Man arrested for stoning President Mutharika’s face on a billboard

1,317
Peter Mutharika

Mutharika: Stoned

Chikondi Saidi aged 26 is in the hands of police after he was seen with a pile of stones at Lunzu, Blantyre stoning an image of Malawi President, Peter Mutharika, police say.

According to assistant Police publicist in the Southern region, Peter Mchiza, Saidi was netted after the law enforcers got tipped by some people in the area about the incident which took place close to Lunzu Primary School .

He was stoning Mutharika’s billboard which has messages about Decent and Affordable Housing Subsidy Programme which is being championed by the Democratic Progress Party (DPP) led government.

Police fear that the acts by Saidi who hails from Mazale village in Traditional Authority Kapeni in Blantyre culd have stirred violence.

Share.

1,317 Comments

 1. kkkkkkk koma Malawi zomangana wafika pena yaaa akayankha mlandu wotichani sono? haaa ine ndikapeza zima post zake ndimang’amba bullshit

 2. kkkkk mbuzi za anthu pali chifukwa chomumangira munthu pamenepo? Kodi mwatha mapulani chani? Mukuwona ngati nthawi yakamuzu ino? panotu tili mu fourth generation sizopusa mukupangazo.

 3. Kkkkkk apolice njala yomweyo mpaka misala. Ndayenda mayiko osiyana siyana ndikumawona zikwangwani za president zikung’ambidwa. What more peter, no,no,no iwe wapolisi wayamba misala. Talimbanani ndi awo akutibela ndalamawo. Apa wawonetsa moyo wawukapolo apa . Kapena anaba ndalama zija ndi abale ako? Bwanji osakamanga awo akugwira ntchito yowona za ndalama. M’masuleni munthuyo , pangani manyazi ndithu.

 4. aa wat z billbords? Z dis 1 maize? Or maybe z electricity? .aaa fokofu peter asandisokoneze mutu wanga owila karewu ndikukwera kwazi2 ngat mukumane naye wagendayo mumuuze kut adzatenge miyala ina kuno kut akammalizepo bwampiniyo. musayerekeze ku ndipeza ku inbox inu aphwawo a pitala ndikuswana ngat lambe ndi2

 5. aah guyz sanatumidwe ndi abigman kuti amumange muthuyo chinari chiganizo cha iye yekha maringa ndinjarayi ndikukhala kwantawuniko mwina angakwezeredwe maripiro zamanyi nkhosi ngati chiwara basi .,,,

 6. aah guyz sanatumidwe ndi abigman kuti amumange muthuyo chinari chiganizo cha iye yekha maringa ndinjarayi ndikukhala kwantawuniko mwina angakwezeredwe maripiro zamanyi nkhosi ngati chiwara basi .,,,

 7. Thats bullshit kodi apolice aku malawi bwanji kupusa? Nde akatsekula mulandu otichani? ok akakalowa mu khoti adzikalankhulana ndi billboard not wapolisi kapena wina aliyese chiboard cho chidzikayankha!! muthalikayo ndi mulungu?

 8. amene mukunyozanu mwangosowa umunthu.ndi mlandu umenewo muziwerenga constitution,after all chithunzi cha president,simunaone apolisi akumanga anthu ochotsa ma polo a magetsi,rubbish

 9. What important or development z the billboard brings to local ppo? N what important or development the so called Peter on the billboard billboard brings to Malawians!! This shows uncountability v that idiot so called Peter on the board stoning him! Malawi z still looking 4 a gud leader not lyk this one! N it was a very big mistake this old man into power! Very shameful!

 10. Nose mwa comenta ndinu anthu oipa osakonda Dziko lanu ndiso atsogoleri anu, muzifusa tidazionapo ife kungotchula dzina lokha umatapidwa basi ndie lero muti palibe mlandu? umene amayankha azake kale

 11. Nose mwa comenta ndinu anthu oipa osakonda Dziko lanu ndiso atsogoleri anu, muzifusa tidazionapo ife kungotchula dzina lokha umatapidwa basi ndie lero muti palibe mlandu? umene amayankha azake kale

 12. Nose mwa comenta ndinu anthu oipa osakonda Dziko lanu ndiso atsogoleri anu, muzifusa tidazionapo ife kungotchula dzina lokha umatapidwa basi ndie lero muti palibe mlandu? umene amayankha azake kale

 13. Nose mwa comenta ndinu anthu oipa osakonda Dziko lanu ndiso atsogoleri anu, muzifusa tidazionapo ife kungotchula dzina lokha umatapidwa basi ndie lero muti palibe mlandu? umene amayankha azake kale

 14. Amene mukuti sanalakwitse kugenda chithunzi cha president pa gulu bwanji inuyo mukazipedza simumagenda ,, tingodikira term ikatha then tidzasankhe wina

 15. Koditu guyz anthu ngati akusangalisidwa nawe sangapange izi anthu koma Vuto mlakuti Akuluwa anthu sakuwuna ayi mchifukwa chake ngakhale kuwona photos yawo angokhalangati awona chilombo chija amati chadzunda .for example inuyo guyz muganiza kuti akuluwa akanakhala kuti anthu akuwakonda A homowa akanamuwonelela anthu ozungulira malowo akuti azigenda? Apa palibe kulakwa uyu amaseweletsa chipilala moti Apeter avulala?moti awatengela ku hospitol ku SA Tandiwuzeni abale inu mwina ndikapeza mpata ndikawone chifukwa ndimakhala kufupi ndichipatala chija anafela abale awo chija ku Johasback. Mkanakhala loya uyu mkanamuyimila ulele

 16. Pamenepo sanalakwire munthu,koma walakwira chithunzi amachigendacho. Ngati nkhaniyi ikafike pa court,akuyenera kukakamba ndi chithunzi cholakwiridwacho osati munthu. Palibe kukhomelerana pamenepo.

