Bingu National Stadium opening to delay

Advertisement
Bingu National Stadium

The opening of the Bingu National Stadium in Malawi’s capital, Lilongwe may well delay as government is considering numerous suggestions of changes

Bingu National Stadium
Bingu National Stadium: Under scrutiny

on the sports facility which will hold up to 41,100.

This has come as the Ministry of Youth Development and Sports has admited that there are a couple of changes that have been suggested by various Ministries and stakeholders on where to change the stadium.

Speaking to the media after the tour on Wednesday, Chief sports officer responsible for infrastructure in the ministry of youth development and sports Joseph Kayamba, said that government will consider adopting numerous suggestions that have been put forward by several stakeholders before the stadium actually starts being used.

“We organized this function for these officials to appreciate the features of the new stadium and at the same time for them to take note of any shortfall that may be there so that these defects could be recommended to the contractor for improvement.

“We have received several positive suggestions from the government representatives which we may wish to take into account. Some officials have highlighted on the need of re-working on the VVIP stand and improve on its current design. For example, there is need to include a canopy, space and maybe even some stairways that may lead into the field.” Said Kayamba.

Advertisement

252 Comments

 1. Amene zikumunyasa zot BINGU STADIUM ma stadium tili nawo ambir mukhoza kumakaonela mpira kwinako… Anakatchukuma yekha BINGU so he deserve IT

 2. BIngu Bingu chani anthu osadziwa kuyankhula waliwononga dzikoli,kwathu ku Lilongwe ndipo Bingu sanakonze Lilongwe musanamepo or akanakhala wina zikanakhala chimodzimodzi. Mundiwuze kutauni nkuti ikakhala Blantyre ndiye idali kale No proper planning ,Very small ,No City Center kungophatikiza ma bulding. Mukunyoza achewafe choyamba we are almost 70Percent in this country that’s why Chichewa its a National Language ku South tiripo ku North tiliponso tikadakhala oyipa sibwenzi titachita za ku Rwanda amphenvu inu mukungotukwananu

 3. BIngu Bingu chani anthu osadziwa kuyankhula waliwononga dzikoli,kwathu ku Lilongwe ndipo Bingu sanakonze Lilongwe musanamepo or akanakhala wina zikanakhala chimodzimodzi. Mundiwuze kutauni nkuti ikakhala Blantyre ndiye idali kale No proper planning ,Very small ,No City Center kungophatikiza ma bulding. Mukunyoza achewafe choyamba we are almost 70Percent in this country that’s why Chichewa its a National Language ku South tiripo ku North tiliponso tikadakhala oyipa sibwenzi titachita za ku Rwanda amphenvu inu mukungotukwananu

 4. Bingu can not be the name of the stadium. Are you mad

 5. mudapha dala bingu eti cholinga muzisewelesa zithu zake mopusa zitsilu nde mukasithesotu kamuzu stadium tiwone ngati simumwalila mawa lino

 6. wat shit are you doing with the name if you want to die tell the whole country that you want to die rather than to change the name but let me tell you, you want to change the name God will strike you to death

 7. Amene akudana ndi dzina la Bingu stadium ndi mfiti. Muziyamika pena anapanga zazikulu kusiyana ndi zinazi. Tingathe kuloza chitukuko chake. Malawi sanali chonchi. Pano mwayamba kunyoza mtembo!

 8. Stadium siya family ya mutharika, ngati akufuna za dzina lawo azimanga za ndalama zao osati ndalama zaboma bcz stadium ndiyadziko.Bingu adali wamanyi, liguluwe bushit.

 9. vuto la amalawi ndi limenelo chinachiri chonse timafuna tilowesepo ndale.ndibwinodi maina azinthu zofunikira asamakhale a anthu andalewa ayi chifukwa ine ndikazatenga boma mu 2019 muno ndidzaisinthanso zina izakhala”francis mezeck mc jolly b jo sholobishoz jokopijo mahalashalahashibazi National stadium”

 10. the stadium named BINGU ? did government ask malawian about this? that is BAD name over all names of stadium lets call it Lilongwe stadium not that thuswhy flames ikungoluza mpira just because we want ma stadium azitchuka ndi mayina aanthu oti anapita kale change tell them to get peoples views first

 11. Amalawi kumakhala nawo umunthu mukafuna kulankhula,bingu mukumunena chonchi apayi ndi munthu ofunikb kulemekezedwa ngati kholo lanu,whatever the case can it be bambo anu atamwalira kapena ngati anamwalira kale u can not be happy hearing anyone insulting him just like u r insulting our late president who during his entire life sanapange zinthu zotiipira zokhazokha but had even positively contributed to our nation-for instance durinp the very first 5 years kumunena mose pa lero pankakwanira,why then all these insults??? We should learn to appreciate other people’s efforts and contributions!! The name of this stadium fits!!!

