Nomads heading to India in June


Mighty Wanderers

Mighty Be Forward Wanderers have been invited to take part in Chief Minister’s Cup in India in June – a tourney whose champions pocket US$25,000 (around) MK17 Million, the team has confirmed.

According to Nomads General Secretary Mike Butao, the tourney is expected to start from June 24 to July 3 this year and it is planned in a bid to provide a platform to young enthusiastic footballers and to encourage the spirit of competition.

Mighty Wanderers
The Nomads heading to India.

It also enables sporting teams around the world to come together and learn from each other. Butao said that the organizers require the Lali Lubani side to pick an 18 man squad.

‘’They (organizers) will pay for the expenses and at the moment we have written the Super League of Malawi (Sulom) informing them about the development,’ he said.

The Nomads remain upbeat that the trip will be a gateway for players to make international switches as the games are watched by scouts from a lot clubs who would want to sign players from Malawi.

Media reports quote Sulom general secretary Williams Banda as having said that they have received the letter and will check whether the trip could disrupt the progress of the TNM Super League, which goes into its third week this weekend, or not and would give necessary advice to the team.

Last year the Nomads’ sponsors, Japanese second hand car dealer Be Forward, told the side that there are plans that the team will have a trip to Japan where it will play against clubs there.

The sponsors poured a bounty package to the Nomads which is now in the region of MK103 Million, at a time the team was in an economic crisis.

625 thoughts on “Nomads heading to India in June

 1. Ndiye kuchoka ku Malwi kupita ku India chifukwa cha MK17.kukwela ndege ndi zingati?,mukagonakuti komanso pobwela nanga?,mesa ndalamayo idzakhala itatha?.Bolani Flames kupatsidwa K40 million,ma jersey kusowa komanso kuluza game.Bwanji inunso mkaludza?.

 2. I am 27 years old guys…koma since i was born aka ndikoyamba kumva kut Noma yatuluka dziko la Malawi even muno mu Africa….Neba panga zoti naweso ukaone mmene kumakhalira kunja…osamangotinena ife a Bullets kut ndife osazindikila… Munthu ozindikila amakaona kunja osati ukati wayenda ndiye kuti wapita ku Silver Stadium. Congrats nyelele

 3. I am 27 years old guys…koma since i was born aka ndikoyamba kumva kut Noma yatuluka dziko la Malawi even muno mu Africa….Neba panga zoti naweso ukaone mmene kumakhalira kunja…osamangotinena ife a Bullets kut ndife osazindikila… Munthu ozindikila amakaona kunja osati ukati wayenda ndiye kuti wapita ku Silver Stadium. Congrats nyelele

 4. Ndinatsara ine koma neba mukamva mutidwa mimba nsimutsengura ife ndife bas kulibenso wina be4wd yomweyo chiteam koma ichi mukapita mukapereke moni kwaamwenye onse kuti mulidwino olend wadwino mujun muno.

 5. Inu mwati how much the prize? Kkkkkkkkkk ndiye mpaka Ku India eeee! Eeeee! That money is too,too much small once again kkkkk hahahaha shame on the sponsors

  1. Sungatifunire zabwino iwe wa kampopi fc. Ndalama amasokhanitsa pang’ono pang’ono mkukhala zambiri. Fufunza kuti kumangland amalimbilina zingati? Shame on you! B 4wd woyeeeeeeeeee

  2. Sungatifunire zabwino iwe wa kampopi fc. Ndalama amasokhanitsa pang’ono pang’ono mkukhala zambiri. Fufunza kuti kumangland amalimbilina zingati? Shame on you! B 4wd woyeeeeeeeeee

  3. Sungatifunire zabwino iwe wa kampopi fc. Ndalama amasokhanitsa pang’ono pang’ono mkukhala zambiri. Fufunza kuti kumangland amalimbilina zingati? Shame on you! B 4wd woyeeeeeeeeee

 6. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

 7. Manoma ndi TEAM yotsogola it has got QUALITY players. Chaka chino ku Asia next year ndi ku Europe. Ndiye NYEREREZO “MB4WDW”

 8. Ndichifukwa azibambo a BB sagulira azikazi awo zovala ati kuwapangira nsanje kuti amuna ena awafunsira kkkkkkkk koma nsanje inayi. Go manoma.

