Bakili Muluzi’s corruption case starts again next month

Advertisement
Muluzi

The MK. 1. 7 Billion corruption case involving the Malawi’s former  President Bakili Muluzi is expected to resume in court in February, Malawi24 has learnt.

For over six years, Muluzi has been answering charges of corruption in which he is accused of squandering public funds amounting to 1.7 billion Kwacha.

According to reports, Anti-Corruption Bureau (ACB) spokesperson says the it will not drop the case as feared by the media, but was preparing for an appearance at the Constitutional Court in February.

Reports that Malawi24 has been following show that with a strenuous effort from government, the case would have been dropped.

Bakili Muluzi
Muluzi; His case returns in court next month.

Reports suggest that this is due to the cordial relationship the current government has with the 72 year old.

According to  ACB the case is coming again in February, 2016, when the High Court will hear from Muluzi’s lawyers and ACB on the application that the matter be referred to the Chief Justice for the Chief Justice to certify it as a constitutional matter and then refer it to the Constitutional Court for determination.

“Both parties were given 21 days to prepare and file their submissions, beginning with Dr. Muluzi’s lawyers as the applicants and then serve those submissions on the State and the court. The bureau is still waiting for those submissions to be served on it by Dr. Muluzi’s lawyers,”  ACB Publicist is on record as having said.

The case which the ex Malawi leader claims was politically driven by late President Bingu wa Mutharika, whom he was not in terms with was recently in the media as Chief Justice Andrew Nyirenda opted to refer back to the High Court his (Muluzi)  application or a  constitutional review on the corruption case.

Muluzi together with Violet Whisky wanted the Supreme Court to direct that the High Court, sitting as a constitutional court, should determine that the charges were politically motivated and, therefore, should be dismissed.

But Nyirenda since faulted the High Court for referring the matter to the highest court before weighing the arguments.

Advertisement

279 Comments

 1. Pangani zoti economy ya malawi ikhale boo not kulimbana ndi achair kupanda ameneyi sibwenzi enanu mutachangamuka ndiye nkhani yokuba isiyeni imadya pomwe yamangilildwa nanuso mukuba nthawi izakwana tizakusokolosani komwe muliko ohooo musiyeni munthu adyerere

 2. Ndagodusa zonse zili bwino kale kkkkkk eni ndalama ali chete akupakula kumapeleka kwa eni ndalama azawo kumaukwati kuzipatala mankhwala kulibe akukasupa kkkkkk Boma lá anthu ophuzila kkkkk pakati PA udf ndi dpp mbuli ndindani?????????

 3. I don’t belong to any party but this is no sense, why are not moving forward with things that can develop Malawi? Let all the saints start stone him. Fellow Malawians let’s forget the past.

 4. missi juma you are out of order if you attended secondary ooxl i think you wil be able to understand the word “multiculturalism”regionalism can not develop our warm heart of africa.lets work together ndife amodzi & am a tumbuka,but i don’t hav time to create a gap btwn tumbuka & chewa people since we are same people

 5. a note of k100 contributes to economy development. justice should take its part. no president has ever been good. imagine you becoming a president today what will you do?

 6. asaah nayeni anawonoga malawi ndi ulamuliro wake mavuto onse alipo pano anayambisa ndi iyeyo anaphwekesa zithu.zonsezi ma cashgate kuzazana pa ADMARC anapasa amalawi ulesi ngati saweruzidwa amuweruza mulungu padziko pompano.

 7. Koma ndalama zaonongedwa pozenga mulandu umenewu sizikuposaso anaba Bakili?mmmm zovuta izi only f i was APM wit de powers to pardon cases ndikanangothesa adarwise tax payers money zikungoonongedwa apa

 8. Bakili in 10years time1.7billion, bingu in 8years tym 577billion, JB in 2years 22billion. Ngati pitalayo ngati akufunadi kuthetsa katangale ayambe ndi 577bn ya bungu then JB 22bn not ka 1.7bn ka chair ndikachani kameneka ku boma

 9. Za zii za uchinyiru basi.Mukufuna muzionongaso ndalama zina ndi ma court anuwo.Tamalizani kaye izi za flesh za cashgate zimenezi ndiye tikuzifuna ife osati za chair ayi.

