Jaffali Chande leads Bullets, Nomads in disputes


Jaffalie Chande
Jaffalie Chande
Jaffali Chande: Causes disputes.

Nyasa Big Bullets General Secretary Kelvin Moyo has called on Football Association of Malawi (FAM) and Super League of Malawi (SULOM) to intervene in Jaffali Chande’s proposed move to Mighty Be Forward Wanderers.

Bullets, FAM, SULOM and Wanderers are in a tug of war over Chande’s controversial transfer to Nomads as SULOM, FAM and Wanderers are all saying the player is a free agent while the people’s team are insisting that the player is under contract with them until August.

Bullets now want Wanderers to buy out the remaining months of the contract for K800,000.

Speaking with a local media house, Moyo stressed that justice must prevail from all angles of the story.

“Justice must always prevail on everything. We submitted the contract papers to SULOM and FAM and today we are told that Chande is a free agent, what do they want us to do?” he queried.

“We know that there is a reason why they are hiding the contracts documents from us, but they are not punishing us, instead they are punishing the player because as Bullets we will not sit down and allow Chande to play for Wanderers before his contract expires,” he added.

194 thoughts on “Jaffali Chande leads Bullets, Nomads in disputes

 1. malawi wathu za changamuka liti? chilichonse timangofuna zachidule basi osasatilanso malamulo kya mwina tikudikilanso mzungu kt azatiuze chochita

 2. Lets count to 1,000 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16 17 18 19 20 21 22 23 24 25 26 27 28 29 30 … …… Just kidding .. I had you starting to scroll faster than mayweather running.

 3. koma bwande wationjeza anzako ampira sanafike APA koma kumene akupita akukudziwa yolilitsa ng,OMA sichedwa kulira ngati kkkkkk wazzwa eti Ali pakati pa mikango nzake wina amkatchedwa andolo anamvutaso choncho kaya pano Ali kuti

 4. Kkkk malawian futbo umburi bas in futbal samaletsa kugula contract en nkhaniyi at the end zipezeka kt chande ndi free agent umburi bullets excutve munakasungabe ma paper documents tizit ku club house kwanu kulibeko ma pc?let chande go

 5. You nomads fools don’t you know that when signing a player that has a binding contract with another team you have to pay for a remaining period? Kapena mulibe 800,000 yo? Forsake

 6. ine ataa sulom sindidzayikhulupiriraso APA akulimba ndi nkhani ya chande ya straight forward Nanga yaDedza ili pati yofunika changu ndi imeneyo coz it involve matimu ambiri osati izi kukonda ndalama zimuvuta kkkkk Ayi Toto ine

 7. ine ataa sulom sindidzayikhulupiriraso APA akulimba ndi nkhani ya chande ya straight forward Nanga yaDedza ili pati yofunika changu ndi imeneyo coz it involve matimu ambiri osati izi kukonda ndalama zimuvuta kkkkk Ayi Toto ine

 8. vuto lake mbuzi za bullets ndikupanda nzeru kwaoko mtima ukuwawa kuti wachokelanji nde fam ilowelelepo xichani get a life u bastards…….

 9. vuto lake mbuzi za bullets ndikupanda nzeru kwaoko mtima ukuwawa kuti wachokelanji nde fam ilowelelepo xichani get a life u bastards…….

 10. Vuto Lili Ndi Neba Uyu Wa Be Backward Wonderloose Ndi Limenelo Kukonda Kugula Dzakuba Zopanda Reciept Chaka Chake Ndi Chino. Tikupsyotani Nonse A Wonderloose Kuzolowela Kugula Dza Belo. Pasana Panu.

  1. Ngati noma yagula chokuba , ndekuti wakuba nndani pamenepa?

   Fodya sakukuthandiza komwe uliko iwe STANFORD

 11. Vuto Lili Ndi Neba Uyu Wa Be Backward Wonderloose Ndi Limenelo Kukonda Kugula Dzakuba Zopanda Reciept Chaka Chake Ndi Chino. Tikupsyotani Nonse A Wonderloose Kuzolowela Kugula Dza Belo. Pasana Panu.

 12. These people called Bullets have got cancer of the mind. When they get players from other teams nobody makes any such noise,but when some teams do likewise they cry cry cry cry cry cry like cry babies. The problem with this team is that they think they should always have others dance to their uncivilized hehavior why, nobody knows. Probably,with their little brains and savagery behaviour they think they can boss over the entire nation of Malawi. These people should once and for all learn to be hamble citizens in the game of football. they should reform and stop to behave like brutes they continue to be. By the end of the day it is Nyasa Manufacturing Company that will pay for the folly of these Ndirande vendors.