 12. Hey why are you debating on useless things? Did bingu construct a stadium? Its the chinese government, iyeyo anali masikini okapempha, why are u speakinga as if the decomposed bingu generate resources locally to build the stadium? Infact the issue here is about extension of other stadium structures and not naming the stadium, zaonetseratu umbuli wa a malawi, imagine ur failing to understand the topic presented here, dull and daft malawians, choncho mungakhale ndi nzeru ndi luntha lotukuka? Nchifukwa mukukhaula ndi njala madzi alipo munyanja, dziko lopusa la a sinamankhwe ofunkha chifyenthe ndiye malawi. continue to be poor and beggars!!!

 13. kkkkkkkkk munthu ngoopsa kuposa mkango. Tribalism is stl wit uncivilised Malawians. Kupepera kumeneko. We r o Malawians.

 14. Time is cominng the name will change coz it doesnt exist, wina afune asafune….Ndiye pali chomanyozeranaso ma tribes apa? Hahahaha we r all Malawian basi za..ziiii as f r the first ever to lead Malawians?

 15. onse akunjoza Bingu panyopanu mwanva kuti lilongwe iwoneke ngati city mesa nchifukwa cha Bingu achewa osayamika munazolowera kupha anthu munthawi ya MCP eti? m’malo moyamika busy kunyoza mbava za anthu ambili akunyozanso apa ndi atumbuka ndawona ndikutchile kwawoku sayamiyakanso

 16. akoma kodi wapeleka chidzina cholemela mkamwayo ndindani akuti big wamtali oro mulomwe wafupi panyapake amene wachula chidzina chimenechi galaundi lokongola kwathu kulilongwe koma fanzi yamu mtandile mwalolazimenezo m’mene ndimayidziwila mtandileyo bwanji simunapangane ndi fanzi yakwagona guys manyaka amenewo salibwino ndimakonda mtandile hvy zandinyasa bingu machende ako wava mbuzi iwe

  1. iwenso mbole yako !! musakawomba njelwa mumange yanu bwanj muitchule kut mtandle !!! mzelu zimenez mumazisya pat mmadikila mupanglidwe kaye kenako muzchuluka nzelu … (shatapoo !!!)

 17. zikuchita kuonetselatu kut panachitika mistake yaikulu stadium kukaimangila ku lilongwe.awa ochewa awa siampira awa. koma ndiye chimaloladi opanda manu chimanga zoonadi.boma kuchedwa kusegula zikutanthauzilatu kut awa ochewa alibe nayo chidwi..kodi munthu wafika ndi bell yazovala pamsika bell yanyowan ndithu koma palibe munthu ndimmodzi yemwe akuonesa chidwi chofuna kuona kapena kugula. ndiye uzit ndichifukwa cha..zimene zikuchitikazo ma coloured kuno ku south african amat …masa pusi,,faken nayi..

 18. Zachamba basi galawundili ndilathu ife amalawi mukudandawula chani agalu inu kumakupangisani kusayenda mukanakhala kuti mumayenda mukanaziwo mwandinyasa kwambili ndi ndakwiya nanu

 19. Zachamba basi galawundili ndilathu ife amalawi mukudandawula chani agalu inu kumakupangisani kusayenda mukanakhala kuti mumayenda mukanaziwo mwandinyasa kwambili ndi ndakwiya nanu

 20. YOUR SOUL REST IN INTERNAL PEACE !!!!
  THE PEOPLE OF MALAWI NATION WILL NEVER FORGET YOUR GOOD
  LEADERSHIP .

 21. YOUR SOUL REST IN INTERNAL PEACE !!!!
  THE PEOPLE OF MALAWI NATION WILL NEVER FORGET YOUR GOOD
  LEADERSHIP .

 22. What a good name Bingu National Stadium. Amene zikukuwawani muphulike! His name will live after his dreams. Ngati sizikukusangalatsani dzakhaleni president nanunso 2019 inu mudzalitche mayina anuwo, so simple osati kumasokosa apa with your empty comments.

