Soldier sings about maizegate, tractorgate in new release


Lucius Banda

 

Malawi’s Sir Soldier Lucius Banda has in his new song sang about two scandals namely maizegate and tractorgate.

In the new song titled “King Solomoni”, soldier has expressed worry over hardships that Malawians are facing at a time when ruling elites are stealing public resources citing the two scandals.

Lucius Banda
Soldier

According to Banda, it is bad for the politicians to be playing with Malawians when the ordinary citizens are lacking basic needs such as medicine and water.

He further alleges that some of the leaders are not Malawian citizens that is why they don’t care about problems that the citizens are going through.

According to soldier, the ruling elites know they are not Malawians and will go to where they came from when things get worse.

Banda, a well-known music icon in Malawi, was born on 17 August 1970 in in Balaka District of Southern Malawi.

His music legacy dates way back in 1983 when he was thirteen years old when he started singing with his brother Paul Banda and leader of Alleluya Band. He first appeared on stage in 1985 with his brother’s led Alleluya Band.

Banda started his music career while in elementary school (Primary) at Mponda Full Primary School which lies near the catholic parish in Balaka. To further his music career Lucius Banda decided to go to music school in South Africa. This dream was fulfilled in 1993 when he joined Dorkey house in Johannesburg, where he spent one full year studying music.

His first album titled ‘Son of a Poor Man’ became popular because of hits like Mabala, Get up stand up, Linda and Life on Earth. From there he launched his long career of music.

 

241 thoughts on “Soldier sings about maizegate, tractorgate in new release

 1. Angofuna kuti atamidwe awa. Umbuli unawapweteka kwambiri, ndichifukwa chake amangokhalira kugula macertificate a fake.

 2. Komano tiuzanepo chilungamo soldier sangafanane ndi wina aliyense kumtundu kwanu onyozanu kwa anthu amene akumudziwa soldier ngati ine atha kuchitira umboni kuti ndi kholo komanso mphungu waanthu wamba akadakhala bingu alipo akadachitira umboni mwangozolowera kumvera nyimbo zotukwana komaso ndinu anthu osayamika Munangozolowera kudandaula mutangokhala panyumba ngati mulibe pakamwa Soldier is fighting for you son of poor zinthu zoti inuyo banja lanu simungalipangire iye akupanga funso nkumati kodi ndiangati akukondwa??

 3. I don’t trust Banda since he was found guilty with the case of having a stolen msce certificate. After he lost the case, he do hate DPP update. Therefore, don’t fool yourself.

 4. Abwana munatha Ndale zinakusasulani. Ndipo sinunso Lucius amene ife timamudziwa kale lathu. Anayimba kale nzanu amene wathanso naye ngati makatani uyu timati NKASA yu ndi nyimbo yake yoti NDALE ndikanyama kowopsa

 5. Amalawi Mumalimbana Ndi Zithu Zopanda Tchito M’malo Momalimbana Ndi Chitukuko Tizakhala Otsalila Mpaka Kalekale Amalawi Kodi Iyeyu Atamupatsa Mwai Olalamulila Angakwanitse

 6. Nawonso akula zikuwavuta pa nkhani yamaimbidwe momwe adayambira kaletu, mzimu wa gadama , Sell 51 , lero akuti maize gate azathera pa locally pompo

 7. Did he Lucius told you that he want international songs he sing for the poor
  If your family is the one who get tractors shame on you one day you will pay

 8. Thank you mr banda for that always i ppliciate you as you a solder i salute u.. Anthu kanyimbo kameneka mwina kazizambidwa munthawi yakampeni chifukwatu paja amalawi sachedwa kuiwala big up mr banda yasala nyimbo ya kuzima kwamagetsi

 9. well done Lucius for remind us others they forget already about maizegate that’s problem we have we forget so quick and if someone by next year make comedy about K5000 I think we will complain again our Malawi is getting rotten let’s ponder that and do something

 10. lusiyasi vomelezan kut nthawi yanu idatha koma choti mudziwe mungaimbe chotan malwi cannot not acknowlege u as a freedom fighter taaaaaaaaaaaaaaaaa u a far wat u know z critisizing u never come wit solutions mmm shame on u ,,,,, anthu omenyera ufulu adakwana nde uzingoimba pot studio ili muklhodekomaso ana amakuperesa pa nyimbo heavy tiyeni tisiyre ena

 11. Some of you commenting here clearly show that your nothing but idiots. Just full of hate. Lucius stands for the poor. Where government can not act like in the case of maize-gate and tractor-gate, Lucius comes in to remind us what type of government we have. So if you think Lucius is not important to you, he is very important to some of us. He speaks on our behalf. So you better know that we stand with those who really represent us. Keep it up Lucius!

  1. Zako izo. Mwalemera chani inu? Just shut your stinky mouth. More fire Lucius! Cadet zamupweteka uyu!! Watsegula mmimba. Simunati mutseguladi.

