![Mayi ouka kwakufa](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2017/08/Jana-235x176.jpg)
Mzimayi wauka kwa akufa Ku Ntcheu
Mantha othetsa mankhalu agwira anthu a m’mudzi wa Bula mfumu yaikulu Kwataine m'boma la Ntcheu mzimayi wina yemwe anamwalira kumapeto amwezi watha ataukaso kwaukufa lamulungu koma pathupi pa miyezi isanu ndi iwiri pomwe anali napo… ...