 23. What a good name Bingu National Stadium. Amene zikukuwawani muphulike! His name will live after his dreams. Ngati sizikukusangalatsani dzakhaleni president nanunso 2019 inu mudzalitche mayina anuwo, so simple osati kumasokosa apa with your empty comments.

 24. Its a Good Development to this Poor nation of malawi, and the Government should also build this new type of Stadium in Northern and Southern region of Malawi, to bring equal n justice on Development of the Pipo of this country,
  I also thank the late
  H.E. Dr Bingu wa muntharika,
  May his Soul
  Rest In Internal
  PEACE !!!!!!!!!!!!!!!

 25. Its a Good Development to this Poor nation of malawi, and the Government should also build this new type of Stadium in Northern and Southern region of Malawi, to bring equal n justice on Development of the Pipo of this country,
  I also thank the late
  H.E. Dr Bingu wa muntharika,
  May his Soul
  Rest In Internal
  PEACE !!!!!!!!!!!!!!!

 26. zakaisara kwakaisara zaBINGU kwabingu ndipo za MULUNGU kwaMulungu. iwe utichani ndipo ndiwe yani kuti upereke dzina la stadium. apitani kwanu mukamangire abale anu akumanya mchimanga aja chimbudzi mwina angakukumbukeni.

 27. zakaisara kwakaisara zaBINGU kwabingu ndipo za MULUNGU kwaMulungu. iwe utichani ndipo ndiwe yani kuti upereke dzina la stadium. apitani kwanu mukamangire abale anu akumanya mchimanga aja chimbudzi mwina angakukumbukeni.

 28. khuku inu osawawuza abambo anu amange yawo stdium muyitchule mayina nuwafumawo awanji agalu osayamika inu bingu kazina kokoma mkamwa aka

 29. khuku inu osawawuza abambo anu amange yawo stdium muyitchule mayina nuwafumawo awanji agalu osayamika inu bingu kazina kokoma mkamwa aka

 30. kusintha dzna la stadium nosense bola muzikambako za mbuli zamaplayer muli nazoz……

 31. Ntchto Kupeleka mayna Ama City Agalu Inu Lilongwe Ikhale Lilolngwe.BINGU STADIUM, Anyan Osayamika Inu Ndakwya Nanu,,,,,,ndzakukhapila Ku Stadium Konko Kapolo Iwe.

 32. Ntchto Kupeleka mayna Ama City Agalu Inu Lilongwe Ikhale Lilolngwe.BINGU STADIUM, Anyan Osayamika Inu Ndakwya Nanu,,,,,,ndzakukhapila Ku Stadium Konko Kapolo Iwe.

 33. Kumalawi zizitelo president atamange stadium basi ayipatse dzina lake, ife tilibe bvuto as long as we move on with development!

 34. Kumalawi zizitelo president atamange stadium basi ayipatse dzina lake, ife tilibe bvuto as long as we move on with development!

 35. Nonse Ndi Makape,nkhani Si Ya Dzinatu Apa,akufuna Kukonza VIP Komanso Stares Yet U Hating One Another 4 nothing.Amalawi? Whats In A Name?Z T Leg Or An Arm.Name Z Nothing Even If It Is Named Mpumulo Wa Bata Ife Tikufuna Stadium Osati Dzina.

  1. ine ndimadabwa coz nthawi yomwe bingu amamwalila anali atasala ndi zaka 3 kut asiye kulamula komanso nyumba yake inali isanathe . ndiye zikanatheka bwanji kusintha ziko la malawi pomwenso forex, fuel komanso mabungwe ndi maiko otithandiza anali atayimika manja. tink about it!

  2. Nkhuku yoyamba ndiwe.Iweyo zomwe Bingu anachita sukuziona? Wabadwa lero kapena? Akutuma achakwera ndi a Jb kapena? Ukuchepatu iweyo.Bingu anachita kwa 7yrs yokha half yazitukuko zomwe kamuzu anachita kwa 30yrs. Ambiri amene amadana ndi Bingu ndi ma vendor komanso ma gay plus mbava chifukwa Bingu sankalola nyansi. Anthu osayamika inu. Ife timanena kuti kamuzu akanasinthana ndi Bingu nthawi imene Bakili anayamba kulamulira ija bwenzi malawi ali patali. Unfortunately kamuzu anasinthana ndi Bakili amene anaononga malawi kwa ten yrs.

