New political party in the offing: Gospel Kazako, Humphrey Mvula, Mathews Chikaonda linked to It

Advertisement
Gospel Kazako

Information that Malawi24 has gotten hold of indicates that there is about to be registered a new party in Malawi.

Gospel Kazako
Gospel Kazako

According to some sources, the new party will be called United Transformation Party (UTP) and it brings together Malawi’s business captains and other old guards in politics.

Unverified information indicates that some names in Malawi have been named to be linked to the party.

A source said Zodiak Broadcasting Station founder Gospel Kazako is among the leaders of the party. Malawi24 is yet to confirm with him if indeed it is true that he is a part to the new party.

It has also been alleged that veteran politician Humphrey Mvula and business captain Matthews Chikaonda will be part to the Political Party.

The unconfirmed reports have further hinted that Newton Kambala will be the interim President of the party.

Advertisement

378 Comments

 1. One thing I know is that our country has so many planners,commentators,critics but few implementers.all our leaders are like that no time to play tangible role but just blaming each other. In Parliament you hear Mps mentioning hunger to gvt &us but if you ask them what they are doing in their areas,to their relatives,zero. The only politian who walks the talk study Felix Jumbe. He is a farmer,gives government constructive criticism and practical advice. To help this country, doesn’t need one to be apolitian but just start doing something

 2. Kazako remember those days at makheta. Now God has put you in a position to be thankful now u want political? Your days are numbered thus a bad idea infact am not surprised becouse u are against the ruling party

 3. sichawo chipani anyamata amenewa. Man of god osati GOD uyu ndamene watuma. uja mmati ndani watchuka ng@ bonyayu!!! Gospel will end lyk Osaweta.

 4. The same people who betrayed malawians now they are changing political parties just to fool us, wake up guys lets not tolerate nonses new blood must rule the country now we are tired of old thieves names.

  1. Mr. William Banda, what do you mean the same people who betrayed Malawians… Lets be honest here and realistic. There’s nothing wrong here with these people. Where is new blood? And what experience do these so called new blood have?

 5. bwana kazako tiuzeni zoona timasuleni kodi kapena tkhulupilire akunena hon ken msondazo? inenso ndikudabwa kuchulidwa kwa dzina lanu, musayelekeze kuyamba ndale makamaka pamene pali mvula ndi chikaonda mubesa bwana. Atolankhani athu muno mu malawi ndiomvetsa chisoni amamulemba munthu nkhani asanamufunse kuti manyuzi awo agudwe, their have never been professional and ethical, no wonder goverment is afraid to bring t parliament access to information bill to be passed, akuziwa atolankhani athu ndi achamba okonda ndalama aboza, shame on you!

 6. GOSPEL KAZAKO?????
  Whoever gave you GOSPEL KAZAKO’S name did not do you justice, and did not tell you the truth; Gospel Kazako is neither one of the leaders in that party nor does he belong to any political party Gospel Kazako has no ambitions of joining any political party or to start one, atleast for now. Please Malawi media houses confirm with concerned personalities on such serious matters of national concern before writingotherwise publishing names of high profile people to attract reader’s attention is a very serious offence, UNETHICAL and CHEAP PUBLICITY!

 7. Gospel kazako, u inspire me most of the tym & I personally satisfied with the good work u r doing @ Zbs. I’m afraid kuti mukayamba ndale ndiye kuti zodiak wl no longer be able educate, entertain & inform us as u r best doing currently. Pliz!!! think twice b4 u come to regret bcoz regrets have no remedy.

 8. Lets think big malawians ngt zipani zinaz zikulephhera penapake bwanj osamangozithandidza nzeru kt zkhonze mfundo zina rather than kupanga chipani china?

 9. Kkkkkkkkkkkk politics can be the badest decision that u have ever made in your life Mr kazako kunali achina Lutepo pano ali kutiko ndale zapa Malawi sizinthu tsegulani ina radio station not this politics thing mungazavale nazo masamba abwana

 10. Kazako asakupusise chikaonda ndi girlfriend wake mvula ,cholinga chao akufuna zodiyaki iziwapangila kampeni mwaulele. Ndipo zodiyaki ndi imene izalile ataluza business komanso ndalama . Choti muziwe ndi choti anthu sangasiye zipani zao azikusatilani inu . Mulomwe ndi njomba sangakuvoteleni inu ,mwina anthu akumpoto poti kumpoto kulibe chipani .

