Work hard to free Malawi from poverty, APM tells Malawians


Peter Mutharika

President Arthur Peter Mutharika has urged Malawians to work hard for their economic freedom  and for the development of the country.

Peter Mutharika
Mutharika: we need to work hard

Mutharika was speaking during the commemoration of the Independence Day at Bingu International Conference Centre in the capital Lilongwe on Wednesday, July 6.

The state president said it is the duty of each and every citizen of this country to change the situation in which the country is going through and claimed that working hard is the best way to end poverty.

“In my independence national address, am asking all Malawians to work hard for economic freedom. It is our duty to change our situation,” said Mutharika.

He added  there is a good lesson people in the country need to learn from the holy Quran on Surat chapter 13 which states that ‘we know that God cannot change the condition of the people until people themselves choose to change that condition’.

The Malawi leader then hailed his presidency saying during his reign he has managed to change a lot of things and to introduce reforms.

309 thoughts on “Work hard to free Malawi from poverty, APM tells Malawians

 1. your thieving acts are making Malawi poor,tell him.All your cronies, your ministers are benefiting from your acts, don’t blame Malawians, change the system uzaona wekha.

 2. That’s not tru.Stop blaming the country!!!…The country deosn’t do anything wrong . The countery is not lazy and the people of Malawi they are not lazy.It is a president who is lazy.He don’t want to help his country on what they can do!!!…

 3. Mr Presdent, plz u must thinking twice b4 open ure big mouth. How pple in ure Country working had while every going up each and every day , maka maka farm emplements. Anthu akuyesetsa koma zukukanika. And its difficult to u, kuziwa kuti anthu akulimbikila or not coz umango khala kuchimpanda. Ndiye plz stop talking nonses speeches.

 4. Hendrick JT Kalewa usanamize anthu police yake yakuti imabwera mma Street kumagwira anthu kuti akapange chitukuko zonama basi ine ndiri ku Capetown anthu akuno amangofuna zolandira kuchoka ku boma usaname even munthu woti akulandira ten thousand rands pamwezi akudikira boma limmangire nyumba osamanama mzayaluka!!

 5. Kuganiza mopepera ife tikakhala ndichakudya chokwanira umazatilimira ndiiwe mmunda mwathu? Khani ndiyoti zipangidzo zaulimi zikudula komaso mvula siikigwa bwino basi.

 6. Tili ndi president opusa am sorry to say that, ndiliti analimapo chpalapala iyeyo mpaseni khasu guys kapena achape zobvala zake ndi sopo wamaluwa atikite lol osamangonena zinazi

 7. Your government is too corrupt Mutharika! Everything we do whether is legit or not, we have to meet a middle man to get through, don’t say that we are lazy people? How dare are you? Do you have any idea how had the Nyasa work to put the food on the table? If you don’t have any plans to sort out the mess your stupid government has created, just shut up.

 8. Ameneyu akakhuta ma laida angonena wamba eti? kodi akufuna tizilima chotani ulesi wache anenawo ndiye uti? wayambira kutiberazo sizinamukwane ifetu ntchito tikugwira koma aba ndi iyeyo, plz tell him dat he mast stop saying marderfacken thingz like dat, ifetu timangomupasa ulemu coz he z our President . koma titafuna akhoza kuthawamo muno, ZAUSIRU ETI.

 9. We are already hard workers your duty as a leader is to just create jobs and a conducive environment for business. We can not work hard on without.

 10. Thus True! Ena Kwacheramu Alawilila Pa Bawo And The Are Complaining About The President How He Runs The Country! How Do You Expect The Country To Develop? Should The President Work For You? Aaaaaa Amalawi Kumakhala Serious! Come To South Africa No One You Can Find Along The Street Playing Bawo And Other Games.Actually Policemen They Come And Take You To Work For The Gvts’developments. But If Malawi Gvt Introduces That Muzaona Omenyera Ma Ufulu Akuti Boma Likupwanya Ma Ufulu Anthu. Amalawi Democracy Tinaimva Udyo Ndipo Izatipweteka

 11. Mthalika nzeru alibe akuti amalawi ndi aulesi anadyesa angati chitsilu kwambili akupanga chiyani chothandiza amalawi ukakhala mtsogoleri ukufunika uziyankhula zinthu zomveka bwino anthu tikuthamangira kunja kamba kuti zinthu si zilibwino mziko mwathu zonsezi ndi iyeyo akuwononga

 12. Kunena mowopa yehova, mavuto ali ku malawi gwero si ulesi. Koma kusawopa yehova kuyambilira ku mipandoko. Ndipo dziko lathu silosauka. Muzanditsimiza kutsogoloko. Ulamuliro wina utalowa mkumatchula ndalama zobedwa ndi ulamuliro ulipowu.

 13. koma abale zna ukanva!!! m’mozi mwa alesiwo ndiiweyo nanga tiziti umagwira khasu iweyo? dats a 2 painful words to us.

 14. Koma Zamuvutad Ameneyi Kuima Pagulu Kumayankhula Zopusazo Ndi Chidzete Komaso Asamaone Ngat Kut Sitdzwa Kut Akupha Anthu Achalubino Tikuzidziwa Zimenez Ndichitsir.

 15. Lazyness how??? If we can go to town during 9t tym to serch de food of tomorrow Vakabu yimatigwira ndiye tipanga bwanji??? Tiyitanire ma minbus masana a police amatigwiranso ndiye ndipange chani??

 16. Lazyness how??? If we can go to town during 9t tym to serch de food of tomorrow Vakabu yimatigwira ndiye tipanga bwanji??? Tiyitanire ma minbus masana a police amatigwiranso ndiye ndipange chani??

