Update: Bakili back in court today

Advertisement
Bakili Muluzi

The High in Blantyre today continues to hear the MK1.7 Billion corruption case involving ex Malawi President Bakili Muluzi and his ex assistant Lyness Whiskey.

Bakili Muluzi
Bakili Muluzi: His case is back in court today.

The court had adjourned the case to today as to allow first witness be present in court.

The court had heard through Anti Corruption Bureau’s Deputy Director Reyneck Matemba that the witness Victor Banda has been sick and will be seeing his doctor on Wednesday and that he would not be resent in the court.

Matemba asked the court to adjourn the case or allow the second witness to testify but the defence lawyers Tamanda Chokhotho and Jai Banda objected.

It is expected that Banda will be in court today as ACB said he met his doctors on Wednesday.

For over six years, Muluzi has been answering charges of corruption in which he is accused of squandering public funds amounting to 1.7 billion Kwacha.

(UPDATES TO FOLLOW)

Advertisement

379 Comments

 1. This is the worst ever President Malawi will never had.
  He found Malawi’s economy hot kicking, and drop it to lowest levels.
  All those monies which he is being accused of stealing would make more advanced economic infrastructure programmes, and put Malawi on the map again as it was with Dr. Banda.
  What he had in mind was to punish and revenge the sins to the former Malawi’s administration, which really cost him dearly deadly.
  This man still remains in the lines of 5th richest man in African soil,
  Hooooooooooow?

 2. This is the worst ever President Malawi will never had.
  He found Malawi’s economy hot kicking, and drop it to lowest levels.
  All those monies which he is being accused of stealing would make more advanced economic infrastructure programmes, and put Malawi on the map again as it was with Dr. Banda.
  What he had in mind was to punish and revenge the sins to the former Malawi’s administration, which really cost him dearly deadly.
  This man still remains in the lines of 5th richest man in African soil,
  Hooooooooooow?

 3. Tamusiyani chair apume mtendere , ntchito yabwino yomwe anagwira polamula Malawi mwabata ndi mtendere, pano ntchito zake tikuzisowa. Agalu enanu dziko likukanikani kuyendetsa koma kufziwa kumanga anthu osachimwa basi

 4. Tamusiyani chair apume mtendere , ntchito yabwino yomwe anagwira polamula Malawi mwabata ndi mtendere, pano ntchito zake tikuzisowa. Agalu enanu dziko likukanikani kuyendetsa koma kufziwa kumanga anthu osachimwa basi

 5. Arresting atcheya will be a great mistake.munthuyu Ndi wachifundo amathandiza anthu ambiri komanso he is a source of security in this country.Munthuyo so munthu wamba

 6. God Bless Bakili Muluzi as yu Bless Me aswell! usabwezere choipa pakusithana ndi choipa komatu bwezerani chabwino pakusithana ndi choipa, si ine koma mau a Buku loyera lopatulika. Amen!

 7. Osalimbana ndi cashgate bwanji mukulimbana ndi ndalama zakalekale kusiya zatsopano bwanji?koma disel abale,ukumusiya bwanji JOYCE MTIRA BANDAH

 8. its about time this old man must go back to jail . Wachake saleka anaba ali kalaliki wa court ameneyi. ndiponso tuvutika ndiachina Mutharika chifukwa chaiyeyu anapasa udindo kwa Bingu

 9. yaah achalume kuchtekete kuchitulo pachanja achakunganya wosope wakuwendesya magambo gakwitelekoku mmatongomo ngawe pachiwandika ningakatile muzumbu kapenakuto yitolo yangaumbalayo yinyaleye kwejinji

 10. how dare u peter? Do u tink u r beta dan bakiri?mwachita chani chani chooneka ndimaso y u r wastin ur tym instead ov maintainin our malawi ,zimenezo zithele2 thats stuipd

 11. kodi dzikoli likulephera kuyenda bwino chifukwa cha k1.7b? mmene wakalambira mu2yu osamusiya bwanji? tiyeni tiphunzire kukhululukira aza2.. zi2 zomwe adapanga akulamulira ndi k1.7b, chofunikira ndi chani? Lets move forward malawi. zambuyo zitichedwesa.