 17. Mwati chani???? kugenda billibord basi wanjatidwa ameneyo?????God forbid!!!osayiwala kuti manwespaper ajatu mumajambulidwaso nkhope zomwezo koma anthu akumakagwiritsantchito kutoilet oyambilira nkukhalanso amene amanga wogendayo!!!mayo Malawi why??????

 18. So how is that a crime? Maybe the government& Malawian judicial system must focus more on pressing issues.

  I will understand if the guy is charged with damage of property.

 19. Ma president wa ndi a kathawi kochepa kumanga munthu cox of muthu wina wake woti akupanga za ana ake not zaziko ayenela kugendedwa kungokhalila kuyenda basi osa sover za anthu womwe ali ndinjala bwanji inunso apolice mulibe ntchito akuba akukanikani uko koma malimbikila zinthu za ziii osamakeyenda ku chigwiri mukasake akuba ku ndilande ku makhetha ku mbayani ku dzolozolo kwa sonda apolice amasiku ano achuluka ndi mantha

 20. Umbuli ndichinthu chotsautsa timalimbana ndizinthu zopandapake mmalo momayanganira mbali yomwe tili maudindo omwe tilinawo ndiye munthu oti ubongo wake ukugwira ntchito azikalimbana ndi kugenda chithunzi chansogoleri wadziko mmalo moti aziziganidzira momwe ali ndidzomwe akuchita zina zomwe timalimbananazo ndizomwe zizapangitse kuti umphawi tsazatithere sidziko lamalawi lokha lomwe lilipamavuto tayendani muone maiko enawo anthu momwe akuvutikira kamudzu adayankhula mau akuti xool sinclass mokha koma kuyenda umaphunzira zina ndiye achimwene mwaugula mulandu ndimapadzi .

 21. Aaaa zausilu basi kungogenda chithuzi basi mpaka kumumanga chithuzi chakecho chingatithandize chani oro tingachipase ulemu ngati iyeyo ndi amene analephera kutithandiza ara kulibwino akanachi otcherathu kapena kuchipyora kuti tisazachioneso apolice nawo ndi amene akuvutika kwambiri kandara kochepa chifukwa cha Wa chithuzi chomenyedwayo asaaaa

 22. kuchepa nzeru kugenda chipepala f0dya ameney0. apitenaye ku z0mba ku mental Hpt. Zikung0 ufanana ndi anthu aja ankakana kugwiritsa ntchit0 ndalama ija ya K200. Yabakiri amati iw0 sangagwiritse ntchit0 ndalama ya Bakiri amene adavutika ndindani? Apas0 kugenda chipepala wavutika ndindani ? 0genday0. F0dya Basi.

 23. Amene amamugenda pa Billboard’yo ndi amene akupangitsa miyoyo ya tonsefe kuvutika,Omanganunso kungoti chifukwa ndi ntchito,zinazi muzikana.

 24. Amene amamugenda pa Billboard’yo ndi amene akupangitsa miyoyo ya tonsefe kuvutika,Omanganunso kungoti chifukwa ndi ntchito,zinazi muzikana.

 25. Alangidwe basi akuononga chitukuko chadziko ngati ali ndi nkhani mumtima mwake bwanji osapita konko ku State house’ko ngati akafikeko apindula pogenda chibillbord’cho

 26. Alangidwe basi akuononga chitukuko chadziko ngati ali ndi nkhani mumtima mwake bwanji osapita konko ku State house’ko ngati akafikeko apindula pogenda chibillbord’cho

 27. This Iz Rubbish Why Arrestin An Inoceot Man 4 Stoning The Foto Of Stupit President? Zikutikwana Agalu A Boma Inu!People Of Lo Intellectual Capacity And Education {POLICE} Muziwona Pomanga Anthu Mumasiya Mbava Zokwiwa Ndikumanga Wosalakwa!

 28. This Iz Rubbish Why Arrestin An Inoceot Man 4 Stoning The Foto Of Stupit President? Zikutikwana Agalu A Boma Inu!People Of Lo Intellectual Capacity And Education {POLICE} Muziwona Pomanga Anthu Mumasiya Mbava Zokwiwa Ndikumanga Wosalakwa!

 29. Ndi zoona amangidwadi. Wina anamangidwa atamenya theche mphaka wakufa kale mphepete mwa nseu, apolisi atamuona anamukwidzinga nawo unyolo. Ndipo a khothi anamuweru zaka khumi ali kundende. Khulupilirani.

 30. What kind of respect is he lukin 4? Alipo anthu amene asali mmaudindo but they do respected alot chifukwa cha khalidwe lawo ndizochita zawo n they deserve. How can u expect someone to respect u yet palibe chanzeru chilichonse ukuchita? Omangidwayo angolemekeza malamulo not mwini chinkhope chopindikacho and ulemu samachita kupempha no,,, uzichita zanzelu anthu akulemekeza

 31. Amachokera kogula shuga ndiye wapeza kuti wakweranso,ndalama anatengayo sinakwanire.akanatani munthu uyu? kugenda woyambitsa basi kkkkk

 32. Man agenda billboard wa angopezera tsoka ku Lunzu konkkuno kuli ang’ambi ama2kwana president za mthupi lonse mot apolisiwa amawadziwa bwno aleka kuwamanga iwowa?

 33. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: dr.collinsherbalhome@gmail.com or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: dr.collinsherbalhome@gmail.com AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS..

 34. So u people u r supporting the guy,now i can see malawi is full of stupid educated people. So if u talk of hanger shud muthalika come and farm in ur farms how stupid ar u,why cant relie on ur on,for how long will u be a beggers. And u ar the same people if u find street beggers u just press up ur wind screen.

