![Malawi24.com](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2016/10/Malawi-24-235x176.png)
Matenda a mphere abuka ku Blantyre
Ofesi ya zaumoyo ku khonsolo ya m’boma la Blantyre, yatsimikiza kuti m’madera ena a m’bomali mwabuka matenda a mphere omwe posachedwapa anasautsa ku Dedza ndi Lilongwe. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe ofesi ya zaumoyoyi… ...