 9. Ndichifukwa azibambo a BB sagulira azikazi awo zovala ati kuwapangira nsanje kuti amuna ena awafunsira kkkkkkkk koma nsanje inayi. Go manoma.

 10. Kod iwe kape wa nbb ukuganiza kut amene alemba invitation letter ngopusa?Football ilipo pa india iwe ukati wapita kunja nde ku komolosi island basi.kkkk

 11. Kodi ndekuti sizingatheke kuti tibwerekere ma player ena ku NBB or 8 okha? Mhuuuu tingakayambe kuyaluka guyz tiyeni tiwadandaulire a Bullets akatithandize pliz. Nyelele kuti buuuuu, ine wa noma foreverrrrr

 12. Kkkkkkkkk team yanga pepa wina indi woooooooye mukachinye zambiri Mwanza iiiiiiii ii Samantha mpira Koma cricket ambuye osadandaula I ya aaaaaa nkhani ndi makobiri basi

 13. mumafuna zabwino zonse zikhale zanu chifuniro chamulungu sichifuniro chanu timakunvetsesani vuto siinu koma kanundu manoma yonse bho God is in control

 14. Awa ngakhale akupanga phuma mudzaona gemu yoyamba yomweyo awasinja ndikuuzilemtuni pano kwalelo ndilibe ndemanga tidikite kaye chifukwa mukulalata ngati mwanyamuka kale kapena mwawina kale mukangoyelekeza kuluza kumalawi kuno musazabwerennso paja zachilendo kulawa kumenya ndimatimu,akunja Nyamolandu fc ndiyochititsa manyazi zedi sananyamuke koma mkamwa mwayamba kununkha kale eshiiiiiiiii

 15. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 16. khaniyi ili bwino kwambili ndipo kumeneko mukayimila dziko la malawi kukayimila ma team ose koma chonde kumeneko kulibe dwangwa united ndati mwazuzika ndi adwangwa united kumeneko kasamaleni mukakachita phala muchita kunoli ife tidzakukanani

 17. unena chilungamo ku india mpira wozikabwino kulibe or titapanga lafukufuku palibe mnthu angachite nsanje zoti noma ipitaku india mziti akaphunzira kupang ma engine azigayo iyo nde ikhala nkhani yosirisa osati mpira moti muziganiza za super legae team yanu ndi ma prayer akunja koma sikuonesa chamuna ayi,koseku ndikulephera ife tifunirani ulendo wabwino kma kumakumbuka kuti kumeneko akanena kuti team ya kumalawi nde zokatichiti manyazi ayi chifukwa inutu munazolowera kuluza .

 18. kkkk.nkhaniyi yandisagalasa.ine ndwa n.b.b.kma india wake uti .kuthawa s.l.g.kma nomas kma ndye mwachta bho kusakha INDIA Ku green city?kkkkkk kma abale kukhuta bonya?

 19. Sono ku india timaziwa za zipatala ndi cricket. Za mpila mmmm noma ikasanduka madolo pamene kuno mmmm 8 years no. Leaguecup

 20. Koma ku India kumaziwika ndi Karate osati soccer. Ndiye team yoziwa mpira singapite kumeneko. B4ward ndiyokwaniradi kukasewera kumeneko paja nawoso zampira sizikuwakhuza mwina kupitiriza nao za karatizo. BB amayiopera maso ma India sangayerekeze chifukwa akuziwa kuti basi cup imeneyo basi ayipasiratu asanasewere.

 21. Koma ku India kumaziwika ndi Karate osati soccer. Ndiye team yoziwa mpira singapite kumeneko. B4ward ndiyokwaniradi kukasewera kumeneko paja nawoso zampira sizikuwakhuza mwina kupitiriza nao za karatizo. BB amayiopera maso ma India sangayerekeze chifukwa akuziwa kuti basi cup imeneyo basi ayipasiratu asanasewere.

