A teacher at Namiwawa private secondary school in the commercial city of Blantyre has died after excessively taking alcohol, Police say.
The deceased, James Banda, 44, died after drinking alcohol at Chilomoni market on Sunday.
Blantyre police deputy spokesperson Andrew Mayawo said one of the deceased’s relations told police that Banda collapsed while he was walking.
“The deceased’s relation Dymon Mhango reported that he collapsed on his way home and he was rushed to Chilomoni health centre where he was pronounced died,” said Mayawo.
Meanwhile, the cause of the death is yet to be established.
The deceased hailed from Mbachudu village, Sub-Traditional Authority (TA) Munyanja in Kasungu district.
Ameneyo Azikafunsana Ndi Mulungu Kafungo Kantonjani/mkalabongo/chingombingo Kali Guuuuuuu
Cifukwa colezela zaoneka ngati mowa koma paliso empty stomac poison. Kupunthwa but ayi rest in p
Ntchito za manja ake zamuchitila umboni mkuluyo.
Ntchito za manja ake zamuchitila umboni mkuluyo.
Ife pano ndiye tayambano kumwa
Ife pano ndiye tayambano kumwa
R.I.P the imbiber…..
R.I.P the imbiber…..
tsiku lofa nyani ntengo umatelela hahahahaha
tsiku lofa nyani ntengo umatelela hahahahaha
This is due to Food Shotages in Admark Markets, RIP Sir
RIP,brother in riquor,its ok to go with wat u lyk,until we shall meet and drink together in his glory
Zaziiii kuli edzi ufiti uhule kuba chigololo zoona mukamuweluze chifukwa cha vinyo?amene akuziwa kuti sanachimwepo ndan apa nthaw ikakwana basi yakwana kwamwalira athu kunjaku osati ngati sir ameneyu sibwino kunyoza enanu muzafa sitizacommenter imfa yanu ya eziyo
wat a shame to ateacher
Matumbo Ake Anali Ofowoka Ndikale. Mowa Mukuwunamizira Ine almost 70 Yrs Ndikumwa No Any Mistake. Kkkk
Achita bwino kumwalira ndiponso azimwalira kumene nzomwe tikufuna. Malemba amati“wages of sin is death”
He reaped what he sow
Ife timamwa bwanji sitifanawo mowawo, zaziiiii!!
Kikikikikiki tkutukwanani ifetu apa chamba eti
Hahahahaha!
Kikikikikikikiki eyetu sinaga iwo amagomwa basi osalekeza man
Ukamapanga chinthu umakhala ndizosatila zake nde zimenezo.
That’s nosense. You’ve already reported that the man died of drinking excessively, and then you say that the police are yet to establish the cause of his death. Where are you up to?
Police are yet 2 establish the cause of de death, and u r reporting dat alcohol has claim a life, wat a contradiction???
ine 15yrs ndikumwa bawa opanda mvuto anywy R I P.
School yanga,komano nkhani ndi kufa ndi mowa kapena poti ndi mphunzitsi,
Everything its on has tym !!! Thawi ikakwana yakwana basi no coplng
Everything its on has tym !!! Thawi ikakwana yakwana basi no coplng
chiwanda cha mowa champhamvu zedi,chimampangitsa munthu wa nzeru kukhala chitsiru pagulu ndipo chitsiru chimangopitilira ndi uchitsiru wake.
chiwanda cha mowa champhamvu zedi,chimampangitsa munthu wa nzeru kukhala chitsiru pagulu ndipo chitsiru chimangopitilira ndi uchitsiru wake.
don’t drunk and die
don’t drunk and die
Sindingasiye bawa
Sindingasiye bawa
Tinena kuti sory but lamulo lamulungu cholezelesa chili chonse mcholesedwa akalowe kumoto basi
Tinena kuti sory but lamulo lamulungu cholezelesa chili chonse mcholesedwa akalowe kumoto basi
Abale anzanga, plz tiyeni tiphe mowa osati mowa utiphe, sizoona
Abale anzanga, plz tiyeni tiphe mowa osati mowa utiphe, sizoona
zaphweka kut mowawu uli m’manja mwa apolisi, muumange mpaka life imprisonment usamaphe anthu chonchi!
zaphweka kut mowawu uli m’manja mwa apolisi, muumange mpaka life imprisonment usamaphe anthu chonchi!
Mmmm sorry
Mmmm sorry
Alcohol must be arrested! For muldering
for sho
for sho
he has died of an empty stomach…not alcohol
m’kala bongo dot com!
I thank God for safeguarding my life throughout my time i have been drinking alcohol to the time i surrender ed.Anthuni sizophweka kusiya kumwa mowa
correct my friend,sichophweka munthu kusiya mowa,umo ndinausiyila ine ndipo sindimasilira konse munthu akamamwa mowa,ndipo sandipatsa chidwi changa chimangokhala chisoni basi
correct my friend,sichophweka munthu kusiya mowa,umo ndinausiyila ine ndipo sindimasilira konse munthu akamamwa mowa,ndipo sandipatsa chidwi changa chimangokhala chisoni basi
May God bless u my bro, keep on choosing that way
malume mulungu ndi wamkulu kamwolo malenga joloza chitanaoni iwonso awone ukulu wa namalenga timakunyadilani
its not bushiri as u said always bushiri is killing people
My condolences to the deceased family may the good Lord comfort them at dis difficult Times.
Its a cheater not a teacher
Malawi 51 the title is alcohol claims life yet yet at the very end of tiding you say the cause of his demise is not known. And he was pronounced died atola nkhani kk go back to xool;(
Man he was drunk as what the friend of deceased told Malawi 24 in such a way it can be other caused him to die like poisoning him at tarven by put poison in his beer who knws dat is what the writer try to say.
This is not news at all chifukwa okufa ndi mowa ngambiri mwina za enawo simumva. Muti wafa ndi mowa then the cause of death not yet known
No Comment……
Rest in piece!
Stroke
I always say this excessive alcohol consumption on an empty stomach is dangerous any way rest in pieces
Pogula mowa sipamakhala chinzele ngat ku admarc. Nde timangogula mene tafunira. Drink beer to save headache of Admarc queues
Kodi chibagi kapena mowa wanji?
Many teachers abrock ass niggers they are not payed well.thats y they prefer buying cheap spirits to have fun.in course of doing so ,they happen not to eat their meals.thats y they are dying like chickens.what type of spirist a these to be drunk with a hundred bags.the gvt is not taken care of its citizens
Hahahahaha mazageti !!!!
What do u mean
What do u mean
Died Hero Rest In Peace
kumamvetsa aphunzitsi ndalama amalandila mochedwa
Anamwa asanadyere….
Amowa zimezo ndizanu ife phee #ganja one levo and will never give up
Halaam kumwa mowa katayeni uko
He bumped into Jesus drunk
mmmmmm
Sad
zakhala bwino mwina a2 asiye kumwa kachasu.
Si Shooter Ameneyo?
Aziphunzitsi mowa wawo ndi umenewo
why alcohol thats babylon! better canabis jahlove!!!
mwina kumeneko pang’ono,kma kno mowa omwewo wapha maziphunzitsi awiri zulo zulori.
Mphoto Yauchimo Ndiimfa “lorani Ntchito Zamanja Ake Zimuikile Umboni”