  3. ndi ziko lanji lomwe linatukuka popanda malonda(mavendor)? ndiye ukamat kukapanda bakili bwenzi ziko la malawi lili patali zikungoonesela2 umbuli womwe ulinawo mdala iwe. ndiye popeza2 pano dpp ikulamulabe tikufuna malawiyo asinthike tione not nkhani izikhala yoti bingu ndimunthu yekhayo yemwe akanatha kusintha malawi. who is fuken bingu over mala

  4. ndi ziko lanji lomwe linatukuka popanda malonda(mavendor)? ndiye ukamat kukapanda bakili bwenzi ziko la malawi lili patali zikungoonesela2 umbuli womwe ulinawo mdala iwe. ndiye popeza2 pano dpp ikulamulabe tikufuna malawiyo asinthike tione not nkhani izikhala yoti bingu ndimunthu yekhayo yemwe akanatha kusintha malawi. who is fuken bingu over mala

  5. ndi ziko lanji lomwe linatukuka popanda malonda(mavendor)? ndiye ukamat kukapanda bakili bwenzi ziko la malawi lili patali zikungoonesela2 umbuli womwe ulinawo mdala iwe. ndiye popeza2 pano dpp ikulamulabe tikufuna malawiyo asinthike tione not nkhani izikhala yoti bingu ndimunthu yekhayo yemwe akanatha kusintha malawi. who is fuken bingu over mala

  6. ndi ziko lanji lomwe linatukuka popanda malonda(mavendor)? ndiye ukamat kukapanda bakili bwenzi ziko la malawi lili patali zikungoonesela2 umbuli womwe ulinawo mdala iwe. ndiye popeza2 pano dpp ikulamulabe tikufuna malawiyo asinthike tione not nkhani izikhala yoti bingu ndimunthu yekhayo yemwe akanatha kusintha malawi. who is fuken bingu over malawi.

  7. ndi ziko lanji lomwe linatukuka popanda malonda(mavendor)? ndiye ukamat kukapanda bakili bwenzi ziko la malawi lili patali zikungoonesela2 umbuli womwe ulinawo mdala iwe. ndiye popeza2 pano dpp ikulamulabe tikufuna malawiyo asinthike tione not nkhani izikhala yoti bingu ndimunthu yekhayo yemwe akanatha kusintha malawi. who is fuken bingu over malawi.

  8. ndi ziko lanji lomwe linatukuka popanda malonda(mavendor)? ndiye ukamat kukapanda bakili bwenzi ziko la malawi lili patali zikungoonesela2 umbuli womwe ulinawo mdala iwe. ndiye popeza2 pano dpp ikulamulabe tikufuna malawiyo asinthike tione not nkhani izikhala yoti bingu ndimunthu yekhayo yemwe akanatha kusintha malawi. who is fuken bingu over malawi.

 36. amalawi umbava basii , kukhalira kumanyoza anthu aphindu basii kuti mupeze po bera boma lisapange zabwino kwaife ofuna zabwino , munya munawabera amyi zambiri mpaka kuwachosa paudindo wao chifukwa chowa kulupilira inu mavamphaya oyamwa anthu magadzi akuyenda, apa nde mumva kuwawa ndithu.

  1. Hahaha akanalitsintha bwanji dzikoli mbewa yanu ija?Mnali kuti that time?Tifuseni ife tinali ku malawi nthawi ija.mdzinamidza ana amene akubadwa kumene enafe ndiye ayi,even history ndimaidziwatso heavy siungandinamize

 37. Kodi inu achewa mumadana bwanji the Muthalikas. Tinakupililani zaka 31 so close ur mouth. The Stadium will be Bingu Stadium. U should be thankful to the Late Bingu. he resorted all Kamuzu names which were removed during UDF.

  1. Mind your language! Achewa timadana ndi the mutharikas? What will we gain if we hate them?? Thats nonsense! As a chewa myself i dont have time to hate any mutharika! Find something better to do!

  2. Mind your language! Achewa timadana ndi the mutharikas? What will we gain if we hate them?? Thats nonsense! As a chewa myself i dont have time to hate any mutharika! Find something better to do!