  1. Kkkk! Ccta Grace, sisanje koma nebayo wakuziwa kuti zoona zake ndizimenezo. Umufuse mobisisalira kuti bwanji sanasankhe BB? Wakuwuza kuti BB ndi team yafuko sangayitane anyamata a karate.

 22. Ku india kulibe mpira wamiyendo hahahahaha kuvina bac ndkumene kuliko! A noma mukufuna mukaphuzre kuvina kwa amwenye motsogozedwa nd khrish? Hahahaha

 23. Ku india kulibe mpira wamiyendo hahahahaha kuvina bac ndkumene kuliko! A noma mukufuna mukaphuzre kuvina kwa amwenye motsogozedwa nd khrish? Hahahaha

 24. Kkkkk!mpaka ku JAPAN,yaaaa!wina usalowelere siikukukhuza bcoz ukati wamenya ndi ma team akunja umanena kuzimbabwe,sono ife ndiwautali ku ASIA mpaka wina team yake izatha sazakupondako,eeeeee!koma B4WD yokha ine yandithetsa mzeruuuuu!!

 25. Kkkkk!mpaka ku JAPAN,yaaaa!wina usalowelere siikukukhuza bcoz ukati wamenya ndi ma team akunja umanena kuzimbabwe,sono ife ndiwautali ku ASIA mpaka wina team yake izatha sazakupondako,eeeeee!koma B4WD yokha ine yandithetsa mzeruuuuu!!

  1. Damson unalikut tym ija tinapita england,mpaka denmak,,,komaso bb ndi team yaikulu sungafanize ndi mphwemphwa, kod mnayamba mwamenyapo caf? Ndiuzen timu yotchuka yaku india ngat foot mmaisata,,,aiopa kuitenga bb coz ikhoza kukakhaulisa tialuya topepelat,,kuvaya indya ndiukape omvesa chison

  2. Damson unalikut tym ija tinapita england,mpaka denmak,,,komaso bb ndi team yaikulu sungafanize ndi mphwemphwa, kod mnayamba mwamenyapo caf? Ndiuzen timu yotchuka yaku india ngat foot mmaisata,,,aiopa kuitenga bb coz ikhoza kukakhaulisa tialuya topepelat,,kuvaya indya ndiukape omvesa chison

  3. mmmm time imeneija inunso mutabadwa eti? osamangowanamizatu achinyamatawa bcoz chomwe ndikuona apa ndi njala, nthenda komanso nsanje from bibi supporters

  4. inutu mumakonderedwa chifukwa cha chair uja koma pano sizikuyendera zoti a president athandiza kkkkkkkkkkkkkkkkKkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ndiye inuso chingambwe wanuyo apange zotheka chaka cha mawa mupiteso ku mangalande munaapitako

  5. inutu mumakonderedwa chifukwa cha chair uja koma pano sizikuyendera zoti a president athandiza kkkkkkkkkkkkkkkkKkkkKkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ndiye inuso chingambwe wanuyo apange zotheka chaka cha mawa mupiteso ku mangalande munaapitako

 26. Koma nyelele nthawi zonse mumayamba ndinu zinthu za chilendo ana achepa basi wa ku india basi enanu muzingosalilabe ndi timu za kuphwazo

 27. Koma nyelele nthawi zonse mumayamba ndinu zinthu za chilendo ana achepa basi wa ku india basi enanu muzingosalilabe ndi timu za kuphwazo

 28. Zulumba Osadandaula Anzakowo Angopita Ku Kawona Ku India Osati Kukasewela Mpira ,akakawevela Chisoni Ndiye Akangowapatsa Zitatu Kwa Ziro,chifukwa Woti Atha Kuchinya Sindikumuwona

 29. Zulumba Osadandaula Anzakowo Angopita Ku Kawona Ku India Osati Kukasewela Mpira ,akakawevela Chisoni Ndiye Akangowapatsa Zitatu Kwa Ziro,chifukwa Woti Atha Kuchinya Sindikumuwona