 35. Better him , palibe chomwe walakwa cuz billboard siimv kuwawa ngati zamunyasa achose nkhope yakeyo munseu n aikemo za ma auto parts cuz imaenda mu nseu ndi galimoto osati iyeyo ekha

 36. bwanji ativomereze tizigenda chilichonse mu nseu?dziko likhala lotani?umenewu ndi mlandu.amangidwe gwapeyo basi.dziko lililonse sangamusekelele finye ameneyo.munthu wa zaka 26 wopanda manyazi ngati uyu sinnamuone.moti azikathamangathamanga kumagenda?nkhope ngati gwaladi

 37. bwanji ativomereze tizigenda chilichonse mu nseu?dziko likhala lotani?umenewu ndi mlandu.amangidwe gwapeyo basi.dziko lililonse sangamusekelele finye ameneyo.munthu wa zaka 26 wopanda manyazi ngati uyu sinnamuone.moti azikathamangathamanga kumagenda?nkhope ngati gwaladi

 38. bwanji ativomereze tizigenda chilichonse mu nseu?dziko likhala lotani?umenewu ndi mlandu.amangidwe gwapeyo basi.dziko lililonse sangamusekelele finye ameneyo.munthu wa zaka 26 wopanda manyazi ngati uyu sinnamuone.moti azikathamangathamanga kumagenda?nkhope ngati gwaladi

 39. bwanji ativomereze tizigenda chilichonse mu nseu?dziko likhala lotani?umenewu ndi mlandu.amangidwe gwapeyo basi.dziko lililonse sangamusekelele finye ameneyo.munthu wa zaka 26 wopanda manyazi ngati uyu sinnamuone.moti azikathamangathamanga kumagenda?nkhope ngati gwaladi

 40. bwanji ativomereze tizigenda chilichonse mu nseu?dziko likhala lotani?umenewu ndi mlandu.amangidwe gwapeyo basi.dziko lililonse sangamusekelele finye ameneyo.munthu wa zaka 26 wopanda manyazi ngati uyu sinnamuone.moti azikathamangathamanga kumagenda?nkhope ngati gwaladi

 41. bwanji ativomereze tizigenda chilichonse mu nseu?dziko likhala lotani?umenewu ndi mlandu.amangidwe gwapeyo basi.dziko lililonse sangamusekelele finye ameneyo.munthu wa zaka 26 wopanda manyazi ngati uyu sinnamuone.moti azikathamangathamanga kumagenda?nkhope ngati gwaladi

 42. bwanji ativomereze tizigenda chilichonse mu nseu?dziko likhala lotani?umenewu ndi mlandu.amangidwe gwapeyo basi.dziko lililonse sangamusekelele finye ameneyo.munthu wa zaka 26 wopanda manyazi ngati uyu sinnamuone.moti azikathamangathamanga kumagenda?nkhope ngati gwaladi

 43. yeah he shld be …thats vandalism at its best…thats the word used when one destroys property ….learnt that in sec school after stoning our own school….period…ndipo he should rot in jail…thats really, really bad ndipo mkudabwanso kuti enanu mudabwapo chani apa…..amalawinso taonjeza …mwana wanu atamagenda chithunzi chanu kamba koti simubweretsa chakudya pakhomo simungamuswe inu……i shld say this “zimenenezi mzopusa ndithu”

 44. yeah he shld be …thats vandalism at its best…thats the word used when one destroys property ….learnt that in sec school after stoning our own school….period…ndipo he should rot in jail…thats really, really bad ndipo mkudabwanso kuti enanu mudabwapo chani apa…..amalawinso taonjeza …mwana wanu atamagenda chithunzi chanu kamba koti simubweretsa chakudya pakhomo simungamuswe inu……i shld say this “zimenenezi mzopusa ndithu”

 45. yeah he shld be …thats vandalism at its best…thats the word used when one destroys property ….learnt that in sec school after stoning our own school….period…ndipo he should rot in jail…thats really, really bad ndipo mkudabwanso kuti enanu mudabwapo chani apa…..amalawinso taonjeza …mwana wanu atamagenda chithunzi chanu kamba koti simubweretsa chakudya pakhomo simungamuswe inu……i shld say this “zimenenezi mzopusa ndithu”

 46. yeah he shld be …thats vandalism at its best…thats the word used when one destroys property ….learnt that in sec school after stoning our own school….period…ndipo he should rot in jail…thats really, really bad ndipo mkudabwanso kuti enanu mudabwapo chani apa…..amalawinso taonjeza …mwana wanu atamagenda chithunzi chanu kamba koti simubweretsa chakudya pakhomo simungamuswe inu……i shld say this “zimenenezi mzopusa ndithu”

 47. yeah he shld be …thats vandalism at its best…thats the word used when one destroys property ….learnt that in sec school after stoning our own school….period…ndipo he should rot in jail…thats really, really bad ndipo mkudabwanso kuti enanu mudabwapo chani apa…..amalawinso taonjeza …mwana wanu atamagenda chithunzi chanu kamba koti simubweretsa chakudya pakhomo simungamuswe inu……i shld say this “zimenenezi mzopusa ndithu”

 48. yeah he shld be …thats vandalism at its best…thats the word used when one destroys property ….learnt that in sec school after stoning our own school….period…ndipo he should rot in jail…thats really, really bad ndipo mkudabwanso kuti enanu mudabwapo chani apa…..amalawinso taonjeza …mwana wanu atamagenda chithunzi chanu kamba koti simubweretsa chakudya pakhomo simungamuswe inu……i shld say this “zimenenezi mzopusa ndithu”

 49. yeah he shld be …thats vandalism at its best…thats the word used when one destroys property ….learnt that in sec school after stoning our own school….period…ndipo he should rot in jail…thats really, really bad ndipo mkudabwanso kuti enanu mudabwapo chani apa…..amalawinso taonjeza …mwana wanu atamagenda chithunzi chanu kamba koti simubweretsa chakudya pakhomo simungamuswe inu……i shld say this “zimenenezi mzopusa ndithu”

 50. Go to America ask Geoge Bush adagendedwa ndi nsapato LIVE kamba ka ulamuliro wake,nde kugenda billboard mpaka kumanga?ichi nchiyambi akugendadi LIVE ndithu…….

