![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2020/03/Stop-rape-235x176.jpg)
Mphunzitsi ali mchitokosi kamba kogwililira mwana
Apolisi m'boma la Rumphi akusunga mchitokosi wachiwiri kwa mphunzitsi wamkulu pa sukulu ya Mzungutwa a Wonderson Shaba a zaka 34 zakubadwa powaganizira kuti anagwililira mtsikana wa zaka 14. Mneneri wa apolisi m'boma la Rumphi, Noel… ...