 30. Zabwino zonse mukaphunzire kalimidwe ka sabola ndi kaikidwe ka ma spice muzokudya kumaendako maiko akunja nanga kungowasiira a bullets okha bac

 31. Zabwino zonse mukaphunzire kalimidwe ka sabola ndi kaikidwe ka ma spice muzokudya kumaendako maiko akunja nanga kungowasiira a bullets okha bac

 32. Utsutsa ndi otsutsa basi olo mutamuuza kuti mu lake Malawi muli Chambo chokoma akuuzani kuti ayi kkkkkkkkkk vuto siiyeyo koma fodyayooooo #VivaNoma

 33. Utsutsa ndi otsutsa basi olo mutamuuza kuti mu lake Malawi muli Chambo chokoma akuuzani kuti ayi kkkkkkkkkk vuto siiyeyo koma fodyayooooo #VivaNoma

 34. Inuuu munamize anthu kuti muli kuburundi pamene muli kumalawi,kungozolowera kunama nambala yakuburundi ndi imeneyo? Kkkkkkkkkkkk kulakalaka

 35. Inuuu munamize anthu kuti muli kuburundi pamene muli kumalawi,kungozolowera kunama nambala yakuburundi ndi imeneyo? Kkkkkkkkkkkk kulakalaka

 36. team yopanda mastriker, ma defender ofoila, golkeeper odabwa/otutumuka, imamenya bwino pakati basi, imaopa kumenya ma international games mukufuna ikatichitiseko manyazi? tangotengani Team Mbambande N B B

 37. team yopanda mastriker, ma defender ofoila, golkeeper odabwa/otutumuka, imamenya bwino pakati basi, imaopa kumenya ma international games mukufuna ikatichitiseko manyazi? tangotengani Team Mbambande N B B

  1. ndimkona tima BB nditimu ya umbuli nkhani zake ndi zimenezi jerasi 2 much ndimkonanso mumamupangira jerasi chande uku ndiko kuipa mtima ndi BB yanuyo

  2. ndimkona tima BB nditimu ya umbuli nkhani zake ndi zimenezi jerasi 2 much ndimkonanso mumamupangira jerasi chande uku ndiko kuipa mtima ndi BB yanuyo

 38. Ife aku bulundi tinali kumufunira noma zabwino chifukwa adzakhala akupereka chitsanzo wabwino. Ifenso adzakhala akumufuna akazakhala akuchoka kumeneko chifukwa uyu buleti adzakhala akusuta fwaka kambere.

 39. Ife aku bulundi tinali kumufunira noma zabwino chifukwa adzakhala akupereka chitsanzo wabwino. Ifenso adzakhala akumufuna akazakhala akuchoka kumeneko chifukwa uyu buleti adzakhala akusuta fwaka kambere.

 40. Koma abale chondeeeeeeeeeeee,a evcutive musamusiye Jaffali Chande adziwe kuti wafika ku timu yotsogola.next Denmark ndi japan.Thats the Nomads.inu mukuti ku India kulibe mpiranu bakhalani choncho mudzimenya wa mmyala,waphuphuphu,wachipoperanji.

 41. Koma abale chondeeeeeeeeeeee,a evcutive musamusiye Jaffali Chande adziwe kuti wafika ku timu yotsogola.next Denmark ndi japan.Thats the Nomads.inu mukuti ku India kulibe mpiranu bakhalani choncho mudzimenya wa mmyala,waphuphuphu,wachipoperanji.

