The most notable data bundles whose charges have been raised are, the Whatsapp monthly bundle, the smart 30 MB bundle and the cheapest, smart 10 MB bundle.
It is only a matter of days before the hike comes into effect, thereby providing room for customers to cope up.
Here is how charges have changed; the Whatsapp monthly bundle has been hiked from K500 to K560, the smart 30 MB bundle will be costing K120 from K99, and the cheapest 10 MB bundle will be costing K65 from K55.
Consumers’ voice, Consumers Association of Malawi (CAMA) is yet to comment on the matter.
Amidst the country’s economic problems, people are expecting the body to take an action as evidenced by lamentation Malawians are sharing on social media following the increase.
With less than 8% of internet usage, Malawi is one of the countries in the world where internet charges are extremely high.
According to consumers, the cost of internet does not tally with mobile operating companies’ services as they have to endure poor network coverage.
However, companies have a right to raise the cost of their services as long as they follow proper procedures.
i don’t blame them. i blame our country’s economic situation …
But y Matafale?
Ok tamva
How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.
Zoti Ndiyakumalawi Much Doubtiful Bolanso Zinazi Koma Iyi Eeeesh!20%discount Chaka Chonse Mwina Kwanuko Anzanthu Enanu Koma Ife Kuno Mavuto Moti Panopa Tayamba Kulowa Kwa Anzawowa Ziliko Bwino Mpaka 99.3% Kupita Kwaiwawa Ndi70%discount,koma Kuchoka Kwa Iwowa Kupita Kwa Anzawowa Ndiye Mpaka 10%discount Zamanyazi Ndithu Koma Amati Ya Amalawi Zonama Ndithu.
Always with us?????
#Airtel….. Wise people’s choice
Tell them…..don’t just hike the charges you should also improve your network…..network yanu panopa siilibwino
Tell them…..don’t just hike the charges you should also improve your network…..network yanu panopa siilibwino
tnm sikanakweza mitengo koma yikanangopanga improve ma services ake monga internet yiri very slow ngakhale akweza volume bundles!
tnm sikanakweza mitengo koma yikanangopanga improve ma services ake monga internet yiri very slow ngakhale akweza volume bundles!
Zantel .Tigo,Airtel,Vodacom .Hallotel. Karonga north network imapezeka fans ikugula panopa simcard aku tz malawi kuba too much
Zantel .Tigo,Airtel,Vodacom .Hallotel. Karonga north network imapezeka fans ikugula panopa simcard aku tz malawi kuba too much
koma malawi mpaka na fb kumalowa ndi mb ife apa Tz watsap fb ulere koma instragra and yotube ndiimene umalowa ndi Mb 50shg ukasungunula umapasidwa 120Mb koma uko nde amakukumbani kwambiri
koma malawi mpaka na fb kumalowa ndi mb ife apa Tz watsap fb ulere koma instragra and yotube ndiimene umalowa ndi Mb 50shg ukasungunula umapasidwa 120Mb koma uko nde amakukumbani kwambiri
TNM has poor internet, very slow even my grandmother is faster than it so they are raising the price the the services are poor, what a shame!
akuba awa anayamba kale kudya ma bundle, anakweza kale,
10mb yimatha kukwana 24hrs @mk55, 30mb imakhalakonxo@mk99, koma pano onsewa 1day mkutali, 1hr , 2hrs koma fone yaying’ono! kuba baxi!
Ndipo simmene network yawo ikubowela olo kugula bundle mpaka nthawi yake kutha ukukanika kulowa pa net nxaaa
ndaganiza mofatsa ndipanga phone SIM yopanda kuyuza ma unis mwajayila koma ndi yamtengo wa phingo amene angayikonde call me 0883333049
Increasing tarrifs for poor internt services… Thats TNM for you
ine ndingopenoha adzanthu mukuphuzira tknlg muphuzire kupanga phone yopanda kuyuza ma unis mwina Malawi angayiwale kubeledwa
Aaaaaa mawa ndigule airtel card nde zichan kuthawisa ma customers
ndizoonadi
Tnm nanu mwayamba zanu.Mumapanga zimaprofit zochuluka kwabasi.zina mukusowa nazo zochita kumapanga sponsor mipira yomweso siyokupindula mudziko muno.Amalawi ka ndalama kawo ndi konkaja kovutaka nde mukufuna muwakaweso zowona.