 11. Kkkkkk Koma ku Malawi mmmm nzosekesa komanso kumvesa chisoni, Bwana Gospel Ineyo ndimmodzi mwana anthu amene amakunyadilani maka pachikhalidwe chanu chofuna kuziwisa mtundu wa Amalawi zoona zokha zokha kuzela pa Zbs ndipo anthu ambiri amayamika pazomwe mudapanga kale , koma ngati zili zoona zomwe zikumvekazi kuti mukufuna kuyamba ndale mmmm Abwana ngati mumamvako maganizo anthu ena mogonja ndimodzichipesa ineyo ndikuti ayi musayalekeze ndale ndiukapolo ndipo mtendere mulibemo , komanso za enawa Amvulawa aaah Ndukuuzani mmalo mopita chitsogolo ndithu muyamba kutsika Asileni omwe awa adazolowela kutukwanidwawa inuyo ayi ndinu munthu waulemu wanu.

 12. Is this the reason why he has been using zbs to criticise DPP and the president,as for mvula a thief at stage coach his sons are thieves akakhala achikaonda press cooperation ayi kama

 13. Mr Gospel Kazako think twice before joining politics remember politics is a dirty game,and me myself i don’t trust politicians they after money not for helping poorest people.i been giving you a huge respect Mr Gospel since you start your own Radio called Zodiac zikachitika mumwera kwa ife,if indeed you preparing to start your own party that’s end your career my man.ndalama munapanga kale bwana kodi chimene mukufuna chenicheni ndi chani ? Kufuna kuchuka ? Kuchuka ndinu ochuka kale no doubt about that. Koma zandale tangozisiyani man kumbukilani kuti ndale ndi bodza.

 14. as far as i know chikaonda and mvula, there will be no transformation at all. posibly kazako may not be fooled by these men regretion time always painful. he has a good living per his profile such none of his best shall back him here

 15. Khutitsidwan Ndi Zomwe Mulinazo A Gospel.Know That Good Things Never End N May Be You See That Zodiak Always Get Number 1 So You Are Thinking That U Will Win.Mmmmmmm Beware

 16. Khutitsidwan Ndi Zomwe Mulinazo A Gospel.Know That Good Things Never End N May Be You See That Zodiak Always Get Number 1 So You Are Thinking That U Will Win.Mmmmmmm Beware

 17. We have a lot of parties in Malawi, do you think you have good ideas to convince Malawians? why cant you join these other parties and share your manifestos? the country is too small to have many parties

 18. pitilizani ndi aganizo munthu asakuletseni aliyese azasankha chomwe chili chabwino kwayeyo tiyeninazoni palibe munthu yemwe anabadwa ali wandale koma anachita kuyamba inuso muzafika pawochuka ndi ndale ngati enawo

 19. pitilizani ndi aganizo munthu asakuletseni aliyese azasankha chomwe chili chabwino kwayeyo tiyeninazoni palibe munthu yemwe anabadwa ali wandale koma anachita kuyamba inuso muzafika pawochuka ndi ndale ngati enawo

 20. Well done Kazako. Achewa analamila, a yao analamula, alhomwe ndi awa likuwakanika dziko. 2019 ndi nthawi ya Asena nao ayeseko asaaah. Chigawo chonse chakumwera chili pa mbuyo pako Kazako. Go Kazako go. Usamvere malangizo enawo akubwera ndinjiru. Uli ndi maso mphenya osintha zinthu mdziko muno. We will vote for you

 21. Politicts is the act of devil,en all who are in politics are ruled by devil.remenber politics started in heaven wt devil as he was tried to against God.everyone doing politict is belongs belongs to satanism.no wonder that everyone want to do politics pamene antchito aMulungu akuchepa.let him start this coz you dont know where he took his money maybe is fr6 the devil,so let the work of the devil be his witness.instead of going out and help the needy he want to waste his money for nothing shame on him.country is busy borrowing the money yet someone is planning for politics shame on you kazako!!

