MEC chair no more


Justice Maxon Mbendera
Justice Maxon Mbendera
No more

Tragedy! Malawi Electoral Commission (MEC) chairperson Justice Maxon Mbendera has died.

This is a developing story, but reports reaching Malawi24 news-desk indicate that Mbendera collapsed during a meeting in Lilongwe this afternoon.

He was pronounced dead upon arrival to the hospital.

“The Chairman was in good health earlier in the day but felt unwell around 11am and was taken to Lilongwe Private Clinic. He died shortly after admission at City Centre Clinic in Lilongwe” said MEC in a statement.

Mbendera, who presided over the 2014 tripartite elections, was accused by the then incumbent, Joyce Banda, of siding with DPP. He wept during the official announcement of the presidential race which Mrs. Banda said were marred by irregularities.

Meanwhile MEC has expressed concern over the sudden death of Justice Mbendera. Justice Mbendera was born Nov 4, 1958.

“The Commission will miss his leadership. Our prayer filled thoughts of peace and comfort go out to his family and all those deeply grieved by his passing”

Justice Mbendera SC was appointed Chairman of the Malawi Electoral Commission on 10th October, 2012. His four year term was due to end on 9th  October, 2016.

261 thoughts on “MEC chair no more

 1. Mudzi amene ayika Malawi Mavuto ndi bambo mbendera pano tikuvutika ndi idiot wake peter chifukwa cha iwo kukondera komaso kukonda ndalama zomwe anapatsidwa ziwa chitila umboni

 2. Palibe zopepesa apa woyipa sakhalisa paziko chimuthu chakhaza wavutisa amalawi 20 milion pachimuthuvchomwe unanena kt wawina chisakho next bwapini then Gondwe kenako Hule kaliati komaso Henry Mussa ndichaponda khalani cheru kwasala inu agalu mwavutisisa amalawi.

 3. Ambuye wodzala ndi zisomo zosath ayang’anire mzimu wa Bambo Maxon Mbendera kufikira tsiku lachiweruzo.Ndikupempherera wina aliyense wagwiritsa ntchito lirime lake polankhula zosachita bwino pa imfa imeneyi kuti Mulungu amukhululukire.Amen

 4. u cried on tht day showing to public tht ur concerned hw fraud election was bt law betrayed u so to me ur not the one to blame R.I.P Mbendela

 5. musayankhule mopanda umunthu imfa ndi yowawa nayenso anali ndi anthu omwe amafila comfortabl with him plz plz bible teaches us about love

 6. All the best kumandako.adagulitsa mpando uyu dziko lapasi silifunika anthu onga amenewa Pano njara yavuta chifukwa chopatsa mpando anthu olakwika osatha kulankhura.

 7. Very sory to all Malawians this is the fate over us let us pray much to see where are we heading to. Sudden death in our Nation why? Stop critising each other for the remaining fingers will adjust to youself. Learn not to implicate anything this is death not politics. May His Soul Rest In Peace.

 8. God is control he bombed Malawi by abusing his power by declared dpp won the vote while he knew they didn’t chikumbumtima chamupha next is u who conerved with him. c u in another life is possible

 9. Lilime polankhula musanyadire moyo chifukwa tsiku lakufa silidziwika,likudikira iwe kapena ine.kwaiye kwapita kwatsala kwainu,Samalani

 10. a Malawi tikuluza anthu abwinoabwino kusiya mbava zomwe zikubera ndikupusisa anthu, ndakwiya nanu, shupit, HolyGhost Fire.

 11. Ma comment enawa musanalembe muziyamba mwaganiza Kaye chifukwa amend mukumuseka chifukwa imfa yamutengayo ndi Bambi ofanana ndi nsinkhu was Bambo athu tingamve bwanji Bambi atamwalira wina mkumasangala kumati achita bwino kumwalira,ziwani may awa: mdani was moyo ndi imfa,mdani wa moto ndi tchire louma inu mulibwino lero chifukwa mavutowa sanagwere mbali yanu moto kwanuko koma simukudziwa

 12. 2014 munamu nyoza kut obera mavoti,okondera,wapasidwa money,zambili mbili but today coz wamwalira ndiye Mukut what a great loose yet he wasn’t great in 2014 mmmmmmmmh malawi sazatheka R.I.P

 13. anthu mlibe pabwino pano wamwalira mkuti anali munthu wabwino koma mwayiwala 2014 mumaneneza zinthu zambiri kuti chisankho wakondera DPP komanso pompano mumanena kuti anaba ndalama za mec rip mbendera only God knows

 14. Innalillahi-wa-inna illayih raajiunah zimu wawo uwutse mutendere inshaallah tidzaonana zoti ndiwa chinyengo aweruze mulungu

  1. Mukukana chani? Mavoti munabera chauta akukantha modzimodzi tsopano,, akagwere ukooooo…. Ife tikadali ndi moyo

 15. Ku Lilongwe kwandiophya. Bingu anafera ku Lilongwe, MP wakumuchinji anafera ku Lilongwe, speaker wakunyumba yamalamulo anafera ku Lilongwe. Nthawi ya Joyce banda wachikulire wina aziombera chifukwa analuza zisankho. Kugwa mwazizizi ndikumwalira zimachitika ku Lilongwe. Rest in peace.Mr mbendera.