 51. Go to America ask Geoge Bush adagendedwa ndi nsapato LIVE kamba ka ulamuliro wake,nde kugenda billboard mpaka kumanga?ichi nchiyambi akugendadi LIVE ndithu…….

 52. Go to America ask Geoge Bush adagendedwa ndi nsapato LIVE kamba ka ulamuliro wake,nde kugenda billboard mpaka kumanga?ichi nchiyambi akugendadi LIVE ndithu…….

 53. Go to America ask Geoge Bush adagendedwa ndi nsapato LIVE kamba ka ulamuliro wake,nde kugenda billboard mpaka kumanga?ichi nchiyambi akugendadi LIVE ndithu…….

 54. Go to America ask Geoge Bush adagendedwa ndi nsapato LIVE kamba ka ulamuliro wake,nde kugenda billboard mpaka kumanga?ichi nchiyambi akugendadi LIVE ndithu…….

 55. Go to America ask Geoge Bush adagendedwa ndi nsapato LIVE kamba ka ulamuliro wake,nde kugenda billboard mpaka kumanga?ichi nchiyambi akugendadi LIVE ndithu…….

 56. Go to America ask Geoge Bush adagendedwa ndi nsapato LIVE kamba ka ulamuliro wake,nde kugenda billboard mpaka kumanga?ichi nchiyambi akugendadi LIVE ndithu…….

 57. Mmmmmmm why those police there are like to arresting innocent people, there don’t have another job, shemmmmm to those employees (police) akupanga anthu osalakwa,

 58. Mmmmmmm why those police there are like to arresting innocent people, there don’t have another job, shemmmmm to those employees (police) akupanga anthu osalakwa,

 59. Mmmmmmm why those police there are like to arresting innocent people, there don’t have another job, shemmmmm to those employees (police) akupanga anthu osalakwa,

 60. Mmmmmmm why those police there are like to arresting innocent people, there don’t have another job, shemmmmm to those employees (police) akupanga anthu osalakwa,

 61. Mmmmmmm why those police there are like to arresting innocent people, there don’t have another job, shemmmmm to those employees (police) akupanga anthu osalakwa,

 62. Mmmmmmm why those police there are like to arresting innocent people, there don’t have another job, shemmmmm to those employees (police) akupanga anthu osalakwa,

 63. Mmmmmmm why those police there are like to arresting innocent people, there don’t have another job, shemmmmm to those employees (police) akupanga anthu osalakwa,

 64. What intrest this 26yrs man had to stone chinthu choti changoima sichinamuyambe???? kkkkk pali nkuluwiko apa,,, afunsidwedi bwino ameneyi, this is what we call organised crime asaa!!!!!

 65. What intrest this 26yrs man had to stone chinthu choti changoima sichinamuyambe???? kkkkk pali nkuluwiko apa,,, afunsidwedi bwino ameneyi, this is what we call organised crime asaa!!!!!

 66. What intrest this 26yrs man had to stone chinthu choti changoima sichinamuyambe???? kkkkk pali nkuluwiko apa,,, afunsidwedi bwino ameneyi, this is what we call organised crime asaa!!!!!

 67. How special is peter asa to hell with him all I care,funken peter must be the one to be arrested coz of causing people to die because of his selfishness

 68. How special is peter asa to hell with him all I care,funken peter must be the one to be arrested coz of causing people to die because of his selfishness

 69. How special is peter asa to hell with him all I care,funken peter must be the one to be arrested coz of causing people to die because of his selfishness

 70. Ha ha ha Malawi is becoming a joke. Stupid indeed. I will throw stones at another bill board ndimangidwetu. Za zii. Dziko lotembereredwa ili. Kamangeni akupha ma Albino osati izi. Wish i wasn’t Malawian now. Ulemu akufuna ndi uti?

 71. Ha ha ha Malawi is becoming a joke. Stupid indeed. I will throw stones at another bill board ndimangidwetu. Za zii. Dziko lotembereredwa ili. Kamangeni akupha ma Albino osati izi. Wish i wasn’t Malawian now. Ulemu akufuna ndi uti?

 72. Ha ha ha Malawi is becoming a joke. Stupid indeed. I will throw stones at another bill board ndimangidwetu. Za zii. Dziko lotembereredwa ili. Kamangeni akupha ma Albino osati izi. Wish i wasn’t Malawian now. Ulemu akufuna ndi uti?

 73. kkkkkkkkkkkkk zafika mpaka pomangana? kapena mwangofuna akaoneko ku office kwanuko? mmmm kulani koma guys. manyazi bwaaa? mmasuleni koma.

 74. kkkkkkkkkkkkk zafika mpaka pomangana? kapena mwangofuna akaoneko ku office kwanuko? mmmm kulani koma guys. manyazi bwaaa? mmasuleni koma.

 75. kkkkkkkkkkkkk zafika mpaka pomangana? kapena mwangofuna akaoneko ku office kwanuko? mmmm kulani koma guys. manyazi bwaaa? mmasuleni koma.

 76. Chindere wongangayo. imeneyi ndi nkhani yakatulusira unyolo. maplezidenti amagendedwa live.mukanene chithuzi. nde akazangenda pamphumi live ndiye muzutani,si kupha basi. chindere.

