![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/03/Malawi-Karonga-Drought-235x176.jpg)
Katswiri pa ulimi wati zoti dziko lino likolora chakudya chochuluka zikupereka mafunso
M'modzi mwa akatswiri pa nkhani za ulimi a Leonard Chimwanza, wati zotsatira zomwe unduna wa za ulimi watulutsa ponena kuti dziko lino likolola chakudya chochuluka ndizodzetsa mafunso kutengera ndi momwe mbewu ziliri m'minda yambiri mdziko… ...