Chakwera blames govt over market fires

Advertisement
Mzuzu Market Fire

Leader of opposition Malawi Congress Party (MCP) Lazarus Chakwera has faulted government on market fires that destroy property of traders.

The sentiments follow an inferno that destroyed property worth millions at Area 13 in Lilongwe on Thursday.

Lazarus Chakwera
Chakwera: Govt. should solve electricity problems.

Speaking after visiting the victims of the fire accident on Saturday, Chakwera urged government to solve electricity challenges arguing that blackouts cause fire.

“Usually it has to do with blackouts and when power comes back something is not quite okay,” said Chakwera.

During the visit, the MCP leader donated K5 million to the victims.

Over 43 traders are reported to have lost property in the inferno with some claiming to have lost business materials worth K5 million.

Advertisement

153 Comments

 1. Iwe chakwera wakuuza ndani kuti boma ndi limene likuotcha misika nthawi zina kukhala pheee osamayankhulapo ndi booo than kumangoyankhula mbwerera

 2. Achakwera ndichoncho awa, chili chonse choipa amangoti ndi DPP… olo ma nudes a jolenta akuti yapanga leak ndi DPP.

 3. Apa za umulungu palibe, mwachita kuposo khristu wakugwa. Although u quit preaching, u should have remain with truth. But if u know that without blaming, opposing, i will not be able to win election; u should now that politics is evil and i have joined it

 4. What the hell now A chakwera…this fire accident hasnt been investigated yet..inu mwapeza kale omu blamer…mmmh mmmh apa ndye mwayamba kuchititsa manyazitu……wats your ideas on how govt and city councils can minimise these rapant fire accidents….

 5. Malawi24 please! Chakwera donated K500,000. not K5,000,000. kkkkkkk you and your empty tin Chakwera.

 6. uwu si ufumu banja limozi lizidya ndalama enaso adyepo tiyang’ane kwina angati feleso pamupando.palibe chazelo chimene

 7. george chaponda ataba ku ministry of agriculture anowotcha offace zabwino za boma mukuziwona ndi akuba.bola chakwela

 8. nanuso musamuzuzule chakwela munthu wabwino,boma limazolowela ngati mbaliyo kunali katangale limawontcha cholinga asowe

 9. Mmm Inuso Muzivera Bwino Munthu Akamalankhula,adati Sitingalozane Zala Koma Zikungofunika Kupeza Njira Yabwino Yothana Ndi Mavutowa

 10. Problem with Malawians kuwamangira msika amawusiya nkumayala ma business awo Kunja kwa msikawo hence amamanga zisakasa zoti ndi moto sizichedwa kukolela .As for the so called Chakwera of yours,he’s only good and blaming the govt.he’s never had anything positive to say about abt the current leadership.

 11. #Ndintawi ya campaign ndiye Amalawi musadabwe Zipani zi kamatchalenjana kulimbirana maudindo, ndale ndi m’mene zilili, Sono antu wambafe tisamadane pocomenta Tsiku muzaona APM ndi Chakwera akumwera Table limodzi Coffee, or Tea pomwe antufe tikumadana

 12. Amalawi Ambiri Ndi Mbulindi Nthawi Yomweyi Kuyiwala Mavuto Anene Takumananawo Ku DPP, Ndikumayoza Chakwela, Which Means The Meaning Of Leader Opposistion Maybe Most Of U ……. Sure Ndinu Mbulindi

 13. Ok ok ndaonetsetsapo yapa.awo ndi ma plan a chakwera potuma anyamata ake KT ayatse mtsika kusowa chokamba after ataona zomwe DPP yachita past ago and zomwe zasala kuti ichite potsiridzitsa manufesto awo.komabe 2019 nonsenu muluza ndipo kanganani owina alipheeee Mzimayi wa LCP Sally Kumwenda awo ndiwo maloto akudza Ku dziko losaukalo LA Malawi likumudikira mayiyu.munaona bwanji 2012-2014 under JB?