 12. kodi dzikoli likulephera kuyenda bwino chifukwa cha k1.7b? mmene wakalambira mu2yu osamusiya bwanji? tiyeni tiphunzire kukhululukira aza2.. zi2 zomwe adapanga akulamulira ndi k1.7b, chofunikira ndi chani? Lets move forward malawi. zambuyo zitichedwesa.

 13. Who Is To Accused Of 92 Billion Of The Late{APWIYA}If U Continue To Accuse Munthu Wachikulire The Real Politician Namanyonyolo 92billion-1.7=phwi, Eesh APWIYA Munaononga Ndikumusiya Malawi Pamavuto,

 14. Who Is To Accused Of 92 Billion Of The Late{APWIYA}If U Continue To Accuse Munthu Wachikulire The Real Politician Namanyonyolo 92billion-1.7=phwi, Eesh APWIYA Munaononga Ndikumusiya Malawi Pamavuto,

 15. Who Is To Accused Of 92 Billion Of The Late{APWIYA}If U Continue To Accuse Munthu Wachikulire The Real Politician Namanyonyolo 92billion-1.7=phwi, Eesh APWIYA Munaononga Ndikumusiya Malawi Pamavuto,

 16. Who Is To Accused Of 92 Billion Of The Late{APWIYA}If U Continue To Accuse Munthu Wachikulire The Real Politician Namanyonyolo 92billion-1.7=phwi, Eesh APWIYA Munaononga Ndikumusiya Malawi Pamavuto,

 17. Leave Dr. Bakili himself he has done nothing. Let him enjoy with his money

 18. Kodi inu , muziyeni dalayo alibe milandu bwanji kodi inu mumango kumbuza ngani zakale nanuzo mulindi milandu yakuba ,why no open caz

 19. Kodi inu , muziyeni dalayo alibe milandu bwanji kodi inu mumango kumbuza ngani zakale nanuzo mulindi milandu yakuba ,why no open caz

 20. Kodi inu , muziyeni dalayo alibe milandu bwanji kodi inu mumango kumbuza ngani zakale nanuzo mulindi milandu yakuba ,why no open caz

 21. Kodi inu , muziyeni dalayo alibe milandu bwanji kodi inu mumango kumbuza ngani zakale nanuzo mulindi milandu yakuba ,why no open caz

 22. Leave a chair alone and concentrate on kuthesa njala ndiuphawi wathuwu, what is gonna be the bennefit of arresting achair

 23. amalawi ndale muzizidziwa.atupere ndi nduna m’boma la DPP bakiri nde adaika chipani cha DPP pamapo.moti mukuganiza kt bakiri angamangidwe? that is trick game akufuna atipusitse anthu.ngati mukutsutsa mungoti pheeeee muwone

 24. Madala awa sangamangidwe muzimangidwa anthu oba ndalama zochepanu am 3 million inu 1- 7 billion sangamangidwe

 25. Koma muziyamika zimene wapanga cheya dziko lamalawi nanga inu atsongoleli mwapanga chani poti mavuto ali mbweee m’malawi musiyeni bakili koma bakili2 ameneyo napolo mwamuwala masiku awiliwa eti oky

 26. kkkkkkkkkkkkkkkk mukunamiza amalawi inu muluzi mlandu wauyambitsa yekha kuti uyambike akufuna ma million alandile atcheya sangamangidwe inu apa angolandila chuma chawo basi kamba kowaipitsila mbiri boma silimawina mlandu

 27. kkkkkkkkkkkkkkkk mukunamiza amalawi inu muluzi mlandu wauyambitsa yekha kuti uyambike akufuna ma million alandile atcheya sangamangidwe inu apa angolandila chuma chawo basi kamba kowaipitsila mbiri boma silimawina mlandu

  1. Ndipo Boma lake la Malawi kudzawina mlandu pa Bakili aaaaaaaaaaa.
   Boma la Malawi limayambitsa mlandu opanda mbonitu…….limafunafuna mboni mlandu uli mcourt,……#Fuck off#

 28. Hmmmm this is just a debate the fact is what you know………. Non of you can judge Muluzi. You are barking here like the dogs in the fence. My fellow Malawians,do not fool yourselves here……..Muluzi is the best…

 29. Hmmmm this is just a debate the fact is what you know………. Non of you can judge Muluzi. You are barking here like the dogs in the fence. My fellow Malawians,do not fool yourselves here……..Muluzi is the best…

