![Evance Meleka](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/07/Evance-Meleka-235x176.webp)
Ubale wanga ndi boma ndi wabwino – Evance Meleka wati sanamangidwe
Katswiri pa mayimbidwe a nyimbo, Evance Meleka, watsutsa mphekesera zomwe zimamveka kuti wamangidwa kamba koyimba nyimbo ya “Tasiyana bwanji” pa maliro a mkhalakale pa mayimbidwe Lucius Banda yemweso ndi mwini nyimboyi. Kumathero a sabatayi pa… ...