Mayaya threatens to organise demos

161

One of the country’s rights activists says the hunger situation in the country is pathetic and has threatened to organise anti-government demonstrations if authorities will not supply maize to Admarc depots.

The activist, Billy Mayaya, last week organised anti-government protests which were expected to happen on 10th march but he later called them off after law enforcers refused to give him a go-ahead.

Billy Mayaya

Mayaya: We need change..

He however said he has been to Karonga, Balaka and Bangula and has not been impressed with the maize situation hence he might be forced to organise demonstrations if government will not address the problems quickly.

Some quarters however said Mayaya called off last week’s demonstrations because he was bribed by government sympathisers.

But Mayaya has trashed the claims saying that they were aimed at destroying him.

”Those allegations that I was bribed to call off the demonstrations are just rumours aimed to ruin my reputation,” said Mayaya.

Share.

161 Comments

 1. Is he broke already, has he used all that money on booze? After receiving those millions from DPP he is back to making his noise for more. I wish to urge all Malawians not to continue being preyed on by this vulture. Let him do that alone, refuse to be taken for a ride by this good for nothing so called third grade activist. If anything he can demonstrate with villagers from his village, and probably his family.

 2. Billy Mayaya ndiwe mbuzi ya munthu wamva.Ukawauze amako,abambo ako akazi ako, ndi ana ako mupite ku mademonstrations-ko.Mxiiii

 3. Mr mayaya, werengani mateyu 24v1 mumalize caputa conseco, mmalo moitanisa mapemphero mukuitanisa mademo, mulungu kumusiya mbuyo?kodi muziyembekeza zabwino zokhazokha kucokera kwa mulungu?ma demo a pa 20 july bwerani mutiuze zipaso zake. Bwanji tipemphe kwa mulungu tisanayambe zimenezo?zanja lake ndilopasa ndipo azatipasa zomwe tizisowa tikapempha mu dzina lake

 4. Uyelekeze ndi uchitsiru wakowo tikawongola chimutu chakocho chokhala ngati phondacho,umawona ngati ndife zitsiru eti?anakuuza ndani kuti uzimenyera ufulu wathu?wapeza njira yoberano zakoma kape!

 5. Kodi Mayaya ndi wa ku Mzuzu? Chifukwa ndikumenetu kuli madolo oziwa kugwira ganyu yomacha mademo. Akamachaso zimangowonjezera mavuto malo mochepesa

 6. zopusa . ngati wakwiya menya akaziako then uswe katunduwako kuti tidziwedi kuti wakwiwa. bwanji mumaganiza ngati mbuzi yamano kusi? ndiye tikapanga ma demo chipindule ndichani ? ngati if property will be damaged adzavutika ndani? hope chomwe chingawonongedwe is in malawi and it has a % it contribute to better if of another malawian ? akulu inu muzinganiza ngiti mulindinzelu

 7. Mayaya waonetsa mayaya. Mmalo mowauza anthu kuti alimbike ulimi wa nthirira ndi ng’ambayi ayi koma mademo. Mkulu woganiza ngati mphemvu

 8. Akulu mukuwasiya ma MP akufuna ndalama zambiri kusiya umphawi wa anthu. Akulu munalima inu chaka chino mwina mukudikira azungu akupatseni ngat zili choncho vry shame . A big man like you dn’t knw hw to hold a hoe kkkkkk

 9. Akulu mukuwasiya ma MP akufuna ndalama zambiri kusiya umphawi wa anthu. Akulu munalima inu chaka chino mwina mukudikira azungu akupatseni ngat zili choncho vry shame . A big man like you dn’t knw hw to hold a hoe kkkkkk

 10. Demo yachakudya yosagwila. Vuto lilimdziko muno ndi utsogoleli wamaso mphenya a chitukuko, kugwa kwa Ndalama yathu, kukwela kwa zinthu ndi zina zotero. Just 4 yr information, instead ov improving or expanding the roads in LL city they making maintenance. LL city iwoneka liti kuti ndi city. Late Bingu anayambapo koma zinadzavuta ndi 2nd wife samapeleka langizo labwino bcz 2nd term take sanachite chilichonse. Komaso inasokoneza ndi infa. Mzimu wa Bingu uwuse mwamtendere.

 11. Demo yachakudya yosagwila. Vuto lilimdziko muno ndi utsogoleli wamaso mphenya a chitukuko, kugwa kwa Ndalama yathu, kukwela kwa zinthu ndi zina zotero. Just 4 yr information, instead ov improving or expanding the roads in LL city they making maintenance. LL city iwoneka liti kuti ndi city. Late Bingu anayambapo koma zinadzavuta ndi 2nd wife samapeleka langizo labwino bcz 2nd term take sanachite chilichonse. Komaso inasokoneza ndi infa. Mzimu wa Bingu uwuse mwamtendere.