 77. Chindere wongangayo. imeneyi ndi nkhani yakatulusira unyolo. maplezidenti amagendedwa live.mukanene chithuzi. nde akazangenda pamphumi live ndiye muzutani,si kupha basi. chindere.

 78. Chindere wongangayo. imeneyi ndi nkhani yakatulusira unyolo. maplezidenti amagendedwa live.mukanene chithuzi. nde akazangenda pamphumi live ndiye muzutani,si kupha basi. chindere.

 79. We must understand de situation we r tody,even de bible cralify dat there wil b de tim where ppl wil suffer alot,this lik drought,war,wogulitsa azasangalara,so plz stop pointing ahuman.nobody wil come and tel u dat this de tym wen human wil b strugle even de nowadys prophet they,re failring to tel de follower about nthawi yowawitsai.koma kumangoti i command any problem to come out wats dat?

 80. We must understand de situation we r tody,even de bible cralify dat there wil b de tim where ppl wil suffer alot,this lik drought,war,wogulitsa azasangalara,so plz stop pointing ahuman.nobody wil come and tel u dat this de tym wen human wil b strugle even de nowadys prophet they,re failring to tel de follower about nthawi yowawitsai.koma kumangoti i command any problem to come out wats dat?

 81. We must understand de situation we r tody,even de bible cralify dat there wil b de tim where ppl wil suffer alot,this lik drought,war,wogulitsa azasangalara,so plz stop pointing ahuman.nobody wil come and tel u dat this de tym wen human wil b strugle even de nowadys prophet they,re failring to tel de follower about nthawi yowawitsai.koma kumangoti i command any problem to come out wats dat?

 82. Kodi ma pholisha mwayamba kumanga amisala moti mudzimanga ma gay? cant yu see madness brought by Bwampini himsef in this man? nyooo! sakukwezani maudindo muona shupiti!

 83. Kodi ma pholisha mwayamba kumanga amisala moti mudzimanga ma gay? cant yu see madness brought by Bwampini himsef in this man? nyooo! sakukwezani maudindo muona shupiti!

 84. Kodi ma pholisha mwayamba kumanga amisala moti mudzimanga ma gay? cant yu see madness brought by Bwampini himsef in this man? nyooo! sakukwezani maudindo muona shupiti!

 85. This is nonses or bullshit how much respect do you deserve to a human even if he is apresdent people they are burning bible,quaran pictures of jesus I didn’t see police arrest people like that but someone he just throw stone on image of somebody who created by God also but you sending him to hard labour this it not true at all

 86. This is nonses or bullshit how much respect do you deserve to a human even if he is apresdent people they are burning bible,quaran pictures of jesus I didn’t see police arrest people like that but someone he just throw stone on image of somebody who created by God also but you sending him to hard labour this it not true at all

 87. This is nonses or bullshit how much respect do you deserve to a human even if he is apresdent people they are burning bible,quaran pictures of jesus I didn’t see police arrest people like that but someone he just throw stone on image of somebody who created by God also but you sending him to hard labour this it not true at all

 88. Ambuye mundimasulile ngati sindikuziwani, ngati ndili ochimwa mundiuze pomwe ndimalakha kodi andiweluza okha anthuwa kapena mundiweluze ndinu? Dziko ndilomwe lija chimozimozinso dzuwa, kutuluka ndikulowa mundigwile zanja mbuye, ndisagende munthu myala ayi ndingazalangidwe. Sitifano mwana wa mulungu ogendedwa myala

 89. Ambuye mundimasulile ngati sindikuziwani, ngati ndili ochimwa mundiuze pomwe ndimalakha kodi andiweluza okha anthuwa kapena mundiweluze ndinu? Dziko ndilomwe lija chimozimozinso dzuwa, kutuluka ndikulowa mundigwile zanja mbuye, ndisagende munthu myala ayi ndingazalangidwe. Sitifano mwana wa mulungu ogendedwa myala

 90. Aatsassa…bas ………ngati mwasowa chochita apolice yaye….kapumeni…..arrested nkhani yake itiyo….iyaaa!

 91. Kumeneko nde kupusa amati kugenda chithunzicho kuthandiza chani? Amangidwe basi kumakhala ndi ulemu amalawi Peteryu ndiamene wabweretsa njala ndi mavuto ena? U savage kumaganiza mwamva? Prezident sangadyetse anthu ose am’dziko muno olo zinthu zitamayenda bwino mwamva? Paja Bakili anakuzowerezani kukupatsani ma k50 pamanja mwaganizaso kuti uyu adzitero? Tiyambe kudzidalira tokha aMalawi.

  • Chokani inu a Mathews! who do you think your! Mufune musafune nonse muchoka pa udindo umene muliwo!I’ll pray, simukudziwa kuti ngati inuyo simukuyendesa zinthu bwino mumabweletsa mavuto mdziko ? idiot

 92. Kumeneko nde kupusa amati kugenda chithunzicho kuthandiza chani? Amangidwe basi kumakhala ndi ulemu amalawi Peteryu ndiamene wabweretsa njala ndi mavuto ena? U savage kumaganiza mwamva? Prezident sangadyetse anthu ose am’dziko muno olo zinthu zitamayenda bwino mwamva? Paja Bakili anakuzowerezani kukupatsani ma k50 pamanja mwaganizaso kuti uyu adzitero? Tiyambe kudzidalira tokha aMalawi.

