War within: Winiko quits DPP executive

Advertisement
Bon Kalindo

Days after Democratic Progressive Party (DPP) summoned Member of Parliament (MP) for Mulanje South Bon Kalindo popularly known as Winiko following his semi-nude parade, the legislator has stepped down as deputy spokesperson of the party.

Kalindo was earlier this week summoned to a disciplinary meeting with DPP officials to iron out issues that emerged due to the parade he held some weeks ago.

After the meeting the lawmaker declared that all was well, but he has now stepped down from his position in the party saying he he wants to concentrate on his private issues.

Bon Kalindo
Bon Kalindo calls it quits.

“I have issues that am doing, firstly am doing my studies, and am shooting a movie, and a movie needs great attention that is why I want to take away some things on my schedule,” said Kalindo.

But he was quick to mention that his stepping down is not connected to the meeting he had with the party officials.

“Those things we discussed and they were ironed out as a family we are on the same page,” added Kalindo.

The parliamentarian recently claimed that the party was trying to kill him after he was chased away from a rally held in Mulanje for staging a semi-nude protest against killings of people with albinism. Meanwhile DPP officials are yet to comment on the development.

Advertisement

198 Comments

 1. Winiko ndiotchuka kale osat afuna kutchuka bodza ,Ife amphawi sitingadziwe msika wamalubino km ao achumao thats wy akulimbana ndiwiniko km chonde musamusake ngat nyama .Dziwan bable limat uchotse chiwalo chokupangitsa uchimo winiko wasiya kaudindo kanu kadziko lapasi ok

 2. Kodi mukanena za choitukuko ndimayesa chimabwerera anthu? Kodi chitukuko sichimakhuza ma albino? Kapena ma albino si anthu? Samalani mukamanena zinthu. A Kaliati mukukambawo sizikuwakhuza za ma albino? Ma albino savotanawo pazisankho?? Hon. mayi Kaliati zimawakhuza kwambiri ma albino akamavutika. ndili ndichikhulupililo choti nawonso azabwera poyera mnjila ina. nonse simungapange bizinesi ya mtundu umozi mdziko. A hon. Kalindo pitilizani. Zandale zilindimalire koma izi mwatumidwa ndi Mulungu.

 3. Makani adzipanga koma akanati adzipanga chitukuko ku dera lakwawo monga achitira Kaliyati ndikanati Winiko ndi dolo, koma ayi angofuna kutchuka kumtundu wa a Malawi pamene dera lakwawo liri mmavuto adzaoneni. Shamee Winiko.

  1. Aaaa abwana ndisaope kulankhula chifukwa choti kuli anzeru ngati inu ayi sibwino ndidzikaoneka wabwino kwa anthu akunja chikhalirecho familly yanga iri mmavuto adzaoneni inu ndi nzeru dzanu dza full dzo khalanadzoni ndipo muchite nadzo bwino.

  2. Iwenso ukuoneka kuti uli mgulu lakupha nawo ma Alubino. Chitukuko ndi moyo wamunthu chofunika ndichani? Pitiliza kupha kuti ulemere mwachangu.

  3. Idzo ndi dzanu kaya ndiri mugulu lokupha kaya ayi ndikudziwa ndi ine ndi Mlungu wanga I don’t care what people says koma ndikudziwa ine ndi kulankhula monga munthu wa ndale. Mutha kumuyamikira Winiko kamba kooneka kulimba mtima koma simudziwa kuti iyenso wakhala akukhunzidwa ndi ntchitidwe omwewu koma poti tingoyang’ana dzochoka pakamwa pake. Shame @mthiramanja.

  4. Ngati zili zachilungamo aulule kuti awonekere. Osamangoyang’anira zinthu ngati zimenezi ayi tonse ndi anthu amodzi. Lero zili kwa ena mmawa zili kwa ife ndiye tiyeni tikondane.

  5. Bwana @gondwe mudzitha kunva komanso kusata chomwe munthu akukamba. Sindikusuppoter kupha anthu amtundu wa chialubino koma kutengera dzintchito dza Winiko ndi dzomwe iye akukamba ndi dzosiyana. Am not a kid Mr Gondwe, i know what am i say.