 14. A DPP SANGAVETSE ICHI ANAYATSA MEC, OFFICE YACHAPONDA, GALIMOTO YA NJAUNJU, MEC OFFICE IN MZUZU . NATURE OF DPP IS OF KUYATSA MOTO

 15. Chakwera we all know that markets belongs to city councils , town councils and distric councils now don’t lie to us by blaming government u can’t live without blaming government

  1. this guy z now blaming everything to the government that’s not the way to solve a problem you must come up with solution not every time u just complain that’s no wise

 16. Mmm #Chakwera ndimakutsata heavy kuyambra mmene unalowa pa mpando otsutsa kma cimoz cimene napeza mwa utsogolen wako ndikutsutsa kalkoxe ngkhale zkhale za bwino iwe #Suyamika akat kutsutsa skut kalikonse kma kuunikira boma pomwe likulakwitsa ask Mr Tembo, He was opposed wth #KNOWLEDGE_N ADVICE_GOVNT whre it requires. To Err Is A Huma, APM. Ur critisism might be acknowledged if u could stand somtime n appreciate bt mmmm mavuto alipo mwa chakwera akulu ofunika malilime ophuzitsidwa rararararabakashakalananana kkkkk Oppose With #sound. APM if cap fit wear it in time.

 17. Kungoti fungo lafisi ndifisi ndithu nkhani za kuyatsa moto zimachokera Ku DPP adayasa maoffice a mec pamene amkati akawerengeso zosatira zazisankho chaka cha 2014
  Adayasa so moto office ya zaulimi atava zoti afuna akakafufuze zakagulidwe kachimanga .
  Tsono mwina apapa sizikugwirizana koma kuti sa DPP koma chifukwa chakhalidwe lawolo ndilomwe likupangitsa kuti anthu awaganizire

 18. Joseph Damiano. achakwera alibe mfundo kwake ndikunyoza basi walemba madzi achure awerenga ameneyi sazalamula dziko lino

 19. A chakwera kodi mudzakambapo fundo ya zeru ngati mtsogoleri mmalo mwakuti mupite mukawapepese amalawi omwe akhudzidwa ndi ngozi yo,

 20. Achakwera Mwapenga kodi?chifukwa chani chilichonse mumagoti ndi boma,musamatibowe ngati mwatopa ndindale bwelelani ku ubusa

 21. I agree with Chakwera.
  And mmalo mokadzika ma tombstone achitukuko kaya kuti bwenzi akusamalira welfare ya amalawi.

 22. Ndale Za u mbuli a chakwera mukananena zoti mudzatipangireukadzalowa mboma misika ikapsa voting you its useless

 23. Uku Ndiye Kusoweka Fundo Kwa Mtsogoleli Wachipani.Ngozi Ngati Imeneyi Zikugwilizana Bwanji ndi Boma.Malo Moti Muzilimbana Ndi Pungwepungwe Uli Mu Chipani Chanu Mukulimbikila Zaziiiiii Nkumati Ndidzakhala Mtsogoleli Wa Dziko Aaaaaaah Ndatokayikadye

 24. Ochakwera I put the blame on you how could you to say that such nonsensitical ideology filled with rubbishes? Find another way of Lies not this one pliz pliz

  1. Wanena wanena basi chilungamo chimapweteka komaso sana blame koma inali apeal ku boma, thats the duty of a leader, AMEN

  2. Chakwera wapempha boma kuti lipeze njira zodalilika zothetsela ngozi zamoto komaso kufufuza mozama mavuto amenewa,AMEN

  3. Chakwerayo Akadanena mmene mwaneneramo a Bernard, bwenzi zilibwino ndiye ndikukupemphani kut muzikamuthandizira kulemba speech yolongosoka chifukwa speech yake salephera kuikamo blame blame blame mpaka mpaka asaaa

  4. Aunt Joyce Banda kwa ine grammar ili makora. Ngat sili bwino ayi ndithu ndikupepetsa koma ndingopempha mutolemo uthenga okhawo. Ngat suli bwinonso uthengawo ayi ndithu usiyeni chomwecho