 22. A Mvulaso bola a Chikawonda tazingopangani zimene mkupanga ZBS yili bwino abwana Mvulaso tazolowera momwe aliri akupanga ma bisness agho.

 23. Go ahead and reshape malawi political outlook,tired of these daydreaming so_called leaders who go to work forgetting that they r in night attire,I support u

 24. Ganizo Labwino Kwambiri Kwa Iwe Gospel. Ungotichotserako Anzakowo Mkupeza Anthu Ena Azeru.No Backward Move Plz!!!!. 2019 Ndi Gospel…UTP…Gospel…UTP

 25. Gud mr kazako u seem to hv no way of giving free money to pipo but for something to request. I hope u r old enough to know which is gud,no one can decieve u about maalawian politics for u hv bn here since ur childhood. here we are failures we want gud position in the parties hence all parties are already occupied. ali dere nkulinga utayenda naye. NAZONI MADALA

 26. No nonono NO Gospel please,,,,,,,, timakukonda with your zodiac,,,,,, I wish you to die a hero as u are than a politician,,,,,,, don’t end like that gospel please

 27. MCP, DPP, PP & UDF are enough political partise. If they have different agendas they must join these partise and compete on conventional not establishing partise like shops. You will end having avote in one constuency

 28. A Kazako dziko la lankhula mokumverani chisoni- pa Chitumbuka pali mau awa- Kamuzganga ntha ndi fwiti, fwiti ndi tilinganenge. Anthuwo amene akuti zitayeni sakukufunirani zoipa koma zabwino.

 29. I tnk if uhav reachd up to ds extent to venchr into politics…..u hav seen wth ur naked eyes that dzko silikuenda bwino..i lyk ur decition bwana gospel…be proud wen we r goin foloward…

 30. A Small country with so many parties.It would be wise if these men just joined to an already existing party lather than forming a new party

 31. This is useless if true Malawi is the same as a diatrict, but over 20 useless parties with no future!There must be a law now which must allow a maximum number of political parties to 3 only others with no mp’s be now de-registered,otherwise Malawi has no future.

 32. This is useless if true Malawi is the same as a diatrict, but over 20 useless parties with no future!There must be a law now which must allow a maximum number of political parties to 3 only others with no mp’s be now de-registered,otherwise Malawi has no future.

 33. Palibe chabwino ndi zipanizi bola akadayambitsa mpingo koma zogofuna kuzilemeretsa rise up guys enawa angofuna kutibera kaya kkkkkkkkkkkkkkkkkk wabwino palibe tilimbike kupephera osati kukhazika pa ndale nothing to involve in politics let them anazolowera jiats in ubava take care asatipusitse let’s have no multpart any more

 34. Palibe chabwino ndi zipanizi bola akadayambitsa mpingo koma zogofuna kuzilemeretsa rise up guys enawa angofuna kutibera kaya kkkkkkkkkkkkkkkkkk wabwino palibe tilimbike kupephera osati kukhazika pa ndale nothing to involve in politics let them anazolowera jiats in ubava take care asatipusitse let’s have no multpart any more

 35. Kutaya nthawi, new comers bcareful old guards wants to turnish ur good reputation, kazako b wise dont b used, but can u manage to oust the election riging masters?

 36. zipani zonsezi palibe chabwino choti mungathandizire kupititsa patsogolo kkkkkkkkkk do you think can convience us mpaka kudzakuvoterani 2019,im not sure,mr kazako,better concentrate on your bznez,timakulemekezani bwana

 37. Amvulawo angofuna akuthandizireni kugwetsa Zodiak,timakudziwani bwino chonde ganizani mofatsa,enawo ali ndi mbiri zoipa,anthu ayenda ndi Muluzi siabwino ai konse,he was involved pa nkhani za Matafale anali kutsogolo amenewo ndi oooiiiiipaaaa ,think twice ,musaipise dzina lanu,mundale ndibodza basi,ena ndi omwewa zikuwakanikawa anawinira dzina la Mchimwene

 38. Inu mufuna ndani yemwe ayambitse chpanichake. Ambirinu ndi akansate sate. At least Kazako.
  Simwana.
  Anaputaku xool.
  Alindi ndalama.
  Sanakhalekunja nalemeraa.
  Asiyeni apange zomwe angakwanitse.