 42. Akasewera ndi ma team ngati Zolozolo united, Kabwafu, Ntcheu Irish Potato Growers united. India ndi yonse koma quality kkkkkkk

 43. Akasewera ndi ma team ngati Zolozolo united, Kabwafu, Ntcheu Irish Potato Growers united. India ndi yonse koma quality kkkkkkk

 44. zisiyeni nyerere zikapondeponde ku india, aneba msadandaule inu mubwera kukaronga muzasewera ndi kaporo stars mzalandira 2bags yampunga pepani

 45. zisiyeni nyerere zikapondeponde ku india, aneba msadandaule inu mubwera kukaronga muzasewera ndi kaporo stars mzalandira 2bags yampunga pepani

 46. enanu simuzisata zampira, league yaku India ilibwino kuposa ya Malawi, chikuvuta ndi nsanje K17m sungafanize ndika K10m ka super league, Go Manoma kayimile Malawi

 47. enanu simuzisata zampira, league yaku India ilibwino kuposa ya Malawi, chikuvuta ndi nsanje K17m sungafanize ndika K10m ka super league, Go Manoma kayimile Malawi

 48. Neba,flag yathu us flag of ure lovely country timayikonda,ndiye Khani ndiyoti osakapangisa manyazi if we gve u flag of national mean we are behind u,as national posayang’anila chipani or club

 49. Neba,flag yathu us flag of ure lovely country timayikonda,ndiye Khani ndiyoti osakapangisa manyazi if we gve u flag of national mean we are behind u,as national posayang’anila chipani or club

 50. Akuluakulu timu ndiimeneyo koma ku indiaku muganize bwino ndani adzakhale m’phunzits bcoz chamangwanayu ndimanyaka ine wa maule.

 51. Akuluakulu timu ndiimeneyo koma ku indiaku muganize bwino ndani adzakhale m’phunzits bcoz chamangwanayu ndimanyaka ine wa maule.

 52. ndye mwat 17 milion akuvutka nayo choncho?palibetu gate collection apa muzkasewera ndi timateam ta pa msika.anthu sakonda soccer uku

 53. ndye mwat 17 milion akuvutka nayo choncho?palibetu gate collection apa muzkasewera ndi timateam ta pa msika.anthu sakonda soccer uku

 54. kumalawi ndichoncho wina akachita chabwino nsanje thoo.ugule kachovala ka china akuti sizabwino pomwe iwo akuvala nsaza zokhazokha mumtima nkumasilira.iwe team yako anayiitanako kuti.mudzafa ndi mtima wansanje womwewo anzanu akupita patsogolo.nyerere ndi deal moto buuuuuu

 55. kumalawi ndichoncho wina akachita chabwino nsanje thoo.ugule kachovala ka china akuti sizabwino pomwe iwo akuvala nsaza zokhazokha mumtima nkumasilira.iwe team yako anayiitanako kuti.mudzafa ndi mtima wansanje womwewo anzanu akupita patsogolo.nyerere ndi deal moto buuuuuu

 56. Ife ku india anasangalala kambiri ndi nkhani ameneyi. ife anasankha manoma bcoz amalankula binobino english kusiyana ndi uyu mumati bibi wafodya uja. well good manoma.

 57. Ife ku india anasangalala kambiri ndi nkhani ameneyi. ife anasankha manoma bcoz amalankula binobino english kusiyana ndi uyu mumati bibi wafodya uja. well good manoma.

  1. Hahaha! Neba ku India kulibe chizungu ukananena za chichwa ndizonadi komaso soccer kulibe koma karate. Ndiye posankha awonaso team limene angakaliwine paja umaziwa sangasankhe team yabwino ngati ya NBB.

  2. Hahaha! Neba ku India kulibe chizungu ukananena za chichwa ndizonadi komaso soccer kulibe koma karate. Ndiye posankha awonaso team limene angakaliwine paja umaziwa sangasankhe team yabwino ngati ya NBB.

  3. karate kulibe ku India koma Cricket. kampira amakaponya ndi manja kaja wina ndikukatibula ndi mtengo basi kikiki apo bola munakapita kwa Nakamura komwekotu bolani kuli mpira kikiki. BB ikakwera ndege imapita kuchimake kwa mpira England osati ku india hahahaha, munayamba mwamva kuti india ikukasewera mpira?????? koma Neba

  4. karate kulibe ku India koma Cricket. kampira amakaponya ndi manja kaja wina ndikukatibula ndi mtengo basi kikiki apo bola munakapita kwa Nakamura komwekotu bolani kuli mpira kikiki. BB ikakwera ndege imapita kuchimake kwa mpira England osati ku india hahahaha, munayamba mwamva kuti india ikukasewera mpira?????? koma Neba

  5. Ife anaona kut bibi wasegula mmimba komanso anachita jelasi bcoz of nkhani ameneyiee.? bibi ali ndi njala nthenda komanso nsanje kambiri kambiri.