  5. Chakwera ndale sizanu inu koma kuba zampingo basi chilichose BOMA talakhulani zoti zingatingwile mtima osati kumangosusa anthu aluza zinthu zambili mupangepo kanthu

 25. Zimene ayankhula a Chakwera ine sindingawakhulupilire chifukwa palibe phindu imene boma ingapeze powononga zitukuko kapena kuotcha misika yomwe adaimanga.Ndipo kudzudzura kumeneku kwakhumudwitsa anthu ambiri ndipo anthu ayamba kale kuwapezera zifukwa zosachita bwino masankho a 2019.Dziwani kuti a UDF imavutika kwambiri kuti ipeze mipando ku Nsanje ndi Chikwawa koma zotsatira zake UDF imapambana ngakhare panali akamuna mndare a John Tembo,abale ndi alongo kumbukirani kuti fisi ndi fisi ngakhale atavekedwa suit ndi fisi basi amakadya zonunkha.

 26. Zimene ayankhula a Chakwera ine sindingawakhulupilire chifukwa palibe phindu imene boma ingapeze powononga zitukuko kapena kuotcha misika yomwe adaimanga.Ndipo kudzudzura kumeneku kwakhumudwitsa anthu ambiri ndipo anthu ayamba kale kuwapezera zifukwa zosachita bwino masankho a 2019.Dziwani kuti a UDF imavutika kwambiri kuti ipeze mipando ku Nsanje ndi Chikwawa koma zotsatira zake UDF imapambana ngakhare panali akamuna mndare a John Tembo,abale ndi alongo kumbukirani kuti fisi ndi fisi ngakhale atavekedwa suit ndi fisi basi amakadya zonunkha.

  1. KOMASO DPP IKAWOTCHE MSIKA PHINDU LOWOTCHELA MISIKA BOMA NDI CHIYANI?? POPEZA KATUNDU WAWONONGEKA KU MSIKAYO BOMA LIMATOLELA MISONKHO KU MISIKA YOMWEYO? KOMA CHAKWELA MUNTHU OMVETSA CHISONI NDITHU.

 27. admin your a big lier we were there wen chakwera made the speech there were no any blame word,dont turnish image ya munthu

 28. admin your a big lier we were there wen chakwera made the speech there were no any blame word,dont turnish image ya munthu

 29. achakwera ngati ndale zakuvutani bwererani ku ubusa before it is very late for you to return….. timaona ngati ndinu Munthu ophunzira koma ai….mavuto tu achakwerawa kenakonso tikumvani kuti mvula ikugwetsa nyumba zi komanso kusefukira kwa madziku likupangitsa ndi boma. phunzirani kusiyanitsa ndale ndi ngozi,,,,,,mukutichitisa manyazi bambo chakwera. Yehova anakwiya nanu munathawa kugwira ntchito yake ndi kusankha kugwira ntchito Za mdima zadziko lapansi kumbukirani yona anamezedwa ndichinsomba chachikulu inunso mwamezedwa chinsomba chachikulu chandale ndichifukwa chake mumayankhula zinthu zochepa mzeru………

  1. Ase first who r u?second wat do u bliv in god’s word ?third is dat do u hav de working brain in ur head?no sense &u r very stupid and lunacy ,vague ,pesmisit as wel as aukward u r a foolish fox oky?ur prezident yo floosh again umuwuze wava eti manyi anu mose, hav u ever heard dat prezdent amalamulira anthu asatana, koma ndiwe chisilu wava eti ?

  2. Tikuvutika apapa winawe udziyankhula dzakumalisece ?umawola tupsvi tamuthalika ndiwe eti?manyi ako wanva ?shupitiiii zako mmene malawiyu wavutikila mumzaka 4lozi iweyo ungamayankhule zimenezi?mapwala yanu akulu mundipeze kuno ku limbi mwava eti?mkongo wanu ndiamene mukumupatsa suport yo! zisilu mose ndi amene adakulembani ntchito yot muzimucosa seteyo

  3. Iwil talk with simbazako frm ntchisi to delete ur life coz u r a useless fox in dis world together with ur floosh plezedentele oky? way u blame de man god?ufe ndithu wanyoza mulungu wava eti?

