Woman claims she was Gwanda Chakuamba’s second wife

179

…She wants first wife arrested

36 year old Grace Mhango has disclosed that she was Gwanda Chakuamba’s second wife and that she married him in 2001 when she was just 21 years old. Chakuamba was 67 years old when the two ‘wedded’.

Gwanda Chakuamba

Gwanda Chakuamba

Mhango made the chilling revelations just a day after late Chakuamba’s burial

Mhango claimed that she married Chakuamba a few months after the two were introduced to each other by Chakufwa Chihana.

She disclosed that he offered her a job to disguise their marriage. He however introduced her to his relatives including the ‘first’ wife, Raima Fatch, as second wife.

She also revealed that Fatch dumped Chakuamba during his illness that that she (Mhango) was the one who looked after him at her Manja residence in Blantyre where she convened the press conference.

She has thus asked the Malawi police to arrest Chakuamba’s ‘first’ wife, Raima Fatch who confirmed knowing Mhango but could not comment whether she was Gwanda’s ‘second’ wife.

Chakuamba died aged 82 and, if Mhango’s claims are true, she married him when he was 67.

Share.

179 Comments

 1. Kachepadi ka mtsikana.Udawafunsira ndi iwe eti?Amangiwe mtsikanayu agogo abuse.Uyunso othawa gogoyu awonedwe mwabwino.Adamchita chipongwe.

 2. Kachepadi ka mtsikana.Udawafunsira ndi iwe eti?Amangiwe mtsikanayu agogo abuse.Uyunso othawa gogoyu awonedwe mwabwino.Adamchita chipongwe.

 3. Iwe Ife tikukudjiwatau wabulukira mthembazakezitizokadi watiberekera mwana? Nanga luphatho apo ukasembiwamboiwe ndimbani akapereka ?nangambo Mbuya mtunzwi wathumbo timudjiwa nkhabevetayu iwe ndi uputa unapangamboiwe mwanambwa buluka!

 4. kunena zoona mkaziyu analidi mkazi wawo ife ndakunsanje mbiri za mbuya zinali nkhani zina ndiye akuyenera kumva kuwawa coz akazi awo oyambawo pamatenda sanapezeke iyeyo ndamene amasamala matenda since he was sick ndiye ubwino wake Patricia Kaliati ananena kale kuti chibwenzi kutha miyezi 5 limenelo ndi banja ndiye iyeyo kuchoka 2011 mpaka 2016 ndibanja ndithu even akumtundu akudziwa

 5. Iam also from Nsanje north but this so called dubious second wife is not known by the relatives of the late Mbuya. Where did they tie a knot ? Was a traditional culture wedding or christian culture?

 6. Kodi young lady where were u all these yrs? oyenera kumangidwa ndiwe, wakuba nthawi yako yatha, had it bn i was a son 2 GC ukanawasatira nditakupha

 7. Za amenewo timamva kuti ndi secretaly wawo ndipo nkhaniyi inamveka kalekale.Nthawi imeneyo zitamveka za chibwenzi koma anakana ponena kuti ndi scretalry ndiye lero likhale banja poti wina wamwalira

 8. Dear Influential Individual, We are delighted that your life’s journey has led you to discover our organization. we value anonymity. We see and know all just as a shepherd sees and knows all of the flock, our eyes peering over the masses to identify any threat. We are the bringers of new dawns, the guardians of the human species. We are the Pyramid, the Eye, the Light, the Eternal. We are the ILLUMINATI. The ILLUMINATI is a collective of prominent figures throughout the world who have united to guard the human species from extinction,we create wealth and make our member famous and rich in their own line of work. Our members bear the burden of a planet’s leadership with the lives of 7 billion in their hands. As the human continues to rise above its other animal counterparts, governing of the planet has turned into a daunting task. In return for their loyalty, our ranking members are presented the opportunity for lives of limitless wealth and opportunity. Once a member, the requirements are unimposing and often spaced between many years. Our requests are simple and therefore may be hard to comprehend, but disloyalty is not tolerated. You must understand this before applying. Members must fulfill their oaths to the Illuminati under every circumstance and recognize that they are merely one part of a much larger Universal Design. For centuries, our organization has separated individuals of outstanding political, financial, or cultural influence from the flock, and established them as shepherds of the human species. Perhaps you have already proven yourself in these fields. For that, the Illuminati officially congratulates you. Your dedication gives hope to us for the future of the human species. If you would like to continue your application,and willing to pay a sacrifice start by reaching us on my facebook account JOHN FRIGHT and you will be added to our list of potential candidates for Illuminati membership,and you instant reward will be given you on the first meeting sincerely.

 9. mayi wazaka 37 mpaka bambo wazaka 67?umafuna kum,bela mamunayo kapena chinali chili chani?mzimu wamadalawo uutse mumtendere cifukwa mai inu size yanu ndi kkkkkk.