 17. the problem isn’t that we r lazy, bt malawians leaders aren’t myopic of malawi’s future, they just wana benefit 4m us, pachakuti pawo!!!

 18. Kod upupresdent umenewu mudangoutenga ngat umfumu wakwazimanu? Aules tkhale ife? Ukadaona zintchto tmagwla kumudzkuno sibwez ukukamba zimenez

 19. Ife ma nurse kusatilemba ntchito ukuonangat tichita bwino bwanji? GALU IWE,IMBWA INUNA ZINA LAKO NDIWE SIKUPI

 20. Not True Dat We Are Lazy We Are Hardworker Kma Zomwe Mumafuna Andale Ndikupondeleza Basi Misokho Tikupeleka Kma Chomwe Tikudabwaso Mbewu Zathu Mukugulaso Molila Mationa Ngat Zinyama Eti? Lingalilaniso Bwino

 21. Atate ndi amaimunthuyu wakura sakuziwa zimene akamba sakuziwa kuti anthufe kungwira tikungwira koma maripilo ndi ochepa komanso ntchito ikusowa ndiye chifukwa akutiuza kuti tizidya ziwara kapena mbewa munthuyu za muvuta msiyeni akwamnilise lamulo po ife amalawi timarekeza lamulo

 22. Kodi akamati amalawi ndiawulesi akutanthawuzanji? Mesandiwomwewa pakampeni paja amkanenakuti adzapeza njirazoyendetsera dziko kuti anthu asadzasowe ntchito, kodi chiyambileni kulamula atsegulapo makampani angati amene amalawi alephelako kugwila ntchito, akadakhala kuti ndimunthu wanzeru sakadalankhula choncho chifukwa iyeyoamadziwa kuti anthu sadakolole akadapeza njira yowathandizira nzikazake zisadafikepovuta. Mwachitsanzo kamuzu amkayenda bomandiboma kuwona kutimmera ulibwanji akawonakuti sizilibwino nthawiyomweyo amathamangiratu kupita kunja kukapempha anthu ake asadafike pomwalira ndinjala. Koma mapresident omwe tikusankha lero ndiye mbuzi zenizeni, amadikila malipoti woti anthu akufa ndipamene amayambakuthandiza.ndiyelero mukuti amalawi ndiawulesi mwawonaliti? Ngati zakuvutani aptsemkoni anzanu ayesepo mwayinu mulibemo ulamulilo wadziko koma ulamulilo wankhondo,

 23. Thats a good piece of advice Professor Peter. We will improve on this. However, you may wish to consider the fact that CORRUPTION is also derailing the economic progress of this country. Too much money is going into the personal bank accounts of very few officials, companies connected to people with names.

  secondly, u may wish to cut on the number of advisors that u have hired on board. Does it mean that the minister do not furnish u with enough information/advice? or should we say it takes a very big team of advisors for you to understand something?

  with due respect professor, u may also wish to cut on the extravagances in the public relations eg the issue of a new convoy, u may just buy one or two cars……not replacing the whole convoy. The number of state houses is also too much for a country like Malawi; How many white houses does USA have?

  I wish you Mr President good health as you govern this land. ( I am just a voiceless citizen).

 24. nde akufuna kut tizigwira ntchito iye aziba? pamsana pake mbambadi, kumakhala kulepher nanga malo momatirimbikitsa pazina ndizina, aziimaso poyer ndikumathokaso mbola, Bushili mulosere akuchodwa ameneyu

 25. Sure, work hard, pay the multiple taxes, more money at MRA and treasury and let those who have the right to steal our taxes steal??……until ACB is freed, Government shows no impartiality in fighting corruption, hard work will not bear fruits. Sad

 26. Pitala can’t you see that people are trying their best. But you and your caligue corruption too much. Cashgate, muuzane kuti muchepetse kuba ndalama zaboma. Where does tax that you are collecting in boarders go? Answer me pliz pitala.

 27. Wasowa chonena iwe kamuzu mu nthawi yake zithu zinali bwino ife sitikanabweraso kuno kumavutika wamva iwe muthalika.

 28. Vuto amalawife, tinazolowera kupempha/ kudalira chithandizo kuchoka kunja, kodi mukufuna presdent abwere panupo kunzakupasani chakudya? Ndimadabwa ndi anthu omwe amanyoza presdent chonsecho mulungu anati, ” muzadya thukuta lanu” ukakhara pa xul kuti ukhoze bwino umafunika kulimbikira, good example tanzania anthu ambiri amalimbika nthito ndikupanga mabizinesi wamuna kapena wa kazi, nkumadzipezera zofuna zao. Presdent is just a leader, do not expect to be given, but work hard you will succeed. iyaaa!!!!

 29. Bwana peter tamva mau anu koma mwina simuziwa chikhalidwe cha a Malawi, a Malawi chikhalidwe chathu ndife olimbikira or maiko anzathu amachita kuyamikira kuti anthu ochokera dziko la Malawi ndi anthu olombikira kugwira ntchito ndiye inu makamaka mukuthandauza chani?

 30. am in south africa and white people they like us because we are the hard workers, so what kind of lazynes is he talking about because the i know malawians we are all hard workers, this muthalika must step down because he failed

 31. mkuluyu bwanji kodi?.create first job opportunities like industries,companies and etc then ndipamene uzinena wat u have just said.iya

 32. Mbava iz osamazimvera, kodi kulimbikila komwe akufunako akufuna tichite pofikana kunyambita pathako pa panti wake ndie atsikimize kuti ndife olimbikila? Yekha sangaone momwe zithu zakwerera mdziko muno? Kuyambila sugar, buledi, tomato,

 33. Maybe Malawians would be freed from poverty much sooner if there wasn’t so much wholesale corruption by politicians and civil servants – and if the President made drastic cuts to his ridiculous personal expenditure..

