The Department of Climate Change and Meteorological Services has said that Malawi will receive good rainfall this year starting next month.
Spokesperson for the department Elina Kululanga, attending a general conference on climate change in Kinshasa in DRC, said most parts of the country will receive very impressive rainfall.
However, Kululanga was quick to mention that any contrary weather indications will be communicated to the public by her office.
“Should any change prevail we will let the public know since we are living in the time of unstable climate” said Kululanga.
Last year Malawi experienced its first heavy rains in January which lasted for over two weeks and led to floods in some parts of the country.
only God know
Mmene chithunzicho chikuonekeramo mwati ndi mvula yabwino imeyi aaa?
anthuwa amanama kwambiri umva makudzakhala mvula yowaza mmadera ena okwela mchigawo chakumpoto koma lili boza tidzakufunsani october ukamatha kuti mvula ili kuti
bola zimenezi nddiye nkhani osati miseche ndi mabodza
F**k dem dey aint God!!
mukakhuta mmafuna kumatinamiza simungadzwe za mawa olo
Inu tamangolandirani ndalamazo osatinamiza apa .
Yobu Kachiwanda
Bodza basi mmagwetsa mvula ndinu!
Anthu onama ngati awa sindinawaonepo tsono ikayamba kugwa next year january nde muzizati chani???
hahaha lekani chabe, makina omwe muku gwirisa ntchito ndi ati? anzanu ati kuli chilalatu
you guys sound like these up to date fake asss prophets on some God told me so so thing!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!shut up you always lying so yeah please just shut up
Ndie tinve ziti ena akuti kukhala El nino?
Asamatinamize Amenewa!
zautxiru iwo ndi Mulungu?
tizionera limodzi koma ndiye yibwera mwachangutu mvukayo
Aaaa,only God knws wen to hv rains
Actually a satellite also knows. Its simple really.
Pano mukuti mvula yabwino posachedwa inuso mzati samkani mmadera osika mvula yoophya igwa kumapeto kwasabatayi
We plan ,God plans and He is the best planner….Azanyengo inu musamatinamizepo apa chifukwa za mtsogolo amadziwa yekha olenga mvulayo.
Sorry. But you’re wrong
is this agood rain?
Moti tisathawe mmbali. mwa nyanja ndu mitsinje ikulu ikulu
Eya
Zikomo
Kkkkkkkkkkk mvula yabwino koma the president will always sound an SOS, due to the impending hunger in the country .
Bola asaname a climate–wo
akadakha olenga nvulayo bola
Nyumba zathu zikokolokeso?musatelo
zachamba basi!!!
Ngat Pal Anthu Onama Pa Dzko Lonse Lapansi Ndy Nda Azanyengo Akumalawi
Kkkkk sukunama …iwo sadziwa plan ya Mulungu antaa
Ndpo Sazazwa Mpaka Kale
The Department of Climate Change and Meteorological Services People bunch of liars.
Amen!
Thahs whah ey said last year.