 16. Anthu ena akupeza mpata ponyozera kamba ka imfai.Dziwani kuti palibe wolungama padziko pano. Kuweluza nkwa Chauta basi. The late Mr Mbendela kwao kwatha kwatsala kwa iwe ndi ine basi. DO NOT JUDGE.

 17. Wolakatula Ontchuka Mmalawi Muno Analakatula Ndakatulo Zomwe Sitizaziyiwala Mpaka Kale. Maka Ija Amati Nonse Ozuza Mizimu Ya Amalawi Osauka, Muzafa Imfa Yowawa. 2014 Pa 31 May Ndisiku Lomwe Amalawi Sitizamuiwala Mkulu Ameneyu. Mbendela Mzimu Wanu Ukause Mumtendele. Tikakumana Komweko.

 18. Anthu ena mukufuna ineso afe musangalare nkuthe mukhoza kukhala inu oyamba kufa anzanuo alipo imabwera munjira zambiri mosayembekezera kut nkufa

 19. He will be remembered as a man who loved his nation so much that he shed tears in public during 2014 elections truth is that Malawi has lost a true son. may his soul rest in peace.

  1. Man Chitete Mulibe Nzeru Ngati Anakuberani Bwanji Simunapite Ku Khothi? Nkhani Siyonyoza Maliro, Mbendera Anagwira Ntchito yotamandika pa chisankho cha 2014, Anaberedwa Chisankho Ndi Gwanda Chakuamba 2004, Osati Makape Enawa

  2. Yudasi betrayed Jesus and committed suicide, Mbendera betrayed Malawi and cried. He has died after witnessing the disaster he brought to Malawians. Though he made Malawi a hell through Mutharika, but may God forgive him and receive his soul. We all make great mistakes in our life.

  3. nothing strange,it s death like any other.RIP someone said ,means Rest in Peace. question:; do Dead people Rest ? How ?

  4. MUNTHU WANZERU ZAKE SANGAMASANGALARE NDI IMFA YA NZAKE MWINA SIMUNAMVE KUWAWA KWA IMFA IKALOWA MNYUMBA NONSE MUKUSANGALALA MULUNGU AKUDALITSENI ZIKOMO

  5. Injust people always hates the Just,its the Malawi ans who voted in2014 not Mbendera. so if anyone goof fed in voting then it us. I still stand for Justice Mbendera. he did better than many of us could have done..

 20. amalawi mukamanenakuti wasalawakuti inu muzapitakuti inundi zisulo kapena muzauluka mulungu akukhululukileni pazomwe,mukulemba mzimuwa ambendela pamozindi mizimuya onse anamwalila muchifunilocha mulungu,iutsemu ntendere,amen

  1. Munthu Ukakhala Kuti Umadya Nawo, Umadandaula Kwambiri. Mwapindula Kuchokela Kwa Iye Nde Simungadandaule. Mzimu Wake Uuse Mumtendele.

  2. Man Mbewe Asiyeni Enawa Ndi opusa mwina kudziwa maliro momwe amakhalira maka munthu akafa osadwala chonchi achibale amasweka mtima, may his soul rest in peace,

 21. Yendan bwino papa moto umapita kwa sala nchire RIP

 22. Ndiye enawo osapanga resin bwanji? Kapena sakudziwa kuti ndi chigumula? Chamba basi Mungamuze anthu kuti azika mbewa mnkhokwe??? Mukazipeza pamene atakakukumbilenipo.. Mwena izozono zikadye inuyo…!

 23. Choipa chisata mwini amawona ngati dpp ndiyabwino afuse chasowa jauju mp wa mcp kumene huli zisankho za pandera nago chura ochepa mwaiwo anthu tigo phedwaopanda chifukwa ndi awa azathu malubino amalawi chitetezo tilimbe

  1. U ar not teling us bt u are givin God a mesurement wat ll use at u, Word said mueso umene muluesela wena ndio umene Mulungu adzagwilitsa ntchito pa inu

 24. Vote yanga sadaiwelenge amenei ndipo adaphesa munthu wachete ku Mangochi lero apezana kumwamba komweko. Good journey Papa!

  1. Guyz mulungu sanalenge imfa,,,he creatd de 1st man&woman dis2disobey him ndeanawauza kuti mphoto yaucimo ndiimfa,,,,anakapanda kucimwa bwenzi kulibe imfa

 25. You will be remembered in the history of mw, especially for the courage during annoucement of results of the tripartite elections on 30.05.2016 @ 11.00 pm.

 26. Ndiyebwino God has decrease de eldery population.kwasala Peter Mutharika,Dausi,saulos,kaliat n many more zikamatere bwezi zikoma pofika 2019 ambiri akhala atamwalira pamodzi ndi ana awo omwe.ndiye mwati pitala amwalira liti?

  1. awa malilo osamayakhula chomcho ngat musangalalai udziganza ali ale ewako wina mkunena chomcho kumayakhula ma speech ena pamalo polondola.Xorry ngat ndayakhula udyo sikut ndineso wachipani chinawinachoi

 27. Photo ya Uchimo ndi imfa…..iwe ungapereke dziko kwa muthu ameneyu zoona

 28. Wafera za eni ake Mbendera. Bola akadamwalira Peter Mutharika

 29. Wafera za nei Mbendera. Bola akadamwalira Peter Mutharika

Comments are closed.