 34. Aaa zinaukaona kamba amakhalangati mwala. Mau apresdnt amenewa? Kkkkk waulesindindani pakati pa ife ndiiye?munthu wosakwanisa kudyetsa anthuake mcp inali njilazothandizila anthu kuti asafendinjala,amapelekandalamakumakampani kuti zinthuzisakwele.tsono anthuakulila iwe ukuti mulindiulesiaaaaaa tikakuyankhani mudzati takutukwanani.siyani kuyanhula ngati munagwelapo mchimbudzi.mwana akuti bambo ndikufuna nsapato iwe ukuti kagwilentchito ndiyeku palizabambo apa?

 35. That’s ark nonsense show them a way by supply them with pumps, give them chemicals, fertilizers then tell them to work hard.

 36. We are hard workers,jst because you’re a foreigner,you don’t know.our parents dying young age because of hoeing now u r talking nonses.

 37. Malawi’s leadership fails Citizens by taking chances. Even Malawians we are also a big problem in our culture praising someone as a leader as their Messiah, Ngwazi, Chatonda, as he/she has not yet delivered.
  To be a leader isn’t to be praised before, but after you fulfill your promised goals and deliver promised standards.
  We feel uncountable not countable as real citizens bekz we sell ourselves to them.
  What assurance will he President make or show to all Malawians that can really motivate them.
  Malawians are number one trade skilful brand in Southern Africa, but you Leaders are a very, very big headache to our goals.
  There are Educated, skilled, business and rich Malawians inside and abroad, but they are failing to invest in Malawi r even to start a business in Malawi you have to go outside borders to order your merchandises, why Mr President? @ 53yrs old Malawi has never civilized on her Industry of manufacturing its local goods?
  Sorry Mr. President don’t blame us blame your greedy leadership styles of which from 1964 to date has never bear ripened fruits to Malawians.

 38. whether u go to Saudi afrikA south Africa ask them how hard Malawians work u will hear that we are hard workers now what kind of hard should we work

 39. Malawians are already hard workers but its the people like you the leaders that deprive them of their benefits and what kind of hardwork do u the leaders want them to do in order to develop the country? Clueless leaders indeed we have!

 40. If Malawians were not working hard,would you find that 577 billion and 61 billion that you and your brother stole in gvt? Mr Ibu you must be ashamed of yourself

 41. We must working harder until when? To be honestly people try to work hard so that they can get something after but the huge problem is your Government are busy robbing people if they want sale their belongs to the markets for buying them on cheap prices.

 42. Amalawi ulesi ukuphani ndi njala ndipo president wanu sakupasani chakudya kapena ndalama za ulere. For example anthu amene ankamanga stadium from China amagwira ntchito usiku pamene ife eni tikugona choncho tingalemere? Mukhaula ngati simuyamba kulimbikira boma lake si la peter. As a teacher he wants to teach as a lesson of hard working ufune usafune….ulire usalire in 3 years time you will rely on your on.

 43. On an age of 53yrs old Malawi, the head of state still doesn’t believe so, that Malawians aren’t hard workers.
  I doubtless his ideas.
  From 1964, the first heads of state Dr. Banda emphasised Malawians to work hard in their fields, but they were let down at the ADMARC, robing them till to date,
  Thirty years from Dr. Banda, came Bakili Muluzi with the same tune, left helpless Malawi’s hard workers empty promises.
  Ten years from Bakili Muluzi to your late Brother Bingu wa Mthalika, Malawians were still hard workers till to date.
  you again applying the same tune that Malawi and must work hard to sustain the economy, really I doubts u leaders are problem to hard working Malawians bekoz u use them as escape Goats to ur dismaly failures.
  There is no country in southern Africa compared to hard working Malawians, but to its leadership.
  Why only you Presidents MPs,
  Ministers becomes multi millionaires?
  Prepare a sound mechanisms to up lift Malawians from their dire poverty by investing in Infrastructure programs of which really can uplift Malawians from poverty.
  Stop criticizing Malawians as the feel embarrassed from so called leaders.
  You educated them from Primary to Universities and skill technical schools, but they are immigrating for greener pastures because they don’t find goals due to government failures.
  Farmers loose their produce annually due to poor roads and Electricity networks, so where is leadership?
  Govt must first support citizens with its resources, in return the citizens will deliver

 44. People in Malawi are already hardworkers but what are you doing Mr president inorder to help them do you see what is happening to tobacco farmers now they are crying and you are just quiet what do you mean?

 45. OFFICIAL NOTIFICATION:
  WARNING TO FOREIGNERS INTENDING TO VOTE IN ZAMBIA’S ELECTIONS: WE SHALL KILL YOU!!!
  With the latest list published by THE POST newspaper with names and centers for Malawians and Tanzanians registered to vote in next months elections, we want to issue a strong warning to our friends from neighboring countries….: IF YOU WANT TO BE ALIVE BEYOND 11TH AUGUST 2016, DARE NOT COME TO ZAMBIA. IF YOU ARE ALREADY IN ZAMBIA, WE URGE YOU TO LEAVE BEFORE 11TH AUGUST.
  To our vigilant soldiers and strongmen in our party, should you spot any Malawian, Tanzanian, Congolese, Mozambican, or Zimbabwean near any polling station on the 11 of August 2016, KILL ….. and dont spare. We are not going to allow any foreigner temper with our democracy…. You come, YOU WONT LEAVE ALIVE….YOU WILL GO BACK AS A CORPSE. Since ECZ has been compromised, we shall physically protect the victory.
  To our well trained protectors of the vote, we are almost there, lets prepare ourselves. Akuna Kulala. Each and every poling station countrywide will have our soldiers, and we shall not spare anyone trying to manipulate this election. Battle lines are drawn, and WE ARE READY.
  From:
  The Chairman,
  UPND Anti Rigging SQUAD..
  Lusaka Region..