  6. Kulikose kuli mavuto koma osati mavuto opha albinos. Chitukuko ndikupha nzosiyana paoziwa chitukukowo nde apanga chani pankhani ya albino? Tikunena zokupha albino osati chitukuko #teamwiniko#

  7. Mudzadzindikira bwino patsogolo dzintchito dza Winiko kwa ine sindingamusupote ndi bwino kupedza dzina dzothesera kupha ma alubino osati mwa Winiko

  8. HARRISON,muphunzire kuyamikira munthu mbali yomwe akuchita bwino,non of us iz perfect,muyamikireni WINIKO he has pray an important part pofunafuna mtendere wa anzathu achi alubino,ISILUTE U MR WINIKO,& mr harison muwafuse akazianu ngati amakukondani akuuzani mbaliyomwe muli perfect komaso yomwe mumailephera,& simungakhoze zose NEVER!!!

  9. Kaliati wakhala m,boma nthawi yayitali almost 15yrs.Pomwe Winiko is less than 3yrs.Ndiye u can’t compare the two.Koma political wise Winiko ndi Dilu bcoz he has got

  10. @lidia ndimayamika poyenera kuyamika, ndimalesa poyenera kulesa. Sindingamuyamikire munthu chifukwa choti inu mwamuyamikira, NEVER. Tayesaninso nanu kuwafunsa bambo akunyumba kwanu adzakuphunzinsani kudziwa chabwino ndi choipa.

 4. Mwayitha a Winiko,,, they must not take a chance bcoz cha udindowo but the truth will remain the truth!.. DPP mmusowese Winiko bcoz we kno your system, ,But know that God z watching you & u shar pay for dat…

 5. Anthu inu a dpp mumaganuza bwanji ? Asatana mbuli za anthu inu walakwa chiyani winiko ? Koma kupha ameneyo tionetsana

 6. akudana ndi zoputsa ndiye a #Dpp paja ndi ozikonda kkkkkk ulamuliro amauika nyumba mwawo amaiwala kt ili ndi dziko latonse Munthu kupempha chitetezo kwa anthu azake walakwisa. bola ife taziwa zomwe akufuna kupanga, mukamupha dziko lonse lizaziwa

 7. Why people gets mad at your personality? Thank you mr mp for defending our beloved country.You re one of the most generous person I know so far.You fought like a soldier, there is no room for giving up untill the issue of killing of our brothers and sisters is deafeated.

 8. DPP ikapanda kusamala ndi tizinthu tating’onoti adzalira pa mawa. Ndipo ngati satsatira maganizo a kalindo nde kuti wamkuluyo ndi business yakedi. Kaya sakudziwa kuti ma albinowa anawavotera nawo? Xory ma albino munavotera ifa yanu yomwe

 9. Winniko anayamba ndale kufuna kuthandiza anthu ophinjidwa osati kupondeleza kapena kuwathila msika ai.Akufuna chilungamo ndipo chidzamutsata kulikonse angapite angakhale atasiya ndale.

 10. I can anticipate the downfall of winiko,chifukwa ng’oma yolilitsa sichedwa ku tsweka.Winiko wanu supita anthu a n’dera lako akukuvutikira kuti akupedze,ukungochedwa ndi phokoso mmalo mopanga chitukuko.2019 is around de corner i can see some1 loosing election miserably..

 11. NO NO LOOK ALL OVER KILLING ALIBONS like in kenya,sela lone plus more than 15 counties these things happen no one protest and these happen just WE GOT HEARTLESS AND LACK OF UBUTHU AT ALL

  1. Enter your comment here…Tapita ukusambe galu iwe kuda kwako.

 12. john Chilembwe2.akhala bwana a winiko.ndipo mulungu akutsongolereni.mimwai ina yochuluka kuti anthu akadukawa.adzachite manyazi.apa mwaonetsa moyo oti.ndinu mzikadi ya malawi.n’thandizi wa anthu omwe akuvutika ndi umphawi,osangoti poti ine ndi MP.bola anakusankhani.kamagwelu akati aphedwe.nonsenu,tiphaaa.abwana.nyansi mwandikwiyisa nonse mulikumbana ndi bwana winiko.mulungu.akudikilani?

 13. Winiko shdnt hve run away .Being inside the party cud ve done him better thn outside hwever expect tough times ahead bcz they ll do evrythng (Dpp)to nail u dwn nd remember Billy kaunda was there nd Joseph Tembo where r they nw?Lucious shd b ur moltivator bt its totally different bcz soldier is UDF nd comes 4m different regions in terms of hw loved one wil b.Be wise in doing things

 14. He was expressing his wrights ngati M’malawi kma timalimbana ndizazii! Sindikuona cholimbanilana ndi Winiko! Boma lina lija ndichifukwa linalira ndi academic fredom coz of kusazimvetsa zinazi!