  • Chokani inu a Mathews! who do you think your! Mufune musafune nonse muchoka pa udindo umene muliwo!I’ll pray, simukudziwa kuti ngati inuyo simukuyendesa zinthu bwino mumabweletsa mavuto mdziko ? idiot

  • Mmmmhi ok mwatero? Tidziganiza kaye tisanayankhule kodi mavutowa achokera pati? Nanga ngati tapeza mavuto tiyeni tipezeso masolution ake tisamangolozana chala ayi I’ll never stop to say truth about our country

  • Mmmmhi ok mwatero? Tidziganiza kaye tisanayankhule kodi mavutowa achokera pati? Nanga ngati tapeza mavuto tiyeni tipezeso masolution ake tisamangolozana chala ayi I’ll never stop to say truth about our country

  • Mmmmhi ok mwatero? Tidziganiza kaye tisanayankhule kodi mavutowa achokera pati? Nanga ngati tapeza mavuto tiyeni tipezeso masolution ake tisamangolozana chala ayi I’ll never stop to say truth about our country

  • Mmmmhi ok mwatero? Tidziganiza kaye tisanayankhule kodi mavutowa achokera pati? Nanga ngati tapeza mavuto tiyeni tipezeso masolution ake tisamangolozana chala ayi I’ll never stop to say truth about our country

  • Mmmmhi ok mwatero? Tidziganiza kaye tisanayankhule kodi mavutowa achokera pati? Nanga ngati tapeza mavuto tiyeni tipezeso masolution ake tisamangolozana chala ayi I’ll never stop to say truth about our country

  • Mmmmhi ok mwatero? Tidziganiza kaye tisanayankhule kodi mavutowa achokera pati? Nanga ngati tapeza mavuto tiyeni tipezeso masolution ake tisamangolozana chala ayi I’ll never stop to say truth about our country

  • Mathews!uchitsluu simuuona moti?president oganiza,angamaikeso msonkho patimatumba ta ufa wa kunja uja?mkumauzaso apolice kut akhwimitse chitetezo mmaboder kut ufau usaloweso?chosecho anthu amene anamuvotela akufa nnjala,mkumat pali umunthuso apa??

  • Mathews!uchitsluu simuuona moti?president oganiza,angamaikeso msonkho patimatumba ta ufa wa kunja uja?mkumauzaso apolice kut akhwimitse chitetezo mmaboder kut ufau usaloweso?chosecho anthu amene anamuvotela akufa nnjala,mkumat pali umunthuso apa??

  • Mathews!uchitsluu simuuona moti?president oganiza,angamaikeso msonkho patimatumba ta ufa wa kunja uja?mkumauzaso apolice kut akhwimitse chitetezo mmaboder kut ufau usaloweso?chosecho anthu amene anamuvotela akufa nnjala,mkumat pali umunthuso apa??

  • Mathews!uchitsluu simuuona moti?president oganiza,angamaikeso msonkho patimatumba ta ufa wa kunja uja?mkumauzaso apolice kut akhwimitse chitetezo mmaboder kut ufau usaloweso?chosecho anthu amene anamuvotela akufa nnjala,mkumat pali umunthuso apa??

  • Mathews!uchitsluu simuuona moti?president oganiza,angamaikeso msonkho patimatumba ta ufa wa kunja uja?mkumauzaso apolice kut akhwimitse chitetezo mmaboder kut ufau usaloweso?chosecho anthu amene anamuvotela akufa nnjala,mkumat pali umunthuso apa??

  • Mathews!uchitsluu simuuona moti?president oganiza,angamaikeso msonkho patimatumba ta ufa wa kunja uja?mkumauzaso apolice kut akhwimitse chitetezo mmaboder kut ufau usaloweso?chosecho anthu amene anamuvotela akufa nnjala,mkumat pali umunthuso apa??

  • Mathews!uchitsluu simuuona moti?president oganiza,angamaikeso msonkho patimatumba ta ufa wa kunja uja?mkumauzaso apolice kut akhwimitse chitetezo mmaboder kut ufau usaloweso?chosecho anthu amene anamuvotela akufa nnjala,mkumat pali umunthuso apa??

  • iwe ndiwe mbuli anthu azidalira bwanji okha if the president is failing to create a conducive environment for its citizens, high taxes, poor economic management just to name few

 93. Palibe chifukwa chomangira munthu pamenepo
  Kodi akamat ufulu ndi kuti?
  Ku south Africa munthu anajambula thupi la JACOB ZUMA ali mbulanda koma sanamangidwe wat about kutenda poster

 94. Palibe chifukwa chomangira munthu pamenepo
  Kodi akamat ufulu ndi kuti?
  Ku south Africa munthu anajambula thupi la JACOB ZUMA ali mbulanda koma sanamangidwe wat about kutenda poster

 95. Koma police alibe ulesi billboard chili ndi ntchito yanji ku mtundu wa amalawi? Oro iye mwini ayenera kugendedwa chifukwa akupanga zautsiru kwambiri. Ndipo aziyembekezera ziphinjo m’nsonkhano mwake.

 96. Koma police alibe ulesi billboard chili ndi ntchito yanji ku mtundu wa amalawi? Oro iye mwini ayenera kugendedwa chifukwa akupanga zautsiru kwambiri. Ndipo aziyembekezera ziphinjo m’nsonkhano mwake.

 97. Hey Malawians war is for uncivilised people speak with vote & pray to OUR JESUS CHRIST so that he can give us a GOD FEARING LEADER .IN JESUS NAME AMEN!!!!!!!!!!!

 98. Hey Malawians war is for uncivilised people speak with vote & pray to OUR JESUS CHRIST so that he can give us a GOD FEARING LEADER .IN JESUS NAME AMEN!!!!!!!!!!!

