Malawi Police in the commercial city of Blantyre have arrested 136 people for the offence of rogue and vagabond.
Speaking to Malawi24, Blantyre police spokesperson Elizabeth Divala said out of the 136 people, 26 are women.
“We arrested these people around our areas under Blantyre police: Ndirande, Chilomoni, Milale, Soche, Mpemba, Chilobwe, Chirimba and Sigelege,” said Divala.
Divala further said some suspects have appeared before court while others are yet to appear in court to answer charges of rogue and vagabond which is contrary to section 184 of the penal code.
The law of Rogue and vagabond recently attracted debate as others argue that it discriminates the poor and that it is prone to abuse by law enforcers.
A study conducted by the Centre for Human Rights Education, Advice and Assistance (CHREAA) also deemed the law of rogue and vagabond as ‘No justice for the Poor’.
Ngankhare muwagwire mfazy idzinthimabe paka kunja mbee mukuremphera kugwira mbamva APA ndye mwaonjenza.
Amangomwa mowa limodzi ndi mbava! Ukunenadi zoona mc loud!
Yaaaaa,ndintchito yawo,bwelani kuno ku jon,muzawone kuti apolise akutani mumaderera aku malawi kkkk
Kuyenda usiku ndi chifukwa nanga osangopita mmakomo ndikupempha bwanji .nanga inu mukugwila anthu inuyo akugwireni ndani zopusa basi
Mbava
This law should be submitted for legal review.
Basi khirisimasi timwera za apolisi nanga ma K2000 onsewo
hahahaha am business man dealer mukidziwa kut dealer amadana nd kuwala shaaaa kma police sitilemeratu ife Dzuka Malawi!!!!
Mbava simungazikwanitse .
Zoti a police amadana ndi oyenda pansi usiku izo zinatukukila kale .
Zimayenda usiku koma pa galimoto , a police wo nkumapeleka ulemu.
“136 People arrested for walking @ night” kikkk! Kusowa zochita kungofuna kukokera tindalama basi. Kumangomanga oyenda pansi pomwe oyenda pa galimoto sagwidwa vacabo
eee ndi azimayi omwe koma akut ndichani kkk
Does FREEDOM do exist in our country?
Christimas yayandikira apolice atolele ya ndiwo,anthu onsewo akapanga ma pinipini akatero zayenda kkk pa malawi
Pin???? 5 bwa?? Ati ku court 10 pin……….
Mwalephela kugwila a #cashgate mwati mugwile oyenda usiku.
Go to Tanzania guys any tym u want u can go wat ever u want thats why akuchita bwino si onse amene amayenda usiku Ali wakuba
kodi kuyenda utsiku ndi mlandu zopusa basi nanga utakhara kuti wasika basi yawusiku cholinga kufuna kutibera basi ndi zopusazi andu
Kumanga anthu chifukwa choyenda usiku? Wat a shame and a disgrace to our useless police! kulimbana ndi anthu osauka pamene zigawenga zili phee kudya ma bulger ndi ma pizza…
aaa. amangowonelera oyendapansi bac.#zazii.
Ngati palibe wa galimoti ,onsewa ndie atuluke palibepo chilungamo apa
ok?
bravo police! tidaunapo ubwino wazimenezi!
boma la bwampini lazingwa.likufuna kupanga ndalama.mk6000*136 people eish
I dislike the Munthalika’s Government becouse they take Malawians as their garden,in short that is one way of collecting monies.
I don’t understand. Why not?
Most of them were bullets supporters kkkkk
Xmass yayandikila muwabele anthu muzinamizila kuti ndinu a vacab
mukulephera kugwira mbala ntchito nkulimbana ndi vakabu machende anu nonse apolisi
Please help me. Is rogue and vagabond an offence of the night? What does the Malawi Constitution say concerning the freedom of movement?