  4. Chakwera ndizobaaa. Enanuuu mukufuna kt president akumangilenii nyumbaa kt muyambee kumuyamikikaaa. Kachakwerakooo kanaona ndaniii akukayatsaa nsikaaa kapena kusasamala kwa enii nsikawooo. #Fenneck let those fool be fools

  5. True chakwera sadziwa ndale koma ma Negative report there4 anthu akadziwa za khalidwe lonunkhali udzazindikira pali tsooo

  6. Ngati CHAKWERA sadziwa ndale inuyo pamodzi ndi Mbwampini muyenera kusangalala chifukwa muthu osadziwa sangakulandeni boma koma inewo mawu anuwa nuwona kuti munama chifukwa sidakamutukwa mmene muchitiramu nuganiza kuti mulira ndiye umangokhalira kuti abwerere ku mpingo.i

 30. Which is Which? NYASA TIMES says he donated MK500,000.00, MALAWI 24 says MK5,000,000.00. Check this out!!!!! Koma atolankhaniwa analidi malo amodzi pamene donation imachitika? Malawi wa lero

 31. Warning: Malawians will never elect leader just because he/she is good at blaming others on each and every matters affecting Malawians!!! Dairy blaming? osanena zamwe mungazachite mukasankhidwa bwa? President akalankhula mukut,mukuti empty speech, msika ukapsa mukut aotcha aboma, kenako tikumvani mukut President atule mpasi, pot Zuma ndi Mugabe atula pansi, kkkkkkkkkkkkkkk munena ndithu, kkkkkkkkkkkkkk kumalawiko mwafasako, kkkkkkkkkkkkkk

  1. Wanena wanena basi kaya mupse mtima bola tikudziwa kuti chakwera wanena zowona, zuma mugabe umo ndizomwe mulungu wakoza,

  2. Zoona!!!! Azingokhalabe no2 each and every elections just because of his indecisiveness, Ndiye nawo masapota ake amakhala ngat abanja limodzi, kkkkkikkkk zachisoni kwabasi, komu muli ma advisor mchipani chimenechi? kkkkkkkkkkkjjjj

  3. Ndiye iwe udandawule kuti chakwera azingokhala no2 ngati kuti chakwerayo ndi bambo ako, ukupangayo ndi miseche,

  4. So which party is running the gvt? if one is blaming the party which is running the government, it is the same as blaming the government, mesa mukumat DPP BOMA!! MCP BOMA!!! UDF BOMA!! etc ndiye mukufuna kunena kut chan apa a Ambwene Shultz Mwakanandi??? if you have no teeth don’t bite

  5. Zamagetsi A leader of opposition mwaziziwa liti?Kunena zoona tidakalirabe ndi ma President opanda mzeruwa.Why blaming blaming. Next you will blame God for creating pple mudakakonda if God could create a MCP wokha .

  1. Ndiye ngati sindiwe politician wasokera walowelera za eni ma politician, ngati nkhani sukuidziwa kulibwino kungokhala,

  2. Nanunso kukhala opposition leader ndiye azingopanga blame boma zilizonse. Mr benard zinazi kumaziona , tangonganizani boma lingatume anthu kuti akawotche nsika? Iiiiiiiii amangwetu ngawa usongole wele wawo

 32. A chakwera mwatuma anyamata kuti aotche msika wawo omwe cholinga muzinyoza boma ine ndekha sindingavotele mcp olo mutati mundipha ndikapanda kuvota ndale zanu ndi zopusa kwambili

 33. Ngati achakwera anena zimenezo ndie kuti awonetseratu kuti ali ndi vuto la muubongo ndikovuta kuti mungalowe m’boma becoz his a useless leader

  1. Mmmmmmmmm ku cape town chan……..jst kip on queuing for drinking water……….And the day 0 is coming muyamba kumwa mikozo yanu yomwe kenakano……

  2. Despite all those prophets you have in South Africa palibe akufikira kwa Mulungu ndi nkhani ya chilalayi Ku Cape Towniko.