 46. Let me agree with Mr president,working hard is the only secret here.. For example malawians ino sinthawi yodalira salary yokha to survive, lets work up and think twice!! Tiyeni tidzipangaso ma business,ulimi and zina!! Palibe dziko mu Africa lomwe silikulira ndi financial crisis,talking of Zimbabwe,South Africa,Angola and likes nawonso akudutsa mu nyengo zowawitsa… Ino sinthawi yomalozana chala kuti uyo nde wayambitsa,mind you analosera karekare aneneri za masiku otsiriza!!!

 47. nde ngati a presidend akuti zilimbikilani kugwira ntchito wina nkumati kulimbikila kwanji unditsoka tayenda maiko ena uwone ndipo uzadziwa kuti amalawi ife ndifedi alesi kuno ife sitigona ndipo kutuuza kuti mawa off timadandaula chifukwa timadziwa kuti taluza ndalama chitsanzo mabwana kumalawi mu office amakalowa 8 o’clock kuyamba ntchito kumaliza 4 o’clock pamene kuno zomwe ndikuona ndizosiyana ndikwathu bwana akuyamba ntchito 6 o’clock kutuluka mu office mochedwa majunior atapita chikhalileni dziko lowo ndilolemela zedi chitsanzo china zintchito zake zimagwiridwa nthawi inailiyonse palibe kuti masana kapena usiku ayi sasiyanitsa koma dziko lamalawi umphawi ilitho magwiridwe ntchito aulesi nde apresident akuyankhula limbikilani ntchito wina wayamba kunyoza thus why anthu inu mumagwira ntchito zaka 20 opanda cholodzeka ayi pamene wina wangotuluka kupita kunja for 2yrs akumanga nyumba zikachita bwinonso kugula or galimoto nkhani kumakhala kuti timalimbika kumakhalanso amalawi ena olephera kumenekop kumayankhula kuti tikuvuti kufuna zaulele monga muchitilamo enanu ulesi.

 48. shame on you that is not the issue of today hardwork for nothing,where is minister of labour no salary policies in most private firms,ife ndi amene timalowa town wapansi kupita ndi kubwera with hope for change but nothing in terms of salary.ndiye mukuti chani hardwork for nothing nzosatheka

 49. Usless president ukufuna tlimbikire motani we try our best koma olo tikulimbikira dziko mavuto alitho katangale mkati. Osangakhara ngati ulibe mfundo bwampini iwe.

 50. Just help him put those missing teeth, may he can sound better! Katundu kumakwererakwererabe nde tilimbikire…tilimbikire kukasiya ndalama zochepa timapezazo mu mashop??? Fokofo

 51. At 1st I thought that u r the wright person 2 rule this country mr presedent, but I have never seen corrupted goverment like this one. Ngakhale A Malawi atalimbikira bwanji sizingaphule kanthu. Zoona aphunzitsi kudikilira ncthito mpaka 2 year? zisanachitikepo. Mudzaziona Mukadzachoka Pampando Umenewo.

 52. The only way you can free malawians from poverty is to move your damn ass from that postion,you can have 190 yrs to rule but you cant free malawi coz you know nothing you are just a puppet.

 53. Malawi wakula zulo-zulori but uli ndivito iwe Malawi kod Ku south Africa ngat sukugwira ntchito ungadye?,eni ake nthakawa mmene tikuvutikira limoz anthu oti ndiakulu akulu oti kuli kwathu kuja bwez tikut akuyenera Kumangodyelera za ana awo koma sakutopabe dairy Ku ntchito ,sopano president wayakhula kut tilimbikire ntchito kut tithane ndi vutoli inu ndiye mukutixo azafa imfa yonga ngat nkulu wake 0!! Mlungu dalitsan Malawi..

 54. We must work hard so that u and ur crew must steal our tax money.First u must act on those 7ministers implicated in that cashget document period.

 55. ,,,WE WORK HARD THAN YOU,,INFACT HARDER, THE PROBLEM Z you think you can develope this country by collecting more taxes,and revenues,, that can’t work,_and stop that sht

 56. President wopanda mano nzeru zake zinatha pamozi ndi mano zimene akuyankhula zausilu dziko lathu larowerathu pamavuto noses mthalika wausilu

 57. APM amadana ndichitukuko,anakweza mtengo wa passport,driving lieces zokolola za alimi sizikugulidwa pantengo wabwino,aziphuzitsi sakulandila.Apolice amamulanda munthu thumba lamakala lomwe wachoka nalo kutali pa kapalasa,anthu akulimbikila koma mwanyanya kutseka makomo

 58. Just create a conducive environment mainly policies for economic betterment of each and every citizen. U cant say ppl should work hard when u block all avenues for economic opportunities. Do u really think we don’t see that?

 59. Matsiku osiriza ano..koma ngati uli ndo YESU,Izi nzongomva kwa inu akudziko.poti Iwo oima mwa Yesu izi sizachilendo.Baibulo lidanenetsa za masiku Otsiliza ano.KWA ONSE OIPIDWA NDI MTSIGOLERI MUKUTAYA NTHAWI.POTI PALIBENSO NJIRA INA NGATI SIMUZINDIKIRA ZONENEDWA M’BAIBULO..IZI MZAZING’ONO NGATI MOYOWO ULIPO MUONA ZAZIKURU KUPOSA MSINKHU WABU.POPEZA VUTO SI PRESDENT MUKUMUNYOZAYO AYI,KOMA NTHAWI..PANO OLEMERA,AZINGOLEMERABE.NDIPO OSAUKA AZINGOSAUKIRABE.KHULUPILIRANI NDIPO IZI MIZIIKE MUMTIMAMOO!!!

