
Anjatidwa kamba kogulitsa zipangizo za ulimi
A Polisi ku Mchinji anjata abambo awiri powaganizira kuti amagulitsa zipangizo za ulimi zomwe anatenga pangongole ku bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) Limited. Malingana ndi bungwe la NEEF, abambowa ndi a Richard Banda… ...