Malawi ruling Democratic Progressive Party (DPP) treasurer for the Northern Region, Happy Kumwenda is admitted at St Johns Hospital in Mzuzu city after unknown men shot him with a gun Monday night , according to reports.
Malawi24 has been tipped that Kumwenda was shot on the back by three men who drove in a Saloon car shot him at his residence as he was talking to his guard at the gate.
“A saloon pulled up, there were three men in the car, one of them took a gun and shot me,” he said.
However, the DPP is yet to make a statement on the matter.
At the moment, Kumwenda reportedly says that he knows one of the people that shot him, something which police are not taking into account as of now and have reportedly instituted a probe into the matter.
Aaa mpaka pamenepo thats politicts
kuomberedwa kwamkuyu kuli ndizosatila zake amalawi takuziwani masiku ano mkafuna kuba mkulola kupha wachibare wanu kuti munamizire zoti ndiwachifwamba (kwa ine ndikuti bwezi akanafelathu madotolo msamupase mankhwala afe ameneyo kuba kwake kwamuyika mmavuto)
Eeeeee mapeto ndiamenewo kkkkkkkkkkklkkkkkkkkkkkkkkkk zorry
I like that,dpp chilungamo,chitukuko,chitetezo kaya kwinako
Kkkkkkkkkk@happy kumwenda
Was not shot with a gun, that’s a knife, after he was caught in someone’s house. Tell people the truth.
wamwano ameneo ku bar kumeneko masiku achisangalalo ano taganizani mozama amalawi fut malo ameneo sangakhale ndimoyo ai akadafa ndithu koma amalimbilana azimai nanunso muzi mukamatumiza khani muziamba mwafufuza bwinobwino kenaka nkumapangano post khanio fut sichida chamasewela ai musatinamizepo apa cholinga akazi ake asakhumudwe, kuti amalimbilana mahule.
What kind of pollitics are now you doing malawian! If you ahave aproblem with someone just approach to him/her and tolk ,if u see is big issue go to count ! Wy actualy u want to killing each other there in malawi there z no money .
Why but Why politics its ended adirt Game
I disagree with you who are saying DPP is worst , you comparing with which party ? We never develop in northern region bcoz we r continue supporting JB but what development did we get from her when she was in power ? Jb is gud leader but not gud politician thus y everything was crazy when she was in power,if you can see Malawi politicians every time is for compain they don’t care about poor Malawians, can some1 tell us how much they getting now per month
Malawi why shoting one another get well soon mr treuser
Killing someone one as if you will live here on earth forever wakeup think smart.
DPP kodi ndaleyanu ndiyophana or bwanja anthu akufa kamba ka chipani chanu ndinu masataniki kapena mukudziwa chani nanu one day mudzafa mulungu naye ndiogwiya nanu pa muchitidwe wanu.
quick recovery m,bale withu soni ziwakole God guide
Ubwino wake akusaka anthu achumao
Why amalawi tokhatokha shooting
Achita bwino kumuombera ndipo ziliso bwino kuti sanafe awonetsetse kuti mzipatala mulibe mankhwala .anthu awononga dziko awa.
Malume sankhani bwino chipani mwalowa chipani cha balaba. Is gd bkz u still alive think about it.
mudzafa imfa yowawa….
Look you r trying to kill a man by name of treasury General kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk wait for the campain time. you will get it.
Very sad news.
That’s very good
that man must shoot all of them useless readers
naeso osavula magalasi..
Where was he by the time was shooting him, oh my brother, sorry recover quickly and may God be with you and heal your wounds in Jesus name.
Sad news kodi Malawi akupita kut?
A Police Akumabwerekesa Mifuti Kwa Zigawenga Ndi Chifukwa Ukuchulikila, A Police Aphetsa Anthu Ambiri
Why shooting tokhatokha? God have mercy to ma nation
I wont judge him untill we here the monster side of the story. Zitha kutheka mwina a maniwa amanyengaso azikazi a anthu. We neva know! ! Its not always abt politics
#FREDOKISS ananena kale
Eeee kumpoto ubwino wake oyimba anayimba kale kuti kukanakhala kadziko bwenzi dziko lake likanakhala DRC Mulungu akusamalireni m’bale.