 99. evn apolice omwe amumanga nyamatayi akudziwaso kuti palibe mlandu….koma poti akuopa kuchotsedwa tchito. kodi ufulu ndiuti gyz? ine ndimaona ngat kuli2 ufulu ku Malawi. ku USA Bushi anagendedwa ndi nsapato nde chinachitika ndichani? bullshit

 100. evn apolice omwe amumanga nyamatayi akudziwaso kuti palibe mlandu….koma poti akuopa kuchotsedwa tchito. kodi ufulu ndiuti gyz? ine ndimaona ngat kuli2 ufulu ku Malawi. ku USA Bushi anagendedwa ndi nsapato nde chinachitika ndichani? bullshit

 101. kkkkkk uyu chilungamo watopa nacho mpaka ugenda chithunzi nanga atamuona peter munthalika sangaphe amenei, kklkk acha saidi akukapeni mwatumidwa ndiwotsutsa.

 102. kkkkkk uyu chilungamo watopa nacho mpaka ugenda chithunzi nanga atamuona peter munthalika sangaphe amenei, kklkk acha saidi akukapeni mwatumidwa ndiwotsutsa.

 103. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk.eeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee koma ndatopa!

 104. Apolice akuno ku Malawi sioti munthu ungawope koma ku RSA kuli etha ola munthu mkumanjenjemera manw anangowa mphamvu ndi omuthandiza anyetse dzitsiruzi kupha njoka mdula mutu wachita bwinokuyambirila mutu wa dzaziwo kenako ine mdyula michirayo

 105. Zopusa zimenezo am’manga bwanji mfanayo? Kodi kape ameneyo mumamutenga ngat ndani? Kunali kamuzu kumeneko simbuzi yamunthu ngati imeneneyo……..akutukwanidwa live #Zuma wat mo iwe? Nanunso a police ngati mwatopa ndikuvala uniform ya ben siyani mukayambe kuswa masitolo……..aamwenye………zopusa

 106. Koma zoona anthu mukufunsa kuti wamangidwa pa Mulandu wanji? Mmalo moti muthamange kuChipatala ku Mlambe mukaone mmene agogo avulalira atagendedwa kamwa ija…kkkkk…..mwanisekesa

 107. gift wilard ngt watopa uzikangotema ng’ombe kupusa eti expsive ndy kt chani fisi ameneyi akanagofa ziko lilipamoto ili samala nkanakutukwana zovuta kwmbili dot talk shit

 108. gift wilard ngt watopa uzikangotema ng’ombe kupusa eti expsive ndy kt chani fisi ameneyi akanagofa ziko lilipamoto ili samala nkanakutukwana zovuta kwmbili dot talk shit

 109. There is no any case u can open against that guy. People stoned jesus christ live even stephen to dealth no one was jailed. How much important is peter mutharika? To myself is just an amateur(pitala)

 110. kutereko iwe patrick sungadziwe kuti ndimulandu ai pepani chifukwa chaumbuli omwe ulinawo ufunse anzako omwe anyenda maiko akutali. chifukwa ngakhale kukoza panapaliponse ndimulandu or osakodzera khoma or kupezeka munthu wavula malaya or kuyenda beya opanda nsapato or silipasi udziwe kuti police ikutenga basi ndie taganiza maiko ameneo ugende chikwakwani mulandu wake ungakhale otani ndie polankhula panetipa kumalankhula moganiza poopa kuti anthu enanso panetpa akuwerenganao maiko ena uwo ndimulandu ndithu kapena uyerekeze kuoloka ukagende nawenso chikwangwani cha president wa Mozambique tione ngati sutsekeredwa ngati suli mulandu tione.

  • sikuti ilolo apolice amalitenga ngati lamulo ladziko ai koma iwo pantchito yawo amatha kukuika pa saspect chifukwa chamalo omwe iwe ukupezeka ndimene ulili. mwachitsanzo ine ndimene ndikuonekera ndimene anthu amandidziwila ndikaime ndikasiye zinthu zomwe ndimapanga ndie ndikaime panseu ndiyambe kugenda or police isadafike koma anthu okha ondiona ayamba kufunsa kuti kodi Ellias uja watani akupanga izi. ndie ndichimozimodzi iwe kudutsa kumalo elemekezeka mosazisamala ngati ku maline kwa azungu kapena kuti kwa anthu ochita bwino komwe police imapanga patrol each and every tminuts akonza kukuganizila mosiyanasiyana malinga ndimene iwe ulili maonekedwe ako ndithu sindikuti ilo ndilamulo koma kuti malo ene ndialemu chotero inu kudutsa kumeneko ngakhale sunapange kanthu police imakaika basi or kungokupeza ukuyenda pansi madela ngati ameneo atha kukutenga kuti akakufunse komwe iwe ukuchokera komanso ukulowera

  • sikuti ilolo apolice amalitenga ngati lamulo ladziko ai koma iwo pantchito yawo amatha kukuika pa saspect chifukwa chamalo omwe iwe ukupezeka ndimene ulili. mwachitsanzo ine ndimene ndikuonekera ndimene anthu amandidziwila ndikaime ndikasiye zinthu zomwe ndimapanga ndie ndikaime panseu ndiyambe kugenda or police isadafike koma anthu okha ondiona ayamba kufunsa kuti kodi Ellias uja watani akupanga izi. ndie ndichimozimodzi iwe kudutsa kumalo elemekezeka mosazisamala ngati ku maline kwa azungu kapena kuti kwa anthu ochita bwino komwe police imapanga patrol each and every tminuts akonza kukuganizila mosiyanasiyana malinga ndimene iwe ulili maonekedwe ako ndithu sindikuti ilo ndilamulo koma kuti malo ene ndialemu chotero inu kudutsa kumeneko ngakhale sunapange kanthu police imakaika basi or kungokupeza ukuyenda pansi madela ngati ameneo atha kukutenga kuti akakufunse komwe iwe ukuchokera komanso ukulowera