At Airtel We Don’t Stress
Liu lakuti tnm alwayz with u ndilabodza komanso lopusitsa kuti munthu uziona ngati ziribwino koma ayi zisali choncho. masiku ambiri ndi malephera kuwerenga nyasa times chifukwa cha poor network ndiye kukweza ma tariff it’s pure daylight stealing.macra nanu mungoyang’anira zinthu zikuonongeka osachitapo kathu zoona? Macra nayonso ndi sleeping dog.tikufuna ma servises abwino osati muzingotibera ndalama thru ma tricks.management ya tnm kulibeko anthu anzeru(lack of crietivity and sound decition within the marketing department)sungatege nsomba zoduma ndi kumagulitsa mokwera ntengo, tnm go back to your desk and think if what u have done is best for your customers(komabe ndi kudziwa kuti ndinu anthu osanva simungasinthe ngakhale mutaona choilungamo.shaaaaaame you!!!

Airtel konzeka ndikubwera kwaiwe, tnm yandikanika ine
Airtel konzeka ndikubwera kwaiwe, tnm yandikanika ine
high tarifs , poor network
high tarifs , poor network
Another option is there Airtel simple wautauli
Another option is there Airtel simple wautauli
TNM. YAONJEZA. BOLA. AIRTEL. BASI. TNM. KUBA. BASI.
TNM. YAONJEZA. BOLA. AIRTEL. BASI. TNM. KUBA. BASI.
Tnm behaves as if it doesn’t know problems in Malawi what’s the meaning of raising tarrifs for a poor network
this iz a wrlcome development popeza tinazolowela kubeledwa kale ; all net work providers ku mw mbava zokhazokha mukweza bwanji pomwe net ili poor in terms of fast
this iz a wrlcome development popeza tinazolowela kubeledwa kale ; all net work providers ku mw mbava zokhazokha mukweza bwanji pomwe net ili poor in terms of fast
kukhala m’malawi ndi kulimba mtima
Asowa chochita tnm inali kale pano kuba kwachuluka timaunits tosachedwa kutha ,ndalama zikuvuta inu nkumakweza cholinga mulemere ndinu ,ala shame on yu
ndinasiya kugula internet bundle ya Tnm
Tnm ine ayi network imavuta chigawo chamazuro even 3g network
chimozi mozi kuno ku jozi mtn ikudula kwambiri
They are failing to satisfy us, interms of High quality service delivery. Anytime when a goods/service provider decides to plaud up the price, comes with a reason that they want to improve on delivery but nothing comes to a drill. I know that they will be tabling the same noise. Ok, lets agree, what if there will be no upladdering in their Service delivery?
The Bible said it.
These are the Last days!
owooh! kodi ? koma asaonjeze kwambiri
Don’t forget TNM Super league has just kicked off!
Ine zanga pheeeee kuno ungogula R5 MTN mkusungunula R3 data ndi 20 MB imeneyo zakumalawi download, fb sikhan, watsapp ndi ankolo kkkk kapena kungo ika R10 amamkuuza use R7 to get 55 airtime yoimbira MTN to MTN and 10 MB internet.
Nde njodulanso kumeneko R3, 20MB?
Kkkkkkkkk Ukuichepetsa
Nanenso phee pa Tanzania Tigo network 50shg ukasungunula MB 120 one week koma fb ndi watsApp ndiulele
Ur internet is a joke u guys
Kaya zanu izo ine kuno kunjoya ndi FREE CELL C.
Kkkkk ndikabwela yanga nd airtel
Tikanakhala ogwilizana amalawi bwenx titasiya kugwilitsa ntchito network imeneyi mpaka atakonza network yawo komanso kusisa mitengo
akuti akufuna kubweza zomwe amapereka ku mpira
Buy Malawi!
They are doing business and you want handouts bundles .
Grow up if you don’t have enough for yourself then don’t feed your phone.
That’s why muscians are not benefiting from their art we enjoy their songs without paying them.All businesses are not their to make you happy but to make and maximize their profits
inu ndiolemela eti?
There not their
Maximise profit?????
Ku Southern Africa konse, dziko losauka Malawi, lodula ma units Malawi! Zopusa basi!
Networ yake yofoyirayo ndiye azikweza mitengoso kuba kumeneko.
Prices r getting high, but network acces is still poor!!