  6. Ife anaona kut bibi wasegula mmimba komanso anachita jelasi bcoz of nkhani ameneyiee.? bibi ali ndi njala nthenda komanso nsanje kambiri kambiri.

  7. Komanso chot mudziwe mchoti ku india kulibe nkhani za mpila.B@ mukanena nkhani za engineering and medicine ndiye ku chimake.So neba ukamasangalara kut yu r going to india mzomvetsa chison kwambili.Ikanankhala kut Noma ndi polytechnic tikanat bravo,zimafunika kut muwauze ma sponsor kut mungopita dziko lina not ku india.Nyasa inadzapita ku England ku training,neba mphamvu yakusamphunzila

  8. Komanso chot mudziwe mchoti ku india kulibe nkhani za mpila.B@ mukanena nkhani za engineering and medicine ndiye ku chimake.So neba ukamasangalara kut yu r going to india mzomvetsa chison kwambili.Ikanankhala kut Noma ndi polytechnic tikanat bravo,zimafunika kut muwauze ma sponsor kut mungopita dziko lina not ku india.Nyasa inadzapita ku England ku training,neba mphamvu yakusamphunzila

  9. Komanso chot mudziwe mchoti ku india kulibe nkhani za mpila.B@ mukanena nkhani za engineering and medicine ndiye ku chimake.So neba ukamasangalara kut yu r going to india mzomvetsa chison kwambili.Ikanankhala kut Noma ndi polytechnic tikanat bravo,zimafunika kut muwauze ma sponsor kut mungopita dziko lina not ku india.Nyasa inadzapita ku England ku training,neba mphamvu yakusamphunzila

  10. Komanso chot mudziwe mchoti ku india kulibe nkhani za mpila.B@ mukanena nkhani za engineering and medicine ndiye ku chimake.So neba ukamasangalara kut yu r going to india mzomvetsa chison kwambili.Ikanankhala kut Noma ndi polytechnic tikanat bravo,zimafunika kut muwauze ma sponsor kut mungopita dziko lina not ku india.Nyasa inadzapita ku England ku training,neba mphamvu yakusamphunzila

 58. Kkkkkk bolanso ku chipiku nanga mpanga kukasewera ndi amwenye kkkkkk fam ilowelelepo zokatipangasa manyazi ai mungote sguad ya pool kkkkkk neba matama osamenya caf bwanji ukhale fombon uone choka usandikwane satuday tikufinya umina mpeeeeeeeeeeeee

 59. Kkkkkk bolanso ku chipiku nanga mpanga kukasewera ndi amwenye kkkkkk fam ilowelelepo zokatipangasa manyazi ai mungote sguad ya pool kkkkkk neba matama osamenya caf bwanji ukhale fombon uone choka usandikwane satuday tikufinya umina mpeeeeeeeeeeeee

 60. ASakudziwa ndani kut wapangitsa gututu nyamilandu,Ku India anawauza a Fam kut atumize champion koma iyeo Poona kuti ayaya sanakwerepo ndege nkutenga nyakanyaka izi,musazanyamule flag ya2 mukabwereke Ku Nigeria

 61. ASakudziwa ndani kut wapangitsa gututu nyamilandu,Ku India anawauza a Fam kut atumize champion koma iyeo Poona kuti ayaya sanakwerepo ndege nkutenga nyakanyaka izi,musazanyamule flag ya2 mukabwereke Ku Nigeria

 62. ASakudziwa ndani kut wapangitsa gututu nyamilandu,Ku India anawauza a Fam kut atumize champion koma iyeo Poona kuti ayaya sanakwerepo ndege nkutenga nyakanyaka izi,musazanyamule flag ya2 mukabwereke Ku Nigeria