 10. Palibe chinthu champindu chomwe ndikuchiona polimbana ndi mulunzi.MK1.7billion mukuilephela cashgate yomwe ili ndi dollar zambili.continue to waste ur time kk.

 11. now 12years singing the same song when will malawi know the truth? i think with the time gone draging this case, muluzi has already saved his sentence while out side prison.so for the sake of economy,government should just withdraw this case and the money suposed to be spent,can be use in a physical development of our country. shame ! 11 budgets this case has had a share but to no conclusion. musatinamizepo apa.

 12. Yense olakwira lamulo, chilungamo mothandizana ndi lamulo zimutsate. Koma pa a chair pokha asiyeni akalambe bwino, angopeza kumene mkazi asiyeni awufile anakhalitsa pa mphepo. Nde zowasokoneza ndi ka change kanuko ai. Taigwireni mbava yaikazi ija ikayankhe milandu. Mzimayi wamtudzu ngati amene uja sindinamuone. Mwera.com no arrest to A Chair Viva a Chair.

 13. 6 years no conviction? What type of court is this? You can’t find him guilty then the man is innocent. Eish rich people money talks.

 14. Boma lathu la UDF lizawinatso mukhaura.palibe chomwe mungachite ndi amuluzi.ndalama mumadya pakhomo panu lero mukutibweresera yanu misala samalani!!!!!

 15. Zanja la boma ndilalitali palibe muthu yemwe angalifikile komaso muyenela kuziwa kuti mulandu sumaola ayi ngakhale patapita zaka 20 azayenelabe kuzengedwa chocho ngati nthawi yafika akuluwa akayakhe basi palibe kuchitila mwinaso ayi muthu okuba amayenela kumangidwa basi chocho boma lipangepo kathu asamusiye kuluyi ayi watibela ndalama zathu zochuluka.

 16. How much has govt lost on muluzi personally ( medical, expenses, fuel,house,allowances ,pay, holiday, benefits) and how much have we lost on his case from investigation, arrest and prosecution? To me its a loss ledger

 17. I have now realised that Muluzi’s case is just very minor as compared to……..hence need to just leave it.However,to deter other would be offenders.kkkkk.Very doubtifull.Start the case and see the UDF MPs changing seats in the next sitting to join the only flag bearer, soldier.lol.Politics in Malawi.

 18. One amene akuimba milandu imeneyi ndi agalu, tiyeni tikumbukire ntchito imene anagwira polowetsa democracy, free primary school, lero lino umbuli unachepa
  Long life Muluzi, God bless you

 19. Banda anaba koma zinthu mkumasinthabe ndalama mkumapezeka koma osabanu mukulephela kutitithandiza. I sayd leav muluzi alone u suckers if u dnt have something to do go and have masterbation at home okey.

 20. Kodi nde olo alimbane naye chingatisinthile ife nchiani ? Amene samaba mmboma ndindani? Leave muluzi a lone u motherfukers nanunso ndi mbava kuno milatho inakokoloka kalekale popanda olo mmodzi odzafunsa fuck u all yo motherfuckers, and if there is someone who is happy wth this then fuck u too.

 21. Tangomumangani wakubayu inu…asatitayitse nthawi. Bingunso tikanamumanga koma basi poti ndi a malemu. Onse obela dziko lathu losauka kaleli ayenera kumangidwa. Boma lathu lilowa pompano ndipo tukonza zinthu momwe akufunira amalawi….watch out….!!

 22. Tiyeni tithane ndi cashget no mattar kt anayamba nd mandalawa muitane masten abwere adzayakhe miladu yao ,B Muluzi musiye kaye .I think masten wa anatinyema pakulu aMalawife .Nanuso zthu zukuvutan School kukwza kumeneku,mafana ambr tasya school chfukw cha kwacha yavuta pa Malaw.