 60. Nonse amene mukuti amalawi ndialesi muzakhumudwa 2019 titagwira ntchito yolemesa yoponya vote. Paja ife anthu osawuka ntchito yathu ndiyomweyo. Timayika komaso ndikuchosa anthu pamipando we don’t care .

 61. U say we should work hard so that we shud make u rich let me school yu AUTHER PETER MUTHARIKA Malawians are hard workig people but there are some politicians who are discouraging us by promoting corruption in this country & one of them is you. Do u remember what yu did with MSB How can people work hard u think we are your livestock so that u should earn on us mind u muzafa infa yochititsa manyazi ngati ya achimwene anu. 577b+61b=638b kwachas just imagen inu kuba ndalama zankhaninkhani ngati zimenezi ndiye inu nkumati nfwenfwenfwe za UTSIRU:):):)

 62. Kulodza chala Presdent/ Boma sikungasinthe miyoyo yathu.Palibe wabwino ingakhake m’mozi Indee palibe…Wabwino ndi m’modzi YEHOVA basi.So tikati boma ili larephera!!!!.ndiuzeni lokwaniritsalo kuti lilikuti?ndipo lizakwanitsadi zokhumba za aliyense payekha payekha?Tisanyengeke…tiyeni aliyense payekha azikonzere tsogolo lake uku tikuima pachoonadi pa pemphero ndi pembezero..Tiyeni tipemphelere dziko lathu..DZIKO LONSE LAPANSI NYIMBO NDI YOMWEYO NGAKHALE KUNO KU RSA,AMERICA,INDIA NDI ENE AMBIRI…

 63. Zoona muchepese kubelekana ngati a mwenye. Indians; are business people ,hard work pays off, imagine 8 children unemployed people

 64. kkkkkkkk hw hard shall we work or hw hard shall the leaders, AMP work i know that people in general are hard working example of famers but the government do not take part to help that what is produced in farming should have market instead vending market the same leaders influence this systeem of market through buying on cheaper price but ur word mr president is good but the problem of malawi leaders i thing there don’t have vission

 65. Ngati pali MBUZI YOLIRA kuti “MAY” mwezi wa may utadutsa nde ndiyi…Zoona kumawalavulira mate aMalwi umvekere “Work hard”..iwe tinakusankhira chani IBU haa?..zinthu zikakulephera ndibwino kutula pansi b4 eniake atsanakutulitse coz azakuchotsa pomwa ukumva kukoma!..Ukanakhala mMalawi bwenzi ukuyendetsa dziko molikonda ngati ndilako,..Amalawi kulikonse amaziwika kuti ndima “wrk harders” ndeiwe kuti udzichita kutituma zikungotsoneza kuti “U R NOT A MALAWIAN, UCHOKE!”

 66. Kkkkkkkkkkkkk Amalawi !!kuphunzira sikupita ku sukulu kokha ndikukhala ndi degree ayi koma kuziwa ntchito zamanja .monga Jonzi imafuna munthu woziwa zamanja basi thus y ku Jonz kwa munthu wochokera ku Malawi olo ali ophunzira amagwira ntchito yausiru .tiyeni tizuke kaya

 67. Wina walima fodya wake throughout the whole season, tiyeni ku msika.>> mukugula pa mtengo $50.

  Mphunzitsi akuchezera kulemba Lesson Plan, Scheming and kubangula mkalasi 1-30/31. >> inu miyezi mpaka itatu vuu malipiro osamumpatsa!!

  Wina wasenza Lichero lake la nthochi pa Nsewu kuti mwina ana akadye kunyumba,>> inu mukutuma a city athamangitse alande…Iwo nkukadya zonse za mu lichero psiti. ..

  Wina anyamule kaunjika, nsapato pa manja kunka nasasitsa malonda mma kwalalamo >> inu mukumuthamangitsa kumulanda…mwati akalowe malo ovomerezeka mu msika,, cholinga mudzitolera bwino msonkho..
  Chabwino misonkho mwatolera kwa a ma business >> inu mukuthyolera mma account anu kunja kuno anthu akugonera thobwa la deya..

  Mwana aphunzire sukulu kuchoka form 1-4 mayi akuphika kachasu ndi zitumbuwa….mwa chisomo akusankhidwa wa ku University >>> inu school fees mwakweza kopyolera muyezo!!
  Walima maganyu mnyamata kuti mwina apeze chitupa choyendera mayiko akunja (passport),,,, >>> inu nomwe mukukweza mtengo x4….
  A MALAWI ASANZE MAGAZI KUTI MUWAONE KUTI NDI OLIMBIKIRA,,,??

  COME TO SA mudzawaone omwe mukuwatcha kuti ndi awulesiwoo!!!!
  INSTEAD YOU THE GOVT MUST FIND MEASURES TO MAKE SURE THEY LOOSEN AND PAVE WAY THAT PEOPLE CAN WORK AND DO BUSINESS FREELY .AND USE THE TAX PAYERS’MONEY ACCORDINGLY…
  OTHERWISE MALAWIANS ARE HARD WORKERS NO WANDER YOUR MINISTERS BENEFITED FROM THE K577 BILLION OF THE TAX PAYERS’MONEY. …

  1. Umakwana munthu osauka ndie akuwadyesa iwowa asatipusisepo apa,kulimbika akunenako akufuna awauze anthu kt chan anthu oipa moyo,anthu okuba awa

  2. #George Daniel thanks for your reply. . .But one thing….. You have judged with no sense…I am not a teacher and after all ,this comment has not only mentioned about teachers. ..
   Read twice. .
   I hate provocative comments!