Panyapanu kusowa chochita kumalawiko basi
Oyenda pagalimptu usiku smawagwra bwanj?Amphawi inu
I’m a music producer, ndikuvuta kwamagesi masanaku tikumadalira kuti tigwire ntchito usiku koma tikukanikanso kuti tigwire ntchito usiku chifukwa choopa vacabu. mkumasauka ndithu munthu zochita uli nazo mxiewwww sitizachoka ndithu pa number 1 dziko losauka padziko lonse lapansi
Mukumawagwira anthu osalakwa pamene mbamva mukuzipasa sawacha,mukulakwa kwimbili.
Samayendera miyendo ya a police,zachamba!!
The first democratic country in African but is the most stupid country you can ask,I hate stupid rules.
Unfortunately this rogue & vagabond law was made for the poor people because the same night some well to do people were driving in the same Blantyre roads..When the police is busy chasing people in resthouses,The well to do people are in Lodges & Hotels doing the same thing freely..Eeeeish.
Pa theba pano ndi 24hrs tikuyenda pa nsewu
Zaziiii Moyo Wa Chitsamunda Basi Koseko Mkusayenda Yendani Muone Momwe Azanu Amachitira Ndi 24hrs service not zimene mukupangaz zompusa basi munthu asayende zompepera basi
Xmas Apolice? Mwayambirira.
Our Neighbouring Mozambique athu amayenda pakana utsiku ine ndinadabwa ngati ndikulota even ma Shop saseka koma timati ndi Dziko la Khonda. Kwanthu kuno kwakula ndikubelana ndalama. Kutenga kwa aphawi opeza movutika WHY ???
Zautsili Basi,osamalimbana Ndi Amene Akuba Mamillion Bwanj?Nchifukwa Chake Akapolo Inu Mukungovutika,kodi Mukawagwira Nde Amakugailani Ndalama Zomwe Amakalipila Pakhothizo?Zaugalu Basi,ntchito Kumangonyenga Mahule Mmastreet Kumanama Kuti Mukugwira Vacab,osamakagwira Anthu Akuba Masana Mma Bankimu Bwanji?Zauphwetelele Basi Kusowa Zochita Eti,ngati Mufuna Ndalama Mudzingopempha Zidzikugailani Mxiiiiiiiiiiie
Amene akudana nazo sadabeledwepo kapena kupangidwa umbanda keep up our police officers
Iwe unaonapo okuba atagwidwa vacab?amagwidwa ndi anthu ngati iwe wemwe,kapena ukumadya nao za bello iwe
Zaziii mwasowa chochita eti cholinga kuwabela anthu ndalama mukagwileso bwampini
bwampin nde ndi iweyo!
Mukukhala planet yanji kodi? Masiku ano anthu sagona. 3d century ino koma malawi ayi ndithu.
Acyen bac sanalakwe thats thier rights
Kupikisana Ndilamulo, Eeeee Umaonadi Kiyama, Apolice Anthuwo Mukawagwila Osamawachita Nkhaza Chifukwa Ena Amakhala Osalakwa.
Kkkkkk.the headline means only 136 people walked at night. The article is accurate. Kkkkk just joking
Dziko losalila ngati ili sindinalione tabwelani muzaone anzanu ma shop amakhala otsegula 24h
What bout those drivin at night?
osakagwila amene akungozimitsa magetsi bwanji kapena jb kunja kuderera anthu osalakwa bwanji ose ameme amakagwila anthuwo ndi aaa
Ntchito ya bwino anyamata fisi yekha ndi amene amakasaka usiku masana amachita manyazi ndi mawonekedwe ake
Good job guys,keep it up!.
ndienso bola kukhala kwaeni kuno
Chonde chosani chithuzicho kodi mulinacho chomwecho khani ili yonse?
kumangogwira anthu olezera basi?
Ee malinga ndi khrismasiyi aliyese ali against ndalama apolisi,akuba,osaba onse.
Vakabu, kuli Shamba agwireni asiye kujoga
zausilu
Ma roadblok azikhala ndi nthawi yoletsa galimoto kudutsa mpaka kuche chifukwa a armed robbery amagwiritsanso ntchito galimoto koma mumangogwira oyenda pansi okha.