 30. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 31. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 32. Abale musiyeni chair timamunyadira kwambiri Mandela wa ku Malawi ndameneyo bwanji osamupatsa ulemu akadzamwalira ndipomwe mudzidzampatsa ulemu, musiyeni mukufuna achokenso ku Malawiko chair ndi Mmalawi weniweni musamuvutitse chonde

 33. Abale musiyeni chair timamunyadira kwambiri Mandela wa ku Malawi ndameneyo bwanji osamupatsa ulemu akadzamwalira ndipomwe mudzidzampatsa ulemu, musiyeni mukufuna achokenso ku Malawiko chair ndi Mmalawi weniweni musamuvutitse chonde

 34. EE AMALAWI MULIBE ULEMU ETI MUNTHU WAMKULU NGATI UYU KUMAMZUZA CHOCHI FUNSO MKUMATI UZATHA LITI MULANDUWU AYIII AMALAWI SICHOCHO SIYENI

 35. EE AMALAWI MULIBE ULEMU ETI MUNTHU WAMKULU NGATI UYU KUMAMZUZA CHOCHI FUNSO MKUMATI UZATHA LITI MULANDUWU AYIII AMALAWI SICHOCHO SIYENI

 36. Za ziii mukhalira yomweyo jb osamumanga bwa?akungoyenda mwezi wathawu anali kuno Ku RSA akulambalala chain kumalawi

 37. mukathana ndi Madalawa kenako Masi10,, kundende sanapangile osauka okha olemelaso akalakwisa azikakuwona,,, Musaiwale kuwafusa Atcheyawo kuti anthu osaona aja anakawasiya kuti..

 38. mukathana ndi Madalawa kenako Masi10,, kundende sanapangile osauka okha olemelaso akalakwisa azikakuwona,,, Musaiwale kuwafusa Atcheyawo kuti anthu osaona aja anakawasiya kuti..

 39. mukathana ndi Madalawa kenako Masi10,, kundende sanapangile osauka okha olemelaso akalakwisa azikakuwona,,, Musaiwale kuwafusa Atcheyawo kuti anthu osaona aja anakawasiya kuti..

 40. My psychic readings focus on positive thinking & positive change. It may assist in bringing clarity to a confusing situation, help you prepare for the future in a more focused way and may empower you with positive potential. If you are seeking spiritual guidance with your relationship, marriage, love, family, career, money, health matters, or life’s daily issues, my insightful accurate psychic reading will help you answer the questions that weigh heavily on your mind. I would love to assist you with making the best decisions for your Future. No matter where you live I can help you.Call +27738951830 MUNIL SALEH, I do Whats-App, Face book/munilsaleh, Phone and personal readings.

 41. My psychic readings focus on positive thinking & positive change. It may assist in bringing clarity to a confusing situation, help you prepare for the future in a more focused way and may empower you with positive potential. If you are seeking spiritual guidance with your relationship, marriage, love, family, career, money, health matters, or life’s daily issues, my insightful accurate psychic reading will help you answer the questions that weigh heavily on your mind. I would love to assist you with making the best decisions for your Future. No matter where you live I can help you.Call +27738951830 MUNIL SALEH, I do Whats-App, Face book/munilsaleh, Phone and personal readings.

 42. My psychic readings focus on positive thinking & positive change. It may assist in bringing clarity to a confusing situation, help you prepare for the future in a more focused way and may empower you with positive potential. If you are seeking spiritual guidance with your relationship, marriage, love, family, career, money, health matters, or life’s daily issues, my insightful accurate psychic reading will help you answer the questions that weigh heavily on your mind. I would love to assist you with making the best decisions for your Future. No matter where you live I can help you.Call +27738951830 MUNIL SALEH, I do Whats-App, Face book/munilsaleh, Phone and personal readings.

 43. Kumanena chilungamo,alietse alindiubwino ndikuipa kwake.koma Bakilimulizi kwakukulu kunalikwaubwino.osati satanawaleroyu mbuziyachabechabe.

 44. Kumanena chilungamo,alietse alindiubwino ndikuipa kwake.koma Bakilimulizi kwakukulu kunalikwaubwino.osati satanawaleroyu mbuziyachabechabe.

