Blaze, Ril B still fighting over Mwini Zinthu ownership

Advertisement
Blaze

Mwini Zinthu fell into the listeners’ zone earlier this year and it has gone all the way to top charts and record high numbers of downloads on Malawi’s music sites but musicians Ril and Blaze are still fighting over the ownership of the song.

A lot has been said about who claims ownership to the hit song and it has been claimed that Blaze was only featured on the song and Ril B is the owner.

Blaze
Blaze performing Mwini Zinthu on stage alone.

Some fans say Ril B who is an up and coming artist used Blaze who is established so as to gain fame on the Malawi music scene which is largely believed to be a game of chance while others claim Blaze does not want to accept the song is not his just because it has become popular beyond expectations.

It has also been reported that Ril B was intending to sue Blaze over the song.

During the Carlsberg Urban Music Legacy Concert that was staged at College of Medicine Sports Complex last Sunday, Malawi24 caught up with Blaze who said he believes he is equally a claimant to the product just like Ril B.

“If ownership is based on who was responsible for the studio charges then it’s Ril B’s song but if ownership is based on who is behind the lyrics then it is mine,” said Blaze when speaking to Malawi24.

The Nzakufusira Chibale hit maker claims to have written the song including Ril B’s verse.

However, the controversy has prevented them from performing the song together during events.

“We are quarreling and that is why you have not seen us performing the song together, but I have decided to put a full stop to all this because I cannot damage my reputation over one song yet I have many tracks,” he said.

Blaze
Malawi24 Entertainment reporter Lyonike Mughogho with Blaze (In white) after the exclusive interview.

The singer solely performed the song during the Carlsberg event much to the audience’s satisfaction as they sang along from the word go to the word stop.

That was after he had performed two other songs, Sudziwa and Bayum Thii. In Mwini Zinthu, Blaze did the chorus and two verses, the first and the last whereas Ril B only did the second verse.

This is one of the many factors that makes the latter to be overshadowed in a project he claims to be its master.

Commenting on Malawi music, the singer who is currently in Blantyre said it is going in the right direction.

He argues that if artists like him can pay their bills out of music then things are fine and okay.

Advertisement

221 Comments

 1. Munthu kulemba ganyu nzako kuti alime munda ndikumupasa ndalama, ndi kudzampeza nzako waganyu uja akukolola munda muja ameneyo ndiwakuba.
  Chifukwa anali waganyu basi.
  CONCLUSION; MWINI MUNDA (SONG); – RIL B
  WAGANYU (FEAT); – BLAZE

 2. ine ndili kunja sindikuziwapo kanthu nyimboyi ndiye ndiyabwino ine nyimboyi ndingomupasa gwamba ikhale yake kkkkkkkk

 3. ine ndili kunja sinfikuziwapo kanthu nyimboyi ndiye ndiyabwino ine nyimboyi ndingomupasa gwamba ikhale yake kkkkkkkk

 4. ma guys aku Lilongwe nanu,,,ndi mbuzi bwanji,,,ndunena inu amene mukuti nyimbo ndi ya blaze,,ine za music industry izi,,simbali yanga koma,,to be honest its awkward kunena kuti nyimbo ndiya Buzi,,kaya mukuti blaze,,,pamene mwini hits akuchita kuziwikila2,,#Ril-b,,,mwini zinthu uyu,,,Rill b ndi konkala pa nkhaniyi,,,kkkkkk

 5. To all the Upcoming artists, get a lesson here. You must have confidence in yourself that you can make it without any renowned artist’s assistance. You should ask yourself, “How did the other artists whom we look up to achieve it before?”. In that way, you will have confidence in yourself that one day, you will achieve it. All hard working pays. Neither of them used charms. Pray really hard, and you will make it . I rest my opinion.

 6. Chilungamo ndi ichi Blaze analemba nyimbo ya mwini zithu Ril B anaigula mapeto ake Blaze akuti ndiyake kodi munthu ukagulitsa chinthu chimakhalaso chako? Tisatalikitse nkhani apa Blaze ndi mbava

 7. Ine ndikuti nyimbo ndiya blaze chifukwa vers loyamba anayimba ndiye,ngati wapanga feature nzako mwini wa nyimbowe umayambilira kuyimba then uja wamupanga feature amamalizila

 8. Koma inunso nde kaya mwangodzitayitsa nthawi… tamaonani amuna ogwidwa nawo ….inunso nde kaya……….blaze tsopano

 9. kuimba kwambiri sikutanthauza kut ndiwe mwina wa zinthu nyimboyi anayimba kwambiri ndi blaze koma mukuona kwanga lil b nde mwini wake. for example dj Khalid ali ndi nyimbo koma sayimba even intro kkkkk

 10. Ril b ndikape chifukwa nyimbo yot ndiyake sangamusiyire opanga feat ayimbe mwa mbiri! mbuli zosaziwa sound nde ndizi achina Ril b zo!