 13. Emanuel eboue has been banned for 1 year due to contract dispute.Chande be warned u might jorpadise ur carrier. Fam Sulom and clubs get civilized its high time we soughtout this mess.

 14. Chingambwe bullets fans plz leave our Chande alone end respect his vital choice. Kodi mulibe zina zochita, kathandizeni ma player anu kugulitsa ndudu mu street uko fusek!!!!

 15. if NBB was once in Love with Chande I think its wise to let him go than wasting time with just one player after all NBB is a Club where players fight hard for game time,I strongly think its time to let it go and if tampers continues to fly its the National Team which losses at the very end of this!! a good example is Tony Chitsulo he is a victim of such Squabbles. That’s why I feel NBB to let him go as an off loaded player

 16. nbb zimuvuta anazolowera kutenga maplay choncho ofunika alandile chindapusa ameneyo mbuli zamapaper zimenezo malamulo akuwaziwa koma kufuna kusokoneza zinthu,koma utapanga motani inu ligi simungate tiwona muthamangisa kochi chaka chino wina atuluka thukuta ndi ukwache chaka chake ndichino maule woye

 17. BB it not change bcause of chande,lets let him & will meat in tnm super leggie with chande & B back ward wanderlaz, & all fans of nyansa BB don’t b cafused with dat. Nyansa BB it b & it will b antill 4 ever, uthink BB it can not whithout chande’s, wat about wen chande in epack. Noma think twice b4 speack. BY BOS MAN in CHILEKA

 18. The lad has a running contract of a year and five months with Nyasa Bullets which he signed on 14th August 2014 until August 2017 in the presence of former General Secretary Harold Fote. Fam and Sulom have this copy but are aiding the player to join the team they support. May justice prevail and rules and regulations be abided to.

 19. hahaha,, i have now realised that Jafali Chande ndi Katswiri kkkkkkk,,,ntchanuyu ndi mbambande,,no wonder NBB ingolongolola ,, musiyeni mwana apange dollar while the sun is still shinning

  1. lets wait and see coz ena akuti ali ndi contract mpaka 2017 while Chande is saying that ali ndi ya 2016,,they will both submit their contracts to Sulom then sulom will decide

  2. lets wait and see coz ena akuti ali ndi contract mpaka 2017 while Chande is saying that ali ndi ya 2016,,they will both submit their contracts to Sulom then sulom will decide

 20. Amalawi tisaxhite zaumbuli,tiyeni tiphunzire kulemekeza chiganizo chanzathu….do u think Chande can save bullets whole hearterdly after forcing him to stay?

 21. Jafali chandeyo ma battery ake, afam wo ma battery awo kaya mukut a sulomwo ma battery awo a bulletswo mabattery awo BIG UP 2 B4WAD ! Ine ndlibe problem!

 22. Let him go Bullets will never change,bb is lyk Arsenal never depend on a player,bt we as a family of bb what we wan’t on chande’s move is justice

 23. tangotayani asatipase masoka ife,bullets de pipos team simadalira munthu mmodzi ayi.Muloleni apite bas akathere komweko kt fanz idziwe kt bullets ndi bullets.

 24. Jst last wk, mr kelvin moyo was asked about the same issue en this is what he said,en l quote,chande’s contract will expire in five month meaning in augast,l wonder to hear that the same person has changed the tune today by saying that chande’s contract wil come to an end by 2017 augast.HOW COME?

 25. Jst last wk, mr kelvin moyo was asked about the same issue en this is what he said,en l quote,chande’s contract will expire in five month meaning in augast,l wonder to hear that the same person has changed the tune today by saying that chande’s contract wil come to an end by 2017 augast.HOW COME?

 26. Kama agulugunyinda awa bwanji osamusiya Chande wasankha yekha basi watopa kugulisa ndudu afuna akagulitse magalimoto basi, KOMA NOMA AAAAAAAAAAAAA

 27. Kama agulugunyinda awa bwanji osamusiya Chande wasankha yekha basi watopa kugulisa ndudu afuna akagulitse magalimoto basi, KOMA NOMA AAAAAAAAAAAAA