  3. fodyanso athunu.bingu adati kudzabwela mchimwene wanga ovuta kuposa ine bt kusamva.mukupatsa dziko muthu oti wazolowela kudya zofewa ku America mukuganiza ameneyo angathandize dziko? njala ameneyo akuyidziwa? mmmm athunu mudasakha molakwika.en vuto ndiloti sititha kupanga fight fr our on gud cz of fear thts wy timangwila Ntchito molimbika bt akudya thukuta lathu ndimabwana okhaokha

 68. Until when?mumangotibera tikagwira From: +260979239116
  Jesus Christ is walking from town to town, from door to door to deposit success for every one of us and to touch hearts. He just left my home and He asked me who the next person would be. I showed him your house. Receive his light and grace. But do not keep it at yor home bcoz it
  wuld be of pride…Snd this to 15 pipo nd u reciev miracle in 60min.Gud even and have a blessed nite .
  2016/07/04 09:43:44PM ntchito

 69. A malawi News 24 Mokupephani ndiposafuna kuyambana nanu. Mtundu wa amalawi ukudandaula nanu kwambiri po mamunjambula chozondotsa nkhope yamunthu ameneyu, tikufuna mudzimunjambula ataimitsa nkhope yakeyo mowongoka kuti tidzitha kumuwona bwino kupangira pamawa tingadzayambe kunamizana kuti sindiye yemwe amafuna kungulitsa dziko lanthu unja kamba kosamuwona bwino nkhope.

  1. Kkkkkk bro we are working for government only is better government must find other ways of getting money not tikapeza ka Panasonic aziti nsonkho wachani pamene ife kuno timagubuduka pa pakapinga kuti tigule Panasonic yo Nawo apolisi si kuba kwakeko this nonsense must stop

  1. Akamapereka feteleza wa ngongole amafuna kuti Boma lizipindula double than poor malawians asaaa ndani akufuna kugwirisidwa ntchito ngati kapolo

 70. It is the job of government to free people economically,if we have to do that on our own then what is your job? To tax us and continue getting fat? Hell no!!! U are elected to run the country and take care of us the citizens,otherwise if u can’t then u must vacate office because u are useless!

 71. Tizilimbikira kuti muzitibera?Mukowona ngati sitikudziwa ma game amene mukuchita?Atonkhwetonkhwe inu eti.AsaaaaaaaaaaaaaA.

 72. That’s true we must work hard yeah but we must tell him also and his cabinet not to cashgate , amalawi ndiife olimbika kwambiri kuti asamabe iwowo sitingatozedwe chonchi

 73. Mu zaka 50 takhala tikugwila ntchito mulimbika kutukula dziko lathu,inu ndi dpp yanuyi mwawononga dziko lathu, ogwira ntchito boma sakulipidwa mankhwala kulibe ulova osanena,anapwele kuphedwa ndalama za boma ma billion kubedwa,zisafike pa zimbambwe mungosiyilatu

 74. Zoonadi let’s work hard gyz mwina zopanazi zisinthe remember aliyense azadya thukuta laka……….. So chikuipa ndichani? Cozz ichichi ndichilungamo chake…

 75. I can’t understand,Pitala ukufuna kulimbikila kotan kod???Ndiwe vumbwe wewen bwanji.Don’t u kut malawians are workng tooth and nail kut ndalama zot upangile cashgate zipezeke??anthu kumagwila tchito molimba koma iwe mkumanyazitsa kut mbewu monga fodya mkumat zilibe tsogolo?mpaka 50 dolarz?uwe uli vwiii! let me tel u,amalawi ukuwanyasa.fwetseke!…

 76. I can’t understand,Pitala ukufuna kulimbikila kotan kod???Ndiwe vumbwe wewen bwanji.Don’t u kut malawians are workng tooth and nail kut ndalama zot upangile cashgate zipezeke??anthu kumagwila tchito molimba koma iwe mkumanyazitsa kut mbewu monga fodya mkumat zilibe tsogolo?mpaka 50 dolarz?uwe uli vwiii! let me tel u,amalawi ukuwanyasa.fwetseke!…

  1. Nyangu President samanena iwe wekha amanena a Malawi onse tsono iwe ukulankhula mwamwano ngati anatchula dzina lako bwanji? Malawi ili ndi anthu oposa miyanda khumi isanu ndi iwiri (17 milion) ndiye ukuganiza momwe amalankhula president anthu onse a msinkhu wogwira ntchito anali akugwira ntchito? Kodi supeza mpata womaona zikuchitika mmaofesi kuti anthu amakhala bize pa bawo,w@up, facebook monga tikuchitira iwe ndi ine ukuganiza nthawi tikutaya panopayi kumawerenga ndi kumacomenta mapost idzabwereranso??.

  2. The president is saying just as the Bible said …..work hard Malawians Vuto nlot tinazolowera kulandila ……mukudikila kuti muzidya thukuta lA wena shame………. aliyense adye thukuta lake

  3. guyz lets b serious.Kod a pitala akamat work akutanthauzanji??Shd we say and wrongly generalise kut amalawi ndi alesi? thats not true!we’r innocent hard workng prisoners in ths autocratic type of regime!Let me ask u guyz,wina wadzala mbewu zake ndi kuzisamalila bwino monga kunthila fertilizer and wina wadzala mbewu ndi kusanthla fertilizer,whc one wud hav bumper harvest??This guestion wud direct us to thnk wizely lukng at strategez that de gvt shd put forward to malawians free from problemz and also whc may help us to erase provacative speechz stickng in our skul!Wawo,luku now,a bag of fertilizer selling at aproxmatly 4 dollas ofwhc 3quarterz of malawian can’t aford.Ndye mawu akut work hard angagwile mepa?Oh we need more changes…..

