![Hudson Chamasowa](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/01/Hudson-Chamasowa-235x176.jpg)
Boma alipempha kutukula ulakatuli
M’modzi mwa anthu opanga ndakatulo m’dziko muno a Hudson Chamasowa apempha boma kuti lilowelerepo pa ntchito yolimbikitsa ndikutukula luso la ulakatuli. Poyankhula ndi nyuzi ino, a Chamasowa anati boma pakali pano likulephera kuvomereza luso la… ...