 39. Kazako for politics? I for one can’t believe it coz he has an enormous reputation to protect as far as Malawi’s politics is concerned.

 40. Kazako ukusochera poyerayera ndithu .usamvere makawalawo what dem do only make tingz bad ,ambiri akuudzani kale warning so choice is urs but uzalira madzi atafika mukhosi you’re giving chance devil to sign you up tink twice MR KAZAKO

 41. thus what Malawiana are known for akalemera, shame. lets develop our country first anthu azakuikani pa udindo opanda vote

 42. Mmmm akazako please amvulawo ndiwokanika kale asakupusiseni mu wonongapo zomwe mlungu anakupasanitu zodiack sizakufunaniso mkazalephela kumene mkufuna kulowakotu paja amati fodya ndiwapa mphuno wapachala ndiwamphepo mzaziwona nkasa adanena kale kuti ndale ndikanyama koyipa

 43. A Chikaonda Ngat Alephela Kuyang’anira Press Coorperation Mpaka Ma Branch Ena Ngat PTC Inatsekedwa Nde Dziko La Over 17 Million People Angakwanitse?Lets Follow!!

 44. Chonena ife tilibe bt the only thing I dnt understand abt all dis is,,hv u ever thing abt poor malawians who always dance up and down voting fr u pple fr nothing,Kazako I got no judgment fr bt think twice before musanabwere poyela

 45. Mukulangiza KAZAKO inu ndi anthu akaduka kwambiri chanunji pa ZBS kuli MARK KATSONGA ma bus awo mukukwerao musamuopsyeze munthu bola ngati ali ndi mfundo anthu azamvotera panonso tikufuna footballer ayambitse chake osachita kaduka ai a Malawi munazolowera ndale zamitundu ndi zigawo ALHOMWE PARTY ASENA FRONT PARTY AYAO KWENDE PARTY ACHIPETA PARTY ATUMBUKA PARTY APHOKA PARTY ANKHONDE UMOZA PARTY ANGONI WAWA PARTY Za nje zopanda mutu KAZAKO MVULA CHIKAONDA go go go ahead masamvere zitsiruzi every citizen here in malawi has the right to be a president.

 46. akalira nyanga yasatsi mulekele imfotere m’manja akazako atidye nawo mwajoina nawowo muona pelekera ngati zakuchulukirani

 47. Politics ndimomwe muli shuga okwanira pa malawi wina afune asafune if u pass pama elections iwe basi zako zayeyera thats y pama compain anthu amalolera kugawa ndalama ndipo akawina zonse amamwaza zimabwelera within one month,ndie pamalawitu pamenepo

 48. Zopusaa. Zodiak radio, Zodiak Battery Zodiak Award pano ukufunaso Ukhale mu UTP. MAU AMULUNGu amalesa kuzikundikila chuma nde kazako ndi anzako Muziona mayhero ake ngati simusitha

 49. Gospel stay away from those crokes . Nobody can trust those monkeys. Gospel why don’t u join Enock chihana or Mark kamsonga .

 50. amalawi akapeza kandalama basi ayambe chipani how many political paties do we need to hav more over we dont need that we need a change in malawi we need better malawi . 20 years to come everyone will establish his own political party poor malawi with hundred parties go to rich countries they hav 2 political parties. chikuvuta ndi dyera alowemo atibele monga akuchita enawa, sizitengera kut munabusapo mbuz ndi nkhumba basi mukatsogolele anthu ena ndi awa tikuwaona zuwakanikawa a leader is born and not made

 51. Mantha basi ndalamazo ndizawo~musiyeni munthu apange mmene akuziwila~musiyeni munthu mantha~Diesel,Petrol,Palibe:Dpp:Pitilizani akazako mwaona nokha kuti alinanu mantha azipani zinazi.

 52. Enanu mukutaya nthawi m’malo moti muziika nyimbo zagaaradi tizivina apa mwayamba ndale muisova .Apeter munthalika owinawana 2019.

 53. This is DPP team B to destabalise MCP koma mulimbe zidakankhara bwino kungojoina zipani zilipo kale becz there is nothing new this party will offer!