 77. Kikikikikikikoki independent doesnot money come down in the shoulder like heaven it means hard work kikikikik mkonono basi amalawi ntchito miseche basi

 78. Chilungamo chimapweteka. Anthu onse amene akumanena kuti tikuvutika ndi omwe sagwira ntchito. Iwo amalephera even kulima. Boma la Mutharika ndilolimbikitsa kuzidalira. Kod amalawi mukufuna a presdent azikugulirani chakudya? Kodi a president azithandiza ana anu ochulukawo? Ana mpaka 7? Ino sinthawi yopuma…ngati mukufuna kupuma musadandaule muzapuma mukazafa. Munthu nkhuku,mbuzi komanso alinazo koma akuti sangalime chifukwa alibe fertilizer…..think big and wise. Yense amene salimbikira yekha akuvutikadi

  1. Mukunama inuyo nonse ngati pali dziko likuchititsa manyaz ndiye Malawi for example Ku South Africa anthu samalima but samadya n dziko la south Africa limalipira anthu awo every month ndi osagwira ntchito yemwe ndiye mudziti work hard hahaha m’malawi ndi Munthu modzi yemwe amagwira ntchito yolemetsa but Boma lathu dyera

  2. Ishmael tell those blind fools,,,they comment as f they stay abroad,seeing things from a far,Galu wanuyu mukuti Peter zamukanika,blv u me,zukuendelani thats simumva nawo kuwawa,How do u define “Hardwork”mufuna aziphuzinsi amene sakulipidwa azikalima afta knocking off?then why training them 2bcme teachers instead of giving subsidised farm inputs?Fools,52 years for nothing

  3. a ishmayele a a esther…inuyo moti mwamuoma peter kufowoka chifukwa sakukulipilani ndalama za ulele??mumafuna muzikhala kunyumba kenako month end mungowona text pafon kuti zalowa basukatape??mukuganiza ngati mwanatu inuyo….and ur not even ashamed.comparing the 2 countries MW and SA..had it been that in the past you were receiving zaulelezo nde zasiyika after kulowa kwa peter tikanati muli ndi mzeru mukunena zoona..koma no..pitani mukakule kaye simukudziwa chomwe mukunena…mukakhala apa next thing mutiuza malawi is weak why does america have nuclear weapons yet we dont have

  4. George mutu wako wamva ngati ali fodya ukusutayo uchepetse. A malawi akugwira ntchito ngati akapolo kulimbika thukuta ndi mkamwa momwe koma akukolola ndi mbava zanu zili ku bomako. Kumapweteka ndi ma surtax pamene iwo ndi duty free, alimi fodya kuwapangila mtengo, K577bn, k91bn, k13bn, k1.7bn ndi zina zotero akugawana anthu awiri penaso mmodzi. Hw can poor citizen get improve while greedy and selfish leaders enrich themselves. While poor citizen are working tooth and nail. Guard your pitlatrine before God ndi mkwiyo wa Malawi usanakupeze. Uzafa imfa yowawa.

  5. Hahaha debate ilibho iyi guyz kkkk hwever,tivomereze atsogoleri amaba komaso sizowona kuti pachaka kulima kamodzi then kumati u r ahardworker aaaah ndakana coz ndalama zimatha kumadikila season ina,muzawapeze apostoli akuwuzeni za ulimi coz iwo sapumatu,komaso musayelekeze dziko lakunja ndi lathu kumeneko kuli migodi yomwe amadalira pamene kuno kulibe!!!!!

  6. @Kareem. Iwe ndi opepera. Go in Limbe, Blantyre, Zomba, Mzuzu just to mention a few….ndiye ukawerenge anthu amene akungoyendayenda m’malo mokalima. Now, anthu amenewo azilipilidwa ndi boma? Kodi boma liziwagulira chakudya. Boma peter likukhaulitsa ndipo linyetsa anthu a ulusi ngat inu. Ana okulira pa mthunzi ngat nkhumba muli m’madzi mpaka mukazayamba kugwira ntchito muzaleka kulira kwanu ngati ana choncho. Ine ndiye zikuyenda coz i stopped blaming government. Paja ku malawi kumapezekanso ana a Masiye oti they are above 20 years. Kkkkkkk usova koma ukamaganiza zifanifani ndi mayiko ena ukuchedwa

  7. Now according to ur comments, u are defining hardworking as kulima. This is so pathetic. We cannot all be farmers people. There are so many industries to explore, not only farming. Everyone can be a hard worker in their industry. But again all that effort will be wasted if government policies are not conducive to these hardworking spirits. So hardworking is not the key factor in the totality. If government can be at ease to embezzle 577bn, the same money Malawians are working hard to pay tax for, whom do u blame? The people are not lazy, the system is.

  8. Ngati Ndiwe Mulomwe Uyenela Kuva Bwino Ndi Boma La Pitala, Koma udakakhala Wazelu Udakawona Momwe Anthu Akuvutikila Chifukwa Cha Atsogoleli Opusa.

  9. You can not compare South Africa ndimalawi,and for our information currently kulibe dziko lomwe siliri pa financial crisis, South Africa mukumunenayu nayese akulira from number 1 in Africa to 3, and on 1 July fuel,water,,electricity and groceries zakwera mitengo… Talking of Zimbabwe,Angola and others nawonso akulira koma vuto we malawians ambiri omwe amagwira ntchito amadalira salary yokha insteady of investing themselves mu business,farming and likes…. This is not a time of pointing finger someone kuti ndiyemwe akubweretsa mavuto but analosera karekare aneneri zamasiku otsiriza!!!