  3. guyz !! tonse nd amalaw asiyen atchule dzina lilironse ndmmene atakonzele, tisadane tokha tokha khaya atchula chan bola ife tizidzwa kut tli nd stadiam kuno ku malaw yapamwamba. nanga tidane nd akunja tizadanenso tokha tokha !! kwasalaku mulungu azakwiya nafe zen zen …!!

 38. nonse mukukana dzinalo chulani la agogo wanu muikepo , dzinalo latengapo ciyani pa mbalili yanu nose?, mwakhalapo mmaudindo osiana siana mwapangapo chiyani chaphindu pa mbiliyanu manyazi mulibe ?.

 39. hw wrong can soccer fans will wait to enjoy games in that stadium.please goverment do us a favour.do right thing.we cant wait any longer.

 40. Inu bingu moved that stadium plan 2 blantyre, jb anaibweresanso kulilongwe coz its where it was meant 2 b,,, nde that name doent fit it better b lilongwe stadium

  1. Let’s learn to be thankful to the Late Bingu for his move to China though those who were naturally born noisy made their noise & here we are today, enjoying the benefits without shame of our critisisms

  2. Even kuwapasa Nyumba yabwino Galimoto,kwa iwobe ndizokayikisa ngati Angayamike. Magazi Awo anawonjeza kuda kwambiri m’paka Anadesaso mitima yawo Moti ndikhulupilira Sangazatheso kuwona chabwino pa Dziko Lapasi lino.

  3. Even kuwapasa Nyumba yabwino Galimoto,kwa iwobe ndizokayikisa ngati Angayamike. Magazi Awo anawonjeza kuda kwambiri m’paka Anadesaso mitima yawo Moti ndikhulupilira Sangazatheso kuwona chabwino pa Dziko Lapasi lino.

  4. was bingu a hero? no no dont confuse people,thanks to jb for the studium to capital city for this,this studium should be called #LL studium

  5. His name shall prevail by his dreams. Take it or leave it, I salute Bingu for dreaming in colours not your so called JB. Apo biii dzakhaleni president inuyo amene muli ndi maina abwinonu mudzatche stadium yanu osati iyi.

  6. His name shall prevail by his dreams. Take it or leave it, I salute Bingu for dreaming in colours not your so called JB. Apo biii dzakhaleni president inuyo amene muli ndi maina abwinonu mudzatche stadium yanu osati iyi.

  7. Kupitisa ku #LL sichifukwa koma amene anaona ndikuganizila chosowa cha a Malawi, ndiye Bingu not jb. Bwanji jb yo sanayambitse yake. Nonse mukudana ndi dzina limeneli paujeni panu mwamva

  8. Bingu was not a hero….about the stadium,its better b called Lilongwe stadium..or National stadium…malawi nde izingokhalira bingu ichi bingu ichiii..anali yekha munthu ku malawiiii

  9. zomayitana ma stadium mayina amunthu ndi mbola komanso uzimwali….sinavepo kuno ku south africa akuti jacob zuma stadium or thabo mbeki stadium..ooooh my malawi zinthu kumazilowesa mu ndale

  10. zomayitana ma stadium mayina amunthu ndi mbola komanso uzimwali….sinavepo kuno ku south africa akuti jacob zuma stadium or thabo mbeki stadium..ooooh my malawi zinthu kumazilowesa mu ndale

 41. Enanu ndi choncho alwayz dzina latani?.bwanji simunasinthe lanulo atakupatsani lovuta kutchula ngati limenero

 42. pafuni ogulitsa delunde apezekemo, not flames akatswiri oluza dziko lose. tisegulamo bar, apo biiiii stadium ya misonkhano.

 43. stadium yakwathu imeneyo LL thx J B pakutibweresera stadium Bingu wachani. mesa anapitisa kumwera za usiru

  1. Haha jb sakuiziwa kuti inayamba bwanji ,osangomuuza kut apite akamalizitse cashgate yake ija bwanji,bingu national stadium

  2. Haha jb sakuiziwa kuti inayamba bwanji ,osangomuuza kut apite akamalizitse cashgate yake ija bwanji,bingu national stadium

 44. Make sure we have a good car ? park and Police ? unit at the Stadium Please please….

 45. Make sure we have agood car ? park and Police ? unit at the Stadium Please please….

Comments are closed.