Mutharika begins campaign: tells Malawians to vote for DPP for development to continue

Advertisement
Peter Mutharika

President Peter Mutharika has urged Malawians to vote for his Democratic Progressive Party (DPP) in the 2019 elections if the country is to continue developing.

Mutharika made the remarks in Area 25 in Lilongwe when he was inspecting a road project in the area. The Malawi leader also inspected roads in Kawale and Area 36 in the capital city.

He said the DPP is fulfilling its promises and Malawians would do well to make sure it retains power in 2019.

“During campaign we promised Malawians to bring development and now the Democratic Progressive Party led government is implementing what it promised, Vote for DPP in 2019 elections if the country is to continue developing,” said Mutharika.

Peter Mutharika
Peter Mutharika asks Malawians to vote for him again.

The Malawi leader rejected claims by other politicians that his government is only developing the southern region of the country.

He added that after constructing roads in Lilongwe, Blantyre, and Mzuzu his government will also do the same in other districts to perfect communication and transportation.

Commenting on the hunger that has affected over half of Malawi’s population, Mutharika said that his government is trying all it can to save hunger stricken Malawians.

“Yesterday I met with donors and we discussed ways on how we should implement the country’s food insecurity response plan,” Mutharika said.

He further advised Malawians not to only rely on Nsima saying they can also eat ‘Mbatata’ ‘Zitchetche’ and ‘Chinangwa’.

Advertisement

345 Comments

 1. Kkkkkkkkkk Malawi dziko lovensa chisoni kwambiri APM palibe chomene angapange ndiwakuba basi afa wakuba tawona chitukuko wapanga lero kwacha yikugwa ngati tilibe President mupaka 55 kuti tigule 57 ndiye kufika December yikhala 100 shame njala siyichoko Ku dziko lathu mulungu wakwiya APM yokha watikwana ife amalawi yowe azavotera DPP sakuyiyana ndi wamisala ayi

 2. Abale mukafuna kunena ndikumanyoza mitundu ziwani kuti chipani chanu chomwe mumasapota sitchizawina mulungu sangalole kuti mulowe Boma .Ngati mukutukwa musanatenge Boma kulibwa muli BOMA. M ukunena zamitundu muli kunja nanga mukalowa mitundu ina muzakhala nayo bwanji ? Mulungu sangalole kuti anthu ozikonda akhale pampando muzandivomereza tsiku lina.

 3. Anthu inu tamakhalani ndi ulemu,Munthu munamuyambira kumutukwana muja?mukupinduranji?Akulamulabetu mpaka 2019 woooo!!!Chauta anatipatsa.Inu misewu akukonzayo simumayendamo?God is good always.

 4. mwina enanu koma naine eeeeeeesh DPP ndikaikonda koma pano eeeeeeeeesh tinadana kundikwezela fees ku university paka ine kuvomeleza kuchepekeledwa kwanga kupanda manyazi bas palibeso wabwino ngakhale ena u r sayin UDF some thea sayin MCP palibe MCP inapha abale athu ochuluka Gadama Sangala ndiena UDF eeeeeeeesh palibe chazelu munachitapo kungobweletsa zifwamba bas zauchitsilu makape

 5. Kkkkkkkkkk koma jacket lokhala ndi mbendela za mayiko onse apansi kkkkkkk Inu a Getiludi imeneyo munakayipeza kuti nsanje bwanji mukufuna njonda isamawoneke bo kwati ma babe eti

 6. palibe chitukuko chomwe chikuchitika m’malawi ngati munthu akunena kuti muli chitukuko m’malawi akunama pali chomwe munthu unga yime pachulu nkumanena kuti ndikupanga chitukuko konkuno ku malawi mwina chitukuko choba ndalama za boma.

 7. why wasting my time to vote for dpp? what kind ov chitukuko chomwe akupanga malawi may be chitukuko chawo ndikumapha ma abino, dpp kadeti kuma sokoneza misonkhano ya nzawo, kuba ma allowances asilikali, kuba chuma cha boma.

 8. Ayiwala, kuti Kuchulukana ndikwabwino kumayipira mbale pokudya, now mwabelekana ngati abakha kumaganiza mudzitola zakudya, pano mukuyang’ana Peter akudyetseleni ana anu. Ka dziko kakang’ono koma is where the population is flying . mukuganiza mukalima kuti??????

 9. abwana muzangowinira poti alomwefe timaswana kwambiri koma mukutichitisa manyazi kwambiri komabe tizakubvoterani sinanga ndinu akumuzi komanso tikazavotera abusa a Chakwera zinthu zizayamba kuyenda bwino ndiye inuyo kulephera kwanu kuzaonekera poyera nde osadanda tizakuvoterani basi kuti anthu asaziwe kulephera kwanu

 10. Walephera ameneyo. I can’t see any tangible development he has done in the last two yrs out of more than 2 trillion Kwacha his government has used so far.

 11. i think this man is somehow eish! what kind of development is he talking about? starving with hunger and getting locust instead of nsima, can he eat beef or sausage without rice? i think twice now, this man knows that he cant win this coming 2019 general elections. we have kept our votes away from this thing so called DPP, Malawians wake up this is not time to sleep!

 12. asamawauze ana ife tatopa ndi boma yili tikomana 2019 yo nanga 577 b yikutani mpaka lero albino ndiye naji mukuwona ngati ife amalawi tangona okey???

 13. Economic crisis is every where why do we contradict with God’s word. This r the beginning of hard times believe me for sure.

 14. Dziko lamalawi ndilovesa chisoni kumayiko osey athu akufa ndijala koma akuti kuli olamula nafeso amalawi tizinganiz tiyeni tisankhe muthu opuzila tikukasisanghila moto.watilamula balewake zikolapasi paka linamuziwa kuti uku kulimuthu ziko walisandusa kukhala lakelake. inu mumati zingasinthe taonani mazi akukwela mitengo kunkhalangati anakatengela ku china mangetsi kukhalangati anakantenga ku somaliya kuzimazima koma mene ankundurilamo Eeeeeeee kusolola kwachuluka. azingolemela omweomwewo sindizavotaso

 15. Mukanakhala mumawerenga bukhu lopatulika anthu inu mukadadziwa zakunyoza atsogoleri,mukadadziwa zamasiku otsiliza,winawe wakhala ukunyoza ngakhale atsogoleri akume ukugwira ntchito moti zinthu sizikukyendera bwino,,zifufuze upeza kuti u dont respect okutsogolera,..mukamamunyoza president yu musamayamikire mphwache bcz ndinunomwe mumanyoza bingu,,komadi mau akulu amakoma akagonera..chimaoneka kuti ndichakuya pomwe chaphwera..mukhala pa fb mwina 5hrs koma kuti muwerenge bible 5 mins kulephera..anzanga apaulendo tsoka nyanja ndi mtunda pakuti oyipayo anaponyedwa kudziko kuno.lemekezani akulu kuti masiku okhala mzikolino achuluke.

 16. he s failing to employ secindary school teachers, nurses, doctors etc, no maize in admarc, hiding th cashgate suspects, security breakdown etc so which chitikuko is he talking about?? am forseeing whats happening in Zambia replicated here the opposition wil take over.

 17. Like facebook.com/nyasascandol and Enjoy the Rest of your Life. Musalore 2016 athe Musanapeze achikondi through page yathu. Like Like Like

 18. If it is a dream,ask kamuzu from the dead
  If its about “brave” visit Chakufwa chihana at kawiruwiru.
  If it’s a jock ask a chair Dr muluzi will teach you nice ones. Other wise back to Ndata.

 19. Mcp ndichani iwe wmangonva kapena kagweleuko kukakamila ntundaopanda mazi Osamangodya mgayiwaobwa haaaaaaa ndalesiphulakanthu kwaife anyamata achichepele keep Quite

 20. Amalawi munthu wina aliyese amakhala ndi zofooka zake palibe amene angakhale 100 percent such pipo do not exist in this planet earth

 21. let’s try MCP or UDF again inu achewa vote wisely ndinu munamuvotela galuyu ..nde pano mwaona mmene akuthela Malawi what wrong dit joice banda did ??? mwaonobga nokha dziko I don’t think amalawi tizabwelezanso kuononga nthawi nkumavotela buluzi wachabechabe 1 term yakwana basi akapume akutitaitsa nthawi

 22. Stupid present government with it’s leadership .we can’t vote for athief person.Infact he has just tested the seat.we will vote for another person whom we know ourself.His fellow thieves will give him votes,but not good people.

 23. Which development are we talking about here? APM’s government has failed us.you have NO vision, jus waisting government resources.
  #Malawian_leaders_though.

 24. This is not time for campaign! Is he feeling the heat?
  If you are doing shit,don’t expect people to jump whenever you command them!
  You will have to do much better to wow people, otherwise your days are numbered!

 25. kkkkkkkkkkkkkkk Malawi Woooyeeeeeee!!!!!!!!!! Dpp Woooyeeeeeee!!!! chipani kawawa pa Malawi pano, ngati ndinu otsutsa pepani this is our time hahahahahahahaha!!!!!!

 26. DPP ndi one a M C P mukukangana musanafuse kut tikuvoteran? Kkkkkkkkkkk sitikuvoterani a presdent anu muwauze kuti anangobesa ubusa kkkkkkkkkk mpando wa opposition umakukhalani mukapanga matama tikusabulanis D P P woye!!!!!

 27. Mungawone bwanji zitukuko zomwe akuchita pomwe maso anu atsekeka ndi nsanje. Ndiye mutukwanatu mpaka milomo yanu kupotoka, chifukwa ndiye DPP ndi Peter ndi Waya waya!

  1. U don’t know anything, just look around and ask neighboring countries how things are , then u will know. Umafuna akupangile chani kuti udziti apanga kathu??? Even some ppo at the age of 100 years samayamika Mulungu kuti wawachitila zabwino ati chifukwa ndiwosawuka yet mulungu wawadalitsa ndi moyo wawutali. Ndiye ngati mukulephera kutamanda Mulungu mungayamikire bwanji munthu wamba. Mukhala choncho ndikusayamika kwanuko.

  2. Fuck u too Stup blind baboon #Aboo. The way I look at ur face u can’t even do anything even if u can be given one million us dollars bcoz ulibe ubongo. Uli manja lende! Kumangokanda machende ako mkumaganiza Peter akusithile zithu m’moyo mwako.

  3. saukila awuze zitsiru zawanthuzo ino sinthawi yomadalila Boma or president kuti azakulimile kumunda kwako ayi ndiyochilimika pawekha anthu ena opusa amaganiza ngati president azigula thumba laufa ndikumawaninkha manyumba mwao koma sakudzi kuti akuzichedwesa ayi. and moreover uyang’ane macoment awo uzapeza kuti ndianthu akhawo amangokhala kudalila Boma kuti liwapangile kanthu nthakufunsani Boma lakuti linawapasa anthu zithu iwo ndikulemela nazo ntchito yaboma ndi president ndizitukuko osati iwe okanda iwe nde eweyo ukhalile zomwezo zomangodalila bomazo anzako tikuzisaka osadalila boma ayi dziko lake lomwelo.

  4. #Alinafe. Ukunama! 2019 boma kachekena. More over u never voted for him. Ineyo ndinavotane I will vote him again even though sindinadyepo olo cent ya DPP but I like that party and is trying only mbava ndizomwe sizikuwona ubwino wake. Akakhala mavuto ndiye sanasiye dziko, The Sadc region njala yokha yokha ndiye Osandiwuza za nyotso apaaa agalu inu.

  5. I support DPP and Peter as l did by voting him with his party,koma nthawi zina kumazipanga weight tikamayankhura coz we know nothing about malawi

  6. kkkkkkkkk mukulephera kupanga zanu kudalila Boma shame on u anthu awulesi komwe kulibe njala ndie kuti koma anthu amapeza ndalama asanagwire ntchito ndiekuti zitsiru inu tapitani pa south Africa apa chimanga chikuchokera komwe ku Brazil ndi zambia pano 3 sakukololabe anthu midzi madzi akuchita kumwa anvula ochita kutchera pamalata kumalowa mu drum magetsi amangonva akuphikila nkhuni koma poti inu ndinu mbuli zosayenda simungadziwe kanthu ayi kumalawi mumalima malo awule pomwe maiko anzanu saloledwa kulima malo opanda chilolezo ayi even nyumba munthu kukalamba osamangako nyumba mpaka kumwalila kulikuletsedwa pomwe inu malo mukukhalao ndaulele pitani pamozambique pomwepa palibe munthu kupanga zake zamutu boma osadziwa ayi musamale muzavutika mukakhalila yomweyo.

  7. In South Africa , Sugar 1kg wosadziwika bwino bwino ali pa 20 rand ndiye wa illovo sim’mene amadulira , thumba la ufa la 50 kg lili pa 400 to 450 depending the location. kungokambapo zochepa, koma nkhani ndiyoti zakudya in SA zikudula than any where in Sadc. Inu muli busy kuloza chala peter, kodi simunawamve a chair kuti analibe grocery, tsono Peter yu ali nayo???

  8. Kusayenda ndi mbuli, chonsecho ati anapita ku chacco koma samadziwa m’mene mayiko akuyendera. Ndalama kwathu kuja zimabwera kamba ka ulimi , koma zoti mvula sikugwa bwino sawona

  9. even xool kwathukuno ndiyaulele primary pomwe mayiko anzunthu kulibe ulele ayi ndiyolipila secondary xool mafees ake kuliku malawi akuposa ku universty. ku universty akuphunzitsa mwana ndimunthu olelemela basi kapena azungu or ma India amwenye, munthu wachikuda akati wasunthako ndiekuti wafika grade 12 secondary xool amathera pomwepo basi anthu akulila ndika K400.000 yomwe ndi R7000 basi per year ndalama imeneyo or primary xool sikukwana fee pa term ayi.

  10. Ayiwala, kuti Kuchulukana ndikwabwino kumayipira mbale pokudya, now mwabelekana ngati abakha kumaganiza mudzitola zakudya, pano mukuyang’ana Peter akudyetseleni ana anu. Ka dziko kakang’ono koma is where the population is flying . mukuganiza mukalima kuti??????

  11. Iweyo ndiye maso ako sakuona, hodeolum intenum, zoona tonse tinganene zaboza, peter akupanga chiyani chabwino? Aaaas, amuchosa ndi ambuye akaksmira, kulibe kubera chaka chino. Akufa

  12. Man #Eliot. The whole world is under recession! And Malawi itself is very far to stand this problem bcoz we don’t have any minerals, pa TV mukuwona mayiko m’mene anthu akupangira ma protest and more over mayiko ochita bwino, kodi mayiko amenewo akulamulilidwanso ndi Peter???? Nthawi ya Bingu mumatelo koma atangomwalira koma mwati emwe uja! Kudula kwazithu kuli mayiko onse, Si zoti akati ku south africa 50kg ya ufa ili pa 450 ndiye kuti ndi cheap ayi, anthu akuliranso kuti ayipeze ndalama imeneyo pamakhala matatalazi . Sizoti ndi 450 kwacha ayi. kubwera nayo ku MW ndi 20 chakuti pin. Ndiye mukati Peter sakuchita kathu mukutathawuza chani maka maka ???

 28. He pretty knows that he became president through back door now he wants if possible pple can vote for him him which is absolutely impossible for his graring leadership qualities! Only those who do not know that he is a rubber-stamper will do!

 29. Ine siwandale ndipo sindimavota ngt kt no side ndizakhala ndichoyankhula mukazampeza sogoleli yemwe mumamufunayo opanga zokukomelani nanga simwina zoti ndale ndi business simaziwa zalowa busness sazapezekaso tiyeni tizingolimbika ntchito apo ayi pitirizani kulemelesa anthu zaka 5 wina alemele,5 winaso choncho mpaka muzalisiya zikoli

 30. I cant see any development during this mad president apart from devaluating our Kwacha and increasing prices of things iyaaaa

 31. which developments is he talking of huh?…….He is just opening and supervising the developments of his Legendary bro Dr Bingu Wa muthAlika ,the late ,,,may he rest in peace.Hunger ,poverty,Corruption ,poor salaries,Albino killing ,high school fees ,Why don’t he stop for a minute and think of these and say if we have developed in any of these areas .kuwina 2019 kuxangokhala kut tili kale Boma koma if Not chawo panalibe ,mwina kwa anthu akonda ma k50 tyms ya Campaign koma for those who know the meaning of development ,I don’t think this is our MAn ,so let’s think twice and Make #ONEMOVE.Malawi DZUKA.

 32. Mu mbiri ya dziko lino malonda fodya sanafike poyipa ngati chaka chino munthu angavotere satana ngati iwe woposa nebukalineza ngati iwe ndani

 33. The truth is that he never win election & wil never do…development my foot,,,is getting money from other people’s land a development? i hate that bill maybe u dnt knw

 34. Kubera ma vote ndi udolo guys,wina kubera kuwina,wina kubera kuluza,what bafles me is hw dd Peter managed kubera ali ku oposition nkuwina yet amama cashgate anabera while ruling analuza?

  1. Mmmmm!!! ndiye zili ndi ntchito yanji #Suzgo? Joyce anali chitsiru cholamulilidwa ndi aliyense! Just imagine anthu kuba mipando after Msokhano awke waku Bangwe, Anthu kugenda convey ya vice president ku ntcheu. Bwanji sizikuchitika mu ulamuliro wa Peter? Ngati anabela ndi dolo, ofoyila anali Joyce

 35. Azimai onse a dpp ali pa njala yoopsya amapita ku nsonkhano asanadye munfunse campaign director akuuzani awuzidwa kuti azidya maungu ndi mtedza dzulo dzuloli ndi life president wao.

 36. hahahaha ngakhale osapanga kampeni koma azaķhalepo pa balĺot paper amalawi tidzamuvotelanso mavoti migolomigolo 2014 ija ikulenga asadziwa ndani kuti muthalika 2019 ndi napolo kutsetsa opposition yonse kukaponya mu lake malawi

 37. Let him treat malawans with love and respect otherwise here in zambia youths have voted agains president lungu and as things stand, he is leading with a very margin line..

 38. Xa 2019 xakale kale m’malo moti mupange zachitukuko zapano iyaa ctidya ndale ife,kaya mudzawina kaya mudzaluza tangopangani xachitukuko za term yanu yoyamba ino,

 39. You nailed it Mr president we will vote 4 u, half time is not full time. But first shortlist wat u hav done so far , coz as 4 me I don’t see anything u’ve done dat wud make me 2 vote 4 u again the only thing u achieve is ur prophesy 4 locusts ov which I don’t eat . This time I will use my vote correctly no mistake.

 40. munthu anakanika kutsogolera mmaunduna onse anakhala ngati nduna ndiye dziko lonse angathe?Koma ndi mulungu di akuyendetsa kkkkkk

 41. Bwana osavutika mutha kuwina opanda kampeni. Ena akut sakuona chitukuko koma ife ku 18b mawatimangila nseu omwe wakhala ukuvuta nthawi yamvula. Ndamvaso kut misinje yonse muchita irrigation zabwino kwambirrrrr

 42. Voting for peter is a very unforgettable and regretable mistake malawians shall make.Ife ma civil servants, we are more than ready to bring this man down.Where on earth would rand cost k53 and still insisting that things are working?DPP should forget rulling this country again.

 43. MMMMmmmm Inu Amene Muli A MCP Munalamulirapo Koma Simunawinepo General Election 1999 Munkat Muwina Munaluza 2004 munaluza 2009 Munkati Muwina Munaluzanso 2014 munaluzanso pano mukuti muwina 2019 kkkkk Shumba Kulota Ali Ndi Mapasa Kkk ngati anzanu mukut amabera inu amakuletsan ndi ndan? Dpp Woye!!!

  1. chifukwa chake dzikoli la onongeka chifukwa chakusankha molakwika munthawi ya mcp anthu anali opeza bwino kusiyana ndipano izi sizolira munthu wophunzila kuti apenye

  2. Mmmmm!!! Nanunso. #sean. nthawi ya MCP kunalibe anthu ambiri, acha bambo athu amalembedwa ntchito ali pa school std 8 kuli kusowa kwa anthu ophunzira, Ndiye tandiwuze kuti ndima company angati omwe anasiya Kamuzu mu population yochepa ija, ndipo ndi angati awonjezeredwa muchi POPULATION chino?

 44. Brother R.Stambuli muuzeni iyeyu sakudziwa kuti anthu ndi okwiya chifukwa chobela mavoti vuto la Malawi samafuna nkhondo iyeyu adzathawira ku America dziko atawononga

  1. NGATI MBENDELAYO ANALI MSUWENI WAKO USAMALE PAKAMWA PAKO KOMANSO UKADZAIMA NAWO PACHISANKHO NDIPAMENE UDZAZINDIKILE CHOONADI

 45. APM sakuziwa kuti akulamula dziko ndi ndani chifukwa anabela thats why akuuza athu kuti azawavotele. Anakakhala kuti akuziwa yemwe akulamula sanakayakhula zoti athu azavavotele 2019 chifukwa thawi ilipo yambiri.

  #Dziko_lamalawi likuyenda_chifukwa_cha_chisomo_Cha_Mulungu Tiyeni Amalawi tizimupempha Mulungu kuti azitikondelabe mpaka azawachose akuluwa mwa ulemu popanda nkhondo ndi ziwawa.

  Ine ndi Wa UDF, bt #2019_i_will_vote_for_MCP

  1. KingVujah Nonyeranani Atima Seleman ll UDF ndi chipani chabwino ndipo sindingatuluke koma panopa mfundo za akulu akulu achipanichi sizingasithe zithu mu ziko muno kusiyana ndi MCP;

   vuto lomwe likumatipwetekesa kumalawi kuno ndi lakuti, timavotela chipani ngakhale chilibe mfundo koma ngati timachikonda timachivotelabe. A good example ndi ku Mulanje, athu ambiri omwe anavotela DPP ku Mulanje,Thyolo and phalombe amadandaula kuti anabesa chifukwa palibe cha nzeru akuchiona mu Usogoleri umeneu.

   Ngati inu mwaganiza ngati ine mwachita bwino, MCP ikazalamulira: zipani zambiri zizaphunzila zofooka zao trast me and ugwile mau anga

  2. At Felix Mwachiwa osusa akuyenela kutero kusiyana ndi olamula chifukwa alibe chochita koma kuyakhula pomwe olamula ali ndi zambiri zochita komanso ali pa mpando.

   Sungamachiuze chibwenzi kuti dres wavalali ndinagula ndine, malaya wavalawa ndagulanso ndine nde uzindikonda. Ngati uli mamuna wozindikila umapanga zithu zoti nkaziyo aziziwa kuti awa ndi amuna ndipo palibenso sindingapeze ngati amaneyu. Boma silikuyenela kumayenda and kumawauza athu kuti tikukonza miseuyi ndife nde muzativotele mu 2019 haa

  3. Sean nakha nsogoleri azitiuza zokudya zitete ndi mbewa zoona?
   Dzuro amawauza athu ku LiLongwe kuti azidya Maungu ndi nteza: kodi ino ndi Thawi ya Maungu ndi nteza? Tasitha thabwa basi

  4. Get my point Saukila, maungu ndi nteza ndi zithu zabwino koma ino ndi Thawi yamaungu and nteza?? Limenero inali funso langa.

   Njala imavuta kwambiri kumizi, kodi panopa Upite kumuzi ungakawapeze Maungu and nteza woti ungaphike ndikudya? Chilungamo ndichabwino A presdent sakuziwa kuti zithu zimakhala bwanji

 46. Munthalika dont waste your time.be serious.. Why Campagning for DPP. Chipani chowinawina kale. In the country without a viable opposition party

 47. He must know that we are not all DPP and must behave as such being the president. Need did not use DPP cash to fund the trip therefore he must talk about the government agenda and not that of DPP

 48. Chiwala chimenechi chitivuta bwanj
  Chikuganiza chizawinaso
  Gay wachabechabe galu ameneyu chitukuko wapanga kut
  Chitukuko muthu apanga kwa ku America uyu apite akamuvotere komweko

Comments are closed.