Phungu aphwanya pangano pa kalipilidwe ka antchito ake
A Yeremiah Chihana omwe ndi phungu wa m'dera la kumpoto m'boma la Mzimba adandaulidwa ndi anthu 24 omwe amawagwirila ntchito kamba koti anaphwanya pangano la ndalama zomwe amayenera kuwalipira. Anthuwa omwe pakadali pano akuswera pa… ...