Musamayambe ndale musanatsazike kwa agogo,
Thus bad plse we trust police help us
Is it a shootgate since it happened at the gate?kkkkkkkkkkkkkk……
TIONE NGATI ANENE NGATI ZA NJAUJU KUTI THEY STILL INVESTIGATING A DPP KOMA ANTHU ALIBE MANYAZI KUOMBERA PA ZIFUKWA ZOFUNA KUBA NDALAMA ZA BOMA KIKI!
ya apandiye zilibwino mumangomvela kwa aneba tiyeni nazo
ya apandiye zilibwino mumangomvela kwa aneba tiyeni nazo
If he waz shot n he is alive he hav 2 stop politics and kuyamba kupemphera coz mulungu alinaye cholinga
If he waz shot n he is alive he hav 2 stop politics and kuyamba kupemphera coz mulungu alinaye cholinga
YDI
YDI
Zosakhalala bwino ayi amalawi zomvesa chison
Zosakhalala bwino ayi amalawi zomvesa chison
results of political
results of political
kaya zanu izo
Who put you plaster on the wound? I think he needs some training
Hahaha mwamba kuphana nokhanokha a dpp mwatani chitetezo chilikuti
mumuze asiye Ndale ayambe kupephera.
Amen
Yaaa thanks guys gud job
Pitilzan ku shootanako mwina mipandoyo mungasiileko anzanu kkkkkkkkkkkkk
Shame the boy he missed the target he should shut up a Man himself because he’s mass up our Country.
Getwell soon
Thus Good..These fucking DPP guyz …they are stupit..Bull Shit…They must die..becoz Malawi is getting worse becoz of these fucking Guyz!!…Akanafa.
cashgate ina mwaona wait
Shame
Uku ndikulakwa
Mwini wake akuti akuwaziwa ndiye inu mukuti unknown assailants mukubisa Chani, akutumani?
bas ukali mesa DPP siyikuthandiza pankhan yakalamulidwe kadziko. ndendibwino kutha azitsongolelewo Malawi yanyanya et
Kkkkkkkkk koma anakusidzatu apa
Another zenofobiaans
ndangowerenga nawo
akupheni kumene ndarama zanu mumadya ndi ife
Eee kwasala trainingiyo akaipangila ku sanjika nonse andale musamale muphedwa ngat mbuz 2016 muziona
Northern region z not for Dpp government, we r independent
Ifenso ku southern kuno Dpp is for Dpp, enafenso ayi taikana
gud news buddy
ifeso pakat sia DDP sitikuiziwa fusani ena aku thyolo ndi mulanje
ifeso pakat sia DDP sitikuiziwa fusani ena aku thyolo ndi mulanje
Kkkkk mtima kunzunza mbuyake
Isaaa ifeso kuno ku Thekelani iyayi taikana mwina ku Lilongwe
ana anjoka opanda chiyembekezo…..mukhalira yomweyo mbuli zakumunda inu…muzafa yowawa imfa mukamachedwa ndi nkhani zandale
ana anjoka makolo ako akuzuzidwa ndiumphawi mbuli iwe fanny
joining politics is like u apply to die
Zalowa m’nyumba tsopano!
These could be the ones that killed Njauju. They are blood thirsty. Remember they have not yet been arrested. Now terrorising the northern state. Kuno ndiye tithana nawo.
Politics is a dirty game, there is something behind remember Paul Mphwiyo’s story. anthu andale Zophana ndiye kudya kwao. akagwidwa anthuwa ziululikaso zambiri just wait see
Tizingo shootana modzi modzi basi malinga ndi mene zilili ,
Phepani, get well soon
Mbava yoba tax payers money ndi mbava yozisaka akumana. Why missed his chest
Mzimu was Njaunju wakwiya…
I can see now malawian we our be cannivals real, stop it doing that
get well soon
New year,New life. Just resign and 4 the foot of Jesus
Sad
Xorry 4 the that’s
Aliyense adzafera ntchito yache..