Mot Ayambe Kaye Akomza Network Yawo Yochtsa Manyazy
koma? mpaka choncho? kodi kuMalawi kuno vuto ndi chiani kapena pakuti kuli anthu amantha ngati nkhuku? iyaaa! zandinyansa kwambiri anduna muli kuti tawalalatirani ngati muja mupangira muja
koma? mpaka choncho? kodi kuMalawi kuno vuto ndi chiani kapena pakuti kuli anthu amantha ngati nkhuku? iyaaa! zandinyansa kwambiri anduna muli kuti tawalalatirani ngati muja mupangira muja
have mercy pls…..
hiking tariffs and yet they can’t upgrade to 3.5G.very crooked macra officials not giving licenses to other mobile companies from abroad.this monopoly is killing the consumer
hiking tariffs and yet they can’t upgrade to 3.5G.very crooked macra officials not giving licenses to other mobile companies from abroad.this monopoly is killing the consumer
Internet tima user Airtel, inu a TNM chomwe munakhonzako nde ndi bundle yama txt basi. Data bundle yanu tikaombora imangopanganxo expire chifukwa chovuta network. Nde mukuti mwakwezanxo mitengo yanu?
Internet tima user Airtel, inu a TNM chomwe munakhonzako nde ndi bundle yama txt basi. Data bundle yanu tikaombora imangopanganxo expire chifukwa chovuta network. Nde mukuti mwakwezanxo mitengo yanu?
ndipo ma txt a airtel ndotchipanso broo… k80 ma text 70
ndipo ma txt a airtel ndotchipanso broo… k80 ma text 70
AIRTEL will follow soon
This is the Government company I wonder why they are hiking the price?
This is the Government company I wonder why they are hiking the price?
Airtel ndi deal man”
Airtel ndi deal man”
Kma si boo
ogulitsa adzakondwa ndipo ogula adzazuzika.kodi dzikoli chokomano ndi chiyani?? mwachita bwino kukweza mtengo koma netiweki yanu silibwino mukoze.pakati tinkaona ngati ndi 99% yanga imapangitsa ndiye momwe mudachotsamu tikungowona palibe chosintha. ikakhala nkhani yobulauza iyi ndi mbiri ya kale….imangoti loading…….. Gudhope Zuze Heinz Matale Aleck Ngusengwa Robert John Jones Magola

after registering a high turnover, so what is this for? malawian businesses ah! leaves a lot to be desired. what is the directionless buy malawian campaign for? empty rhertoric. why should someone buy malawian goods and services which are generally of poor qaulity.

#Vote with money i.e. buy shares in TNM if you think the hike will generate more profits. Otherwise invest in the competition and sell your TNM holdings.
#Vote with money i.e. buy shares in TNM if you think the hike will generate more profits. Otherwise invest in the competition and sell your TNM holdings.
ZIKOMO BWANA kUMAKWEZA CHONCHO MASIKU ÔTSIRIZA AWA http://www.666.com
aaah tingosiya za internet tnm tipeza line ina
These network provider just findout that these days people depend on internet, but mtn always expensive
These network provider just findout that these days people depend on internet, but mtn always expensive
Tel them netwek yawo ikuvuto
too much
Mutikhululukire pepani.
kkkkkkkkk. ok!?
tnm mbuzii
Milking an already thin cow, koma pcl as a shareholder amachita behave as if siamalawi
Milking an already thin cow, koma pcl as a shareholder amachita behave as if siamalawi
Shame
Have U Seen That bro Chiku Fumbauzi
munakayamba kukonza internet yanu musanakweze. Internet yovuta koma kudula
munakayamba kukonza internet yanu musanakweze. Internet yovuta koma kudula
Akawalala
kupanda competitor ko anthu amenewa, kodi za new one zibwera liti ife tizisiye iziye izi?! aah!
kupanda competitor ko anthu amenewa, kodi za new one zibwera liti ife tizisiye iziye izi?! aah!
That’s good news thanks tnm
bola kugula Aitel sim card ndithu
kuba tnm
eeeh maluzi ake amenewa nde kutipwetekatu uku
eeeh maluzi ake amenewa nde kutipwetekatu uku
Mwina uhule wa PA net ungachepeko
Mwina uhule wa PA net ungachepeko
Kudzolowera kubera anthu a mphawi basi.
Kudzolowera kubera anthu a mphawi basi.
kaya!
Mxiiih jausilu yeleyo!