 11. mkamaonela olokumvemuzizitsa kwambiri one day #saint anazamupanga mainterview #blaze pa radio 2 kufunsa kut nyimboyi ndiyandani olo pali featuring blaze ananena yekha kut nyimbo yija ndiawosn palibe zafeaturing anafotokoza bwino bwino blaze kut musatengele kut zina la ril b lili kumayambiliro olo kapena iye blaze anayimba kwambiri munyimboyi

 12. Chomwe anthufetikumasokozera ndipakuti Ril B anatenga vs Imodzi Pomwe Braze Anatenga ambiri kuphatikza Bridge ndiyensondikutchuka Kwa Braze panyimbondikale ndifukwachake tikumasokoneza but the song nd ya Ril B

 13. Onse awiri eniake akuziwa who is the owner wanyimboyo,kungoti akungofuna kutchukitsitsa mpaka mbewa ziwaziwe!.sindife mbuli kuti atiputsitse!

 14. Inetu nditaiwonera, ndinawona.. Ril-B feat Blaze. Ndie ukapanga featuring mesa kumakhala kuti wathandizira? Koma pothandizilapo pamakhala zinthu ziwiri,.. Ulemba wekha zoti uimbezo kapena mwini nyimboyo analemba kale akuuza mmene iyeyo akufunira kut uyilowere.. Kumbali yanga mwini zinthu ndi Ril-B, koma Blaze imamukhala coz anailowa bho.

 15. kumalawi kunoku si flames yokha imene siizatheka maiko anzathu sitimamva kuti akukangana chifukwa cha nyimbo koma kwathu kuno ha nazizwa vuto ndilakuti aliyense amafuna kuti atchuke ndiye panalibe vuto apa nyimbo anayimba onse thats fablous but now one wants to be more famous than another thats foolish.

 16. Kkkkk koma guys but to say the fact nyimbo ija anayimba kwambiri anali blaze nde kaya ndi ya rib b koma mukuona kwanga itha kukhala ya blaze not Ril-B

 17. Akazi awiri olimbirana mwana wina oti mwana siwake,mfumu Solomo adangoti adule pakati mwana uja kkk!nyimbo ija ndiya RIl B not bless kuba mkwanji ife tidavera kuyambira intro

 18. Kunena chilungamo anthufe timafuna chabwino chilichonse chikhale chathu nyimbo ya MWINIZINTHU ikanakhala kut sinatchuke ngat mmene inatchukilamu sibwezi tikunva nkhani zot eee Who is the owner.penapakeso ngat amalaw sitikutukuka ntchifukwa chanchitidwe oophangira

 19. Then both of you own the song,u know u young musicians u fight over useless and trivial matters,this song came out good coz u worked together,so stop embarrassing urselvestisiya kuyikonda nyimbo yanuyi.behave urselves

 20. Ife bola tikuvina…Nanuso aLil B osangothokoza Blaze pokutchukitsani bwanji…He even made some killer vocals that added ice on cake

 21. ma zoba akumalawi…kenako muziti Chipapapa ndiya 2face olo Sweet banana ndiya Kcee!!!!! shame on these rats any song has one owner and you feature someone to help boost the morale not that he or she should claim ownership.

 22. ma zoba akumalawi…kenako muziti Chipapapa ndiya 2face olo Sweet banana ndiya Kcee!!!!! shame on these rats any song has one owner and you feature someone to help boost the morale not that he or she should claim ownership.

 23. ma zoba akumalawi…kenako muziti Chipapapa ndiya 2face olo Sweet banana ndiya Kcee!!!!! shame on these rats any song has one owner and you feature someone to help boost the morale not that he or she should claim ownership.

 24. Ril B dne evrythng mentionng kt song tittle ikhale “Mwini zinthu” includng möney yaku studio ,so Blaze amagotegedwa kt akagoilowa muzwa pachi frnds.. To me the song is 4 #Ril_B

  1. kkkkkk komano nyimbo ndi ya real B yo.azingoimbila mma show limodz ka like mmene ankachitila nesnes ndi gwamba in bola kusache.ndipo ablaze wo adziwikanso kwambiri cos of that song osangoyamika bwanj?

  2. kkkkkk komano nyimbo ndi ya real B yo.azingoimbila mma show limodz ka like mmene ankachitila nesnes ndi gwamba in bola kusache.ndipo ablaze wo adziwikanso kwambiri cos of that song osangoyamika bwanj?