Yamikani Ambuye poti wakupulumutsani ku imfa ya dzidzizi.
Muli ngati wina pompo nkungosiyiratu za ndale, nkukayamba kutumikira Mulungu.
Mukuona bwaaaaa??????????
Anangova kut treasurer at alinazo
Wadyapo
room yomupanga admit nsungwi chuma wachipani imeneyo.!??
i dont need this gay
Kwathira zipolopolo basi akupanga zopusa, ndikamabwera kumeneko anga ma piston awiri alipo kale opanga zachambayo kungondiuza ndizidzagwetsa m’modzimodzi bola sodayo osaumila!
quick recovery
Kkkkkkkkk, zayambika?
May God give him happiness during this hard time.
Mmmm God have mercy on Malawi
Sit down and talk. Guns aren’t part of us
Am very Sorry. Get Well
DPP woyeee! boma langa likuyesetsa kupereka chitetezo kwa anthu ake, DPP woyeee! zikutheka bwanji?
ukunena zoona
uziona wakula watha umaona ngat peter nd bambo ako eti,,,,,uisoVa
GET WELL SOON BIG.TIWAPEZA ACHITA CHIPONGWECHI MULUNGU SIMUNTHU AJAWA ANAGWIDWA BWANJI?
Akudziwapo kanthu ameneyo .
Zikukhala ngati za Lutepo.
Musathe mawu anthu, nkhani yophana ndi mfuti ndi ya chilendo ku Malawi kokha kuno.
Osadanda a treasurer kungoti amangofuna kuyesera mfuti ngati ilibwino. Muafunse abro mphw….. zinali ngati momwemunso kenako nkumamva kuti dollar zasowa, watch out!!!!!!!
Kumalawi kwasanduka ku moshiko kapena s africa?komabe chipanichi nichophesa n chopusa.
Tangokumana akuba okhaokha pepani aTre. Udindo ukuphetsani lowani china chipani, kkkkkkkkk
Tangokumana akuba okhaokha pepani aTre. Udindo ukuphetsani lowani china chipani, kkkkkkkkk
The result of insecurity in Malawi no foul play. I assume!
Mwati Dpp? Nkhani Ya Bho,keep The Fire Burning,koma Kuphonya Too Much Guys,aaa! Tapangani Training Yamphamvu!
Chinaphesa amako@John
Sanaone bwino unali mpeni umenewo
he was mphwiyod….kma makape amenewa mumawapeza kuti amangophonya
comment initializing….
Mfuti yakenso inali ya plastic.koma apa myenera kuti ndinu nokhanokha chifukwa maprophet analosera kale kuti m dpp mzakhala chipwilikiti
What is happening malawi,A God fearing nation,the warm heart of Africa now guns all around # why shootings
Malawi is no longer fearing God nation bro, how can you say that yet satanic are ruling us?
tell me how can we say that we fear God yet we accept homosexuality?
Disappointed
On day God wil judge if indeed we’re a God fearing country
DPP CADET ….osati zomwe mkutinamizazo
reaping wat you sowed.
ndiyomwe adalembetsa!
conglats
ukuziputa limbanazo..munasankha u treasure BaBa
Pepan kwambiri but munajoina chipan chophetsa n chopusa
Third comment
Dausitu ameneyi
khaida
That’s not the way to enjoy freedom
chikhalireni pabedpo buanj sakugona?
6th comment
Inu amene mwachita izi pitilizani kutero kwa anthu amene amati zikuenda pamene anthu ena akuvutika, tienaoni mmodzimmodzi.
napepe boss
Nkhani zake chipani?? Pepani
second coment
Second coment
Boko halaam
Mmmmmmmm mmmmmmmm..????????? Malawi.
First comment