 23. Umbuli ndi matenda dont you know this economic crises began during pressure group foarmed by this stubbon politician who stand against kamuzu from that time till now our kwacha is not stable the ones who is behind this are those we call them donours what we could know is this we are in last days lets pray togather be united only one king will refeal all the wounds Jesus tisamangolozana zala uyu achoke abwele wina mavuto azakulabe

 24. what this stupit govrnmt want 2him,in short they want 2 transfer our money 2 their accounts cozz nobody can trust this trush,if they faild 2 lead,hw they cn manege 2 sotout this cas,if u hve nothing 2sy,shatup ur mouth en waiting 4 jagement in 2019

 25. paja mumatero mukasowa pobera ndalama za boma agalu inu. case ya muluzi ife tinayiwala kalekale. osamusiya apume bwanji ? dziko liri pa mavuto azachuma ndi pomwe inu mukufuna njira zoonongera chuma chochepa chomwecho. inu ndi mfiti za atsogoleri ndithu .

 26. kufuna kutchuka pandale ndidzina lamunthu wina sibwino, ngati mufuna kutchuka tchukani powagawila waanthu zitukuko zomwe munkawalonjeza zija, mafactory aja a manga kuti? Boma la DPP linasokoneza ma Billion angati? Munamangapo ndani? Joyce Banda ndi PP + cash gate wanthu sitinaiwale nobody arested. Now we are fast approching Elections mufuna kuipitsa mbiri zaena? amalawi osadzapusitsila ndi u profeser kapena PHD; is just a name, chose people who understand the poverty of malawi

 27. How many times u will be talking about the SAME CASE.
  NGATI SIMULI SURE BWANJI OSANGOSIYA,
  WHAT ABOUT CASH GATE?
  BOMA SILITHA KUKAMBA NKHANI MPAKANA 8 YRS NKHANI IMODZI NO NO THIS IS BORING.
  BWANJI OSAPEZA ZOCHITA ZINA?

 28. Bakili ndimuthu wamkulu amaziwa mozembera mwake Mulandu ukayamba muyamba kumva muluzi wapita ku garden city afuna akaonane ndidotolo wake

 29. Kutukwana Kukupindulira chani #missi juma? Kukuonetsa kuti kusukulu sudapite ndiwe moron a simple idiot pali zokhudzana ndi mtundu apa? Ukuoneka ndiwe otembereredwa makolo ako adakutaya chifukwa cha ubongo wako wowola wonunkha wosaganiza bwino fb sudziwa meaning yake ndiwe khakhakha.

 30. Bakili is da bastard dat made our country suffer.from corruption..education down fall.increase in criminals en hunger.iwish after kamuzu was out bingu was da next prez.ihate bakili to da bone

 31. Akuyenera kuti ayakhe milandu basi AMalawi tilibe thawi yoti tizilakhula pakhaniyi siyani boma ligwire ntchito munthuyo sanasiyene ndiwina aliyense olakwila dziko kukanakhala kuti wina wake waba khuku bwenzi tikupita kti tikamenye pomwe muludzi anaba ndalama zoti zikanathandiza dziko ndipo ambiri mwainu abale anu anamangidwa khani zopanda umboni mpaka kukakhala kundende moyo wawa onse koma palibe chomwe mumakambapo kapena kulira walakwa akuyenela kulandila chilango basi palibe zokambakamba apa

 32. They jst wasting nthawi fr nothing hw mne tmes we hear about zopusa zt muluzi’s stry? Where iz the out come?. musamangotiputsitsa ife simakanda mmusiyeni chair mzangayo azipuma kambani zothandiza anthu cz nx elctin iwl chase u.

 33. 6 yrs mlandu woba ndlama zothandzra zko lose usanathe kmaxo osamangidwa, woba khuku kuxungidwa m’chitokosi……….osangozxya bwanj ? kumangotiphimba mmaso ife mmat osazndkrafe, snanga tribe ndalama nde tmakhala opanda zeru……..