 45. Kumanena chilungamo,alietse alindiubwino ndikuipa kwake.koma Bakilimulizi kwakukulu kunalikwaubwino.osati satanawaleroyu mbuziyachabechabe.

 46. Bakili Muluzi z our Malawian Hero and we believe tht no one ‘ll rule as gud as hw he wz ruling. If it had been all presidents who r coming after him r wise lyk our X President Bakili Muluzi the Malawi would hv been improved than b4. If it had been also Malawi z still in the hands of Dr Bakili Muluzi am assuring u tht Mw would b beultiful and selfcontained…….warning!!!!!!! Once u try to do something bad on him; his supporters ‘ll spoil and damage all of u. Leave him alone to breath fresh air from heaven…….

 47. If u had done this bfore I think during the pp, cashgate wud no longer be there. Bt bcoz u were neglecting to judge it bfo these pipo they took advantage to hassle that such amount of kwachaz.

 48. Please finalise this case once and for good.We are tired of this.some of the cashgate cases have been dealt with and people are in jail now.What is so special about this Bakili case.If he is guilty put him behind bars if not free him.Inunso amakhothi munayambira ndi case iyi.Why is it dragging?Anthu akaba nkhuku matsekera kuchichiri.Let the truth prevail and come up with judgement.

 49. Mboli za amanu! Mukulimbana ndimunthu oti iye kwake kunatha bwanji? Bwanji simunamutengerele #bingu_ku court b4 kumwalira? Even #joice banda nkhani za cashgate? Kodi #bakili chitulileni udindu pansi papita zaka zingati achule inu? Pathako panu nonse omwe mukuyendetsa zamulandu wa Bakili

 50. Mboli za amanu! Mukulimbana ndimunthu oti iye kwake kunatha bwanji? Bwanji simunamutengerele #bingu_ku court b4 kumwalira? Even #joice banda nkhani za cashgate? Kodi #bakili chitulileni udindu pansi papita zaka zingati achule inu? Pathako panu nonse omwe mukuyendetsa zamulandu wa Bakili

 51. Mulibe ndimzelu zomwe akapolo inu akukanikani J B uja kut abwele kuno azengedwe mlandu mukulimbandana ndi ameneyo kumuwonelela?ife wat pangila zazkulu anatmangila depot.mtsika ndi brige lactima kuno ku B L K ndiposo tala wakuno chpangilen achair mpaka lelo amango mata bac agalu anyan mbuz afit inu munalekelanji kumumanga 2005 ija?bwez pano atatuluka mukufuna pomuphela kapena?samadya mmakwanutu muleken alinaye cholinga mulungu

 52. Ku malawi anthu amene anali anzelu ana mwalila mwalila kuna tsala mbuli zokha zokha muma tinyasa kwambili zinthu za chaka cha 2000 ndiku masokola pano ku choka nthawi imene ija nanga aka khala wa mwalila nde ndibwezi muku maka imba mrandu chiliza chake ndietu eeee anthu aku malawi kuti pangitsa manyazi nde poyambitsa nkhaniyo nde mumati bwanji popeza ndizakale kale kudziwa nkumadziwa kumva nkumamva kuti #mbuzi_imadya_pomwe ai mangilila koma basi ndiu mbuli mwati koma amene tipezele mwayi nde ata bweza munga pangile chani ndalamazo munga chape dziko lino makape inu munga sinthe dziko lino ndiku fika pa huf landani ndi 1.7 billoni demeti ndinu zitsilu bwanji osama panga zija dziko lose lina dziwa ndimwana emwe ana dziwa kuti ku boma anthu aba ndalama osa panga za akuba anzanu aja muku malimbana ndi muluzi ntaeni guys kusowa zochita kapena zinthu za fika pena ku malawi eti osango yamba kunpha mbewa bwanji

 53. Anthu enanu mukuda peter pakhaniyi chifukwa chan? Peter yotu anaipeza khaniyi……inu idan lamuro coz nobody under the law no matter who ur white or black gati wapwanya lamuro amayenera ulandile chilango(mongokumbutsana lamuro limamanganso….olipangayo ngat walipwanyanso)

 54. This is buuu** let this man go u robbed him enough, he’s a founder of freedom in Malawi there’s a lot new cases out there for billions and billions, is Muthalika perfect then? look at our country now kungokhala ngati khosa zopanda busa this guy is a hero just try to harm him and see wat the results will be, buuuuuuu shit!