 54. Ana mwachepa inu mukusewera ndi mimbulu Humphreys Mvula ndi Mathews Chikaonda mbola zachabechabe mafile awo ali bii mbava zotheratu tiyenazoni uzilira pwiyoo maka iwe Gospel Kazako uli ndi mdede kobasi.

 55. A word to Gospel, i know u are a good salesman, u know how to advertise low quality products to my fellow poor malawians thru radio adverts and it works. Then u think it’s easy to advertise and sell a political party? Think twice.

 56. Dats The Earth Ukampempha Mun2 100 Akatulutsa Chi Mpukutu Umasintha Nkufuna 200 Ameneyo Ndiye Mun2 Sakhutira Ndi Chomwe Ali Nacho.

 57. USA, Britain, Canada, and most countries have two political parties contesting in an election. I don’t mean to insinuate that its a perfect system. Here in Malawi, since the adoption of multiparty democracy in 1994, we have seen a floodgate of political parties on the scene. Legally, it is a political right for someone or a group of people to form or join a political party. Malawians are entitled to this political Right. HOWEVER, the floodgate of political parties is NOT helping matters. At this Juncture, let me invite my fellow citizens to do a sole searching; cant we find a way to DETERMINE THE NUMBER OF POLITICAL PARTIES IN THE COUNTRY? If i were somebody with a voice, I would have suggested that we should hold a REFERENDUM on this point; perhaps we should limit the number of political parties in Malawi to 2. Those interested in the presidency should battle it out during primaries. ( That’s my opinion, the voiceless citizen).

 58. Tizipani ngati timeneti nditija timafuna kuti zisankho ziziwelengedwa kawili zija,,, kungofuna kutipasa busy ovotafe

 59. Moti Zingayambe Kuiwalika Uja Unkazembera Apa Eti? Unkangotola Zofowoka Za Ma President Nkumaika Pa Radio Pakopo Wat Nanenso Ndidzakha President Ooooo Akazako Uku Ndie Kupempha Umphawi Bwezan Maganizo Opusao Pangan Busines Mudasolola Ku Ti Akaluluto

 60. Our nation is so small mpaka 13 political parties Mr Kazako ndalama ngati zachuluka tiuzeni tikuthandizeni kuphaka life zandalezi simuphurapo bola kuphakira moyo anzanuwo angokupusitsani bola msagulitse ZBS muononga tsogolo la ana

 61. Go on, Viva . This is true. One member of Parliament from Machinga posted on his wall about this new Party last month. We hv said it before kuti This Gospel thing is hiding behind speaking for the poor. The truth is, he wish he could be voted president of Malawi. Yes it is everyones ambition but hiding behind the poor, syphoning donor money thru Radio station, Telling donors to stop funding malawi so that u get news at zodiac that exposes the poor status of this country etc, etc,, Today he has come openely. Dont criticise him… Nomwenu mumaombera mmanja Zodiac ikunyoza boma.. lero mukumudzudzula kkkkk mwamupangira ndalama lero akuyambitsa chipani. Ku MRA misonkho mpaka Billions not paid by his zodiac but shamelessy nomwenu u backed him… Now let me tell u who are behind New Transformation Party…..; UDF mps, PP mps & MCP mps. Now why UDF mps, its because the UDF_DPP alliance means in 2019 UDF goes to the polls wothout participating onthe presidential race… PP, everyone knows its DEAD, ~MCP, these guys knows that It shall be amiracle to Outsit DPP thru MCP & Chakwera because its too regional and tribal unlike DPP its all over Malawi.. So this is an attempt to hv anew party and attract new votes.. kkkkkk … Mwalemba mmadzi guys.. One free Advise to u Gospel; No matter how rich u are but game yochotsera ndi yovuta… uzatha iwe….. Gvt will squeez u @ once even mabungwe azayamba kuopa kulengezedzetsa malonda ku station yako powopa kuoneka odana ndi Boma… koma iwe iwetu iweeeee…. Wakulodza ndi mwana ndithu…. Ican see DPP sweeping the divided opposition kkkkkkkkkkkkkkkk.