 63. Kwa nose amene mukut ku india kulibe mpira zangoonetsera2 kut mpira mumangoysata wama venda anu okhawo…zangoonetsera2 kut olo titat Noma ikupita ku U.S.A mudzit kulibr mpira kuli basket ball yokha…mudzazindikira koma mocedwa kut soccer is all abt entertainment osta zaufisi zanuzo…mtima wakaduka munakhala bwanji…google if ver z no futbol in india…shupit mwandikwiitsa… #TEAM_NYELERE…

 64. Kwa nose amene mukut ku india kulibe mpira zangoonetsera2 kut mpira mumangoysata wama venda anu okhawo…zangoonetsera2 kut olo titat Noma ikupita ku U.S.A mudzit kulibr mpira kuli basket ball yokha…mudzazindikira koma mocedwa kut soccer is all abt entertainment osta zaufisi zanuzo…mtima wakaduka munakhala bwanji…google if ver z no futbol in india…shupit mwandikwiitsa… #TEAM_NYELERE…

 65. Kwa nose amene mukut ku india kulibe mpira zangoonetsera2 kut mpira mumangoysata wama venda anu okhawo…zangoonetsera2 kut olo titat Noma ikupita ku U.S.A mudzit kulibr mpira kuli basket ball yokha…mudzazindikira koma mocedwa kut soccer is all abt entertainment osta zaufisi zanuzo…mtima wakaduka munakhala bwanji…google if ver z no futbol in india…shupit mwandikwiitsa… #TEAM_NYELERE…

  1. am nt a noma sapota bt zea z much sense in ur coment,if bullets were invited,such jealousy wud nt exist,ufiti,nsanje,kaduka siziphula kanthu pomwe God wachita bless. u wil die with ur envy

  2. am nt a noma sapota bt zea z much sense in ur coment,if bullets were invited,such jealousy wud nt exist,ufiti,nsanje,kaduka siziphula kanthu pomwe God wachita bless. u wil die with ur envy

 66. Mbalame zofanana mapiko zimamwela dziwe limodzi,mukadapeleka chitsanzo nokha nokha kukondana ngati ana adziko limodzi.Mukutukwanizana ulendowo usadafike ndiye kweni-kweni nthawi ikadzafika kudzakhala zotani?.Mukupeleka chitsanzo chonyansa kumaiko ena ozungila ndi ena akutali,n’chifukwa chake mpila pa Malawi sudzapita patsogolo kamba kokhomelelana pazinthu zopanda pake.Tiyeni tisamale malankhulidwe athu komanso ulemu ndiwabwino.

 67. Mbalame zofanana mapiko zimamwela dziwe limodzi,mukadapeleka chitsanzo nokha nokha kukondana ngati ana adziko limodzi.Mukutukwanizana ulendowo usadafike ndiye kweni-kweni nthawi ikadzafika kudzakhala zotani?.Mukupeleka chitsanzo chonyansa kumaiko ena ozungila ndi ena akutali,n’chifukwa chake mpila pa Malawi sudzapita patsogolo kamba kokhomelelana pazinthu zopanda pake.Tiyeni tisamale malankhulidwe athu komanso ulemu ndiwabwino.

 68. Mbalame zofanana mapiko zimamwela dziwe limodzi,mukadapeleka chitsanzo nokha nokha kukondana ngati ana adziko limodzi.Mukutukwanizana ulendowo usadafike ndiye kweni-kweni nthawi ikadzafika kudzakhala zotani?.Mukupeleka chitsanzo chonyansa kumaiko ena ozungila ndi ena akutali,n’chifukwa chake mpila pa Malawi sudzapita patsogolo kamba kokhomelelana pazinthu zopanda pake.Tiyeni tisamale malankhulidwe athu komanso ulemu ndiwabwino.

 69. All the best wishes neba,if will win that match you will raise up our Country flag,we are all Malawian the different is only the colour of jeyz.All Maule lets give our neba disregard the team we follow.