 10. Koyambila lero ndisanzamvenso kuti apolisi anjata mzibambo wazaka 20 kamba kogonana ndi mtsikana wazaka 18 ndizakuthyolani, nanga taonani apa 67 zinatheka kulowa mu 21 koma sitinamve kuti akuluwa amangidwa

 11. Mkazi wachakwamba ndi glace coz wasamala yekha matemda ndewinawake asangobwela kumadziti mkaziwake thaw yonseyi analikut,bwanj samabwela kudzasamala matenda akubanja kwa chakwamba musalole kut zimayi ameneyi adyelepo analikwazungu uko palibe akudziwa amachita iye ndeasachenjelepo apa

 12. Why first she should be arrested Gwanda ngati amkamkonda oyambayo chimnampangisa ndi chani kufunsila wachiwiri?chikondi chao chinali chitatha palibe kumangidwa

 13. Thats how Malawi goes….. I remember late Kamuzu Banda, Juma…….he was also says he was his son….. Malawi…. Any way RIP the late Chakuamba

 14. If proven, I don’t see any problem of this claim more especially that the first lady herself wasn’t around during that Gwanda’s painful moments. If he married both of them then i wish the young lady best of luck. But there’s no point of any arrest here

 15. Zinazitu Grace ukuziputa dala mwana ngati iwe chinakukonda n’chani kukwatiwa ndi agogo ngati malemuwo. Pepani utha kumangidwa nazo zimenezo zitaye

 16. Unless she can produce enough evidence that they were legally married people will take her seriously but as of now her claims are baseless. Currently w’ll take her as one of the marauding women who are busy snatching other women’s husbands.

 17. Grace: Sorry 4 tht my cc* your time is over tangomuthandiza nzakoyo kulira maliro,,, nkazi ndioyamba iwe unali chair holder mmene wamwalilira nkuluyu basi iweyo u have to go back where u came frm..

 18. Where were she ooo… ds tym? Aku nsanjenu tatiuzen zoona kod mumamuona mkaziyu ali limoz nd malemu mgwanda kunyumba kwake? Komasotu kazinaka kakumveka kuti mkachitumbuka ndthu nene kut malemuwa anachoka kunsanje mkupta kukakwatla kumpotoo? Mmmmmmmm pankhaniy ndachepapo ndthu

 19. Akubanja akuti chan?Iwe ndi ine titha kunena zambiri, Ene pamalilo amapelekampata kuti amene anali ndingongole ndi malem anene koma akhale ndi umboni this is what can help not just talking

 20. MAIYO MWANA NGATI AMENEYO ANKAMULOLA BWANJI GOGO WAKE NGATI AMENEYO ZAKE ZIMENEZO AZIONA YEKHA ASIYE CHOKOPEKA NDI NDALAMA NKUMALOLA AZINGANGA.RIP MR CHA K.

 21. Ooo km anthu mulibe manyazi et mukufuna mua kumbuse anthu malilo or mukufuna muzionesele uchisilu wanu km amai inu manyazi bwaa

 22. Mvula ikagwa bongololo amatulutsa mau nkhululu zimamveka mau. Padzabwelanso ena mudzamva ndine mwana wa Chakuamba mundigaile chuma cha bambo anga ….

 23. Komaso iweyo Grace chinakupangitsa mchani iweyo wa zaka 21 kukwatilana ndi mdalayu wa zaka 67 eee shame maths 67 yrs -21 yrs =46 yrs iwe panga manyazi dyela lako lakupweteketsa kk

 24. Kodi myeyu amusiila mwana kkk chakuwamba anali dolo unali ukwati wa fack umenewo iwe unali kankha ukwele wake kk cash and eat …..

  • so wrong 2 come out this time,u can’t get wedded without marriege certificate,so u need to bring it out as your testmony,failing which nothing gud for u.Regardless of the differences upon ages,coz it’s what u chose,i can’t compromise i hv 2 respect your choice but no one can b arrested here,get it right okey?

 25. Mmm ali ndi zaka 46 maboza bwanj inu a mw 24…kuchipataladi samasowako amamusamala chakuamba ndiiyeyo nde zitha kukhala zoona nanga angamangokhalako daily

 26. Zitha kukhala zoona coz bwana uja amakonda kukwatirakwatira,osamangotsutsa zili zonse Ana midzimu Ali bweeee Ku Salima,ndangodutsa

 27. Anali wantchito,ngakhale Kazamila mpakana pano munamumva akunena kuti adali mkazi waKamuzu?Atsikana amasiku ano phuma.Ukanangokhala phee ukanapeza saizi yako koma pano mamemba azikuopa kuti ndiwe mkazi wamadala.

 28. Achina tidye nawo awoo! Soon you will here someone claiming to be Late Chakwamba’s Child lol,May Chakwamba’s soul continue resting in peace.

 29. ndiopusa bwanj komanso unuo muli ndiumboni wanj wot iyeo sinkazi wake mwina ndixiona mwina ndizabodzs coz anthu achuma amakhala ndiakazi ambirmbri ena odziwika ndi athu ena osadziwika ngt ameneu

%d bloggers like this: