Obama’s brother to vote for Trump: ‘My brother is weak!’


Malik Obama

…endorses Trump’s plan to ban Muslims

Washington D.C.| US President Barack Obama’s half-brother, Malik Obama, says he will vote for Republican nominee Donald Trump in the forthcoming election slated for November because he is unhappy with his brother’s leadership.

Malik Obama
Malik Obama: To each, his own!

Malik, who is in his 50s and a US Citizen told Reuters he supports Trump’s policies, especially his focus on security.

“He appeals to me and also I think that he is down to earth and he speaks from the heart and he is not trying to be politically correct. He’s just straight-forward,” he said.

Trump’s stance against Muslims coming in to the United States was understandable even to Muslims like himself, Malik said.

“I’m a Muslim, of course, but you can’t have people going around just shooting people and killing people just in the name of Islam,” he said.

He said he does not care what people will say for bashing his brother.

“To each his own. I speak my mind and I’m not going to be put in a box just because my brother is the President of the United States,” said Malik who said Obama has not lived up to the expectations that accompanied his election in 2008.

Malik joins Bingu wa Mutharika’s brother who endorsed Bakili Muluzi’s candidacy in 2009 in the lead up to the Malawi Presidential elections before Muluzi’s candidacy was invalidated by the High Court.

135 thoughts on “Obama’s brother to vote for Trump: ‘My brother is weak!’

 1. Malawi 24 tatopa ndi nkhani zanu zopanda pake,mumatiuza zamaiko akunja kuti ife titani????mmalo mokamba zomwe zikuchitika mdziko lathu (Malawi) kuti mumve mfundo zaathu osiyana siyana ,muli buzy ndi America.America alibe ntchito ndi Malawi.

 2. Zawo zimenezo,,mapazi awo,,angokhuta atondido basi,,,andale ndizidole amatikonda tikamawavotera akawina achule amenewa kuchuluka zokamba,,eg,,,,”anthu openga mwapanga bwanji” mmene ndimakuvotera sumadziwa kuti ndine openga? Mapazi anu

 3. Za chisoni zed matsiku omaliza, ndi kale lomwe kunalibe zithu ngati izi FB, Twitta, whatsap and many more. Kubwela kwa izi athu ena apezelapo mwawi omalemba khan zopanda malango ndi kunyoza ena bas, u jus westing time for nothing

 4. He’s wasting vote. .or maybe bought. ..OBAMA IS A STRONGEST PRESIDENT OF AMERICA WHO STEPS WHERE NO AMERICAN PRESIDENT STEP…SPEAKING AGAINST CORRUPT AFRICAN LEADERS IN AU. ..THOUGH IT FELL ON DEAF EARS AND THEY ALWAYS SAY IS AN AFRICAN WAY….DEMOCRATS ARE HIGHLY RESPECTED AND HE MAKE SURE HE PAVES WAY FOR DEMOCRATS TO CONTINUE GOVERNING USA…

 5. ine kaya ndichimwa koma izi ndizopusa,,, ife tikulira ndi umphawi pomwe inu mukuchita kunenepa ndi mavuzi omwe. Zadziko lapansi iz kumwamba kulibe iyah!! Osandichimwisa ine

 6. Kumvetsa chisoni a Malawi. Za social media zidabwera usiku sitimazitsata. Ntchito ya ma media sitimaidziwa. Omwe mukunyoza apa mukusonyeza kuti mitu simagwila ntchito. Even Radio imakupatsilani nkhani za kunja koma chifukwa mulibe mwai oyankha pa radio akamalengeza mumakhala mukukambanso mbwelera ngati izi mmitima mwanu. Tamatsegulani ma page amaiko ena muziphunzira kuti kodi dziko likuyenda bwanji? Mumamva bwino mukalemba zonyoza koma simudziwa kuti mumasonyeza umbuli. Get a life my fellow Malawians. Kunja kudacha kalekale but u are still sleeping!

  1. Same father Different Mothers,Malik’s mum was Black[Kenyan] while Obama’s mum was white[American] thats y they look Diffnt.

 7. Kumeneko ndiye kupusa imu 24,simungabwerese nkhani zaife amalawi or arubino story,,,,musamatitenge ngati tose tinakharako kwamereca ko,tiuzeni zazitukuko,kapena zamagetsi akuvutawa

 8. I Wish Bingu Culdav Done The Same Not Left In Hands Of His Brother! Daz It Mean They Didnt Kno Each Others Weakneses? Ndale Zakumalawi Zomabisana Zoipa!

 9. Kodi mumalemba zamaiko aeni bwanji?
  Ndiye zikolimene mukumaliremba apa lingafanane ndi Malawi?
  Asiyeni ndi olemera kale awa, lembani za wathu uyu piter akuti apanga zotani kuti athandize anthu kunjala, nanga Feterezar , kukwera kwa katundu! talembani mutiuze akuti bwanji?

 10. Inu a Malawi 24 b serious popeleka nkhani ntchito ya editor nkuona ngati nkhaniyo jothwakuka mbwerera ife ayi. Mmalawi muno muli nkhani zambiri koma vuto akakudyetsani chi mtuwitsa ndichi cup chajomera inu zokamba ziiiiiiiii

 11. What makes this man a brother to Obama. Look at him he is mbuuu kutuwa akagwere. Even azungu akomweko are worried with his Tremp what about him mulendo ngati uyo. Akagwere

 12. Nkhani imeneyi Ili ndiphindu apa? Mudzitiuza kuti atipasa matumba achimanga tigawane. Aaaaa! Wina akufuna kuvotera wina nde ikhale Nkhani? Mawa mutiuza kuti Peter ati lero samwa tea koma coffee.

 13. So Who Cares About Obama,isnt He An Animal Who Kills Enocent People In The Name Of Demon Cras(the Hand Of Satan)stupid Malawi 24 &ur Leader Obama

 14. So Who Cares About Obama,isnt He An Animal Who Kills Enocent People In The Name Of Demon Cras(the Hand Of Satan)stupid Malawi 24 &ur Leader Obama

 15. Zinthu zopanda ntchito ngati izi! Mukuwuza mtundu wa Amalawi kuti titaninazo ife!. musamatitenge ngati zoseweresa ife! please, ifeso! ndi zolengedwa zake za Namalenga tilemekezeni ifeso tizakulemekezani.

 16. Zinthu zopanda ntchito ngati izi! Mukuwuza mtundu wa Amalawi kuti titaninazo ife!. musamatitenge ngati zoseweresa ife! please, ifeso! ndi zolengedwa zake za Namalenga tilemekezeni ifeso tizakulemekezani.

  1. Trump samanyoza anthu akuda. Osamangokhulupilira zilizonse #Dolo. Chiyambire campaign Trump zonse zili pa YouTube palibe pomwe adakamba zonyoza anthu akuda. Pa internet pali tima Link tongopeka nkhani zabodza inu ndikumakhulupilira.

 17. So what ali mbuu mkumati m’bale wake wa obama what malawi can get with his words? Timakhala ndi obama ife? Obama adabwerako kuno? mbuziii

 18. So what ali mbuu mkumati m’bale wake wa obama what malawi can get with his words? Timakhala ndi obama ife? Obama adabwerako kuno? mbuziii

Comments are closed.