 55. mlandu wa boma sumatha pokha pokha kusowa ma file kumbukilani iyenso muluzi amkafukula anthu mmanda kuti ayeze mafupa a wathu okufawo apeze umboni weni weni mlandu wa JB sunathe mukudziwa kale guys kuti akubitsala kwa eni

 56. Mukulimbana ndi mtunda kuchitekete lipupa achalume anyamata a pa town, kunena moopa MULUNGU Bakili muluzi ndi amene amapanga chitukuko kumalawi kodi inuyo mwapanga chani? Kukweza ma passport lero chimanga thumba 15000 koma muli m,boma nde mukulimbana ndi munthu amene 10 yrz sukulu paliponse mijigo zipatala msewu shop right

  Koma inu mukulephera kugawa chimanga malata kukwera ngati oonse angathe kugula

  Mukapitiliza timupempha Tcheya ayimilenso 2019 inu mukapume

  Amalawi uno ndi nthawi yochita osati kumangolankhula

  Iyaaaaaaaaaaa

 57. Mukulimbana ndi mtunda kuchitekete lipupa achalume anyamata a pa town, kunena moopa MULUNGU Bakili muluzi ndi amene amapanga chitukuko kumalawi kodi inuyo mwapanga chani? Kukweza ma passport lero chimanga thumba 15000 koma muli m,boma nde mukulimbana ndi munthu amene 10 yrz sukulu paliponse mijigo zipatala msewu shop right

  Koma inu mukulephera kugawa chimanga malata kukwera ngati oonse angathe kugula

  Mukapitiliza timupempha Tcheya ayimilenso 2019 inu mukapume

  Amalawi uno ndi nthawi yochita osati kumangolankhula

  Iyaaaaaaaaaaa

 58. Mwachepa muuzane bakili muluzi kkkk ameneyi mungampange ofunikira ngati ameneyi muwafunse a mfumu alero akudalira tiyeni tizingodya mkhwani basi

 59. Mwachepa muuzane bakili muluzi kkkk ameneyi mungampange ofunikira ngati ameneyi muwafunse a mfumu alero akudalira tiyeni tizingodya mkhwani basi

 60. Nde zachamba zimenezo mukulimbana ndi atcheya mmalo molimbana ndi kuthetsa mavuto omwe ali thoooo mdziko muno?xopusa bax

 61. Nde zachamba zimenezo mukulimbana ndi atcheya mmalo molimbana ndi kuthetsa mavuto omwe ali thoooo mdziko muno?xopusa bax

 62. Mukuluyu amangidwe basi, malawi is in undefined poverty today bcoz of him, nthawi anali president was a waste of time for malawians. Had it been he continued where Kamuzu stopped malawi wud be a better place to live, but instead he brought in thieves and thugs who ransacked malawi to ground zero. Today 52 years after independence we are still looking to donors for food and aid.

  1. If we all wud be thinking of moving forward there wud not be history. Komanso do you mean that amene anaba dzulo ku oibm basi milandu alibe just bcoz its zulo. Muluzi ngati ali ndi mlandu amangidwe basi ndalama anabazo ndizambiri. Komanso sizokhazi amufufuze kwambiri.

  2. If we all wud be thinking of moving forward there wud not be history. Komanso do you mean that amene anaba dzulo ku oibm basi milandu alibe just bcoz its zulo. Muluzi ngati ali ndi mlandu amangidwe basi ndalama anabazo ndizambiri. Komanso sizokhazi amufufuze kwambiri.

  3. If we all wud be thinking of moving forward there wud not be history. Komanso do you mean that amene anaba dzulo ku oibm basi milandu alibe just bcoz its zulo. Muluzi ngati ali ndi mlandu amangidwe basi ndalama anabazo ndizambiri. Komanso sizokhazi amufufuze kwambiri.

  4. True solomon, the time muluzi was president is a wasted time and it will never be regained. He created a vacuum that will never be filled.