 34. Team ikaluza imachulutsa zokamba…..DPP palibe chomwe ikupanga…..busy kulimbana ndi nkhani zoti sizingatheke anzanu adaziyamba kom adazilemphera ndipo lero kulibe……kut muyendetse nkhan zimenezi mpaka pamapeto mupeza kut mwaononga ndalama zambiri zot mukadapangira chitukuko……zomwe mukuba inu pano zidziwika mukadzapuma…….ife sitikudziwa bwana…..samalani zidzakutembenukirani bwana……kkkkkk ndiye ndinu omvetsa kale chisoni….

 35. Milandu ya mabwana imakambidwa zakazaka mwini wake osadzamangidwanso koma mphawi ndiye mlandu wake umakambidwa tsiku lomwe walakwalo and kundende amakalowa mawa lake

 36. Panthawi yomwe Muluzi amalamulira sizidavute ngati mmene zuvutira apamu oky. Nde boma la DPP zinthu zikuvuta hvy nanga inu a DPP nde mukuba zingai popeza zinthu nde zingolowabe pansi. awo mukuti mbavawo sizidafikepo apa. khozekani nanu kuzamangidwa mopyola malinga ndimmene mukuchitira apamu cz mukuwanzunzawo adalamulira kale kwatsala nanu azakumangeni ndi mmene mukubelamu t

 37. I would love to see justice prevailing on this case. The guy got himself rich from the money meant for the government, that is if it is true and the only to find out the truth is to get him in court again. i will be following every step of this case. I don;t hate the guy but i hate when i hear that someone stole government resources, whoever the guy is.

  1. But you know what? Mark, Peter Mtharika is more than blind and blurted man, He forget what his Brother did for us, okay by the way, who help his brother to be a President? I think its better Peter Mthalika must resign.

 38. My fellow mlawians just leave Muluzi alone focus on improving the life of ordinary mlawians thez stinking poverty in our country.lets remove poverty mentality lets build our warm heart of Africa ( Mlawi)

 39. Pandalama palibe wokhulupilika osakakamila kukamba nkhani zabakili .nthawi imeyo inali ya cheya inunso ino ndinthawiyanu panga zoti zikuthandizeni muluzi ndinthiyake yake yodyerela

 40. Sopano bwaphiyo akayankhe za 92b yabale wakeyo komanso awudze anthu kuti pa chaka chimodzi ndi 6moth waba zingati asanafe kapena asanachoke pa phando.

 41. Make money without side effect !!! .are you a business man or woman, are you a musician or an artist, or a footballer,do you want to be famous or you want to become rich or powerful, is better you become a member of the Illuminate and make your dream come through, this is the chance for you now to become a member of the temple and get what you seek from us, if you are ready to become a member and realize your dream then email us now [email protected] you call us through this number: +2347065758576

 42. presedent Peter walephela kulamulila dziko. akungo kamba zamilandu malo mowona zosowa zaanthu ife tidya milandu iye waila kuti Bingo naye akukhuzidwa kuba ndalalama zomwe anthu amkagawana munyumba mwake amazisunga nchipinda zija peter nayenso wakuba obela mavoti amalawi anthu awa andalele akupusisani muonetsetse akuba kulibwinpo kukhala

 43. Kodi mlandu wa JB NDI PETER uyamba liti ?mukulimbana ndimuthu amene analamula bwino economy inali stable koma inu ama degree ikukukanikani .simumumanga mungonamiza anthu kuononga misokho yathu .zopanda nchere zaziiii

 44. Malawi politics is always basing on messing other peoples integrity and courts nothing else and no development.We are fed up with this srtupid issue.