  3. Felix ,You can say like that because you don’t know. u people u just here to someone. tango bwerani muzadzi onere nokha man.

 34. Chakwera amakhala ngati amagwa khunyu,mmutu mwake munadzadza manyi. Zoti imeneyo ndi ngozi sakudziwa kukula konseko? Nde mkumati angakhale a president amenewa? Headless chicken. Ndicifukwa akulephera kuyendetsa chipani gwape ameneyu.

  1. IWE UMATI MUNTHU AKUNENA ZOTI NDIVOTELA DPP AKAKHALE ALI KU AMERICA?? DPP NDIYE YOVOTELAYO UMATI TIKAVOTELE CHIPANI CHA NG’ONA?

  2. Musatiuze chochita inu votelani MCP yanuyo ine ayi vote ndi muntima osati pa Facebook ndipo muzalila yanu ija DPP BOMA

 35. Wasala pang’ono kunena kuti boma labweretsa chilala ndi mbudzi yeniyeni.Amaganiza ngati nkhuku yakuda basi.

  1. Eee umati? Chifukwa cha kusamva za ena, boma labweretsa chilala, mbodzi ndi zina zotero (Deuteronomy 28:15 etc). Mmalo moyitanitsa mapemphero muli busy kutukwana Chakwera. Izi ndi zina zimene Mulungu sakondwera nazo. And for your information Chakwera wapepesa ndi ndalama kumene. Nde inu amene si inu achitsiru, mwapepesa ndi zingati?

 36. Chakwera akhalira kuyankhula zopanda mutu chonchi,winanso akuti dpp ikamapanga campain imaotcha misika!.Vuto latsogoleri komanso masapota a mcp ndi umbuli.Inu muzakhalira kunena zoipisa azanu mpaka kale osazalamula zikoli,amzanuwo akulamula,komanso ndipamene mukanazifusa kuti pano timatha zoyankhula koma palibe chikuchitika.Taziyamikani kuti muli ndiutsogoleri wabwino.Mukumasiya mbaula utsiku onse mmalo mosasesa cholinga misika yanuyo ikayaka muziti boma laotcha msika??,kodi muzazindikira liti anthunu??.Mukufuna boma lizibwera kumazimitsa mbaula zanuzo utsiku??.Mcp masapota mukumachita mwadala kufuna kunamizira boma. Komano mukukhulupilira kuti a dpp angamataye nthawi ndikumayasa misika m’malo monyadila kuti akulamulira ngakhale ndi mcp yomwe??.Samalani misika yanu,mukayiyasa chifukwa chosasamala musamanene kuti ndi a Boma ayasa.

  1. Ineso amandinyasa bwanji ankandisangalatsa 2014 koma ndinaona kuti ndi munthu opanda nzeru bakha weni weni

  1. Amayankhula zimene anawuzidwa kwa amene katundu wawo waonongeka koma pakuti chomwe wanena chakwera sichisangalatsa boma,

  2. Nanga boma nlimene limayatsa motowo? Mesa moto wina umakhala wouputa dala?
   Chakwerayo bwezi atabwera ndi mfundo zothandiza kupewa ngozi not blaming others.

  3. Am agree with you BIG BOSS MCP ilibe mfundo zoti ingatiuze chilichose kulila basi 2019so alilaso yao ija

 37. Uyu ndi bakha eti? Can one connect the Area 13 market inferno to black out? Do u really know this market? Uku ndiku ma restaurant obvious source of fire ndi mbaula or abandoned moto osati za nyau zomwe ukukamba apazi.

  1. Bakha ndi agogo ako azaka 81 opanda manu aja, chakwera wakamba za mablack out kulumikizana ndi zomwe amanena ma vendor,

  2. Upite ku Area13 then ubwere uzakomente nonsense, nonse ndinu mbuzi zokhazokha u don’t what u are talking about.

Comments are closed.