 12. Apapa nde mwabwerera chikale man musadande nd okunyozan chomw ndimaziwa nd choti ku malawi kuli anthu ophunzira odzaza nd uchitsiru komans anthu osaphunzira koma okhal nd nzeru monga malemba anenera kuti Nzeru ya dziko lapans Mulungu anaipusisa nde Mr Soldier imban zomw mwaziona

 13. Cease fire, take over, yahwe,, not easy…….,freedom ndikamanvera nyimbo zochokera kuma albums awa mumtima ndimamva tseke tseke. Kma zalerozi mmmmmmmmm nzovuzedi wawa, poti zangolowa chipwilikiti basi.

 14. Kod amene mukumunyoza soldernu kut amangoimba zandale kod simudziwakuti lucias ndi freedomfaghtor?Ngat simudziwa mufunsekaye musanapange ma coment anuwo.

 15. Solder ndiwewekha mwana opanda mamtha wachidwi padziko lake.ukaimba amachitakomanyazi mkuyamba kukomza zolakwikazo.Moti usaleke mpaka matractor onse atuluke.Abingu siopusa pokawagula ayi adaonakut alimi atopandikulimira makasu.Sikut zinali zachipan koma zadziko.Ena ochenjera mopusa anazitengangati zafamilly.

 16. Whatever guys,u Malawians mulibe pabwino,soldier akayimba nyimbo yoti mudziwe choona mukuyankhula mbwelera,Bushiri athandizeko mwati satanic,uyo wakubayo akaba mumangolira,lero magetsi ndi awa Malawi yangokhala ngati Ku manda tsopano,wake up guys,iyeyu simunthu wamba ngakhale mukuti sanaphunzire koma Ali ndi zonse zosowa pa moyo wake Chifukwa cha Khama lake,enanu mpaka Ku chanco lero panopa chamba ndi mowa basi, ndi uyu osaphunzirayu bwaaah shame on u Malawians.

 17. Soldier, uyimbenso nyimboyo uwonjezere kuti nduna ina inakabisa tractor yakubayo ku Ntcheu cha ku Kasinje uko. Ukafuna dzina la ndunayo ndikuuza. Panopa tractor’yo ili komweko.

 18. Ndiwe wachikulire Banda, asiye azibwebweta choncho, mukukamba za Chanel 0 I’ve Ku Malawi tili ndi Chanel 0? Umbuli basi, amend alinayo anditumizireko kuwhatsapp pa number iyi: +27791649206

 19. l dnt like this coward man! komaso too much kufuna kukhala ozindikila koma ali mbuli yachabechabe if you have nkhani timapita kucourt! Nyimbo zimafuna kusangalasa anthu osati milandu mbweee!!!! zimenezo zakale kake lomwe lija dziko lili ndi mazoba like you!!! kumachita kukuposa Gwaladi yemwe kuganiza!! iweyo ndi nkhasa mbuzi zokhazokha!!

 20. Lucius mwana wa nabanda okana bambo ake ngati amapangidwa ndi mayi ekha,omangisa mchemwali wake,olephela kuthandiza Mchimwene wake Join?,Group la atcheya?,angathandize ndani pa malawi awa,ineyo ndikadawonela oyimba amene atukuka ali ku zembani ie mlaka,nsaku, billy,b4 asanayime pa okha,odzuzula nzake ayambe wadziweluza kaye b4 acusing ena mMalawi

 21. How ever you criticize Lucius Chiccio Banda shows you are nothing . Did he mention your name in his songs? He was there in music industry before you born and still there. Do you know the means of what you are saying? Why don’t you go in parliament if you have an original certificate. Wakeup My country. Don’t forget “SAYENDA ADABALA MWANA OYENDA” He can fight freedom for you educated people . Mark my words Nsanje kaduka lekani . Iye ali ndi mwai otilankhulira ife anzeru fe. Kupanda apo aaaa kaya. Tizingolira kuutsibe Chomcho. Big up Soldier Lucius Chiccio Banda. Patsogoro ndi ndi Chilungamo. Osafooka munayambira kutali kulimbana ndi Kamuzu . Be civilized Malawians truth pains. Be Blessed Lucius Banda

 22. His songs are not competetive internationally. His songs are for malawian politicians and some of their followers. His music can not be played on puopular tv stations like channel o. He forged a Malawi certificate inorder to become a Member of Parliament we have not forgotten.

  1. You guys why are you not mentioning the current diploma that he is holding? Where did he get the diploma? Which coarse did he study inorder for him to be awarded the diploma?

  2. Sitikulimbana naye man uyu kuzuzula kwawo nkosathandiza ayambe wadziweluza yekha mu music industry anatukula ndani ie nsaku,mlaka,billy,

  3. The guy is talented and you you know it leave him alone he made a mistake and admitted him so why crucify him?are you perfect yourself?

  4. Let us continue to correct mistakes here.I have seen that most you malawians you waste your time correcting spellings as if you are English Teachers from England.English is your second language. I have been reading stories from malaw24,nyasatimes,malawi voice with wrong spellings but you people because of ignorance you always waste your time correcting new reporters instead of commenting or keeping chete. Anthu opusa mulipo ambiridi ndaona tsopano.