And what if you are travelling or coming from a long distance ?
The same applies to pedestrians.
Amageni basi osawasiya, ameyo ndi ye mbavazo, mukawagwira muziwakozakoso pakali patali monga munja muchitila kuti asiye kuyenda usiku
iwenso kesten ulibe nzeru koma sudziwa kuti kuyenda usiku ndimulandu maiko ambiri too much umbuli ndumene wakukulila ufunse anthu ku RSA kupezeka ukuyenda usiku mulandu wake ndi R500 kuti utuluke ndie iwe utichani kodi sukudziwa kuti ateteza anthu a blantyre kuphatikizapo anthuonso
Musanamizepo anthu apa bodza lanulo RSA yake Itiyo? Munene kuti public drinking akakugwila ndi R500, koma kuyenda usiku anthu amayenda kuno
I though cities never sleep? I think time has come for real democracy. We are in the twenty first century
Who said that?
We have a real democracy, but with robberies everywhere and prostitution the police have to be extra careful
a kuti vakabu a kuti vukabu ine ndiri musero
kumanga anthu nde nambalà wani, mmalo mot muziganizìra njira zopangira survive dziko lathuli
Akungofunapo Dollar Basi
KUNO KUTHEBA ZAVAKAB ZO NDI NKHANI ZACHIKALE KUNO ANTHU AMAKAYALA MALONDA NGAKALE USIKU MMAWA NDIKUMAWELUKA. KOMA MALAWI DZIKO LOTUKUKA MASANA WOKHA KKKKKK, KUNO DZIKO LIMATUKUKA MASANA NDI USIKU OMWE.
Man chauluka mwanena ngati osaganiza. Akamati chitetezo ndichimenecho. Kodi munthu oenda usiku ungamuziwe komwe akupita ndikomwe akuchokera? Bwanji asanakawagwire anthu ma pub ndi ku depot? Achita bwino ndipo asalekeze pomwepo ai.
Oyenda pa galimoto usiku amaziwika kumene akupita ? Nanga bwanji samawagwira ? Onse a armed robbery othyola ma bank,filling stations amayenda pa galimoto.
who said pipo mustnt walk at nyt whose business is that day or nyt its ur country guys no boundaries shame to police
Anthu amenewa amafuna awone fisi paja kuwona fisi sikukula koma kuyenda usiku
Agwidwa bkoz sanaziombotse
Apolice amalawi ndi amenewo
Ndiye m’malawi ameneyo.
mwina amafufuza timaganyu kkkkkk anthu openga inu mwatani kodi?
This is violating their rights these pipo got the right to sue against government kumalawi kulibe malamulo oletsa kuyenda usiku, sungangozindikila munthu wamangidwa with no reason,sizowona siwomse oyenda usiku omwe ali akuba, siwomse oyenda masana amene ali angelo
Ndiye chitukuko mumadziwa chimenecho basi! Shame
Apolice akumalawi sazatheka,m’malo momagwira anthu okuba. Akulimbana ndi ongoyendera zawo mwina amachoka ku mowa,
Fabrications
ask them what they search 4?
Atuluka FEBRUARY AMENE-WO.
Eish! Koma zimenezi
Inu anthu mwa…..ta ndikumawamangaso
Vakabu yasala mdziko la malawi lokha mu Africa muno,,,,anzanu kuno timangoyenda mpaka utope wekha palibe zaVakabuzo,,,,,umphawi ukuphani
Kutulu ndi chaka chamawa basi
Awabereso ndi ndalama za bail ija amati ndiyaulele zovuta ndithu
Nde tikumveka2 zili bho
Tiuzeni nthawi yogonela…
mmmmm women vagabond??? Ndee zaFkapo2
Vakabu.@ .wmen? r thy prosttutes
keep it up apolisi athu, mwina December uyu tigoneko tulo