![TP Mazembe beats Big Bullets](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2023/09/Bullets-TP-Mazembe-Malawi-DRC-e1696092216983-235x176.jpg)
Tembenuza galeta andilasa! Ulendo wa CAF wathera pamebepa
…Bullets yakanika kuzemba pa Mazembe Zikakhala nyerere zikuti ndi chifukwa kunalibe ma ref ogulitsa, eni ake a Bullets ati bola anafikako ku CAF. Koma lero pa 30 Sepitemba ulendo wa Bullets watha basi. Mazembe ya… ...