El Nino abweretsa njala mmaiko a kummwera kwa Africa
Maiko ambiri a chigawo cha kummwera kwa Africa akupempha thandizo kuchokera ku maiko ena kamba kokhudzidwa kwambiri ndi mphepo ya El Nino yomwe inayambitsa chilala maikowa ndipo zadzetsa kukolora zochepa. Izi zadziwika pamene tsogoleri wa… ...