  10. Iwe PITALA ukusuta etiiiii what do u mean if u r saying that we must workhard? Mwina unayamba wapelekelapo ndalama kapena chakudya chaulele (manna) mumakomomo araaaah zachamba etiii anthu akumavutika kulima kuyamba kalekale kuti apeze chakudya ndi ndalama iwe uzingolarika malawians must workhard. Feteleza nayoso adulanso kuti poor malawians can not afford to buy nde ukuti azikathira zala zakozo mumbewu ngati nthaka. Preaching nosense mukati anthu azitenga ngongole boma kufuna kupindula double than poor malawians nde ukufuna azikhala akapolo ako

  11. ndikugwilizananu inu alomwe vuto sipitila nde ndi khulupililanso mukuyimba nyimbo yomweyo kuti vuto thawi ija sanali a JB koma amalawi ulesi ( nde kusowa kwa mnzelu kwa alomwe ku maoneka pa ma coment awo)

  12. kkkkkkk koma #pitala akuti hardwork cholinga chongofuna kutiponderezabe asaaaa broz ndi teacher now three months without salary ndiye pa khalanso za hardwork pamenepo kkkkkk a M’phudzitsi akungogona m’ma office mwawo pomwe iweyo pitala ukungophwanya misonkho ya anthu osauka kale…..Ndani yemwe angati kumalawi anthu samapanga business azimai a tomato Ali mu msikamo nanga azibambo a Msomba ndiye mwafunse kuti ticket yogulitsira malonda ili pa bwanji n chonsecho ndi choti business yake akuyenera achotsepo fees ya mafana ake agulepo chimanga… Plz guix ndi bwino kuganiza mozama not kumangokuwapo zili zonse ndiye wina kumalawi kulibe migodi Lake Malawi. Malombe. Chirwa Chikukuto. Chia. + kayerekera zikuimira migodi but vuto ndi awo Ali kutsogoloko coz akufuna zonse zikhala zao

  13. Muzafa manja ali pachinena ngati simuyamba kupanga zanu zopezera nalama. Kulilira zaulele basi. Fuel watani? Ndi angati amene ali ndi magalimoto? Usanamizidwe mphwanga #Kareem China inatukuka coz of ulimi. RSA kuli ma farm ochuluka. What matters is that what kind of farming are you involved in basi. Ana olimbikirafe tili pheee kuphaka life. Think big think wise

  14. Akulu ngati anthu akuvutika siulesi,koma ndi anthu angati akugwira ntchito yolandira pakutha kwamwezi? Ndi anthu angati amamwa tea each and every morning? Ndiye ngati inu mukugwira ntchito ndi mwayi wanu ochokera kwa Mulungu.Anthu ena ndiwophunzira kwambiri koms ntchito sakuyipeza,ndiye inu mukuti ulesi!! Samalani ponena ntchito imatha any time.

  15. Vuto lomwe ndalipeza ndi kusankhana mitundu a Malawi ……mukulimbana ndiye alomwe za chan zimenezo? Mufune musafune work hard apo biiiiii ng’oooooo kagulen ma kakuleta muzisova

  1. Thats what am talking about nagative minds abusa akamalimbikitsa kuti tizipemphere kapena kupita ku church zimatanthauza kuti sudziwa kutsutsa zoyenera kutsutsa

 79. he must also work hard in 577 billion, Killing pipo like Issa Njaunji, 20 July killing, Robert Chasowa

 80. In what way….cholinga adzidula misonkho yochuluka..kkkkk!!koma abale…sindikumvetsa…mutu wanga sukugwira..

 81. hmmmm,one of waste goverments in decades.Malawias are arleady hard working pple bt the problem is corruption in your gvt,this hs resulted to low or no development in many areas.

 82. Asanabadwe, Wabadwa, wakhala President, amalawi adali akudzilimbikira mwa iwo wokha ndipo palibe chomwe mtundu wa amalawi sudziwa kufunika kwakuzipangira wokha zinthu pa umoyo wawo.

 83. Govt must creat a conducive environment for hard work. Eg civil servants going two years without any salary increment is saying the opposite. Improve working conditions before making a lot of demands. In simple terms, your demands must be proportional to working conditions. Otherwise do not expect a 1980’s hilux to outclass a D4D

  1. Bodza galu iwe,…ukufuna anthu azigwira ntchto chotani… Venezuela ili pa mavuti kamba ka poor leadership sikuti anthu sakulimbikira.. Amene angatukure dziko ndi boma akabweretsa ndondomeko za bwino…. Tikufuna dziko lisinthe ma service delivery azioneka mmuz umu… Zambri zili kuno zinamangidwa ndi MCP those days.. Osangoikira kumbuyo galu uyu palibe akupangapo. Ngati zamuvuta asiye basi ena ayeseko.

 84. Bravo Your Excellency,Mr President Sir!but why these city officials are denying us running small scale business?kodi geni yamu lichero mpaka tizikayala ku flea market?kulimbikira timayesesa koma boma lomwelinso limatibwezera m’mbuyo?

 85. How hard Mr Pulesidenti? Tikhale akapolo aku#NDATA? 4 your profit. We have done our part. As for Goverment its yo turn now to meet us half way. When voting time comes u must also work hard.

 86. Oh yes mr presedent you are saying the trueth to all of us well done,you have done your part its now to us to use it.you are wise mr presedent even the bible says saw amen.

Comments are closed.