  5. iwe kuoneka pa chanel O si udolo ayi koma udolo ndikuziwika kudziko lako….Dolo ukumunenayo ndi tate wamayimbidwe ndani amaoneka pa ma tv oziwikawo wamuno mumalawi anakhalapo tate wamayimbidwe??unyoze ena olo kuwakumba uyo yekhayo sungamake olo mutabwela nonse ndinyimbo zanu zopanda tanthauzo.ikuchedwa ndyimveleee.

  6. Ife tigula CD yake unya ndi millionaire pano Luscious ndipo amatha kuyimba Nzomwe anatchukila sanayambe lero,,remember mabala nthawi ya MCP nde lero ayipe coz wanena zoyipa za DPP? Panya pako!

  7. Edward Songini i think you are dumb and dull ,un educated fool. Your mouth is dirt, you dont wash it i can see from a far. What benefit do you get from some one who stole a certificate.?

  8. Iwe Delgado usalowelere nkhani za ku malawi. Iwe ndi mkilimani wa mozambique udazolowera kukhala mtchire ndi malume wako Alfonso wokonda nkhondo.

  9. mukhalila zomwezo anzanu akutukuka muzochita like it or not he is well recognised musician and timamukonda

  10. kuzolowera kunyamula mitu ya anthu mmisonkhano azanu akupanga ndarama zao uchutsiru ife tigula ndipo ikuchedwa kufika kuni

  11. Mai Dolika ndinu aboza lankukuniza ngati Banda wanuyu komanso achinyengo.You want to tell us that those who dont like Banda’s music are poor? I can see from a far that yourself you are one of the poor people who listen to this guy’s music.Let me tell something listening to Banda’s musica can not eradicate your poverty .I feel sorry for you poor girl.

  12. Anthu ena ndinu zitsuludi eti? kuteroku simudziwa kuti nkhani ya certificate inabwera chifukwa cha impeachment bingu atasowa chochita ndale zitamuondetsa…komanso inuyo ophunziranu tikuvutikira limodzi kusowaa tchito pamene soldier ndibwana, koma akukuyankhulira iwe oponderezedwa ulibe kalikonse kunyozaa anthu oti akhoza kukuthandiza…

 23. even ma show ake akayamba kuyimba iyeyu fans imangokhala inanso kuyamba kutuluka pano anatha ndithu

  1. Ndiye anthuwo amakhala kuti alowako ulere kapena ndi ndalama ndiye cholipilira nchiani chimadziwa kuti oimba wake ndi soldier.mwanenaxi doensnt make sense sir

  1. Wamva zomwe Peter Mutharika wanena pa za ma educational certificates a Lazarous Chakwera? APM says Chakwera’s credentials are fake.This is a political way of making Chakwera suffer public ridicule for playing his oversight role in checking excesses and ineffieciences.Do u remember the issue that touched on Bingu’s raw nerve? it was impeachment procedures for a president.Both his conviction and sentence were quashed by the appeal court.

  2. Certifocate issue is almost personal boss but kuba chimanga plus kudzasowetsa ma tractors and ndikudzamiza a Malawi on genisets its a national and has brought national debate….anthuwa aba mokwana, thanks to Soldier,tamvako za tractorgate”hehehe

  1. Mmmmm! Yambani inuyo kuyimba brother si nanga LB anatha komanso pa chichewa pali mau oti pachoka mzako pali malo ndiye inuyo mulowe malo LB wo basi zatha ife okonda kumvela nyimbo tizimvela zoyimba inuyo finish

 24. Akuruwa Amankhara Ngati mutu wako Sumagwira ntchito Bwanj Osamankhara ngati Akuru awo aja Zipindurira chani Marawi zimenezi??

 25. i dont like this he would like to go down as a freedom fighter but he is just a typical malawian politician who makes music.PRETENDER A PRETEND

 26. Nice songs but why does he not seen criticize the relevant people in parliament like how kamlepo and others does

  1. nde kuyimbako,iwe umaona kuyimba zanzeru umayimba zinthu zoti sizinachitike?chifukwa chake oyimba ambiri nyimbo zawo mulibe ukadqulo.ada amenewo ndi tate wamayimbidwe alibe zake pamalawi.

  2. I think you don’t know that nyimbo ndi expression of feelings….amadikila zobhowa,zachisoni, zopysetsa mtima zichitike ndpamene angayimbe …that’s why akuimbabe till now!

  3. Lucius banda adayamba kuimba iweyo uli mwana kamuzu bakili bingu Joyce banda ichitso chilipochi osewa adayimbidwa nyimbo ndiye mukamakamba nkhani za Lucius banda osamafananixa ndi mbuxi xomwe xilipoxi

  4. Nyimbo ukamayimba muthu umadikila uwone chomwe chichitik basi kungofikila kuyimba makawa kapen nkasa kapen gwaladi Lucius banda ndi Lucius banda paka iweyo zizakunyasa

  1. With good leaders and self-motivated ones, malawi will excel brother!!!!! Hon Banda is just putting a cry on these disgusting gates which is the same as murdering your own brother..,…,maizegate and tractorgate is witch craft ideeed.

Comments are closed.