 70. All the best wishes neba,if will win that match you will raise up our Country flag,we are all Malawian the different is only the colour of jeyz.All Maule lets give our neba disregard the team we follow.

 71. All the best wishes neba,if will win that match you will raise up our Country flag,we are all Malawian the different is only the colour of jeyz.All Maule lets give our neba disregard the team we follow.

 72. kodi mukuti sitimwa madzi chifukwa cha India trip mwayiwala kuti Bullets went to UK ka India ndikachiyani. Bullets ndi deal camping yokha Uk kuposa flames ndiye nyerere ndi chani

 73. kodi mukuti sitimwa madzi chifukwa cha India trip mwayiwala kuti Bullets went to UK ka India ndikachiyani.

 74. Kkkk Neba kuthawa league ikhala itatentha June and akhala ali No10. Pano wapempha SULOM kuti game ya saturday asinthe sunati neba!

 75. Kkkk Neba kuthawa league ikhala itatentha June and akhala ali No10. Pano wapempha SULOM kuti game ya saturday asinthe sunati neba!

 76. Kkkk Neba kuthawa league ikhala itatentha June and akhala ali No10. Pano wapempha SULOM kuti game ya saturday asinthe sunati neba!

 77. I have not believed this tabloid giving true and accurate info may be on politics but if it’s true that’s a good development although there is no competitive football in India. Longing to seeing this materialize

 78. I have not believed this tabloid giving true and accurate info may be on politics but if it’s true that’s a good development although there is no competitive football in India. Longing to seeing this materialize

 79. Thats A Very Good Development To Our Local Players Playing In Be Forward Wanderers.

  1. Nsanje simapindula nthawi zonse ndipo ikakhala nkhuku imatha kuswa mazila ali ake omwe nkulephela kuwundatila,koma akadati inuyo mupite kumeneko kukadakhalanso mitodzo kwa anzanuwo.

  2. Nsanje simapindula nthawi zonse ndipo ikakhala nkhuku imatha kuswa mazila ali ake omwe nkulephela kuwundatila,koma akadati inuyo mupite kumeneko kukadakhalanso mitodzo kwa anzanuwo.

  3. Nsanje simapindula nthawi zonse ndipo ikakhala nkhuku imatha kuswa mazila ali ake omwe nkulephela kuwundatila,koma akadati inuyo mupite kumeneko kukadakhalanso mitodzo kwa anzanuwo.

  4. Pamenepo sizinaipe bola ngat kumalawi kwanu kuno mpira uliko ndekuti zili bwino, but what i know is when it comes to fifa ranking india is better than malawi

  5. Pamenepo sizinaipe bola ngat kumalawi kwanu kuno mpira uliko ndekuti zili bwino, but what i know is when it comes to fifa ranking india is better than malawi

  1. Gaggaaggagagaggaga mwana Danny, kungoti ineyo ndinazolowela kuonelanso mipila yakunja ngat ku SA kuno tikamakaonela game tonse timasakanikilana. nde kumalawi ndine wa bullets ndithu usakaike…..

  2. Gaggaaggagagaggaga mwana Danny, kungoti ineyo ndinazolowela kuonelanso mipila yakunja ngat ku SA kuno tikamakaonela game tonse timasakanikilana. nde kumalawi ndine wa bullets ndithu usakaike…..

  3. Gaggaaggagagaggaga mwana Danny, kungoti ineyo ndinazolowela kuonelanso mipila yakunja ngat ku SA kuno tikamakaonela game tonse timasakanikilana. nde kumalawi ndine wa bullets ndithu usakaike…..

  4. Thanks, Ambudye,,, kumeneko nde kuzindikila usapotawo nde umenewo, inenso ndili kunkuno ku RSA, am a NOMA fan 100%…Hakuna mathatha,

  5. Thanks, Ambudye,,, kumeneko nde kuzindikila usapotawo nde umenewo, inenso ndili kunkuno ku RSA, am a NOMA fan 100%…Hakuna mathatha,

Comments are closed.