  • sikuti ilolo apolice amalitenga ngati lamulo ladziko ai koma iwo pantchito yawo amatha kukuika pa saspect chifukwa chamalo omwe iwe ukupezeka ndimene ulili. mwachitsanzo ine ndimene ndikuonekera ndimene anthu amandidziwila ndikaime ndikasiye zinthu zomwe ndimapanga ndie ndikaime panseu ndiyambe kugenda or police isadafike koma anthu okha ondiona ayamba kufunsa kuti kodi Ellias uja watani akupanga izi. ndie ndichimozimodzi iwe kudutsa kumalo elemekezeka mosazisamala ngati ku maline kwa azungu kapena kuti kwa anthu ochita bwino komwe police imapanga patrol each and every tminuts akonza kukuganizila mosiyanasiyana malinga ndimene iwe ulili maonekedwe ako ndithu sindikuti ilo ndilamulo koma kuti malo ene ndialemu chotero inu kudutsa kumeneko ngakhale sunapange kanthu police imakaika basi or kungokupeza ukuyenda pansi madela ngati ameneo atha kukutenga kuti akakufunse komwe iwe ukuchokera komanso ukulowera

  • sikuti ilolo apolice amalitenga ngati lamulo ladziko ai koma iwo pantchito yawo amatha kukuika pa saspect chifukwa chamalo omwe iwe ukupezeka ndimene ulili. mwachitsanzo ine ndimene ndikuonekera ndimene anthu amandidziwila ndikaime ndikasiye zinthu zomwe ndimapanga ndie ndikaime panseu ndiyambe kugenda or police isadafike koma anthu okha ondiona ayamba kufunsa kuti kodi Ellias uja watani akupanga izi. ndie ndichimozimodzi iwe kudutsa kumalo elemekezeka mosazisamala ngati ku maline kwa azungu kapena kuti kwa anthu ochita bwino komwe police imapanga patrol each and every tminuts akonza kukuganizila mosiyanasiyana malinga ndimene iwe ulili maonekedwe ako ndithu sindikuti ilo ndilamulo koma kuti malo ene ndialemu chotero inu kudutsa kumeneko ngakhale sunapange kanthu police imakaika basi or kungokupeza ukuyenda pansi madela ngati ameneo atha kukutenga kuti akakufunse komwe iwe ukuchokera komanso ukulowera

 111. he is the president..no matter what he deserve some respect u keep on saying Malawians are poor how do u expect to become rich when u get drunk early as 9 am.. 365 days.. come on Malawians palibe dziko lopanda mavuto

 112. you know why #saidi was stoning that?,,,,,poor leadership under him next time it will be him direct,,,,just let him go,#police find something to do!

 113. you know why #saidi was stoning that?,,,,,poor leadership under him next time it will be him direct,,,,just let him go,#police find something to do!

 114. KKKKKK…nawe iwe busy bax miyala kudzadza thumba kumagenda bilboard…chamba chan…wamputa dala ndithu…!!! uidziwa bangwe apolice m’mene amapondelamo eeeissh!,!

 115. KKKKKK…nawe iwe busy bax miyala kudzadza thumba kumagenda bilboard…chamba chan…wamputa dala ndithu…!!! uidziwa bangwe apolice m’mene amapondelamo eeeissh!,!

 116. Osadanda mzanga wateremu walowa mu politics next time udzakhala mtsogoleri wadziko•History so wayipanga the first brave youngest man in Malawi to stonned Mr President big up!

 117. Osadanda mzanga wateremu walowa mu politics next time udzakhala mtsogoleri wadziko•History so wayipanga the first brave youngest man in Malawi to stonned Mr President big up!

 118. I thought he stoned a president on his face but billboard ? There is no case there,the man display anger on disatisfication to a president.And we call it a freedom of expression lol

 119. I thought he stoned a president on his face but billboard ? There is no case there,the man display anger on disatisfication to a president.And we call it a freedom of expression lol

 120. M’masuleni munthuyo,mwina anava kut iye ndamene wabisa chakudya mdziko muno,piteryo ndikape,iyeyo amakakhalilanji pamenepo.

 121. M’masuleni munthuyo,mwina anava kut iye ndamene wabisa chakudya mdziko muno,piteryo ndikape,iyeyo amakakhalilanji pamenepo.

 122. nde mulandu wake mkumati chani? nawo a Police!! ?
  ukuposa amuna or azimayi kumapanga Sodommy??
  Malawi police b serious!
  tamufuxeni vuto ndichiyani kuti mmalo mogenda mwiniwakeyo pankhope wagenda chithunzi chabe!

 123. nde mulandu wake mkumati chani? nawo a Police!! ?
  ukuposa amuna or azimayi kumapanga Sodommy??
  Malawi police b serious!
  tamufuxeni vuto ndichiyani kuti mmalo mogenda mwiniwakeyo pankhope wagenda chithunzi chabe!

 124. kod apolisi kodi muti mwachita malungo nde mwamwa raah opanda panado tsano mutu wawawa?????Abale lekeni muthu walakwanj anga pitala watuluka magazi??? mesa muti wagenda chikwagwanie ? tsano lakwanj pomunjata?My Malawi wea r u going ?

 125. kod apolisi kodi muti mwachita malungo nde mwamwa raah opanda panado tsano mutu wawawa?????Abale lekeni muthu walakwanj anga pitala watuluka magazi??? mesa muti wagenda chikwagwanie ? tsano lakwanj pomunjata?My Malawi wea r u going ?

 126. malawi akuwawadi uyu! mkaka ndi uchi uja zidamka kuti? apolice musapezelepo ma promotion mtayeni tisanapite pamsewu! kayendatu mukapanda kumutaya!

 127. malawi akuwawadi uyu! mkaka ndi uchi uja zidamka kuti? apolice musapezelepo ma promotion mtayeni tisanapite pamsewu! kayendatu mukapanda kumutaya!