 28. Koma NDUDU FC!!eish!!kodi pakati pa ASULUM,AFAM ndi inu anzelu ndani?nankha ngati contract yakeyo siinathe mukulekeranji kubweretsa fairo yakeyo?ngati zakuwawani mungonena,ife maplayer ndiwazi tikhonza kukubwerekani,koma zoti jafalie abwereranso izo muiwale olo mwini wake adanena ekha tikumva ndimakutu athu.ngati zavuta muisova nokha JAFALIE pakadali pano ndi wa B4WD wamkaka okhaokha basi

 29. Koma NDUDU FC!!eish!!kodi pakati pa ASULUM,AFAM ndi inu anzelu ndani?nankha ngati contract yakeyo siinathe mukulekeranji kubweretsa fairo yakeyo?ngati zakuwawani mungonena,ife maplayer ndiwazi tikhonza kukubwerekani,koma zoti jafalie abwereranso izo muiwale olo mwini wake adanena ekha tikumva ndimakutu athu.ngati zavuta muisova nokha JAFALIE pakadali pano ndi wa B4WD wamkaka okhaokha basi

  1. Mukuona Ngat Kutenga Chande Ndie Mwatenga Bullets? Mukuona Ngat Mutenga Super Leage Mwauponda? Mwalemba Mmadz Awelenga……… Maliza Wekha Kape Wa Be Backwardswe Coz 4ward Mudafoila Magiya Woooooo Pepa Neba

 30. Kupusa kwa ma oficial a bulets, munthu achoka bwanj ali nd contract? mwaziwa lit kut contract ikutha 2017? koma neba usandichitise manyaz wamva!

 31. Kupusa kwa ma oficial a bulets, munthu achoka bwanj ali nd contract? mwaziwa lit kut contract ikutha 2017? koma neba usandichitise manyaz wamva!

 32. Ife ngati a Bullets Fc sitilola mpaka Chande ndima Player amene salemekeza ma Contract awo ndi mateam a Lape basi and SULOM FAM aphunzile kuyendesa mpila mosakondela mbali, tikafika ku Court muziwiretu SULOM & FAM, milandu ku court yampira izazako muziwe zimenezi mathelo ake wina atulapansi ku FAM & SULOM

 33. Ife ngati a Bullets Fc sitilola mpaka Chande ndima Player amene salemekeza ma Contract awo ndi mateam a Lape basi and SULOM FAM aphunzile kuyendesa mpila mosakondela mbali, tikafika ku Court muziwiretu SULOM & FAM, milandu ku court yampira izazako muziwe zimenezi mathelo ake wina atulapansi ku FAM & SULOM

 34. Zinakumana mbuli zokhazokha!!…nzamapepala izi zimafuna sukulu!! pilizi…koma inu wandaloose …kuzolowera zapawindo basi!!….watitopetsa neba ukafune kwina kokhala …kkk!!!!

 35. Bullets is like will Arsenal never change evin if he can go, bt what we wan’t justice at Arsenal we had fabrigas,nasri,Rvp,ardebayor,song,clichy and so many athers bt they ar all behind arsenal. bullets without chande will never change.

 36. Fam ndi sulam muphunzire posalowerera nkhani yomwe simunafufuze kweni kweni iwe walter nyamilandu wa mau ngati uli munsuko iweee

 37. Jafali chande APA afanana ndi Tony Chitsulo. Sitimuonaso mma ground athu. Zikomo chandy, pita kumuzi,akakulembe pamakopon achaka chino then mlime fodya. Mukamaliza muzatipeza kuno Ku Mzuzu timatrainer lachinai pa prison ground. #socialfootball

 38. Ngati akunganiza kuti nbb itha pogula chande akunama, ngati akufuna kuti ithe izichinyidwa apeze njila yo ngula masapota onse a nbb ndipamene izathe, akubukile atamunamiza kanaje kuchoka ku nbb kupita kwa nyelele zinawakanikaso osatichinya ata, nbb simuthu imozi ayi ,

 39. Jafa ali ndi matha akuona m’mene team iliri panopa koma akanadekha noma kwa munthu oganiza sangapite ku noma kodi chande osafusa doni chisulo anathera kuti mesa ndi noma yomweyo inathesa doni ngati zili ndalama zake zida.akuganiza zoti bb itha akachoka akunama tizathyolera limodzi apite azipita akathe azatifuna bb sizatha ilipo neba akupanga matha aziona.

 40. Bring the documents tione kkkkkkkkk.Nkhani ndiyakuti Chande anali Bullets ndiye kuchokaku zasonyeza kuti Bullets yatha.