 45. Malawians zosankhana mitundu ndi kupepera.Dziko lililonse limapangidwa ndi mitundu yosiyana siyana.Even south afrika kuli ma Zulu,khosas,thembus,vendas etc.Phunzirani xul kuti muone kumbwambwana kwanu kuipa kwake

 46. Boma la malawi linadzazidwa ndi ziwanda za satana silidzakonzeka pano tukamba za bakili muluzi okay akulamulayu panopa waba zingati kuchokela chikhalileni ndikuti kuchokela pa kamuzu muluzi bingo joyce peter anthu oyipitsitsa mapeto a kuyipa bingu nd peter koma anthu sumukuwona ena chifukwa cha madyelelo ena chifukwa cha kusadziwa ndiye polankhula kumangolankhula mosayang’a za lelo

 47. DPP some how you have to thank and appreciate this fossil he surrender the position to alomwe but u can’t say thanks. Wat more do you want apart for wat you ‘ve got already? PRESIDENT. LET It go let’s focus for how we impliment the development

 48. An2 openga mwapanga bwanj, asiyen achair au3re osat zachamba zomwe mukutiuza apa cashgate yakunyeran ndyeno apa mukulimbana nd za

 49. is mk 1.7billion enough for the economy of malawi? probably the answer is no.y the government leavin behind the cases of cashgate and money fraud in the government of DPP.iam not accusing Dr Muluzi inocent,he dd corruption during his time…but when we talk economy of malawi in those years was atleast stable than the malawian economy today….following the case of Dr B Muluzi is nosense,malawi only need the wise and sophisticated leaders,not like ones we have. think clearly..ya comfusing citizens of malawi…….

  1. Ndimafuna ku commenta koma basi you said everything, Peter Mutarika admitted that his brothers regime misled 92 billion Malawi Kwacha yet they want to put a fight over 1.7 billion kwacha! what a shame!

  2. Mau opatulika akunena kuti: Uchotsa bwanji chitsotso chili mdiso lanzako pomwe iwe chako chipanda chikukulephera kuchotsa. Kodi iyeyo Peter akuzitenga ngati yani? Waiwala malemu uja ndalama zimene anatibera AMALAWIFE?

  3. corruption has nothing to do on who got more than that or this. a note of k100 contributes in running economy so let’s justice do its best to all. corners

 50. Mmalo moti muzilesa zonyengana akazi kapena amuna okha okha bizy kukamba za anthu oti analamulira anapita. Mulungu akakulangani asogoleri inu ndithu kuvomera tchimo kamba ka ndalama? Mulungu perekani chilango asanamwalire

 51. kod enanu mudana nazo bwanji chonsecho muthuyo anaba why malawi? muthu ameneu ndiamene akusaukitsa malawi chifukwa…….akanachoka boma osaba ena obwela pambuyo pake bwez akuopa chimodzi modz bambo akakha oimba ana ekenso amakhoza kukhala oimba ndiye umbamva ndiumbanda wavuta pa mlw his responsible amangidwe akunzuza myoyo ya athu ambili

 52. leave Dr Muluzi alone.We ate together that money,remember he used to come in our areas and give out the K50z and he used the same money to compaigne for Bingu Mutharika

 53. Pajatu ife Anthu akumwera ndiamene tikulamulira malawi ndipo Muluzi sangamangidwe. Ngati ndiwe Mchewa kapena Mtumbuka, Panyapako!

  1. Everybody is savage we know something you don’t know” Stop pointing fingers each other don’t educate urself rubbish! F*ck u all useless people mada f*cker

 54. Stupid ……leave him alone….why can Thy arrest Joice Banda???stupid Leave acheya alone .
  Kumbali yawo anapanga chitukuko…
  Nanga zinazi zapanga Chani…

  Asiyeni Acheya apumule..

 55. Muluzi stole our money and he must pay for this, this is fact whether u like or not.if you want to make Malawi a better nation arrest all politicians who steal our money , Malawi is a small country but we suffering bcoz of these foolish politicians who just inrished themselves ignoring us who put them in power

 56. Dpp= translation: devolpment poor proqram. Kukanikatu uku khani kungoti thoooo, ajoyce Abakili, atani? Tasiyeni amzanu anagwila ntchito yolemela, kumangoyakhulayakhula, Tapangani zanu anthu akuyamikileni, panotu chatha chaka and 6 month. Koma palibe kamene tamva, kuti bwampini apanga chitukuko kwinakwake, mukungolongolola basi. Mpaka 2019 wwooo, mukungolongolola mmalo mopanga chitukuko, eti amvekele ine professer. Professer wakuti sibolaso wa standard 8, kumphunzila ndiwutsogoleri ndizosiyana.