  5. Olo atakhala kuti wamangidwa iwe chingakhuzepo ndichani? Uwafunse makolo ako kut b4 #bakili adasa motani? Ukulankhula izizi bcoz you r stll young

  6. Ndatchula kamuzu kumbali ya chitukuko osati zinazo. Muluzi nayenso apart from failing to bring development to the pple. Anthu anafanso muulamuliro wake monga matafale ndi ena ambiri.

  7. Ine mbuzi ya munthu iwe mbuzi ya mbuzi waona kusiyana kwake davie gamalimoto maluwa. Still muluzi amangidwa ngati anaba ndalama kapena amuuza kuti abweze.

  8. Ine mbuzi ya munthu iwe mbuzi ya mbuzi waona kusiyana kwake davie gamalimoto maluwa. Still muluzi amangidwa ngati anaba ndalama kapena amuuza kuti abweze.

  9. Koma anthu a dpp ndi udf ndinu mbuzidi eti just bcoz ndikukamba kuti amangidwe azitsogoleri anu mukundiukila. Koma inu nomwe mukufuna anthu anaba ndalama za cashgate amangidwe. Why kuba ndi kuba basi. Kwatsala chuma cha bingu, peter mutharika komanso jb afufuzidwe kenako alandidwe zinthu zimene anaba amangidwenso.

 63. kusowa chochita bwanji cant you just leave him and forget you have been westing alot of since why cant you take that money and help poor peaple in our country than to continue troubling our Fomer president thats not good remember where were caming from and where we are now Muluzi he did he’s best but you forget anthu openga inu munakhala bwanji?

 64. Bakiri’s case will last forever untill his dirth.what will happen if they can just take this #Guy in court coz we’r tired with his case.

 65. #PETER treat every part of your towel nicely because the part you wipe buttocks to day will wipe your face tomorrow be were

 66. Munthu uyu anagwetsa Malawi mpaka Lero.. amati zithu zasitha ndikubweletsa zachilendo kumpha ulimi ndi mamphunziro then za umoyo.. Atsogoleri alero onse atuluka mwa iye mbamva zokha zokha too much Cushgate

 67. #BAKILI MULUZI WILL AGAIN BE IN COURT TODAY hahaa..! . Malawi MUST CHANGE some of its LAWS. Of which ONE must be that ” President azizengedwanso mulandu akalakwa monga ichitira South Africa “. I think #BAKIKI will be troubled throughout his life, I dont think things could be like this IF THE FORMER PRESIDENT WAS ALREADY TAKEN TO COURT WHEN HE WAS ON THE POSITION, and I hope he could have saved some years already. . Akazakufelani ali mmanja mwapolisi mutadzaonezo ndizomwezo, fufuzani mbiri ya #KAPOLOMA before going far

 68. Munthuyo musiyeni alibe mulandu ai ndidzakale zimenezo pangani zasopa,bwanji osalimba ndi Anthu acash gent amudzaka zomwe?zopusa basi

 69. Ok ndakunvetsani. Kom lero ndikapanda kunva kut mwa mmanga…. ndisazamvenso kut akupita ku court. Milandu yonse yatha h z free period!

 70. Iweso bizy cautino ndiwe waboza ufulu unabwela ndi chihana nt cheya . Chihana watabwelesa ufulu ndipomwe acheya amathawako ku mcp kusiya mpando wa secretary gerenal.kuyambisa chawo nawoso chipani cha UDF.

 71. Tired of this case now ….. cashgate cases are new but some have been concluded, conclude this case aswell b4 our taxes are drained further. Jail him or free him to close the chapter

 72. koma zinazi zovuta kuzivesa ndinthu nkhani yakale kale osanoyisiya bwanj paka munthu wakalamba pano nthawi yonse ija munali kuti agalu inu munthu musiyeni malo momalimbana ndi chitukuko kuti anthu aone kusintha mukulimbana ndi munthu wakuti pana wakalamba kuti mumuonenele pano kale mukamuopa kodi?