 41. Chingambwe bulet koma kaya kkkkkkkkkkk Eeeee bola kunthazi basi…………….chande kkkkk

 42. Harold Fote Wakana Zoti Chande Anasaina Contract Yotha 2017.Akuti Naye Akudabwa Kuti Abullets Akuzitenga Kuti Zimenezo.Iye Wakanitsitsa Ndithu Kuti Sakuzidziwa.And Zikunveka Kuti A Bullets Apanga Forgery.So Lets Jst Wait Kuti Zitha Bwanji Bt 4gery Is A Dangerous Crime.

 43. Should this little boy cause merhem ??????just let it go Remember what the shoulder has failed to carry the neck can not carry!!!!!Sulumba was there he failed to tick look @him know @ pples team ask Red lions

 44. I want to give a testimony on how I get cured from HIV/AIDS. As I was browsing through the internet on how to get cured, I saw a lady testimony praising DR Williams I never believe it before until I tried it and it really work for me am very happy right now may God bless him. this is an opportunity for you to get cured contact him via [email protected]….. and also you can contact on whatsapp number +2348143143878 THESE ARE THE DISEASE Dr.DR WILLIAMS CAN CURED. HERPES. HIV/AIDS. CANCER. LOVE SPELL VIRUS.

 45. Ndizimene Ife A Nyasa Timadzwa .Chande Anabedwa Nd Majapanese Osat Kumugula Mwa Peace.Ndie Ndizimenezi.Inu A Sulom Komanso A Fam Solve This Case Amicably Otherwise You Will Continue Bringing Misunderstandings.More Fire Maule!

 46. Ndizimene Ife A Nyasa Timadzwa .Chande Anabedwa Nd Majapanese Osat Kumugula Mwa Peace.Ndie Ndizimenezi.Inu A Sulom Komanso A Fam Solve This Case Amicably Otherwise You Will Continue Bringing Misunderstandings.More Fire Maule!

 47. tizngovomerza kt kwath kuno ckwampla bttler tzngoonera wa azunguwo bac nanga tzt samadzwa momw amkachokapo kt contract synathe & contract imakhala yoxapatsana ndalama….tzngolima bac malamuro ampira xtmawazwa tonxe

 48. No no mr Masapo,before we let him go lets teach them a leason first,kupanga izi sikuti kumufuna koma maplayer ena aphunzile pa CHANDE KAYE kuchoka pakhomo mwamwano next time ukafuna kubwelela umapanga manyazi now lelo ndizi CHANDE AKUYENELA KUKHALA UNTIL 2017 ASAKUMENYA.awo ndimalipoti tikumva

 49. Blazi itanva kuti Jafali chande ali ndi contract ku nyasa Bb inagwa pansi kulila kkkkkk iiiiiiii nyamata wanjomba ujaaa

 50. musaiwale kuti Kelvin Moyo wayamba kupanga demand 800.000 werengani nkhani yomweyi muone, za 2017 ndizabodza ndipo ndibodza lamkunkhunidza kunama kuti contract ya Chande yapezeka

 51. Osalimbana naye chandeyo azatha ngati katani ameneyo kunali jimmy zakazaka lero anatheratu bullets ndi timu yomwe sizaguga mpaka kale ine ndiwa bullets basi noma ndi manyaka.

 52. Nkhani ya Jafalie Chande pamene imaoneka ngati ikupita kumapeto,kwaphu likanso nkhani ina.Ngakhale zimaveka kuti Jafalie Chande contract ya Chande simapezeka,ngakhalenso zimamveka kuti contract yake imayenera kutha mu August 2016.Zonse zaululika ndipo umboni wapezeka pamene contract ya Chande yapezeka.Contract yomwe inasainidwa ndi General Secretary wakale wa Bullets Bambo Harold Fote komanso mwini wake Jafalie Chande,zikusonyeza kuti Contract ya Chande inayamba pa 14 August 2014 ndipo imayenera kutha mu 14 August 2017 Mukuyankhula kwake Technical Director wathu Bambo Billy Tewesa wanena kuti poti Jafalie Chande anasankha kukasaina contract ku Wanderers mopanda kutsata ndondomeko zake,iwo anena kuti ngati wanderers ngati ikufuna zokambirana ndi Bullets adikire 2017 basi kutanthauza kuti Jafalie Chande akungoyenera kudikira mpaka 2017 kuti azatumikire Wanderers.Copy ya contract yatumizidwa kale ku Fam ndi Sulom kuti awone kuti nkhaniyi athana nayo.Koma akapezeka olakwa Chande pankhani imeneyi,alandira chilango.