 12. Anthu enanu mumadabwisa zochitika zanu munthu wankulu ngati iwe basi nkhani ikhale yachisokonezo basi kodi mumagani ndikuphazi kapena inosinthawi yoti nkumaloza munthu zala kapena kumuika wina pa pressure ngati kuti iyeyo ndimulungu ayi bwanji osanena kuti tonse tikhale ndi special day of praying mwina mulungu nkutikomela ntima bwanji mwina zikanatanthauza kanthu kusiyana ndizopepela zanuzo mumakodwa ziwawa zikamachitika eti chifukwa choti mwina ambilinu chili mmagazi chuma chanu cholinga anthu osalakwa azivulala kapena kuphedwa kumene mukatelo inu ma benefits lololo think twice zikoli sila ma davals ayi ndi mulungu kumwamba so take care chiweluzo chingazayambile paiwe

 13. Anthu enanu mumadabwisa zochitika zanu munthu wankulu ngati iwe basi nkhani ikhale yachisokonezo basi kodi mumagani ndikuphazi kapena inosinthawi yoti nkumaloza munthu zala kapena kumuika wina pa pressure ngati kuti iyeyo ndimulungu ayi bwanji osanena kuti tonse tikhale ndi special day of praying mwina mulungu nkutikomela ntima bwanji mwina zikanatanthauza kanthu kusiyana ndizopepela zanuzo mumakodwa ziwawa zikamachitika eti chifukwa choti mwina ambilinu chili mmagazi chuma chanu cholinga anthu osalakwa azivulala kapena kuphedwa kumene mukatelo inu ma benefits lololo think twice zikoli sila ma davals ayi ndi mulungu kumwamba so take care chiweluzo chingazayambile paiwe

 14. Shupiti zako,iwe kaya akuti Mayaya ukufuna kutivulalitsa,uzitipeperetsa eti? Ndisaname ayi Admark yakwathu kuno chimanga chumabwera kwambiri, nthawi zina kawiri pa week.

 15. Shupiti zako,iwe kaya akuti Mayaya ukufuna kutivulalitsa,uzitipeperetsa eti? Ndisaname ayi Admark yakwathu kuno chimanga chumabwera kwambiri, nthawi zina kawiri pa week.

 16. nkhope ngati manyi amowa wa napolo.kape iwe ukatenge anthu akuntundu kwanu udzapange nawo match.mxieeeeeeee.ku mango pus is a anthu basi

 17. Osamatitenga ngati opusa tisiyeni tizivutika koma musatitenge ngati makasu mavuto athu asapange kuti inu mulemele zoputsana osangopepha ngati mulibe ndalama bwanji mukutengela kambakoti ndi ife akumuzi kapena kusaphuzilakwathu kapena uphawi wathuwu musati ngwilitse ntchito pazithu zosayenela palibe chomwe ndimapindulapo

 18. Ichi nde chitsilu chophumzira basi,ufulu mumamenyerawo wa ife?tinakuuza kuti uzitmenyera ufulu?ma demo anuwo simukhalapo pamangopezeka mbava zokhazokha.uzavale suit yakoyo uzamatche ndi ana ako ife ayi,#mbuzi

 19. Ameneyo ndiopenga kwambiri. Ngati anthu ali ndi njala ndiye mademo angawapatse phindi lanji? Bwanji osapeza zina zoti muzichita bwanji? Nyengo inayamba kuvuta mu 2014 mpaka pano zokolola sizikuonaka bwino ndiye inu mukulimbana ndi munthu oti za nyengo sizikumukhudza. Maiko ambiri mu Africa muno zomera zaonongeka kamba ka ng’amba yomwe yavutayi, bwanji osangogwada pansi nkupempha kwa yehova kuti atichitire chifundo. Mademo achani apapo?

  • Sukunama ife tikumayenda mnjira monsemu mu Zim,mmozambique monsemu even parts of SA chilala chokhachokha zitsiru nzimene zimayimbira mmanja anthu ama bungwe enawa nkumapita ku ma demo iwo osaitanitsa chithandizocho bwanji ngat ali akufunadi kwabwino?zotumidwa ndi akapasule basi.

  • Muyende muone mmene dzuwa likung’ambila ngakhale mbali ina ya south africa komwe amadalira ulimi anthu manja ali mkhosi cha ku rustenburg uku. Ndiye mukamapanga mademo anuwo muzafikenso kuno muzapangenso ma demo . Koma ndikuchenjezeni mukangophetsa anthu osalakwa mudziwe kuti mwazi wao uzafunidwa kwa inu pa judgement day

 20. Why ddnt u go wt the Parliamentary Committee to the Mwami Border in Mchinji to witness with your own eyes the arrival of 30trucks carrying Maize frm Zambia?

 21. Ngati ukufunila agalu ako nena usanamizile ife, unawona kuti nthawi ya chisanu choyela chimakhala ndi zovuta? Siya ife week ikubwelayi tikuchoka mumavuto limodzi ndi yesu wathu.

 22. Kma Mayaya yo ndosaganiza ndee akumupanga threaten ndaa? or apange ma demo akewo ndee zmenezo zbwerexa chmanga? nd anthu ngat iwowa who r misleadin’ Malawians mmalo motuuza znthu za mzeru apa bas kukhala mkumaganiza za ma demo

 23. Chimtuwitsa anakupatsa chakuthera nthawi yomweyi? Ukayenda wekha ku msewu kumeneko, munthu wa njala ine mphamvu zomatchira ndiribe. Usandisokonsere, nsete za..!