  1. DON’T READ THIS! Just thinking aloud, are you a patriot? (Written after checking your profile. No comment expected).

 62. Kaya amwene ndi amalawi amenewo, ufulu wawo, anthu adye nawo mawini aku zodiak, shire bus services ndi za ndaba ndekha ku udf. Tiwakwera si bola kutipatsa basi

 63. mau amozi kwa gospel kazako usandipatse BP ayi zikhala mene umakhalira basi ndipo ndisamve zoipa zo kuti walowa ndale za malawi ndi satanism be carefull

 64. Why do you just restructure parties parties like Aford and PP than starting from the scrutch.

 65. it could have been good decision if you could choose to support government rather than to start new party…what we need is not party bt to support government to develop this country…oh plz mr kazako turn your tune coz we honor you.

 66. Ngati nkhani ndiyoona, ndiye ine ndikuti pepani a Kazako inu tsogolo lanu munakonza kale, zanu zinayera kale, zandale zisiyeni, imeneyo simbali yanu, muja munachitira zaka zapitazo basi zinkwana, ndale zalerozi ai, pepani ndivereni asiyeni enawo achite, mudetsa dzina lanu

 67. Ngati muli ndi ndalama zochuluka mangani nyumba yaitali kwambiri yofanana ndi ya Kenya kapena ija ili mu Joberg ndipo mukhoza nso kulimitsa mseu ndikumanga Toll gate mukhoza kutchuka dziko lonse

 68. A word is enough for the wise. Malawi’s political system very dirty cheap, hence it’s got it’s own translation ( Ndale).

  Mr Kadzako must think twice.

 69. bambo Kazako mungothandiza chipani chimene chimene chili ndi maplan otukula kapena kukomera munthu wakumudzi osati ngati chili m,bomachi ichi ndi chokomera amwenye ma Chinese ndi anthu aku Burundi ndi Nigeria koma munthu wamMalawi yekhayekha ali wandalama kale zikumuyendera ndipo inu ndalama zanuzo thandizani MCP ndiye chipani chomwe chili ndi anthu ochuluka ndipo musakwanilitse lemba lakuti adzakhala odzikonda okha anthu ,chonde ngati ndi zoona pangani

 70. That is Things Fall Apart for some individuals in that forums. Let us wait and see.Chipanicho chikakhazikitsidwa mutiuze tijoine mwakathithi

 71. A kazako munamvapo mbiri ya makhumula mwini wake wama bus a #yanuyanu kuti company imene ija idzitha ndale sichithu chamasewela bwino musawamvele amvulawo ali ndimilandu yambirimbiri angofuna akuyipisileni mbiri bwino

 72. Clear signs of brain exaustion. Malawi has millions of unemployed youths who don’t even dream of working for a salary anytime soon and yet a few more heads come together to form yet another useless Political Party. Investments are left to foreign Investors & those we call Malawians of Asian origin as if Asia has Asians of Malawian origin. We hear of Malawians trafficked & stuck in Kuwait cos Malawi has nothing to offer apart from politics, what a shame. We import almost every thing & now even our staple grain though with all the land & waters. SHAME!

 73. Akazako timakulemekeza potibweretsera zodiak,koma uku mwalowaku mukuzichotsa ulemu wanu simudziwa kundale kuli bodza.kuba,kupha komanso dyera ndiye mwavomereza zonsenzi,ulendo okagwesa zodiak tsopano

 74. watsalaso wa radio ina ija muntenge akhale cmpaign director kweni kweni radio ujeni phokoso komaso mwano mungowapatsa aneneri achipani axisintha okha.

 75. Is this some kind of joke? Or a Modula’s operandi for self enrichment?
  Of all the 50+ political parties there, how different will this party be from the rest? Why can’t all the opposition parties unite and take on Mutharika then?
  Malawi does not need a new party to bring about transformation!

 76. I love you Baba Gospel. I respect you Baba Gospel. I salute you Baba Gospel. Many love, respect and salute you Baba Gospel. Once you join politics, you will become an enemy of many. You’re rich today but once you join politcs, ACB will be on you. Please Baba Gospel think twice.

 77. Koma anthu inu mukufuna chani?Akazako Muzalila kutsogolo mukutseka Zodiak ndithu Mulungu Osamamuyesa,anakudalisani kale Ndale mukuyambazo muwona zosatila zake. Ena mwa anthu mulinawowo ndi Osokoneza analephera kale kwina,Muwononga zinthu zopezapeza ndithu.