 15. now that heis out of the executive let him come out and tell Malawians where he knows is market for albino bones since he told the nation that some big name government officials are involved.Dont try to be clever when u cant prove ur argument.this is a very important issue that has to be adressed soonest.

 16. kodi a DPP mukuchitilanji zimenezi? zowona Winiko akumenyela woti azibale athu achalubino asamaphedwe, inu mukulimbana naye. Kodi inuyo aDPP mukudziwapo kanthu? mudakakhala kuti simukudziwapo sibwezi mudana ndi Winiko.

 17. We have always been saying this tribe is a curse, they don’t love each other because everyone want to be a hero even if he has nothing tangible to be of that heroic stance

 18. This is a good example, koma chifukwa chakuti anthu amalowa ndale bcz of greedy,that’s why anthu ena akuwona ngati walakwitsa.Political career or no career,but he got a good heart and care

 19. Wachita bwino winiko kutula pansi udindowo.Ndiza dziko lapansi izi,zosala.Enawo anachalira kufuna kuchotsa moyo wako,poti ndiye chinkhalidwe chawo.Amaliza kutafuna ma albino onse mu dziko muno.

 20. ku malawi kuno kunachuluka mbuzi za anthu.sindiye kuti munthu ukawina pa ticket ya chipani,ndiye kuti basi uzilolera ndi zopusa zomwe ayi.dpp isanabadwe winiko amadya,kuvala and anaphunziranso sukulu yakamuzu.olo atasiya dpp sangagone ndi njala.nonse amene muli against winiko muli behind the albino killings

 21. Go Go Go Winiko…ur fighting for the rights ofAlbinos..not govt..leave everything in God’s hands,He’s gonna fight back for and protect you ..our beloved country need jack up people like you..Bravo!!

 22. So you stupid people are at hand defending this labolousing regime which keeps on killing the innocent people? I wonder why malawi will never move forward with these rubish citizens who just accept anythng cos of laznes to make money. Killers deserve to be killed too

  1. That’s why u r getting everything wrong, the Government is not killing people and Kalindo was voted as an Independent candidate and has been asking to join DPP ever since. If u can understand this u will know where our Malawi is now

  2. At the mean time we dont have to care which party he was voted for but all we seeking is protection from government. We are being emberrased enough with rubish stuff internationaly as if we dont have government. Extraordinaly this is a worst regime ever since we gained independence. Mthalika is out of ideas , cabinet ministers are just interested in enriching themselves and right now they are killing people who voted for them……

 23. mmm banbo winiko dont knw wat he want in life…lyk a train wf no destination…pipo of mulanje muzionesesa when chosing ma mp…enawa nda sewelo bxi sangatheke

  1. hahaha govt z doing enough evry public adress th przdnt owz tolk abwt albino en we c police workng day en 9t arrest these pipo hence stiff punishment by our court..wat else du want???diso kwa diso..we dnt want blood in hands of our God feling przdnt,,en he wl neva sign death pernalty…judgement z fo him mulungu..ngat simuopa chauta zanu izo ziphani nokha wanva a Gertu nd aPart

  2. mungamve bwanji ataphedwa wachibale wanu bambo nowa????how z winiko becoming judas??mumafuna akhale mbali yosekelera zophanazo???do u even have a human heart???

  3. doez wo support winiko u dnt knw hm wel amangofuna kutchuka b4 he wz an MP he wz pressuring za malo ku mulanje …..where is he nw wth de issue after he won a seat……

  4. Nowa jst open ur eyes & c…Yes judgmnt z 4 hm…Nw y do u lyk klng dnt u thnk tht ts sin 2….hw wl u feel if u gat an albino and 1 follws 2 kill ur own blood…Thnk ma frynd…

  5. Bambo Nowa,infa imaphweka ikakhala kwa nzako,umatha kusamba ndikudya komano zikakhala mnyumba mwako ndipamene umawadziwa maliro,yankhulani ngati ndinu obereka mwanva

  6. ooh yes..infa ndyowana ua ryt..knw this 2 wrong does nt mak ryt,,understnd guys thus y ophawa akumagwidwa nkuponyedwa ku ndende ngat chilango pa chimo lomwe achita..munthu alibe ulamulilo opha anzake mlengi akutelo..musakhale ngat aluya inu

  7. Kumangidwa for 3 years iz not enough for albino ndiye iwe nowa ukuganiza kuti akazatulukanso okuphayo sazaphanso albino ena think about 3 short years

  8. Albno nd muthso, malamlo aimile aliyense.Winiko ali m’boma demo amapangira nda?Bwanj osanena ku ma meeting monga iye wa exective.Dziko likulira iye wapeza mwai wasewero.Usamunthu.