 73. Ya! They must learn that no1 is above the law, thieve is athieve no matter what position some1 has. arrest him

 74. Kulimbana ndi Tcheya mdala otentha kwambiri kafunse ku Gettoh fanz timamukonda, ndiposo amatikonda, mafana onse omulonda muzatenga tsoka. Cahs gate yakudutsani palibe chokamba lero mukulimbana ndi ka k1.7 billion kusiya zambiri kwambir zija. Anakudziwitsani zambiri tcheya, ka ufulu mukunyadira lero ka kanadza kamba ka iye. Kma palibe chomwe mumamulipilira chokwanira, iyeyo uko kunali kuzilipira kwa padera. Musiyeni adyelel anenepe akhale noni noni. Amangwetu, awa achalume, kuchitekete, lipupa, anyamata pa town

  1. Macholowesotu anali otentha koma anakathela kuti?? Kamuzuso anali otentha sanamangidwe ndi Tcheya yemweyu??

  2. Macholowesotu anali otentha koma anakathela kuti?? Kamuzuso anali otentha sanamangidwe ndi Tcheya yemweyu??

  3. Macholowesotu anali otentha koma anakathela kuti?? Kamuzuso anali otentha sanamangidwe ndi Tcheya yemweyu??

 75. Try to put him in jall and see what is gonna be happen here in Malawi our weapon is ready for any attack especially south of malawi

 76. Ngati kumalawi kuli mi jigo ndi atcheya, ngati kuli msewu Wa m1 from mulanje border via Thyolo nde ndi atcheya apanga zambiri zomwe inu simuzatha mpaka kuchoka pampando. Mungolongolora osapanga chitukuko mu kuchedwa. Kwambi

 77. mukusiya za cashgate zimene zasowetsa mankhwala nzipatala mukulimbana ndi kuntunda while his tym mankhwala ndi mafuta sizinkasowa was cheap than ever

 78. Vry noses kulimbana ndi muluzi osasiya adyele ufulu omwe enanu mukudyelerao kamba ka iye.anatimenyela khondotu.mangeni muone ngati malawi siitha ndi #Bokohalam

 79. Eeeeiish,but this case will last forever why cant you leave this man,akutumani et?kapena mwasowa zochita?milandu ya fresh ili thoo!FOTSEKEE!

 80. Malawi is malawilano. Bakili he was the best president to me. Not ena awa. He is a human being he made a mistake. Instead of u new government concentrating on country crisis u bisy fighting with bakili. What about cash gate?? And you all eating money like a tomato. Eish

 81. no more droping of cases like this one, anthuwa ndi akuba anaba ndalama za a Malawi. Justice shud prevail whether he is old or not but he has to face the long arm of the law no mata wat. Akasiidwa ameneyi mbava zina zomwe zikutibelazi zidzamangidwanso? Ndaona anthu milandu yoti akhoza kungokambilana kumudzi ndikutha being sent to jail for 10yrs. if we say he is old then, government shud consider first releasing all old pple from criminal storages in Malawi (jails) then he shall be left Scott free. Why shud he go jst like that. PATIENTLY WAITI FOR THE PREVAILANCE OF JUSTICE

  1. go to hell man, yo an idiot. DR bakili muluzi anabweletsa chitukuko chooneka ndimaso, now yo talkin shit… aliyense ndiokuba koma sanabe moti malawi nkumasowa mafuta komanso mankwala nzipatala

  2. A sensible,capabld & knowledgeable man understands things deep from the root, bt u are jst sm1 with a shall mind. Think of the people who steal chicken,duck and the likes. If we take the Muluzi case is’nt this killing people. Whats the difference? If this mane is used 2 buy medicine,maize and what have, do u think the country won’t move forward. Don’t rush vomiting senseless ideas when u completely knw nothing. I think u’ll be matured enough to be a true partriot.

  3. zinazi zikungoonetsela2 kt sm of us are Malawians who do not have love for our country. we’re young leaders of today!! let’s we rise up & shine, no one wl cm from smwea 2 chang Malawi, we’re a change ourselves for a better Malawi 2dei & nt 2moro coz 2moro is now. TOGETHER WE MAKE MALAWI A CONDUSIVE PLACE FOR EVERYTHING

  4. zinazi zimangooneselatu kuti munthuyo mumadana naye ndalama zomwe zikubedwa pano ndizomwe akhala akuba enawa sizingafanane ndizomwe zikunenedwa apazi muluzi anali munthu wabwino olo atabweza ndalamayo chitasinthe ndichani hahaha

  5. Ndiye mukuona ngati a chair angamangidwe……! Tikuzinamiza tokha amalawi bwanji ndalama zomwe zikuonongeka kuyendetsera mulanduwu, zikagwire ntchito zina and 4get about this case…. Bakhalani ndi long arm of the law yanuyo kwinaku mony za gvt zikupita!