 78. koma ngati zili zoona ndiye kuti kazako kutha ngati makatani ndikumeneku.aMathews anakanika ali ku udf,a Mvula ndimagulu osokoneza…kazako kuononga mbiri yako yabwino yosatengela mbali pa #ZODIAK.

 79. ka Malawi kake komweka zipani Mbweee ! dyeratu linali ili ; U S A 50states zipani ziwiri basi Yea neh; ask Y; ans : this is Africa

 80. Formulating a party nowadays is busines….The existenc of several parties in Malawi,the aim behind is business..They use to request money from donors which much of t is 4 personal benefit wit very little 4 the party….Its just “business-aimed ” nt politically aimed….

 81. Panopa dziko lonse la Malawi likumakhala modandaula chifukwa cha azitsogoleri andale kuba ndi kuzuza wanthu . Ndiye wina akamati akuyamba ndale tikumaona ngati chiwelengero cha otizuza chakwera .

 82. E tu Kazako! You will be a disappointment. Leave politics. U are doing good at ZBS and people love you for it. You want to leave people?

 83. One word for you guys, don’t listen to spectators who have never accomplished anything in their lives. People who are outside the box always try to look wise and look for mistakes because they never act and therefore immune to criticism. Don’t listen to them, follow your dreams as long as they are good for the nation. If there is someone to listen to then it has to be a person who is already in the game not everybody. Who knows, may be they might contribute to the socioeconomic status of our country.

 84. One thing i dont like about our country is that when everybody feels has got money and a little famous they join politics. When one retires from work, instead of venturing into entrepreneurship and help reduce unemployment and thereby improve the national GDP, feels a best place to go is politics. Whenever anyone starts a business, for the laziness of strategizing on how to make their businesses thrive, they join politics to win all contrants easily, thereby killing and suffocating businesses of non-politicians. If only politicians stop dominating govt contracts i can take mw serious in its efforts to promote SMEs and only then can i have hope in our economy of doing better some day.

  1. More than 65% of all supplies from our local businesses go to govt (to all ministries whether broke or not) because if otherwise or constructions, building etc would have stopped. About exports, then i think is outside the context of my comment and a new topic altogether.

 85. Please dont judge,leave Kazako and his friends to do what they wish,if they are to waste money,let them its theirs.You cant say its the end of Kazako,what do you know about Kazako?Watch your comments

 86. MALAWI FLAMES NATIONAL TEAM MUST CHANGE ITS NAME TO ASHES AND RELOCATE TO A NEW COUNTRY WEST OF ANGOLA! THE SMOKE FROM FLAMES HAS POLLUTED ZAMBIAS CHIPOLOPOLO AS A RESULT ZAMBIA CANNOT BEAT SWAZILAND!

  1. Kkkkk just shut up wena you got alot of work to do your president Edgar Lungu need you election is just around the corner

 87. If this is TRUE, that’s the end of Gospel & Zodiak kumakhutira ndi pomwe Mulungu wakuyika. Uku ndichimodzimodzi kuyamba kusewera mpira uli ndi 40 years, no impact kkkkkkk

  1. wait, pliz dont dare 2 biliv this malawi 24,their journalists are full of drama,hw can one publish the story without getting the right info from the concerned parties? hehede! ulu!

 88. Thats the falling of my hero #Kazako! On the other hand ndichan chachilendo chomwe Amvula ndi a Chkaonda Angatibweletsere? Kaya tiziona, pot zipanizo nde zilipo pamalawi pano.

 89. kkkk koma ndie, come on Mai Malawi now..! abale kodi wina sangapange chipani chake chokhala ndi maina chichewa..mmesa kodi ndife amalawi koma zachizungu basi UTP, DPP, PP, UDF ena ndie ndachita kuyiwalako. kwinako mutikumbutseko

 90. zaziii kusowa chochita eti ingolowani zipani zili ndi mphavu kalezi basi, ngati ndalama zakuchulukilani thandizani osowa basi mulungu adzawonjezela pamene muchotsepo.

Comments are closed.