 24. winiko ndiwe bulutu iweyo wayenera kuvala nsanza ndi kukapanga perform pa bwalo anthu nkumaseka that’s all not to be a parliamentarian as such.

 25. When people elected u they means that they were trusted u so nw u 4got the all things what u promised to in your area whats wrong of kalindo.?

 26. I see hon kalindo if it true that since organising the demo was already out from his family party but was next expecting an apology otherwise aproverb ” do not trouble trouble otherwise trouble will trouble u” so far i see no future of kalindo in politics and hs dirtened all ama drama kuti si anthu owa voteraso poti amatenga zonse monga madrama ndi thabwara 4getting that being voted to parliament as honouble member MP u hv to respect urself first ndikusiya kaya apo zonse zawusilu,zamasache, zosekesa,zamanyi,zadrama etc koma iwowo ayiwala kuti panopa ndiwolemekeze ka anyway “POTI GALU NDI GALU BASI NGAKHAL E KUMUPASILA CHAKUDYA PAMBALE ACHOSABE NDI KUDYELA PA DOTHI”

  1. winiko ndi ufulu wake, kodi mutakhala inuyo mukuphedwa kapena m’bale wanu inu mungave bwanji? tiyeni kagweleni ukoo!! ndi DPP yanu yopusayo, Winiko wachita bwino kwambiri chifukwa waonetsa kukhwima nzelu kwake pandale.

 27. mwadya mfulumira Che winiko.nkhondo mumamenyayo mukanaiwina muli nchipani cholamula but now mwaluza basi.bvuto mukumvera kwambiri anthu apa social network.fb ndioputsitsa iyi.simudziwa ndale inu anu ndi.madrama basi.uzifunsa nzeru kwa kweni kaliati ndiye Eni ake ndale.mwachepa nazo.mutchuka kwakanthawi kochepa kenako fwakalala. unakwera tu ya DPP usaiwale anthu ammidzi ambiri savotera munthu amavotera chipani.samalaaaa

  1. sanatulukekoma wangopanga step down as deputy spokespersonkoma inu mmene mukuzioneramo zikupita kuti.@chippie chalunda.

  2. kkkkkkkk ma brouse @ wezzie aziletsi mmikonomu…zoona @ patie msiska ndale angogwera kkkkkk timugulira ina nyt dress yofira yofana ndi boxer anavala pa ma demo ija kkk

  1. Anthu ngati Winiko ndiofunika kwambiri ndipo munthuyu Chauta amudalise,sizomangoyamika zilizonse cholinga uzikhutisa mimba yako kuyiwala chigulu cha anthu omwe anakuvotera.

  1. or atakhala pa rent vuto nchani?? omwe akukhala manyumba awo akukanikilanji kumenyela ufulu wa ma albino, ine i can choose wapa rent ( winiko) coz he is trying his best

 28. he is acting too fast if he wanted to correct things then it waz good while inside but now he is getting out of it…mmmh it will be hard

 29. …. problem he listens too much to social media supporters forgetting kuti DPP is his identity, let him go it alone or with Facebook fans and see how far he’ll go. tiyenazoni ife kwathu nkuona..

  1. ngati akulakwitsa mulungu achita naye koma ngati akukhoza mudzachita manyazi mulungu ndi amene adziwa tsogolo lamuthu osati wina adzichuluka mnzelu

  2. .. Guys what he did was right thing,but we must know kuti every mudzi/nyumba/banja limakhala ndimalamulo ake, so dont just do it on your own way bt follow the employer’s rules, or else he supposed to resign first and go it alone, dnt abuse freedom in the name of albinos to gain political mileage…..

 30. Winiko umandisewresa, umandiseweresa, asiyileni kumene ngakhale chipanicho tulukani zisiyeni mbavazo zopanga zokonda a Peter ntundu onse wa Malawi ukuvutika. Shame my mother Malawi

Comments are closed.