![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/03/Gwengwe-e1680291723842-235x176.jpg)
Atangwa kuvundukula ma siketi uku mmalo mokonza chuma: mzimayi wayalutsa Gwengwe
Bodza lonamiza dziko kumati mafuta atsika mtengo mu December lija ati amapitilira nalo. Ati amanamizanso amayi osiyanasiyana amene tikunena pano ndi oyembekezera. Anawaimikawo ati ndi a nduna ofatsa aja a Sosten Gwengwe. Munthu wina wamayi… ...