 25. RIL B NKOWONDA NDI MMAGANIZIDWE MOMWE,ANZACHE AMAKAKAMIRA WOTHUKAYO KTI AMENYE MA PROJECT ANGAPO LIMODZI,KOMA IYE AKUTI CHANI?? KUMBWAMBWANA,AYIMBE INA TIONE NKONONO UNGATULUKEWO!! NZACHEYO NDI DOLO KALE! BIG UP BLAZE! FEEL UR TUNES,YOU ARE THE NEXT BIG THING

 26. RIL B NKOWONDA NDI MMAGANIZIDWE MOMWE,ANZACHE AMAKAKAMIRA WOTHUKAYO KTI AMENYE MA PROJECT ANGAPO LIMODZI,KOMA IYE AKUTI CHANI?? KUMBWAMBWANA,AYIMBE INA TIONE NKONONO UNGATULUKEWO!! NZACHEYO NDI DOLO KALE! BIG UP BLAZE! FEEL UR TUNES,YOU ARE THE NEXT BIG THING

 27. Chomwe ndaona ine ndichakut a blaze akufuna kumukhomelera ril b coz ndiwosantchuka kwambiri pamene blaze ndiontchuka malawi yoseyi

 28. Some times oyimba akwanthuko akaona kt zinthu zawo zayamba kuyenda bwino amayamba kukanganapo tinene apa osachosera nyimbo analemba ndi ril b othandizila wake braze.

 29. en i quote “If ownership is based on who was responsible for the studio charges then it’s Ril B’s song but if ownership is based on who is behind the lyrics then it is mine,” said Blaze when speaking to malawi 24

  1. Ownership is not based on studio expenses nkhani ili apa ndi luso lomwe sitigula choncho nyimboyi ndi ya blaze

 30. Koma abale ablaze akufuna kuyaluka ndi za zii apanga featurng ndi anthu angati ndipo chavuta ndi ciani ndi mwini zinthu cifukwa ngati kuli kuchuka anachuka kale iwowa asakhale ngati mfumu david anali ndi nkhosa zambirimbiri koma anapha yamthu wosauka yemwe anali ndi lmodzi ,

 31. Thats Typical of Malawians. How many pipo know CHILAWE CHANGACHI is never NEPMAN’S Song and How many thousands of kwachas did Nepman made out of that Song and Look at the owner Nina? Featuring a song a song doesnt mean owning the song by anymeans. So its critically unfair that brainless minds are getting rich just coz they are more popular than the real brains behind a particular project, take that pill

  1. Feli…..u r vry tru n brenlss pple hav bkam rich on top ov ril brenz,,,,,Blaze being fichad basi nyimbo nd yache?????kkkkkk,,,,,,y kudn’t he manage even stdo expensez????? Am rlly in a dilema!!!!!!!!!!!!

  2. Feli…..u r vry tru n brenlss pple hav bkam rich on top ov ril brenz,,,,,Blaze being fichad basi nyimbo nd yache?????kkkkkk,,,,,,y kudn’t he manage even stdo expensez????? Am rlly in a dilema!!!!!!!!!!!!

  3. mayaz, i dont agree with u, aliyense amapindula, kaya dolo_yo, kah the upcoming artist, winayo will benefit Atchuka kwambili cos waimba ndi #mtondo en that will do him good, whilst the other will get more money than him, simple

  4. kodi munyimboyo anamveka kwambiri anali ndani komanso anapangitsa kuti yibebe anali ndani chifukwa penapake munthu amakhala ndi nzeru koma luntha samakhala nawo ndiyeno tatiyeni tiyang’ane munthu yemwe anathyakula nyimbo yija kuti ikome osati opeka.

 32. Mr Blaze tangovomerezani munangopangidwa feature, zimenexi ndizomwe zinachtka ndi desiigner, anagula panda mental for US$200 then kuhita lol

 33. Inetu when I was watching on YouTube nawonatu ngati analemba Ril b and Blaze …not Ril b featuring Blaze ..mukudziwa kwanga nyimbo akalemba wakuti and wakuti that means nyimboyo ndi ya onse..full stop

 34. kuno kumalawi vuto lanu ndlimeneli dats y am lov us muxic lyk fat joe wiz khalfa lil wayne chris b and etc osat nkhumba iz zkulimbana apazi

 35. sidelining all the negativeties and judging from the angle of honesty…it belongs to Ril B…him wanted to feat the famous Blaze so that he boosts it.if it was for Blaze then he could feature someone better than him since Ril B was not far much known than this before this so called”Mwini Zinthu song” otherwise kutchuka munthu samakakamira!!!

