![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/08/Joe-Gwaladi-Gibo-Pearson-235x176.jpg)
“Tikupititse kwa sing’anga kapena ku mapemphero?” – Gibo Pearson wakwiyira Gwaladi
Zitsulo kunolana: Oyimba Giboh Pearson walangiza oyimba nzake Joe Gwaladi kuti achepetse uchidakwa, ndipo wamuuza kuti asankhe kumutengera ku mapemphero kapena kwa a sing’anga. Nkhaniyi yadza potsatira kanema yemwe anthu akugawana m’masamba anchezo yomwe ikuonetsa… ...