 57. Zidzatitengera nyengo kuti Malawi wathu atukuke chifukwa boma lili kalikiliki ndi nkhani za ndale pomwe chuma sichikuyenda bwino. Milanduyi ikayamba mboni za bomazo zidzigwititsa ntchito ndalama zanthu za misonkho zomwe zidakathandiza zipatala ndi ena aja omwe mpaka lero alibe chakudya chifukwa cha kusefukira kwa madzi

 58. Next time is your turn.You are owning infrastructures which are mixed with Malawians taxes.You were busy creating earth’s paradisal with our money.Soon there will be eviction & confiscation if you are owning properties which are mixed with the taxes of poor Malawians.

  1. ndiponso achawa sadziwa chomwe amafuna coz kamuzu anasiya ziko lili bwino jomba wawoyu waba chuma chonse koma kumukondabe muzi za athu mchikwa chake akungoseza makaton kuno idiot

 59. Mwasowa chochita Joice wakuthawani,za Bingu sizikuoneka ndalama kumene zili,Tembo naye nthawi ya Kamuzu nayenso wapangapo ,osamangokadya maungu ndi gogo wanu kumudzi?malawi aliyense amadziwa kuti ndi katangale ngakhale inu amakhoti mwatsala bodza ndi njala!

 60. Mukamamuyimba mlanduyo muzimuyimba mlandu wa ndalama yokwana K1.7 trillion chifukwa nthawi yomwe amabayo kwacha inali ndi mphamvu

 61. agalu alomwe mulibe ulemu nzelu mulibe, achair ndi 1 mkhope zonyasazo mnxiee ngat zakuvutan siyan ayao amakwanisa zomwe mukanikazi

 62. Boma la peter wamtalika liribe nzeru Asiyeni a chair six years kuzitenga wanzeru kuposa azako anse ngati dziko lakukanika kuyendesa tangotulani pasi musanamwalire

 63. Cholinga chanu kuononga ndalama za boma basi,, ndi mlandu ingati yomwe mwakhala mukuluza nkumalipila ndalama zambiri? musiyeni anazilipila yenkha pa ntchito yomwe anagwira pa Mw pano a Chair!!

 64. Moti muzitiuza zopanga chitukuko mukutiuza zopusa apa, Ndiye mukalimbana nawo ndi amane atabweletse chitukuko muno, Mwalwphela achina Peter Kulamulira inu

 65. aaaah zilibe phindu kuntundu wa amalawi izi kuyambila olo kosayambila ndichimodzimodzi inu asatipusutse iya

  1. kma akanakhala osauka waba kuyesa kukuwa mutentheni amaneyo but 1.7b misonkho yaanthu osauka mukut alandire ulemu chaa*poor mind*

 66. Are scared of joice banda who stole de money openly pano mukfuna kumuzunza muthu amene kungo ganizira,nanga padutsa zaka zingati u gyz uare all fools stupit mukumbutsa zithu zinachitika tisana badwe

  1. cisale what shall it benefit us as a nation? instead of focusing on the corruption which is on now. stop corruption that is at stake..Bingu and Joyce banda also stole money from gvt.. these cases will just milk money ftom gvt

  2. We are in the sme page Neddie Charwita y aklimbana ndizakare kare zithu zoti till 2day sitkudziwa kti amaba munjira yanji pamene Bingu zinapezeka nyumba mwake Joice ndiye malawi yense

  3. u mean nawonso pakatha zaka 6 bas azasiye kuwayimba milandu no@Maulana and Ned. Milandu yaanthu andale imakhala yobvuta worldwide imeneyo ndi ntchito ya ma judge another arm of gvt amagwira ntchito independate

  4. Sis iyiso ndinjira imeneso boma lizipitilira kuba ndrama kdi judge amalandira ndrama zinga pa hour? athutu akfa ndinjara ziko muno ngati smukziwa muvaso akukuuzan kti boma la ononga 20milion pa mlandu omwewu inu muli dyoo!! Muli akchita bwino

Comments are closed.