 36. Collaboration!!!! Be who u are!!! Honestly is two efforts in this song! Ft ft ft!!!

 37. Mbuzi zoimba zaku malawi pali chifukwa chosephanilana apa nyimbo muna imba nose ku studio voice ali ese anaithila mu mento pali so kusalanaso pamenepa oimba osewa ama lowa mento imodzi anthu five wa sinnaveko akukangana nde kuti anthu awiliwa ayamba kuimba ku mene ndekuti eti nyimbo yoti mwaimba nose wina sangakwanitse kumba ekha pa steg singakome ife ngati tiku ifila nyimbo yanui chifukwa choti mwaimba nose mumauzana zanzelu ikuveka ilibe mulobulemu nde muku funa kugawana zida nyimbo ikadali fresh bwanji mbuzi inu mwandibhowa ndichi dereter mu computer yanga chinyimbo chanuchi demeti

 38. Za chamba apa ayi feat means nyimbo ya anthu oyimba awiri or ambiri ndiye wina asamatukumuke kunena kuti nyimbo ndi yake nyimbo iyo ndi ya feat anthu awiri zopusa apa ayi

 39. Kkkkkkk nyimboyo angololana coz popanda mmodzi singakome pafunika onse bas koma kuma show payekha azikayimba sizoona or ine zingandinyase sindingalore mpang’ono pomwe

 40. enanu mungocomenta mwina braze simukumudziwa ndi yemwe amanveka mawu uja komanso amaoneka bwinobwino pa nyimbo ija osati obisalabisala uja nde mungati nyimbo nja ndani wina akuyichitira manyazi wina akuyilowa bwinobwino nde mungati nja ndani

  1. nde nyimbo zonse amakhala kuti wachita feat ndi athu ena kapena tikunenatu za munthu yemwe wachita naye feat osati ongooneka mi ms video komanso ukuti Dj khaled mwambiri imakhala kuti ndi ma mental no voice so ukuphatikiza zinthu ziwiri zosiyana enanunso mumsngisatira ma coment ngakhale wina angakomente zosaziwika simumadziwa chomwe muli

 41. What I knw is that when u feature someone on ur song,that person got all the rights to perform the song anywhere anyday.He must do his verses.So no need of claiming to be the owner

 42. nyimbo ndi ya rill b ndipo blaze popanga feat munyimbo imeneija Rill b anapeleka ndalama kwa manager wa blaze bensam kuti blaze akaimbe naye ndiye blaze chifukwa analipilidwa anaimba mozipeleka sinanga analipilidwa..ndipo blaze sakuyenera kuitanidwa ku ma show kukaimba nyimbo imeneija ngati real b palibe chifikwa Rill ndiye mwiniwake nyimbo

  1. pamenepaja zinalakwika sinanga Rill b siotchuka ngati blaze ndiye opanga edit video popanga amayambila dzina Lampard celeb wamkuluyo..zimene zimavuta kumalawi ndizimenezo celeb aliyese akapanga feat mfana obwera kumene mu music amaona ngati ndiya celeb uja …chitsazo nepman wapanga feat mafana ambili anthu amaona ndi nyimbo za nepman ngati iyiii waduxa pompa akayesa timadya moni anthu ambili kuwafusa akuuza kuti ndiya nepman pomwe Ayiii ndithu ..

  2. mayaz, i dont agree with u, aliyense amapindula, kaya dolo_yo, kah the upcoming artist, winayo will benefit Atchuka kwambili cos waimba ndi #mtondo en that will do him good, whilst the other will get more money than him, simple, ilibe mwiniwake nyimboyo, ngati iyeyo Ril B amati ndiyake bwanji sanalembe kuti feat Blaze

  3. limenelo ndi vuto la ma edit a video m’mutu mwao mumkayenda za blaze koma video imene ndakhala ndikuonera ine ku ma tv ose kumalawi kuno imalemba Rill b feat Blaze

  1. Aaaa Dj khaled samaymba,he z th Dj.same applies here Dj sley samaymba koma he z seen as an artist.koma Ril b,one verse kubwera Blaze 2 verses plus hook kumamenya yekha..haaa anapoyra Ril b ngatidi inali yake.

 43. kamufunseni gafaa…ndiamene akuziwa zoona..coz ndi amene anapanga mental..ndikuipereka kwa mmodzi mwaiwowo..ndipo opatsidwayo anaitana nzake kut ayimbe limodz after winayo atapanga kale concept…ya nyimboyo…

Comments are closed.