  1. forging zopeka, apa omwe akuyenela kusamala ndi a bb chifukwa zikapezeka kuti mapepalawo ndiabodza alandila ban yoopsa kwambiri chifukwa Fote akuti wakana zamphekesela zimenezo ndiye asamale a bullets angaone mbonaona kukakamila satero ayi

  2. Signature ndiyomwe imakamba kut anasaina yekha nanga bwanji mwini wake wakhala sakuyankhapo kanthu zomwe zili zoona signature yanu munthu angasaine? Zitheka bwanji zimenezo @ mussa waison

  3. Am bb fan koma i dont care kuti chande asewera kuti……..koma kumalawi ngati akuyendera fifa rules tiziwona……….ukanakhala mpira wakwanu/wakwathu kumuzi bwezi tikuti asiyireni a Nomads

  4. Am bb fan koma i dont care kuti chande asewera kuti……..koma kumalawi ngati akuyendera fifa rules tiziwona……….ukanakhala mpira wakwanu/wakwathu kumuzi bwezi tikuti asiyireni a Nomads

  5. ma vendor ogulisa ma memory card anyimbo kale inu simumadziwa poyamba paja za 2017 mtima ukukuwawa kasambeni asasamba inu….

  6. ma vendor ogulisa ma memory card anyimbo kale inu simumadziwa poyamba paja za 2017 mtima ukukuwawa kasambeni asasamba inu….

 53. pano ndiye avomelezano kuti alandila ndalamazo? Kkkkkkk koma bullets umbuli siudzatha mpaka kale. Asadandaule ndalama tipeleka bolani ationetse Duplicate ya contract yo chifukwa sitingapeleke ndalamayo popanda kuona contractiyo chifukwa mwina akutinamiza

 54. KODI INU MUKUFUNA CHANI SULUMBA MUNAMUTENGA KOMA IFE SITINAVUTE KOMA CHANDE KUNGOCHOKA IIIIIIIIIII KUVUTA BWANJI TANDIYANKHENI SIMUMATI ASASEWERE MPAKA AUGUST MWAKANA KUKUPATSANI 7 LERO MUKUTI 8 FODYA WAKUZUNGUZANI MUTU ETI ENA AKUTI CHANDE OFUNIKA KUMUDULA MIYENDO ZOONA AWA NDI MASEWERA OSATERO

 55. Why don’t you let him go?bullets idzakhalabe olo without chande. Panali maplayer otchuka pa Malawi lero as likuti?(proud to be a NBB fan)

  1. Its true Bullets will be their without Chande but we must teach these players 2 respect their contracts we know maybe their was some problems which he was facing but he was suppose 2 follow the right way.

  2. The player will be let free but procedures should be followed. Fam and Sulom should rise above all and not take sides like in this case we have already seen them allowing wanderes and chande finalizing the deal without the consent of the parent club in this case Bullets. This clandestine move is orchestrated by the two bodies having interest therein. I hope NBB officials are working on this and that at the end of bussiness they should emerge victors.

 56. Time to honour contractual obligations. Mr Chande musove zimenezi but with these unproffessional SULOM and FAM zitivuta. I see another court injunction like that of Dedza…

 57. Koma ndie kt chande ameneu amauona kwambiri? eish khan kumangokhalira chande, chande amatero? lne kutopa bwaaa chaka chino kwa NEBA N NBB chikopa pa ground ndikasewere ndine mwina naneso ndikutchukako kumat aminah, aminah kkkkkkkk maule woyeeeee wakaka!!

 58. Fam and solom instead of kukhala khala pakati obweletsa mtendere kuma club mukubweletsa mikangano plz sithani tikukhulupilirani bwanji

 59. Neba atamva kuti Jaffalie Chande ali ndi contract ndi NBB yomwe ikuyenela kutha mu August 2017 ndikukutsimikizilani kuti ma Japanes mitu siyikugwila pano onse a Nyerere aliku Zomba mantal hospital

 60. Chipuwa adachoka ku noma amati alibe contract ndi noma neba umatseka lero zili paphuno mwambi walero “maliro ngajenu kunong’a kwembera nsona “

 61. Zaululika kuti jafali chande ali ndi contract ndi BB mpakana August 2017 osati chaka chino mu August ngati mmene timadziwira, izi zili chonchi ma paper a contract a jaffali chande atapezeka ndi bungwe ra Sulom. APA tsogolo ra Jafali chande rili mmalele chifukwa akuyenera kuyamba kusewera mpira mu chaka cha 2017. Big chim for the people’s team.

Comments are closed.