Chiukepo Msowoya’s debut to forget

Advertisement
Chiukepo Msowoya

Former Nyasa Big Bullets forward Chiukepo Msowoya had a debut to forget for his new side Golden Arrows after scoring an own goal in a 2-5 defeat to Absa Premiership leaders SuperSport United on Wednesday night at Lucas Moripe Stadium.

Unlike Gabadinho Mhango who scored twice for Bidvest Wits on Tuesday after coming off the bench, Msowoya scored in his own net on 61st minute before being replaced on 69th minute.

Chiukepo Msowoya
Chiukepo Msowoya scored an own goal in a debut.

Msowoya, who only joined Arrows on a six-month deal during the January transfer window as a free agent following the expirerly of his contract with Bullets, has joined the list of players who have had debuts to forget.

Meanwhile, Gerald Phiri Jnr made his debut for Platinum Stars in a goalless draw against Orlando Pirates, with Robert Ng’ambi cementing his place in the midfield. Looking shaky, Phiri Jnr wasn’t at its level best as he looked short of confidence before being replaced in the 90th minute.

It seems it was only Mhango who had a week to remember amongst Malawian players playing in South Africa but the rest of the guys had a week to forget.

Former Silver Strikers and SuperSport forward Atusaye Nyondo saw his side going down 1-nil to defending league champions Mamelodi Sundowns at Dr Molemela Stadium.

Msowoya saw his shot cleared off the line just a minute before the interval and went on to miss numerous chances before being replaced just 11 minutes after the recess.

Advertisement

139 Comments

 1. wathu wathu wa bullets ameneyo amafuna kuwoonetsa kuti kutchinya zigoli sinkhani ndi chifukwa anakhala wogoletsa zigoli zambiri mu tnm 2015

 2. Ma supporter apa a fb sindimakhala nao busy coz amangoyakhura basi, amene mumautsa tiyeni tikakumane Ku Lukas moripe stadium weekend imeneyi Ku Pretoria

 3. When one popular defender who replaced Lucas Radebe also did the same mistake on his debut but he later became one of the best defenders in PSL in RSA

 4. foolsake mariavegor supermilk mix ma yu zam…………..mpira baba mu hiter thawi yambiri mtima pasi mumatha kuposa akunseka ngat akhuta chinangwa cha tomato,

 5. A A kodi pano ndi defender?????kapeni gori??????kugolo kwake amakataniko???????anachitibulira pa center nkulunjikisa kwake komwe???????hard lucky ulendo winawo ziyenda

 6. That’s football no wonder. But he played well besides that OG. I WATCHED full game. Forget the past. Chiukepo. What happened has happen. Pull up your togoh. You are star

 7. Kkkkkk…….Eeeeehe,ndemapuleya Aku chingambwe FC Amenewo Anangothaku bandachakumaliwa Nde Mglaundimo Samawonansokusiyanamagolo Amangotibolandafikapa golobasi Mr Pnt Nkungozigoletsa.Amangoyendelamawuot pafupimpomwewafika bas.

 8. I think Chiukepo knows what he did,,more over it was his first game so i think he was under pressure.But I know Chiukepo he will be ib good position to fight for goals.

 9. Wayamba bwino. That goal counts in absa premiership. So far it means has one goal to his credit and that goal will help him to become a Top goal scorer kkkkkk.

 10. Nde chachilendo ndi chani mpaka ikhale nkhani yoti mutitsekule nayo mmimba,azizichinya yekha Ronardo. Nde Chiukepo ndi ndani,osalemba zina zanzeru bwanji

 11. my name is Chris Mhango doctor abumen help me to cure my HIV/AIDS virus with an herbal medicine, am sharing this to the world to save some lives, believe me there is a cure, you can contact dr abumen on his email address [email protected] and you can also call or whatsapp his number which is {+2347085071418} please share to save lives.

 12. Mmm zikudabwitsadi kumunyoza choncho munthu? Ngati mudayambana naye muzakambilane naye koma apa tikukamba zampira osati mpaka chitsiru chimenechi no no no it’s too much

 13. ndi zoonadi kuti “mlomo umakutsatadi” ndipo “msamathe mau” malata ali ku silver amkazichinya yekha ndipo ambili mumkamunena pano chiukepo wazichinya yekha mkumati “zimachitika” mmmmmh! mukamayankhula muzilinga/muziganizira mawa lanu! abwela kuno posachedwapa,zavuta basi! adolo a penalty,kuchokekeraso ku penalty fc.

 14. Palibe chachilendo apa,kulikonse zimachitika ndiye isakhale nkhani chifukwa choti anachita mistake imeneyi. Ubwino wakenso ngakhale umutseke, koma contract yakeyo ikupitilira samuchotsa mpaka uzamva kutinso waseweranso. Kulandiranso, mwezi ndi mwezi iwe uli choncho ndikutseka kwakoko zachabetu zili pano.

 15. Sinaonepo chi player chokakamiza mpira ngati chitsiru chimenechi amati chiukepo!! Chimunthu chachikulu chokhwima ngati chimenechi, chifukwa chake chikuzichinya chokha. Kkkkkkkk. Mwazolowera Ku Malawi amangokubelekani ma ref agalu a bullets inu eti. Suchinyako chigoli kumeneko galu iwe!!!! Kape ngati iwe wofunika socials basi

  1. machende abambo ako wava nyani iwe pa mtuzu pako ndipo yemwe anabeleka iweyo bola akanakozela pambali apo bi anakabeleka nkhuku anthu anakasusa ndukanyera umphawi uli thoooo namapwala iwe

  2. jack banda,kweni kweni chavuta ndi chani?anakulanda nkazi kapena?timu imene wachinyisayo sukuiziwa ndipo sizikukukhuza its not flames ndipo asova kma iwe mpaka wawawawa!! bwanji man??

 16. Kkkkkk hahahhahahaha komanso zinazi inu kkkkkk mwati chani ?? aaaaa Zampira amazichinyira CR7 nde Chiukepo ndindani kkkkk Keep Forcus bola zimasachitikechitike inu tchito yanu ndikuchinya adaniwo osati kumawanthandiziraso kuzichinyira ayiiiii…

 17. Kkkkk kod man amenewa akumenya kumbuyo? Kapena pot anayandikila golo anangoganiza zocinya basi, mmanena malatatu paja ndiye uyu muzit its pat of fotball no osamayankhulitsa guyz kkkkk apa bench waiyamba basi mpaka abwelaa!

 18. hahahahaha paja mumati Lucky Malata amazichinya yekha, Pano mukuti zimachitika mu mpira? hahahah Amakatani kumbuyoko? Mesa amaima kusogolo kumadikilira penaty?

  1. E neh sea ndi nger moo e key lay cool mbu yaw ma knee call zee Lucky Malata zee der moo cheati killer paul zee may neh zee ndi paul zee nah lee zo sir der bwi tsa, Hi ease a dee fender amer pay ze car cool full pea ndi ney tea ya key , wool yu ndi zee ner n saw. Moo n car tall car she tea , wool you mwa tea zee mer cheati car??

  2. Ma defender kudzichinya zimacitika or David Louis ku world cup anadzicinya kupangitsa Brazil kutsalira koma Chiukepo ndi striker.

Comments are closed.