • Akuchita bwino kamulepo katangale wacjuluka

 • Kamulepo akudziwapo kenakake kwa Peter nde iwe ndi ine tikumunyoza Kamulepo ndi chinthu chopanda mzelu kufulumira kunyoza pamene sitikudziwa chilichonse, ine funso mkumati chifukwa chani Peter sakuwachotsa anthuwo pamene Malawi yonse ikudziwa kuti anthuwo ndakuba? Tiyeni tidzuke Malawi plzzzzz

 • No one will kill you Kamlepo stand justice keep fighting we r behing you

 • Gift Banda says:

  Kaya Ndizanu Ife Akumudzi Timadandaura Tikagona Ndi Njara Osatizopusa Zomwe Mukunena Agalu Inu!

 • VIVA KAMULEPO .KEEP burning Ndimwana Pitala kwa iwe

 • Malawi Will Never Grow Big, Only If We Could Have A Group Or Gang Like Bokoharram Things Could Have Change. May God Bless MALAWI, 2019 Major 1 Bushiri You Must Stand As A President.

 • Mbava za pasana ma 24 hrs k k

 • Kaya Zanu Idzo Tizingova Nawo.Koma Mudziwe kuti Anthu ndiwomwe ali pamavuto.Kuzipatala Akubwera wopanda Mankhala ndikumati Mukagule Panado.Kupusa Nose Mukukhuzidwa

 • kodi ati chani mbwenu wa diso ĺimođźiyu wayambira ķutsokotsa mkaĺe

  • Iwe sukudziwa kuti ndalama zambili mbiri zidabedwa m’boma? Peter muthalika payekha adaba k240billion plus nyumba ku malawi housing thats why akukana kuulura maina

 • Kamlepo! Akuphadi iwe!

 • God plz helps !

 • Nanga poti mkuluyoso alimomwemo mokubamo ndiye awachotsa bwanji azakewo poti iye akuopa kuululidwa ndiochotsedwawo

 • My name is Fedencia Mokaya and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past six years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { doctorolumo@gmail.com} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) together we can live an HIV free life.

 • Vingachitika yayi tili pamoza naimwe Mr Kamlepo

 • Kamulepo kanundu fodya wankulu Mpoto kaya mpaka kalekale simuzaununkha mpando wau President.Zidzatenga nthawi kuti Southern Regionazakutulireni dzisokosani choncho adzingosinthana basi.Inu kwanu kuzingokhala kuweweta basi

  • Anthu akuba koopsa sizoona kuti peter muthalika payekha atenge k240 billion plus nyumba ku malawi housing. Thats why akukanika kuulura maina.

  • Anthu akumwela ndinu zitsilu chomwe mumaziwa ndikunyoza anthu akumpoto basi. Nchifukwa chake Malawi sazatukuka coz anthu akumwela mukuba kwambiri komanso kususa zinthu zanzelu

 • He will never kill u my brother jst stand for the truth» otherwise this monkey is gona dance kwasakasa no more here in nothern region

 • Ayied Alif says:

  ndani saziwa kuti DPP ndi boma lakuba?amalawi nthawi yakwana tiyeni tisagone koma tikhale maso.wankulu pofika kutero kalipo kalipo,tiye kamlepo asakuophyezeni!

 • Mlomwe up against Mtumbuka….Check my sir name for you to know which side i have put my money on kkkkkkkkkkkk Malawi @ 52

 • Kamlepo wakwana iweyo ife sanatitwane bravo kamlepo

 • keep it kamlepo

 • Nkhani ya Gwaladi inatha bwanji

 • Foolishness at its peak

 • That’s Kamlepo I know.

 • kungosowersa kamlepo,,,winayo sadxaponda kumpoto kuno…Azagendedwa…Kill him and dance to the music that will follow…Mumaba ndalama ndiye pano mwati maphunxiro adakwera ndiye fiz ikwerenso…Chikweze fiz ndchani mabrothers akuphunzirira mmaroom a kamuzu,,mabukhu akamuzu,,diet yakamuxu yafull chiken mwaichotsa mwati mulibe ndrama…Pitni ku makerere,kubotswana ndi kujoni then decide if fiz hike z sensible…Kwatsala pangono kuti tingambe kamalawika mzigamba….

 • rascrat presidend end his bloodcrat party dpp goverment fire gonna burn you end your family

 • Koma kamlepo watikwana

 • Joyce Banda,,, where are? Malawi was a country to live in during your presidency,,,,, sizinazi ayi ndithu,,,,,, there is no visionary leadership now!!!!,,only encouraging kuba,,,

 • poor minds reader why are you fighting where we’re you all this time we don’t have a history for you in this country you must think twice before you go far why you behave like headless chicken what I know is that you are little boys you can’t soive the probiem of malawians never you are readers without future shame on you

 • poor mind reader why are you fighting where we’re you all this time we don’t have a history for you in this country you must think twice before you go far why you behave like headless chicken what I know is that you are little boys you can’t soive the probiem of malawians never you are readers without future shame on you

 • Naah !!!!……..they got not teeth to bite you Sir Kamlepo!!! These wacky dogs gotta get a life Malawi is sliding to the dark hole.Its only Kamlepo who is trying to shade light here and bcs the fucking majority still sleeping in their cocoons thus why they wanna silence you fuck that shit!!!! Malawians always hate the truth!! Jealousy,hunger,gossip and so on thus their everyday job wake up Bitches let’s support Kamlepo bcs he’s got a crew here!!!

 • I think munthu wamkulu akuziwapo kanthu zizaululika akazavaya ku ndata

 • boma la ili ndilakuba gyz likukana bwanji kugwira mau a kamlepo….ngati pali mbava zosaukitsa mtundu wamalawi ndizimenez zimaba zija zoti amalawi osapezekaso ndi ndalama m’thumba, amapanga chilichose choti amalawi ovutika kumudzi avutikitsitse….bwanji nthawi ya JB mumati ndalama zimabedwa koma zimapezeka m’matumba a anthu samavutika chonchi ? nanga bwanji mumati ndalama zimabedwa nthawi ya JB koma chuma chimayenda bwino mankhwala mzipatala amapezeka,,,,pomwe boma ili silinagwilepo akuba koma ndalama sioneka m’matumba a anthu komaso chuma sichiyenda bwino anthu amavutika .. bolani boma la JB ndalama zimabedwa kubomako ngakhale zimabedwa, chuma chaziko ndikumayenda bwino osati boma ili kumati ndalama sizikubedwa kuboma koma zika zadziko kumangosauka kumalira ndiumphawi