Floods besiege Blantyre


Floods besiege Blantyre- Malawi24

Walira mvula, walira chigumula cha Noah! Flash floods have submerged Malawi commercial city of Blantyre today as people blame Blantyre City Assembly for poor drainage system in the city.

Malawi Blantyre Floods Malawi Floods Blantyre

 

More details to follow

62 thoughts on “Floods besiege Blantyre

  1. Koma ndiye chinali chimvulatu…… Dela la Blantyre Chigumula labweretsa Chigumula Ku BT kkkkkkk pepani anzathu mumakhala muja mu mati ndi mu city yapamwamamba pa dziko lonse lapansi

  2. Kkkkkkk bt tikolola chakachino ndi mvula imenei. Amene zawonongeka boma silithandiza mwachangu zipepesen panonokha. Apm alibe ploblm.

  3. Takhonzani ma drainage system kumeneko ma engineer inu. Bwanji kuononga zinthu za anzanu?chonchi madzi alowa mmashop. Magalimoto anzanu chonchi mmaganiza bwanji Kodi? You should replace for something for those damages u have caused. . Be competent pliz!

  4. Town planning okay but problem is that drainage system has been blocked. Poor allocation of structures blocking waterways. This is not flooding. Most of structures that are being constructed are blocking waterways. Theres poor interpreration of town plan system that was developwd way back. Let town planners wake up; see this and interprate their capacity as regards to this problem. Uku nkuyamba chabe ikafikapo kukhala bwanji?

Comments are closed.

Discover more from Malawi24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading