136 people arrested for walking at night in Blantyre


Malawi police

Malawi Police in the commercial city of Blantyre have arrested 136 people for the offence of rogue and vagabond.

Speaking to Malawi24, Blantyre police spokesperson Elizabeth Divala said out of the 136 people, 26 are women.

“We arrested these people around our areas under Blantyre police: Ndirande, Chilomoni, Milale, Soche, Mpemba, Chilobwe, Chirimba and Sigelege,” said Divala.

police malawi
Police in action (File Photo)

Divala further said some suspects have appeared before court while others are yet to appear in court to answer charges of rogue and vagabond which is contrary to section 184 of the penal code.

The law of Rogue and vagabond recently attracted debate as others argue that it discriminates the poor and that it is prone to abuse by law enforcers.

A study conducted by the Centre for Human Rights Education, Advice and Assistance (CHREAA) also deemed the law of rogue and vagabond as ‘No justice for the Poor’.

98 thoughts on “136 people arrested for walking at night in Blantyre

  1. Kuyenda usiku ndi chifukwa nanga osangopita mmakomo ndikupempha bwanji .nanga inu mukugwila anthu inuyo akugwireni ndani zopusa basi

  2. Mbava simungazikwanitse .
    Zoti a police amadana ndi oyenda pansi usiku izo zinatukukila kale .
    Zimayenda usiku koma pa galimoto , a police wo nkumapeleka ulemu.

  3. “136 People arrested for walking @ night” kikkk! Kusowa zochita kungofuna kukokera tindalama basi. Kumangomanga oyenda pansi pomwe oyenda pa galimoto sagwidwa vacabo

  4. Kumanga anthu chifukwa choyenda usiku? Wat a shame and a disgrace to our useless police! kulimbana ndi anthu osauka pamene zigawenga zili phee kudya ma bulger ndi ma pizza…

  5. I dislike the Munthalika’s Government becouse they take Malawians as their garden,in short that is one way of collecting monies.

  6. I’m a music producer, ndikuvuta kwamagesi masanaku tikumadalira kuti tigwire ntchito usiku koma tikukanikanso kuti tigwire ntchito usiku chifukwa choopa vacabu. mkumasauka ndithu munthu zochita uli nazo mxiewwww sitizachoka ndithu pa number 1 dziko losauka padziko lonse lapansi

  7. Unfortunately this rogue & vagabond law was made for the poor people because the same night some well to do people were driving in the same Blantyre roads..When the police is busy chasing people in resthouses,The well to do people are in Lodges & Hotels doing the same thing freely..Eeeeish.

  8. Zaziiii Moyo Wa Chitsamunda Basi Koseko Mkusayenda Yendani Muone Momwe Azanu Amachitira Ndi 24hrs service not zimene mukupangaz zompusa basi munthu asayende zompepera basi

  9. Our Neighbouring Mozambique athu amayenda pakana utsiku ine ndinadabwa ngati ndikulota even ma Shop saseka koma timati ndi Dziko la Khonda. Kwanthu kuno kwakula ndikubelana ndalama. Kutenga kwa aphawi opeza movutika WHY ???

  10. Zautsili Basi,osamalimbana Ndi Amene Akuba Mamillion Bwanj?Nchifukwa Chake Akapolo Inu Mukungovutika,kodi Mukawagwira Nde Amakugailani Ndalama Zomwe Amakalipila Pakhothizo?Zaugalu Basi,ntchito Kumangonyenga Mahule Mmastreet Kumanama Kuti Mukugwira Vacab,osamakagwira Anthu Akuba Masana Mma Bankimu Bwanji?Zauphwetelele Basi Kusowa Zochita Eti,ngati Mufuna Ndalama Mudzingopempha Zidzikugailani Mxiiiiiiiiiiie

  11. Kupikisana Ndilamulo, Eeeee Umaonadi Kiyama, Apolice Anthuwo Mukawagwila Osamawachita Nkhaza Chifukwa Ena Amakhala Osalakwa.

  12. Ma roadblok azikhala ndi nthawi yoletsa galimoto kudutsa mpaka kuche chifukwa a armed robbery amagwiritsanso ntchito galimoto koma mumangogwira oyenda pansi okha.

  13. Amageni basi osawasiya, ameyo ndi ye mbavazo, mukawagwira muziwakozakoso pakali patali monga munja muchitila kuti asiye kuyenda usiku

  14. iwenso kesten ulibe nzeru koma sudziwa kuti kuyenda usiku ndimulandu maiko ambiri too much umbuli ndumene wakukulila ufunse anthu ku RSA kupezeka ukuyenda usiku mulandu wake ndi R500 kuti utuluke ndie iwe utichani kodi sukudziwa kuti ateteza anthu a blantyre kuphatikizapo anthuonso

    1. Musanamizepo anthu apa bodza lanulo RSA yake Itiyo? Munene kuti public drinking akakugwila ndi R500, koma kuyenda usiku anthu amayenda kuno

  15. KUNO KUTHEBA ZAVAKAB ZO NDI NKHANI ZACHIKALE KUNO ANTHU AMAKAYALA MALONDA NGAKALE USIKU MMAWA NDIKUMAWELUKA. KOMA MALAWI DZIKO LOTUKUKA MASANA WOKHA KKKKKK, KUNO DZIKO LIMATUKUKA MASANA NDI USIKU OMWE.

  16. Man chauluka mwanena ngati osaganiza. Akamati chitetezo ndichimenecho. Kodi munthu oenda usiku ungamuziwe komwe akupita ndikomwe akuchokera? Bwanji asanakawagwire anthu ma pub ndi ku depot? Achita bwino ndipo asalekeze pomwepo ai.

    1. Oyenda pa galimoto usiku amaziwika kumene akupita ? Nanga bwanji samawagwira ? Onse a armed robbery othyola ma bank,filling stations amayenda pa galimoto.

  17. who said pipo mustnt walk at nyt whose business is that day or nyt its ur country guys no boundaries shame to police

  18. This is violating their rights these pipo got the right to sue against government kumalawi kulibe malamulo oletsa kuyenda usiku, sungangozindikila munthu wamangidwa with no reason,sizowona siwomse oyenda usiku omwe ali akuba, siwomse oyenda masana amene ali angelo

  19. keep it up apolisi athu, mwina December uyu tigoneko tulo

Comments are closed.

Discover more from Malawi 24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading