Malawian man shot dead in SA

168

Thugs in South Africa have shot dead a Malawian man who was guarding a school in Johannesburg.

South Africa PoliceAccording to another Malawian staying in South Africa, Maimba Chingati, the deceased has been identified as 27 year-old King Kaira Nkonje who was working as a security guard.

Maimba said that on Thursday night Nkonje was guarding the institution and the thugs shot him dead when they wanted to rob the place.

The remains of the deceased are expected to land in the country soon since the man’s boss has promised to be responsible for all funeral arrangements.

Nkonje hailed from Nkhandwe village in the area of Traditional Authority Malengachanzi in Nkhotakota district.

In a related incident, another Malawian Katasefu Kamwendo has died in the rainbow nation after he was involved in a taxi accident.

According to Adam Bulian who knows the deceased,   the man was staying in Limpopo in South Africa.

Kamwendo hailed from Chisoti village, Traditional Authority Malengachanzi in Nkhotakota district.

Share.

168 Comments

 1. Tionge ngati uli ufiti anakuphuzitsayo pasana pa agogo ake ndipo iweyo udzafa uli osawuka kapolo wa kapolo iwe koma kwanu pali amene anamwalila kulankhula ngati chitsilu koma uli opusa ukanakhala okongolaso ndikanati bola kapuku wa munthu mulungu adzikukhululukila

 2. Sorry anthu anayamba ndikale kugwira job yaulonda yinalikut yakwana kale time mukhoza kunena zambiri pena paliponse imfa yimamupeza munthu . R.I.P

 3. Chamba sizifunika tionge ngat kwanu kulibwino osapanga comnt zopanda pake.wukakwela pamsana panjovu usamati kunja kulibemami. RIp zandikhuza.

 4. Nanunso Mwanyanya,otsalao Bwerani Muzizandigadira Zosowa Zanu Muzazipeza,Nanga Kofuna Ntchito Mwakagula Imfa?Nanga Ife Kumudzi Kuno Tidziti Nchiyani?,chipitileni Opanda Chithandizo,mudatisiya Kale Pa Umphawi Sitinaone Kusintha Kuchoka Kwainu,mwina Ndidandaulo Lathu,mumasiya Mabanja Kuno Kumakakwatiranso,tikondwa?

 5. Ndipotu ulonda waku Joni ndikuno Ku Malawi ndiosiyana even ndrama ya mulonda Ku Joni ndi wa police wakuno Ku Malawi ikuchepa, nthawi yangokwana basi kaya kumalawi imfa ikadampedza Rip mchimwene

  • Kungoti chilungamo chimawawatu,, olo abwere kuno adzataniko anthu ntchitonso kumangolembana nokha nokha bola kumangokhala Ku Joni konko,, komanso ndanena izi chifukwa anthu mumanyoza kwambiri ulonda waku Joni siwachisawawatu

 6. chonde abale nonse mukamafuna kuyakhula mudzinganizila ali bale wanu ataphedwa motero. musaone ngati kugwila tchito yaulonda kunali kufuna koma amafuna kupeza zofuna moyo wake ndizomuyenereza nsamafuna kupepha kwa munthu komanso panali achibale amene amadalila kuti achimwene kapena amalume atithandiza. pakadali pano manja alI mkosi kuti angwila mtengo wanji mzelu zawathera ndimavuto ali kumalawi nsikuli bwino ngakhale enanu muyakhula zambwerela mugoyakhulila kusavinidwa. Kodi ndinu mtundu wanji wa anthu opanda mzerunu ? mukuona ngati ife kunzagwila tchito kuno ku joni tonsefe tigakhale opusa inuyo kumalawiko mwalemela muli ndi chani ?mukanakhala olemera nsibwenzi mutathandiza anthu ndi njala yavuta kumalawiyo. musanzabwerezenso kuyakhula mwamatama ndinzakutukwanani motheratu. Munzilemekeza imfa palibe amafuna kumwalila mwina inu kwanu nsumafatu kuyakhula motero. Ambuye akukhululukireni palibe mukuchidziwa ana Anjoka inu

 7. A S is a fucking country i rather just go for business there.people dont respect life they are somany loosers. people who just want easy money but thats not way things work work first and get money

 8. A S is a fucking country i rather just go for business there.people dont respect life they are somany loosers. people who just want easy money but thats not way things work work first and get money

 9. Abale imfa ya anthu ena musamaphwekese ganiza uli ngati iwe kapena bale wako ungatani muzibweza mau moto umapita komwe kwasala tchile tionge ungatani ali brother wako ku malawiko wayankhula kupusa kwambiri ndipo zandinyasa wava

 10. Abale imfa ya anthu ena musamaphwekese ganiza uli ngati iwe kapena bale wako ungatani muzibweza mau moto umapita komwe kwasala tchile tionge ungatani ali brother wako ku malawiko wayankhula kupusa kwambiri ndipo zandinyasa wava

 11. Jean ntchito ya ulonda iri pena paliponse padziko pansipa, ndiye makamaka ukutanthauza chani? Nawe Tiwonge ukafuna kuyankhula udziyamba waganiza kaye. Sikuti anthu amene amapita maiko akunja amakondwera ayi amasiya banja ndi abale chifukwa chamavuto ndiye ngati iwe wakwanira tangoyamika mulungu wako.

 12. Jean ntchito ya ulonda iri pena paliponse padziko pansipa, ndiye makamaka ukutanthauza chani? Nawe Tiwonge ukafuna kuyankhula udziyamba waganiza kaye. Sikuti anthu amene amapita maiko akunja amakondwera ayi amasiya banja ndi abale chifukwa chamavuto ndiye ngati iwe wakwanira tangoyamika mulungu wako.

 13. Anthu amene muli kumalawi inu kuno ndikovuta zikacitika zinthu sibwino kumati zofuna kumeneko sikulankhula. Komaso amene alankhula zacambawo adziwe kuti nawoso yawo ilipafupi.

  • what do u mean buy that do u know minimum wage 4 security personel here its 180rand per day convert it into kwacha its how much think b4 u comment

  • yes its 180rand..but its nothing there..think about accommodation ..kumeneko..athu mmayenda mobisala y..bola nzilima olo business hiyaaaa uphawi sumapha aaaa

 14. #Tionge uziyamba waganiza bhobho usanayankhure chinthu anzako sikufuna kupita mayiko ayini ake amafuna kuti apeze chosowachaw kapena kuti athetse umphawi wayo kusafuna kuti aziba kapena kuyamba uhule ndengati iweyo uliochita bwino kaya ndkwanu ingomuyamika ambuyee kti sumawaona mavuto chifukwa ukanakhala kuti umawaona sibwezi utalankhura zopusa zakozo wandbowa mxiew

 15. Dziko lathu lili ndi vuto presdernt.saziwa chochita angayitanitse zovala kuti anthu azimugula pamene dziko ndila umphawi moti aganizile ayankhule ndi makamupane afataleza awapatse ndalamayo kuti atsitse iye kukagula zovala ndiye ndichani zachamba eti{kulikose ukhoza kufa} R.I.P basi wawutali mani