  6. ngat ati apezeke olakwa akuyenera kubweza ngakhale zuma ananaso kuno kuti abweza ndalama zomwe adaonga pomanga zuma village 210 billion R . ndalama anabazo anakakoka mazi kuchoka kunyanja ndikutsegula ma farm mphepete mwa nyanja nde bwezi akulila ndi njala . azitsogoleri athu ndiozikonda i salout Dr H kamuzu banda sadayanga’ane mbali adayesesa popanga zinthu.

  7. ngat ati apezeke olakwa akuyenera kubweza ngakhale zuma ananaso kuno kuti abweza ndalama zomwe adaonga pomanga zuma village 210 billion R . ndalama anabazo anakakoka mazi kuchoka kunyanja ndikutsegula ma farm mphepete mwa nyanja nde bwezi akulila ndi njala . azitsogoleri athu ndiozikonda i salout Dr H kamuzu banda sadayanga’ane mbali adayesesa popanga zinthu.

  8. ngat ati apezeke olakwa akuyenera kubweza ngakhale zuma ananaso kuno kuti abweza ndalama zomwe adaonga pomanga zuma village 210 billion R . ndalama anabazo anakakoka mazi kuchoka kunyanja ndikutsegula ma farm mphepete mwa nyanja nde bwezi akulila ndi njala . azitsogoleri athu ndiozikonda i salout Dr H kamuzu banda sadayanga’ane mbali adayesesa popanga zinthu.

  9. Mo Phex Phekani ngakhale nthawi yatcheya mankhwala amasowabe mwina mkuti uli mwana . unice wakhala akufunsa mafuso ovuta kwambili okanika kuyankha.

  10. Mo Phex Phekani ngakhale nthawi yatcheya mankhwala amasowabe mwina mkuti uli mwana . unice wakhala akufunsa mafuso ovuta kwambili okanika kuyankha.

  11. Mo Phex Phekani ngakhale nthawi yatcheya mankhwala amasowabe mwina mkuti uli mwana . unice wakhala akufunsa mafuso ovuta kwambili okanika kuyankha.

  12. nonses live Muluzi alone, y cant these pipo concentrat on how to stop ziphuphu u think even peter sakuba ryt now… olo alimbane ndi chair sangamumange its all tricks these pipo r the same komanso muluzi cant pay back the money olo atakhala nazo

  13. so why are you bothered. this one is for true patriots not smone who loves who jst coz of political affiliations,tribe or racial connections. we’re not into that, we are for justice

  14. Mr Sydney you have a good point but as usual your point is worthless to the worthless of the worthless justice in MW.How many times muluzi has been incripted to court??nad when did his trial begun and what happened up to now?When you manage to answer this on your own you will realise that you have voice of voiceless coz the system is the same and you can’t change it as result it suits and change you that’s politics of Malawi.

  15. Mr Sydney you have a good point but as usual your point is worthless to the worthless of the worthless justice in MW.How many times muluzi has been incripted to court??nad when did his trial begun and what happened up to now?When you manage to answer this on your own you will realise that you have voice of voiceless coz the system is the same and you can’t change it as result it suits and change you that’s politics of Malawi.

 82. throw this munthu in jail ma cashgate anayamba ndi madala awawa,,,,,nothing to smile about,munthu wamba kuba bankha ndi 15 yrs in jail koma awatu awa mabillions kwacha

 83. osamamvutisana sibwino ayi cox mziko muno muli mamvuto ambiri bwanji osakhoza izi kaye mwayamba kutiona kupusa mukufuna tiyambilenso xoosha matayala patsewu ?

  1. Mulandu Uwu Wukubvuta Coz C Muluzi Anaba Kma Office Ya Wupresident Ndikabinet, So Mlandu Anamanga Eleson As Aperson. Ife Maloya Apa Tidyamoso Muboma La Apeter. Maumbon Aboma Anathawa Kalekale. Ndiye Chiyambireni Mlanduwu Paonongedwa Kale 22 Million Sapepesa Ndi Billionio?

Comments are closed.